ku banja lofedwa, akuti bwanji???

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 22 ก.ค. 2022

ความคิดเห็น • 10

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 2 ปีที่แล้ว

    pelekani katundu wa mudzi inu..aaah katunduyo siwa banja ..achita bwino kunyanyara ndinu anthu osaganiza kwabasi...kapelekeni apaa mulipiratu

  • @lukainnocent5380
    @lukainnocent5380 2 ปีที่แล้ว +1

    Taperekani zinthuzo anyakwawa sadya zithandiza inuso mbalezo

  • @joegibsonzulu2599
    @joegibsonzulu2599 ปีที่แล้ว +1

    Zosakhala bwino konse ayi

  • @samuelsimaolinguissoneling2884
    @samuelsimaolinguissoneling2884 2 ปีที่แล้ว

    Zazikulu...

  • @promise3693
    @promise3693 2 ปีที่แล้ว

    Zikomo kwambiri mumaitha guys 🤗

  • @peterbanda7003
    @peterbanda7003 2 ปีที่แล้ว

    Kayikeni malilo nokha bas limbani ntima

  • @inamastudios3086
    @inamastudios3086 2 ปีที่แล้ว

    Estava proibir material para uk?isso quer dizer ele é nyakwawa também,entao é asua vez d utilizar esse material. Dirija vc mesmo

  • @promise3693
    @promise3693 2 ปีที่แล้ว

    Koma mafumu asamatero kulakwatu kumeneku.... akungofuna podyera cholinga alipidwe

    • @simangodickson1794
      @simangodickson1794 2 ปีที่แล้ว

      Akulimbilana unyakwawa ,koma nkhany zina inu

    • @promise3693
      @promise3693 2 ปีที่แล้ว

      @@simangodickson1794 mmmh koma zovuta kwabasi