tikupirizabe

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 18 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 67

  • @FatsanTobiyas
    @FatsanTobiyas 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mulungu awalenge ndithu 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @alicehananiya
    @alicehananiya 11 หลายเดือนก่อน +1

    Lest in well Lameck 😭😭😭😭 mulungu azakubwedzelela

  • @EnelessLangisoni
    @EnelessLangisoni หลายเดือนก่อน +1

    Mmmmm kulakwa abale mmmm kupha mwana ngt ndinkhuku zooona mmmm

  • @vatineseduwin
    @vatineseduwin ปีที่แล้ว +1

    kulakwa zed

  • @EdwardGeorgeKasabola
    @EdwardGeorgeKasabola หลายเดือนก่อน +1

    Ziko lasowa chikondi pakana kupha mwana wanzanu nkhani yansomba sichoncho ayi moyotu sagula bwanji mukanawauza makolo ake akanapeleka chilichonse koma paka kuchosa moyo 😭😭😭😭

  • @HellenKanyemba
    @HellenKanyemba 20 วันที่ผ่านมา +1

    Koma ukuku anthu amaphana ndipo nkhani zake mmm

  • @landiraniwhite2756
    @landiraniwhite2756 4 หลายเดือนก่อน +1

    Kulakwa kwambiri

  • @emosichimphengula8655
    @emosichimphengula8655 ปีที่แล้ว +1

    Yiii kulakwa

  • @frankmmadi3773
    @frankmmadi3773 ปีที่แล้ว +2

    Mwasowatu kungoti zee this days I like to follow you your videos

    • @Mollineysembah032
      @Mollineysembah032 3 หลายเดือนก่อน

      Km ndiye kulakwa kwambili mnpaka munthu kuphedwa chifukwa cha bakayawo somba yowawa mnchele Ngati imeneijaaaa kmso ya ndrama yokwana kwacha k 2 ,000 ?

  • @NigeriaSomaria
    @NigeriaSomaria ปีที่แล้ว +1

    Pepani akubanja 😢😢😢😢😢

  • @MosesMussa-w2f
    @MosesMussa-w2f 20 วันที่ผ่านมา +1

    Analinao kalendicholinga osati zasombazo ayi

  • @MariamTwanky
    @MariamTwanky 16 วันที่ผ่านมา +1

    Uwu nde ufiti sopana kupha munthu chifukwa cha nsomba

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr ปีที่แล้ว +2

    Nsanje majerasi kuyipa ntima kusazilimbikira ndizimene ziri mwaanthuwo

  • @dhaoudhiabedinegomaseko2363
    @dhaoudhiabedinegomaseko2363 ปีที่แล้ว +2

    Zomvetsa chisoni zisamafike apa anthu tikalakwilana tikambilane mwa mtendere

  • @EdwardGeorgeKasabola
    @EdwardGeorgeKasabola หลายเดือนก่อน +1

    Iiiiii makolo kubala ndikopweteka inu osamapanga choncho kumakhala ndi chikondi ndi anzanu

  • @christabel994
    @christabel994 ปีที่แล้ว +1

    Koma anthu anapha mwanayo Nayenso aphedwe kuno Zambia

  • @joegibsonzulu2599
    @joegibsonzulu2599 ปีที่แล้ว +1

    Nkhani ngati imeneyi ikadatha mwamtendere kudzera mu zokambirana osati kukhetsa magazi chonchi ayi. Anthu oyipa mitima

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd ปีที่แล้ว +1

    Nsomba kuphera munthu mmmmm

  • @ritabani274
    @ritabani274 ปีที่แล้ว +1

    Mukapeza bakayawo wina mundionetse chonde sindimadziwa ine osamakwiya kwambiri mukakhumudwa kumayesetsa kuzipanga control please

    • @VFS3
      @VFS3 2 หลายเดือนก่อน

      Ndi nsomba ya ntchere ya kumozambique

  • @meganabigail-ye7fw
    @meganabigail-ye7fw ปีที่แล้ว +1

    Mmmmmmm koma sambi somba mpaka kupha mwana eeeee ayi mukalipile mwazi wamwayo

  • @DicksonLozani-fu2ny
    @DicksonLozani-fu2ny 5 หลายเดือนก่อน +1

    Koma Zina zikamachitika boma lizitengapo gawo

  • @meganabigail-ye7fw
    @meganabigail-ye7fw ปีที่แล้ว +1

    Ntchito mkuigwila a Gova komanso mr kadewele keep it up

  • @louisbonongwe8537
    @louisbonongwe8537 ปีที่แล้ว

    Oooh jehovah😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd ปีที่แล้ว +1

    Km mmmmm zovuta kwambiri 😢

  • @joegibsonzulu2599
    @joegibsonzulu2599 ปีที่แล้ว +1

    Koma abale zoona kutenga moyo wa munthu chifukwa cha nsomba basi ?? Kuyipa mtima kotani uku? Ufiti chiyani?

  • @muhamadshaibu9261
    @muhamadshaibu9261 ปีที่แล้ว +1

    Anthu amenene akapezeka aphedwenso athu woyipa

  • @ephramkokolole3386
    @ephramkokolole3386 ปีที่แล้ว +1

    Dziko layipa

  • @eunicemoyo6024
    @eunicemoyo6024 ปีที่แล้ว +2

    Ayi adali ndi zifukwa ndi kubanja lofedwali anthu oipa kwabasi

    • @joegibsonzulu2599
      @joegibsonzulu2599 ปีที่แล้ว

      Zikuoneka chonchodi. Zidani zakale kale zimenezi

  • @raimundoeufrasio1792
    @raimundoeufrasio1792 ปีที่แล้ว +1

    Koma dzikoli

  • @sergiopauloposse7610
    @sergiopauloposse7610 ปีที่แล้ว +1

    Obrigado pela informação. Koma ngati mzotheka tamayesetsani kumva mbali ya apolice Kuti atipo chani, chifukwa iwo ndiye amatiteteza. Kumva mbali yawo ndikwabwino zedi angatitsekule mmaso.

  • @lukainnocent5380
    @lukainnocent5380 ปีที่แล้ว

    Bakayawo amaoneka bwanji male osamujbula ai

  • @molicieeosama8877
    @molicieeosama8877 ปีที่แล้ว +1

    Ufit

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM4787 ปีที่แล้ว

    Mamvuto amalawi

  • @AdiruMatola
    @AdiruMatola ปีที่แล้ว +1

    Zomvetsa chisoni

  • @MaxwellMustafa-ec8fc
    @MaxwellMustafa-ec8fc ปีที่แล้ว +2

    Pali nkhani zina zimagwesa misodzi tikamazivela

  • @sheenahmwalabu
    @sheenahmwalabu ปีที่แล้ว +2

    Kubereka nkowawatu, ndipo kuluza mwana eish so painful. Nkhani yake nsomba yosakwana 5pin 😭😭🙌🙌

  • @jameschipula4475
    @jameschipula4475 ปีที่แล้ว +1

    Mmmmmmm zachisoni

  • @mbawabuliyan9704
    @mbawabuliyan9704 ปีที่แล้ว +1

    Ulemu ndapeleka kwa abambo awo andiyakhulira bwino

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 ปีที่แล้ว +3

    Dziko lafka posauzana ,chikondi chinantha mpaka mitengo...kubeleka ndikowawa...ampha munthu osalakwa ambuye atinthandize..chikondi chija chidapita kuti..May his soul continue resting in peace..ndizowawa kwabansi..

  • @aliciabanda3656
    @aliciabanda3656 ปีที่แล้ว +2

    Nsomba ndi chiyani ndi moyo wamunthu abare inu😭😭😭😭

  • @Bushiriderick811
    @Bushiriderick811 ปีที่แล้ว

    Following you from lilongwe mw plz osasiya mix with chichewa

  • @aleksawilliams710
    @aleksawilliams710 ปีที่แล้ว +1

    Mmmm koma zomwe zikuchitika nthawi ino

  • @mbawabuliyan9704
    @mbawabuliyan9704 ปีที่แล้ว

    Apha munthu osalakwa Mulungu amuyang'anile

  • @EstherMsambala-th1hk
    @EstherMsambala-th1hk ปีที่แล้ว

    Akutonthozedi mulungu bambo😢

  • @ziyamikanmakowa5981
    @ziyamikanmakowa5981 ปีที่แล้ว +1

    Nsomba mpaka kumupha nzake ,galu wamunthunso ameneyo eti

  • @ririvilla1423
    @ririvilla1423 ปีที่แล้ว

    Wish I could contact a bambowa ndi apepese ndichithandizo

  • @alicegama8138
    @alicegama8138 ปีที่แล้ว +2

    Sambi

  • @NicelyKasambala
    @NicelyKasambala ปีที่แล้ว

    Nkhani yomvesa chisonu kwabasi kuchotsa Moyo wamunthu kamba ka nsomba mulungu awone

  • @yvonnechinangwa
    @yvonnechinangwa ปีที่แล้ว

    Very sad 😭😢😢😢

  • @slyviakalivea4333
    @slyviakalivea4333 ปีที่แล้ว

    Koma anthu paka kupha mwana chifukwa cha somba zovesa chichoni kwabasi koma ziko lafika poipa

  • @Eonesmusmughira
    @Eonesmusmughira ปีที่แล้ว

    Zovetsa chisoni z osha

  • @newtonmitambo1092
    @newtonmitambo1092 ปีที่แล้ว +1

    Yoooo so sad may his soul rest in peace 😢😢

  • @martaarauio1347
    @martaarauio1347 ปีที่แล้ว +1

    Zovetsa chisoni

  • @EstherMsambala-th1hk
    @EstherMsambala-th1hk ปีที่แล้ว

    Kulakwa abale 😢

  • @MariamBanda-p9t
    @MariamBanda-p9t ปีที่แล้ว

    Koma ndizovesa chison

  • @promisebanda8785
    @promisebanda8785 ปีที่แล้ว

    Abare inu😢😢

  • @rabeccagama4067
    @rabeccagama4067 ปีที่แล้ว

    Kumvesa chisoni

  • @chifundomhango3324
    @chifundomhango3324 ปีที่แล้ว

    Eish so sad 😭

  • @ishmaeldouglas5962
    @ishmaeldouglas5962 ปีที่แล้ว

    Mmm mm why people

  • @florencebonga3211
    @florencebonga3211 ปีที่แล้ว

    Zovutatu izi😭

    • @joegibsonzulu2599
      @joegibsonzulu2599 ปีที่แล้ว

      Osati masewera ayi ndipo udani umenewu ukhala ukupitirirabe zaka zikubwerazi

  • @frankmmadi3773
    @frankmmadi3773 ปีที่แล้ว +1

    Mwasowatu kungoti zee this days I like to follow you your videos