Atolankhani ndinu ana chonde mukamafunsa mafunso funsani Ngati mwapita Ku school chifukwa amene mukuwafunsawo Ali ndi nzeru Za chibadwidwe Za umunthu Ngati mumafunsa mafunso oimira chipani funani ntchito ina chifukwa inuyo a lasta zautolankhani pitaniso Ku school chomaliza ulemu wanu azipani zonse ife achinyamata tikutseguka nzeru mwayankha bwino kwambiri
Boma lathuli siliganiza bwino popanga zinthu zake, company yomwe atengayi ilibe mbiri yabwino pa kayendetsedwe ka zisango. Ndizomwenso zinachitika ndi nkhani ya fetlizer kukabetsa ndalama ku Butchary zija.
Good answer akwene
Well done ✅
Well done our leaders , Malawi hope is in you please make citizens happy 🤝
Kkk😂😂😂 kma mayi awa
Well done mabig nose for good
Again thank
Nzimayi wanzelù amaganiza fuso asanayakhe mayiwanga❤❤❤❤
Good guys ❤❤
Nyatwa akweni❤❤❤
Kachale abwerenso kapena anastasia nsosa abwere
Kweni ndi one more 🔥🔥🔥🔥
Well done 👍 kaliyat kuyakha Kwa lero Ndi mmawa omwe😂😂
😂😂😂😂😂😂😂
Kkkmkmmm you guys option tizaziwona tikamavota
Akweni anabwera eee😂😂
Atolankhani ndinu ana chonde mukamafunsa mafunso funsani Ngati mwapita Ku school chifukwa amene mukuwafunsawo Ali ndi nzeru Za chibadwidwe Za umunthu Ngati mumafunsa mafunso oimira chipani funani ntchito ina chifukwa inuyo a lasta zautolankhani pitaniso Ku school chomaliza ulemu wanu azipani zonse ife achinyamata tikutseguka nzeru mwayankha bwino kwambiri
Kuyakha mwa nzeru🔥🔥🔥
Zithu Ngati zimenezi amakhala Ngati sakuva Koma akava Kuti president. Kukhala Ngati akudwala amayakha nsanga
Ifenso ma votes tilimbe mtima tisawasiye onkha please anthuwa aliyetse avote basi aliyetse ndi malawi mafutso Ngati mwatumidwa bwanji kodi
kamtolankhani kayankhidwa nd akweniko kakundimvesa chisoni🙃
Boma lathuli siliganiza bwino popanga zinthu zake, company yomwe atengayi ilibe mbiri yabwino pa kayendetsedwe ka zisango. Ndizomwenso zinachitika ndi nkhani ya fetlizer kukabetsa ndalama ku Butchary zija.
Kkkk nose muli apa ndinu a zodiak?!!! Yankhoo kkkkk
Ndimanva kukoma ndi akweni amaziwa kuyakha kkkkk
Komat akwen😘
Machine akweni kkkk
Akwen
Viva utm, viva dpp, viva aford
Akweni amayakha mothamangira tym tu 😂😂😂
😂😂😂😂 Akweni inu ndi one
Chibaba cha utsogoleli chavuta chavuta apa dyera dyera dyera
A kweni amatha
Chisankho chilepheleka ichi. Chakwera Motu kuti buuuuuuu, ana akuopa awa hahahaha
Koma Akweni inuyo 😆😆
Akweni woyee😂😂
Mbambande kweni
Komat mai kaliyat mumayankha mokwanira ,
Nthaw Zina zimaoneka ngt atola nkhani amafika pamalo asanaziwe cholinga cha nsonkhano😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂 koma kaliat amwene
Eee koma akweni
Mtambo uyu ofunika kumuthila machaka 😂
😂😂😂😂😂😂akweni
Akuopa masankho kkkkkkkk. Shaaaaaa opposition mantha
Inu muli dziko lake Liti Kodi ?
Inuso Inu.usatana tu uwu
Sakuwopa dzisakho ai koma mudziti akuwopa kubeledwa bas
Eeeeee! Koma kweni anakonza
Kkkkk
Akusephana Ndi fuso Galu uyu