Ine Ndimalimbana Ndi Area 30 - Bon Kalindo
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 14 พ.ค. 2024
- On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo, would like to comment on fake news and other issue including charcoal burning and the scuffle at MUA involcing MDF personnel.
Pa Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo, akufuna kuyankhapo ndemanga pa nkhani zabodza ndi zina monga kuwotcha makala komanso chipwirikiti cha MUA chokhudza ogwira ntchito ku MDF.
#malawi
Ife a Malawi tizavotela bon kalindo ku sogoloko umbon ku bokina faso❤❤❤
Bon kalindo umatiimilira keep it up
I'm with you mr president bon kalindo
Your only our representative the Dc
The DC and Bakili Muluzi Tv our freedom fighters❤
Umskwans
Booooooni Kalindo.... The DC
Booooooooon kalindo 🙏
Kalindo best ever
Proud of you always our own president, president for us the poor Malawians, may God bless and continue to protect you, the Dddddd Cccccc!!!!
I like Mr kalindo
God ahead u bon
More fire Kalindo❤❤❤
Ulemu wanu Mr President
Mulungu azimutetezela boni kalindo
Good luck bon
Ngati inu mwabisa ine ndimutchule bwaaa😂😂🎉
Bon kalindo ❤❤❤❤
kkkkkk kma Born kalindo nd 1 and he speaks the truth mmmm
Asilikali amalawi olo atapita kukamenya nkhondo ku drc even pamozambik pompaapa, azikangophaphalisidwa/amangogwesedwa ngati ziwala, mbewa, iwo koma kutukwana ndikumenya amalawi anzawo nde Number one
❤
Akakhala amene anathawa ku sasafilikawo musamudandaule, anafwifwa kalekale ameneyo ndipo zake zinada basi kkkkkkkkkkk, ndimwana opusa kwambiri
Ben Longwe Ndiamene Amaba Magalimoto Ku South Africa Olo musamutchule Dzina Aliyense Akumudziwa Kuno Ku South Africa
Tikanakonda kti 2025 tizavote ngakhale tili ku Johannesburg
Bon azatiyimilila upule ndithu mulungu azikudalitsa ndi lutha kut mwina make Malawi ixasitha
Ndipo tinalipila kaye Ku escom mpaka lelo atitizapatsa ndalama Kaye ...escom simasewela
😂😂😂🎉 ziliko ziliko 😊
Athombo thombo a billy malata mbuzi ya munthu yadya 6 million
Mwana oopsa kwambiri olimbana ndi state house
Dc volume🎉
Kodo a kalindo wa amangwira ntchito yotani tsiku ndi tsiku amadya amavala amasamba enafe tikuvutika kuti tidye iyeyu mwina ndi wa businesses kapena amalandila ndi kulakhula ku
Makala akalanda amapita nawo kt
DC🎉🎉🎉
ulemu wanu KALINDO
Awa fodya amampweteka
Inu ndi anthu anthu sitigakusiyen mwapwiya dc
The Dc
God bless you Bon.Kalindo ❤❤❤
Chakwera sakuona zosez