Zauchitsiru, Mesa ndi malonjezo anu a bodza, kodi DPP mumamaisata mapazi bwanji? Kodi amayenda ndi zikwanje aja bwanji kunkuyu sunabwere kulankhula, Shane on you. Akugenda ndi a Malawi okwiya, not DPP.
Ngati a Malawi mukufuna kudzakhala pa ntendere , smartmatic ikuyenela kuchotsedwa through ma demo woyipa kwambiri, mademo sakhala a bata, otherwise mcp idzawononga kwambiri and a Malawi adzavutika kwambiri kuposa pano
A Kumkuyu mulibe manyazi. Inu ndi azomzanu mwaononga dzikoli. Ngwirani omwe amayenda ndi zikwanje ku Lilongwe Kaye ndiye mukagwire ku Ndirande. Dzenje lomakumbira anzako kuti agweremo umagweramo wekha. Chauta akuyendere mwa padera iwe Kumkuyu.
Aaah pa u cisilu pa mako cisankho cake citi cimene mudzawineco? Mukudalira smart matic mukunamatu inu smart matic sikugwila tcito.ukuti a police ayamba kale kufufuza, nanga aja munawatuma kukagenda a a oposition ku mademo mwamangapo ndani zisilu inu?
First investigate people from mbowe, azikwanje then ndirande ..... Police officers and all high positions when it happens in Lilongwe nothing doing but at Southern part of Malawi 😅😅😅😅
Sono lero apolice ayamba kafukufuku chifukwa chakuti angendedwawo ndi duna za boma....ngati zili choncho kafukufuku akuenela kuyambira ku Lilongwe kwa anthu omwe anatenga zikwanje
Komano mpofunika kumadzifunsa wekha why anthu sakundikonda usanaweluze Kaye. Coz tawona APM dzulo it was quite. Check your errors and collect it. I remember the Bingu Wamunthalika was saying let the work of my hand be my witness. If you are good who's gonna hate you? Tiyeni tikwanilitse zomwe tinawalonjeza a Malawi.
Akugenda si a DPP, akugendatu ndi Amalawi omwe akumva kuwawa ndi Ulamuliro wanu wa Uchitsiruwo Nduna za mamina. Ana anjOKA Inu ntchito Kupha anthu.
UYU tizingomugenda daily 😅😅
Zauchitsiru, Mesa ndi malonjezo anu a bodza, kodi DPP mumamaisata mapazi bwanji? Kodi amayenda ndi zikwanje aja bwanji kunkuyu sunabwere kulankhula, Shane on you. Akugenda ndi a Malawi okwiya, not DPP.
Chokani inu amoze akugendani si adpp km. Amalawi
Please anthu a MCP ndiwokupha Ifeso tizibwezela agaluwa aphaa anthu ambili
Ndadandaura kwambiri pomusiya ndimoyo nyani ameneyu.
Kunkuyu ukunama ,amagenda si ana ndaadzibambo ngati iweyo
Inuyo mwaononga economy anthu ali ndi nkwiyo
Okey ndizomwe umapanga eti...umagwiritsa ntchito Ana eti😂😂😂
Chisiru chamunthu kodi kulilongwe kuja bwanji sunayakhulepo? Unya uona dpp ilowa ndipo mcp uzaluza movesa chisoni
😂😂😂😂😂😂 nanga azikwanje aja ku lilongwe mwayiwalatu😂😂😂😂
Ndimadabwa ndi kunkuyu kundlani sikuyamba munthu wandale kugendedwa koma nduna imeneyi china chilichonse amati DPP ndipo dzomwe apanga anthuwo ndidzochepa akanangomupha basi
Mwagendedwa ndi anthu amene mukuwazunza ndi ulamuliro wanu, musanamizire a DPP.
Ndirande well done ndirande sisunga cape
Akugenda ndi anthu omwe atopa ndi bodza lako.Ukuona ngati mukhalabe m'boma kani?Mwauponda
Auze
Waiwala ndiwe aise kodi sindilande yomweyo inagenda apm 2020 waiwa ,,, malonjezo omwe munalonjedza mu 2020 pofuna athu kuti akuvoteleni , atakuvotelani inu munawaiwala ndipo imeneyo nde miyalayo komaso nduziwa simunati madelamutu mugendedwa ndipo muziyenda mukulimba athu inu mwalowesa ziko pasi ndipo a mcp mau amenewa muavese ziko ilili mwaonongerati ndipo chikangawa kuyelekedza kuyenda opanda achitete sangayende kuchoka pa gilime ton of kufika pa kamwendo ataphe ndiwana athu atopa atopa atopa ndati atopa ndi mcp
Ngati a Malawi mukufuna kudzakhala pa ntendere , smartmatic ikuyenela kuchotsedwa through ma demo woyipa kwambiri, mademo sakhala a bata, otherwise mcp idzawononga kwambiri and a Malawi adzavutika kwambiri kuposa pano
Chipani chioyendesedwa ndi zigawenga komanso mbava ....Ife amalawi sitikufunanso chakwera munthu wopepela ngati ameneuja
Koma khalidwe la zikwanje?
Akugenda sia dpp ayi
Aaa nde bwanji ku Lilongwe kuno panalibe kafukufuku kwa azikwanje aja dziko ndilokondela guz
A Kumkuyu mulibe manyazi. Inu ndi azomzanu mwaononga dzikoli. Ngwirani omwe amayenda ndi zikwanje ku Lilongwe Kaye ndiye mukagwire ku Ndirande. Dzenje lomakumbira anzako kuti agweremo umagweramo wekha. Chauta akuyendere mwa padera iwe Kumkuyu.
Nkukuyu yamba kuzifusa zikwanje zaku Lilongwe zinatumidwa ndindani?
Si ndi MCP lero zakuwawa
Amange akwasundwe Kaye ni akulilongwe aja mesa ndi àmene anayamba
Poti zachitika ku Ndirande ndiye zalalwika.Koma sikale kuchitika Roadblock ku Lilongwe sitinamve a Thindwa atalankhulapo ayi
Aaah pa u cisilu pa mako cisankho cake citi cimene mudzawineco? Mukudalira smart matic mukunamatu inu smart matic sikugwila tcito.ukuti a police ayamba kale kufufuza, nanga aja munawatuma kukagenda a a oposition ku mademo mwamangapo ndani zisilu inu?
First investigate people from mbowe, azikwanje then ndirande .....
Police officers and all high positions when it happens in Lilongwe nothing doing but at Southern part of Malawi 😅😅😅😅
Koma mkuluyu ndaona Kuti mutu wake sugwira osayankhula zogwira mtima bwanji
Nanga ku Lilongwe sumunawamange
Iwe ndiwamisala kunkuyu. Sukuona kut anthuwa akwiya ndizochitika zanu
Kunkuyu kukamwa ngati chimbudzi, akuyankhula zopusa. Ndipo simunati munya
AKunkuyu awawa siana aDPP koma anthu okudzidwa aluNdirande
Kodi anthu amaopsyeza a mademo ku Lilongwe agwidwa?
Aaaaaa ukulamula ngati dziko ndilako kumkuyu mkamwa monumkhamo
Waiwala kuti Peter mutharika anagendedwanso imeneyo ndiye ndix Village sigawa kamba si nyau tu
😂😂😂😂😂Kape iwe. Nyau za ku Lilongwe zija ndi ana?????. Usalimbane ndi DPP
Inunso a mcp munakhapa ku Lilongwe anthu zikwanje, inu nde oluza kale zauhule basi
Chakwera akangowina tonse tifa 😢😢😢 ,,,,
Apa ndunai yadzuka ndikudzudzula zomwe zamuonekela ku ndilande ,
Ku lilongwe nthumbidwa zawo zazikwanje zija bwanji sanazizuzule zauchigawenga zomwe anapanga zija .
Tikupemphanso kuti muzabwelenso kuno ku ndix ndi mr zikhale ng'oma .
Lelo mukudzudzulano azikwanje aja simumadzudzula mumazitenga ngati ndinu Angele zitsilu za wathu oipa ngati manyi
A MCP zitukuko zanu ndi kunyengana komanso kupha.
Kwabwera Kabamb🎉pa ground...
Khunyukhunyu ndiwe chizete kwambiri
Akuthamangitsanibe a kumkuyu manyazi bwa? Udolo wonse kutha mumazimbva inu
Hahahaha 😂😂😂 nde adzadzivotela okhatu
Inu muli ndi umboni wanji akunkuyu kut ndi a DPP amene aja? Nanu bweletsan mboni paja ena akamat anyamata azikwanje ndi a MCP mumati kubwere mboni nzimayi wanu uja amalankhula mosaona udindo omwe alinawo kut sizoyenera kulankhula motelomo uja alikut nawe kunkuyu akuuze kut ubwere ndi umboni wakut ndi a DPP amene aja.
Chitsiru iwe garu kwabasi kunkuyu machende ako wava
Nde zakupwetekani😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂 Maloto 😂😂😂😂 kukunyu😂😂😂😂
Ukunama iwe...saanatumidwe....akuonetsa taoni
Ndangotalikila ndikanagenda nawo Iya nanga mkuluza zonse 😂😂😂😂
@McshonWilliam kkkkkkk...ndipo anamuchepetsa..kkkk
Inu munatuma azikwanje bwanji??? Mbudzi!!!
Boma ndi lomweli tingosintha nsogoleri basi
Kkkkkk muzingoti chilichonse DPP nde kunkuyu mukuiopatu simunati adzikugendani. Ndi ana
Ndiwe galu kwabasi kumkuyu,ufufuze azikwanje aja
Kod otsutsa boma alipo ochuluka koma mukafuna kutchula dzina mumatchula dpp why?
Sono lero apolice ayamba kafukufuku chifukwa chakuti angendedwawo ndi duna za boma....ngati zili choncho kafukufuku akuenela kuyambira ku Lilongwe kwa anthu omwe anatenga zikwanje
Panya pako kumkuyu president wake utiyo wakuphayu akawinila kwaotu , akuphonya galu iwe akanangokumaliza galu
Achimwene umbuzi sudzakuchokani, mufufuze zolakwika zanu osati mudzidzudzula azanu
Kod ukuona zomwe zikuchitikazi usamale upililize kwamamia anthu akunyumbakwako
APM my vote
Ndiye yake ndiye yake apondeni pa mtima agalu amenewa amanyada kwawo kuja mboli zawonso pati
Wasati ndiaDPP koma ndiaMalawi akunyasidwa nalo boma lomwwro
A kunkuyo thwi yakutherani inu kwasara pangono kuyithwa Malawi inu
Koma akunkuyu ndi Dpp eeish ...mmailota ndithu kkkkk
Koma zogendanazi sizikukhala bwino ...komaso zomatenga action coz aboma apangidwa chipongwe sizithandiza nyengoi tonse ndife aMalawi.. andale nonse langizani okusatirani pliz pliz ..
Sagonanayo tulo kkkk atsekuka mmimbatu ameneyu
@@MemoryZiyaya ndi boma ili nzosatheka mpaka tivota .....
Ukudziwa bwanji kuti ndi DPP? Anatenga zikwanje aja anali aDPP ?
Zisamakomere galu kugunda mbuzi
Dziwani kuti ili ndi dzikotu a Kunkuyu
Nayenso abweletse mboni paja ena atadandaula za zikwanje amati apititse umboni.
Anthu Ali pa que ma filling station inu nkumapita ki ndirande kumakawanamiza anthu..mbuzi zenizeni
Nanga nkhani yazikwanje bwa mapondo ako wanva kunkuyu
Amugenda nd akwa sundwee Brax machende Ake patii
Kunkuyu boleyako ukuwona ngati Malawi ndi ya bambo ako
Chobwezela chimawa mulungu atithandize amalawi
Kod Zipan zilipo zingat kumalawi ko yilipo DPP yokha iweyo chisilu kwambili
Esime chombo esime chombo ndakuyitana kangati mayi oyipa
Koma dziko rawora ndithu,
Akanika kutchula anthu omwe anawotcha magalimoto pa mbowe ndye only few hours akubwela kumakamba kut a dpp amugenda this guy its puppet
Zikwanje zija anatulutsa ndi a dpp?
Musalimbane ndi DPP..Anthu ndi amene atopa nanu
Kunkuyu ndiwe chitsiru. Ukuyiwala kuti kumwela. Kuno unapha witika ukuona. Ngati anthu sakudziwa chakwela sawina zamanyi basikkkk
Ukunama iwe kape weniweni MCP out!!! DPP come in
Munawongoka pati akukuyu munatinamiza za ndege azakuvotelani ndindani
Kunkuyu pa kholo pako amene anatenga zikwanje aja inu munati chani apapa ndi 50- 50 basi zisaphweteke
Wadeya wachita makwinya kumkuyuu😂😂😂
Azikwanje aja nanga bwanji simukwamanga
Aaaa a za ku Lilongwe sizinafufuzidwe koma za kunkuyu akufufuza zoona zimenezo umunthu palibepo
Iye ndiye wasintha kupha witika
Osangovomeleza bwanji kuti boma lanu ndilolephela kunamizila dpp zautsilu basi chokani apa
Lerolomwe wapolice wayamba kufufuza pamene sikunatuluke or ndi chikwanje chimodzi chomwe pamene ku zikwanje kuja kulizii mpaka lero,Mulungu ayankhure nayo MCP
Akukuyu akulakwitsa kwambiri si a DPP.Iwowo akuyiwala Munthalika ananyozedwaso komweko.Anthu panopa ndi otopa ndi ulamuliro opanda masophenya.Anthu akuvutika kwambiri.Iwowo sakuona mmene anthu akulilira.Sidzikuyenda bola Boma lomwe linali mm'buyomu.Anthuwo sakulakwitsa chifukwa ndalama zomwe amayendera mmaderamu ndi zamitsonkho yawo ndi zawo.Olo atawaphanyira galimoto zawo.Apa zinthu zafikapa palibenso za ndale.
Inuyo munatuma anthu akhape anthu ku Lilongwe. Iwe Kunkuyu ndi mbuzi.
Kulibe kuwinanso MCP Ziwawa mukumayambisa ndi inuyo a MCP komanso inuyo ndi amene mulli mboma mukanayenelabkumazuzula Nyau zanu zija
Inu maona ngati mukumatulutsa anyamata adzikwanje mukuona ngati ma m'boma mwinamu mudziyenda bwino bwino a mcp muona mavuto pa campaign imeneo.watsala Wadowado naye akalowera kumweraku akazionaso
Iwenso umayenera kuganiza bwino....
Kunkuyu panyapako what about kulilongwe zikwanje apolice anafufuza??????
Amuchita bwino ifeso zimatinyasa zija zimachitika kulilongwe
Munagula zikwaje kt mukhape athu amadem relo mwava kuwawa.? Mmm chakwera sangawine pokut mukudalila mashin obera ,kupusa muziwaso
Inutu ndilande sikukufunani Munapha Mavuto,akufuna kutuluka Mcp
Munaona kuti anthu ambiri athawa ndinkona munamupha akunkuyu
ngati pali munthu ofunika kumenyedwa ndi moses kunkuyu munthu wamabodza kwambili
Nkhani ya kugendedwa, kwa kunkuyu, asaname kuti ndi a DPP. Bodza limeloooo! Akuyambitsa zipolowe ndi a MCP.
Komano mpofunika kumadzifunsa wekha why anthu sakundikonda usanaweluze Kaye. Coz tawona APM dzulo it was quite. Check your errors and collect it. I remember the Bingu Wamunthalika was saying let the work of my hand be my witness. If you are good who's gonna hate you? Tiyeni tikwanilitse zomwe tinawalonjeza a Malawi.
Apa nde kuyakhulatu nde zaku lilongwe zija osayakhulatu manyi ako
Ng@ ndtukwanet... Mxiewwww..
Akunkuyu mubweretsa nkhondo mudziko muno ndithu. Dziwani ngati simuzitenga bwino muzalephera kupanga control ziwawa.