MALOZA AAKULU KU MALAWI ~ MPAKANA MAI KALIATI LERO KUNYANYALA CHIPANI CHA UTM CHIFUKWA CHA MA VOTE?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 16 ม.ค. 2025
  • MALOZA AAKULU KU MALAWI ~ MPAKANA MAI KALIATI LERO KUNYANYALA CHIPANI CHA UTM CHIFUKWA CHA MA VOTE?
    Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
    Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
    Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
    NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
    #MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

ความคิดเห็น • 409

  • @KotzenLuwe
    @KotzenLuwe หลายเดือนก่อน +16

    It's sad that most of our politicians are not politically mature

  • @DouglasMbendela
    @DouglasMbendela หลายเดือนก่อน +11

    Mayi munapanga mistack kusiya mpando wanu wa u secretary kumakhutisidwa ndizomwe mulungu wakupasani

  • @hastingskalambo8502
    @hastingskalambo8502 หลายเดือนก่อน +13

    Ifw tomakond UTM osati munthu. Kabambeyo ifeyo tikamuvotera.

    • @ElizabethNdelemani
      @ElizabethNdelemani หลายเดือนก่อน

      Koma ndiye komaso apopo zaonekelatu kuti ngoioa Mai kaliati

  • @LinlyMathewe
    @LinlyMathewe หลายเดือนก่อน +2

    Dr Kabambe my vote ❤❤❤❤

  • @FebbieNjewa-g3k
    @FebbieNjewa-g3k หลายเดือนก่อน +13

    Komano aunt Pat,,munawapangatu welcom Dalitso kabambe nokha,,mukacita kunena kuti cipani cathu cikulandira aliyense,,lero ndiye mwakhumudwa coz mwalephera??l don't support what yu have done,,munayenera kukhala courageous n strong,,remember konse mwacokera kuja??nguluwetu inalira msampha utaning'a,,what if cipani ca utm citawina mudzatani???you r a woman of faith l Kno yu,,come back aunt,,this party z yrs,plz plz aunt,,

    • @emmanueljelemani4203
      @emmanueljelemani4203 หลายเดือนก่อน +3

      I support every word you have said bro.... Mai Kaliati be courageous and support Dalitso Kabambe the one the people have chosen with one voice.... Remember God raises the the humble hearted

    • @GetiverMbewe
      @GetiverMbewe หลายเดือนก่อน +2

      Amai Kaliyati mumanena nokha kuti osatopa osafoka lelo osatopa mikufookaso ayi mai bwelelani ndithu cipani ndicanuici

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 หลายเดือนก่อน

      Ndipo inu munthu ndiwo vuta mwamva🙌🙌

    • @PetrusTlhokwane
      @PetrusTlhokwane หลายเดือนก่อน +4

      Ndipo ngati Mulungu angatimve kumafunika Dr DK adzawineso Chaka chamawa kulamumulira dziko la Malawi ndani akanadziwa zoti Kabambe angazawine Mulungu ali ndicholinga ndipo adzakhumudwa enawo

    • @WysonChilonga
      @WysonChilonga หลายเดือนก่อน +3

      Very bad decision 😢😢😢,koma mistake yomwe anapanga ndi kusiya kupikisana nawo pa mpando wa GS ndi kuimira u president.
      So she's counting herself useless ku chipani

  • @wisemanjere6572
    @wisemanjere6572 หลายเดือนก่อน +13

    Joseph was appointed Governor to lead Egyptians while in a strange country. I like Mai Kaliati, but I am worried about her political decision. Most of our political leaders have the same problem. Being one of the founders of the party is not a guarantee to be a life time leader. This is where political Maturity apply.

    • @MollenMponya
      @MollenMponya หลายเดือนก่อน

      😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊

  • @kondwanigalamala-zf5ri
    @kondwanigalamala-zf5ri หลายเดือนก่อน +5

    Kabambe uja ndi mtondo.Economist,banker, politician.Legacy ya late Chilima iyenda bwino ndi Dalitso Kabambe yemweyu basi.

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd หลายเดือนก่อน +6

    What are you trying to say....??? Nonsense don't confuse people.....DK MY VOTE❤❤

  • @Gracedindeed
    @Gracedindeed หลายเดือนก่อน +3

    He will always have the people. Not your usual politician!

  • @Josephiriillovo
    @Josephiriillovo หลายเดือนก่อน +6

    KUSONYEZA KUTI ZA SKC LEGACY ZIJA MUNKANENA ZIJA NDIMABODZA HEEEEEEE AYI NDEKUTI MICHAEL USI UJA AMANENA ZOONA NDINU ANTHU ACHABECHABE ZAONEKANO

  • @Josephiriillovo
    @Josephiriillovo หลายเดือนก่อน +4

    Iwe wako ndiwu secretary General aaaa kaliati for president my FOOT

  • @emmanueljelemani4203
    @emmanueljelemani4203 หลายเดือนก่อน +4

    A Usi UTM inakukanikani be humble and support DK, we cannot afford to have another group fighting the chosen UTM leadership as we are drawing near to tripartite elections

    • @CollinsMwachuma
      @CollinsMwachuma หลายเดือนก่อน

      All of u supporting dk you are dpp not utm

    • @BarbaraTembo-rr8yr
      @BarbaraTembo-rr8yr หลายเดือนก่อน

      His just being foolish there is no seriousness in him, we need leader's who can think.

  • @wisemangama-s1k
    @wisemangama-s1k หลายเดือนก่อน +4

    Akufuna kumudyera Utsi, empty tins makes loud noise.Osangopita kukapempha bwino bwino

  • @shadreckphiri1799
    @shadreckphiri1799 หลายเดือนก่อน +3

    Kalyati made a mistake. She overrated herself. I wrote sometime back that Kalyati should mantain the position of Secretary General.

    • @mollymasangano473
      @mollymasangano473 หลายเดือนก่อน

      Yes l heard this Advice from Malawian's Chaka chino tiwona zithu.

  • @trizamtonga1514
    @trizamtonga1514 หลายเดือนก่อน +2

    Mmmmmmmmm ambuye akukhudze kwambir mwina zija anakumangan zinal zoona

  • @PhiriChiyambi
    @PhiriChiyambi หลายเดือนก่อน +8

    Kabambe emweyo mwamusakhayo timuvotela pambuyo pa utm

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe หลายเดือนก่อน

      Ndipo azachita manyazi Kabambe 2025 boma

  • @lindadzaoneni
    @lindadzaoneni หลายเดือนก่อน +11

    Amai awa akupanga mistake yaikulu kwambiri, lero akayankhule mwano wokuti sangaipangire campaign UTM, ndiye kuti akakhalako chifukwa cha Chilima? Chipani sankachikonda

    • @chawanangwamkandawire5850
      @chawanangwamkandawire5850 หลายเดือนก่อน +1

      Chilima anabweretsa pamodzi anthu oti pawokha sakanagwira ncito limodzi, nkona zikuvuta pano now that his gone.

    • @BrightMatola-c5y
      @BrightMatola-c5y หลายเดือนก่อน

      Ilsimukudziwa chomwe mukulankhula kma ineyo ndkumuvesa anthu ndamene samamukonda mchipanimo ndye iyeyo choti akawapembedzele anthu otelowo ndichan or muli inuyo mungave bwanj zinachitikir kumenekujakumu?

    • @HondaFredzoG
      @HondaFredzoG หลายเดือนก่อน

      Thawi zina utha kumawada akaliat koma or muli inuyo ma vote 21 wokha ndekut ukufunidwa nchipanimo mmmm

    • @chawanangwamkandawire5850
      @chawanangwamkandawire5850 หลายเดือนก่อน +1

      @@HondaFredzoG zikutanthauza kuti anthu sakumufuna pa udindo umene iye akufunawo, osati kuti samukonda iyayi. Koma ngati izi zili zowona, zikusonyeza kuti amayiwa atopa kulondola anthu, amafuna kukhala ndi chipani chawo ngati mayi Joyce Banda ndipo amawona ngati mwayi woti zitheka unali ku convention ko.

    • @andymasingajunior
      @andymasingajunior หลายเดือนก่อน +1

      ​@@BrightMatola-c5y anthu sanafune kuti iwo akhale president, osati sawakonda ndipo adalangizidwa kuti imani pa spot pompaja iwo sanamvere. Owina ndi mmodzi ndipo adasayina kuti abvomeleza zotsatira koma izi ndi chitsanzo kuti andale ambiri amanama. Remember uku sikuluza koyamba, aluzapo u MP, mwamvapo kuti adachoka kwa mkando chifukwa anthu sadawakonde? Hope this is not a kick of a dying horse

  • @AngelineDumha-ec5le
    @AngelineDumha-ec5le หลายเดือนก่อน +1

    We knew it that things will turn sour

  • @James-v8v8d
    @James-v8v8d หลายเดือนก่อน +1

    Please please do that I'm asking you go to Michael USI

  • @JaneMasikini
    @JaneMasikini หลายเดือนก่อน +6

    Ndipo sizoonayi kukhoza kwanji out of 748 kalliati kumpatsa 21 or ine sizinandinvekere bwino aaa ayi

    • @BrightMatola-c5y
      @BrightMatola-c5y หลายเดือนก่อน +1

      Ineyo ndkuwavesa kma or ndli ine mzowawa ndthu zinachitika zija

    • @jameswajumpha6790
      @jameswajumpha6790 หลายเดือนก่อน +2

      Kaliat position ija siinamukhale athu amalondola Muthu malingana ndi mfundo zake DK uja anakoza

    • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
      @HappyAbyssinianCat-xt2bm หลายเดือนก่อน

      Km ndi zoona kaliat ndamene anapangisa chipani cha utm kut chikhare chilipo mpaka pano chilima atamwalira panalibe ntsogoleri km kaliat anaima nacho chipanichi ndie izi zinapangika ndi zosakhara bwno

    • @DaveChinomba
      @DaveChinomba หลายเดือนก่อน +1

      Basitu chipani chapita ngati masewera ziwani kuti chuma chamasiye chimalaura chifukwa sitchitchedwa kutha olo utachipangira plani titani😭😭😭😭😭😭

    • @PriscahChikaonda
      @PriscahChikaonda หลายเดือนก่อน

      Mesa ankati mdizopangana, anthu mumazitenga kut?

  • @trickermussa472
    @trickermussa472 หลายเดือนก่อน +2

    Ndiye ngati mulungu wakupasa mphamvu zoti azifufuza kuti anthu adya ndiye tikudya

  • @DanMwatchipitsa
    @DanMwatchipitsa หลายเดือนก่อน +1

    Kabambe my vote

  • @emmanuelmtambo3040
    @emmanuelmtambo3040 หลายเดือนก่อน

    DK is loved... Palibe angaletse

  • @LucksonKumwenda-p2f
    @LucksonKumwenda-p2f หลายเดือนก่อน +1

    Mr Usi Izi Simbali Yanu Just Going Back KuMasewero Konkuja Hiyaaaaaaaa

  • @CatherineKatsonga-f6z
    @CatherineKatsonga-f6z หลายเดือนก่อน +1

    Adyereni

  • @nenaniechambwinja4261
    @nenaniechambwinja4261 หลายเดือนก่อน +5

    Anthu tamavomelezani please zinthu zikachitika
    Chabwino mumafuna mukanawina inuyo?

  • @MathiasJoseph-xv1hj
    @MathiasJoseph-xv1hj หลายเดือนก่อน +4

    Km inuyo mumawona ngat maikaliat angakhake president?awa usectary general uja bs

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 หลายเดือนก่อน +8

    A kaliati akungoziyalusa apa mulibe usogoleli mwa mayi kaliyati

    • @EnockMvula
      @EnockMvula หลายเดือนก่อน +1

      zowona komaso mayi nanuso Kaya angayendese utsogoreri asiyire achimuna ndithu

    • @AlickjoiceMatchipisa
      @AlickjoiceMatchipisa หลายเดือนก่อน +1

      Ndipo palizithu zina zimafunika azipange ndi mwamunache osati kuyalukakwapangaiyeku tinakangozindikila walowa chipan china akuchifunacho koma mfundo zalakhulidwa apa zadyera zokhazokha technologies inalowa akazitape alipaliponse azisamala

    • @ElizabethNdelemani
      @ElizabethNdelemani หลายเดือนก่อน +1

      Komaso ndi mzimayi oyipa uyuuuu number zomwe akunenazi kukimbilana chuma chamasiye utm next year ikuwina mundikhulupilile yakwiya ndi mizimu

    • @chrissyamanda5510
      @chrissyamanda5510 หลายเดือนก่อน

      Kwabasi àli ndi mwano .ngodzikuza and alibe malire akayankhulidwe
      Chipani sichingathe chifukwa iwowo achoka
      Azipita atiwonetsa mawanga awo
      Akakhale presdent iwowa ndi mwano wonsewo aaaa

  • @DumisaniMkandawire-h5w
    @DumisaniMkandawire-h5w หลายเดือนก่อน

    It is when I remember comred mthanyiwa

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i หลายเดือนก่อน +4

    DC ananena kuti utm igawikana sizi? Apapa akweni ndekuti aya,bisanso utm yawo,manganyanso wayambitsa utm yake ai ife athu mmaso

  • @AngelaGraysham
    @AngelaGraysham หลายเดือนก่อน +1

    Kaya zako izo Dk my vote

  • @LuckyBenson-p9s
    @LuckyBenson-p9s หลายเดือนก่อน +2

    Dyela lapangitsa kuti chipani cha utm atole ndi odutsa ndi njila😢😢😢😢😢

  • @ElizabethNdelemani
    @ElizabethNdelemani หลายเดือนก่อน +3

    Nde akut sangachite manyaz ngat chilima alipo alimoyo mmmm kuyakhula kwanji uku koma

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg หลายเดือนก่อน

      Thus very sad, ndipo zodabwitsa out mau amenewo akuchokera pakamwa pawo.

  • @VictorBarratt
    @VictorBarratt หลายเดือนก่อน +1

    Mama Kaliati please don't do that for the sake of SKC

  • @JerryamoseAmosejerry
    @JerryamoseAmosejerry หลายเดือนก่อน

    Work had ausi

  • @SaidSamuden
    @SaidSamuden หลายเดือนก่อน +3

    Apa UTM yathapo basi yakawikana

  • @DanielGanizani-h8r
    @DanielGanizani-h8r หลายเดือนก่อน +6

    Koma achinyamata,umphawi ndi umbuli sizinthu,

    • @LymanChimdike-tv7bu
      @LymanChimdike-tv7bu หลายเดือนก่อน

      Akanangonena kuti anapita kukapempha. 😂

    • @MalamaMithi
      @MalamaMithi หลายเดือนก่อน

      umbuli ndi matenda brol, sakudziwa zimene akuchita anthu amenewa

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani หลายเดือนก่อน +1

    Anthu anakukondani pokulangizan mai SG umakukhalani any way may God help us

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon หลายเดือนก่อน +1

    KOMA ONESTLY WITHOUT KALIAT UTM IS FINISHED, SKC SOUL REST IN PEACE

    • @JohnmarkNazombe-hi9xd
      @JohnmarkNazombe-hi9xd หลายเดือนก่อน +2

      NEVER WHO IS SHE.....???

    • @ElizabethNdelemani
      @ElizabethNdelemani หลายเดือนก่อน +2

      Nde kuti utm ndikaliatiyo or ndi anthu

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon หลายเดือนก่อน

      @JohnmarkNazombe-hi9xd to don't know nothing that's why you said whi is she, you have to follow Malawi politics

  • @emmanuelmuyilaa
    @emmanuelmuyilaa หลายเดือนก่อน +1

    Kunyanyala kwake, inu accept defeat... Its politics aaah

  • @AngelaMhango-c2i
    @AngelaMhango-c2i หลายเดือนก่อน +1

    Ma vote akwanthu kumalawi maphokoso hee vote is inside they heart yo can force a cow to drink water to liver if they don't want to drink believe me the will come without drink

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson หลายเดือนก่อน

    Bon kalindo ananena izi Za UTM esh

  • @MusaLion-os1lx
    @MusaLion-os1lx หลายเดือนก่อน +3

    Zilibe ntchito kut mai kaliyati atuluka owina pamasankho ndimodzi basi eeetu komaso mr madrama palibe chazeru chomwe angayankhule apa anthu afuna ndalamatu awa

  • @EmmanuelSimthole
    @EmmanuelSimthole หลายเดือนก่อน +1

    Sir mau omwe mukayankhula aja munali mutaona lero a2 aukila ch2 chja komwe muliko

  • @Thokozanikawanga
    @Thokozanikawanga หลายเดือนก่อน

    Kkkkkk ndaseka heavy usi sadzatheka

  • @RuthKaledzera
    @RuthKaledzera หลายเดือนก่อน +2

    Kunena zoona maiwa zinawamvekera mowawa ndiomomwe achitumikilila chi Pani chanUTM

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe หลายเดือนก่อน

      Koma sakanawina pagulu PA azibambo 3 aaa

  • @edsonphangula5817
    @edsonphangula5817 หลายเดือนก่อน

    Problem Michael usi still VP of which more supporter 🔥

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 หลายเดือนก่อน +1

    Ayi zikomo skc mzimu wanu wuuse mmtendere athu wonse akukanga mpando tindikuti askc analindiadani ambiri eeeee zoopsa😢😢😢

  • @FaithMatitha
    @FaithMatitha หลายเดือนก่อน

    @Prophet senior rodreck mtupa

  • @McanthonyNdau-m4y
    @McanthonyNdau-m4y หลายเดือนก่อน +2

    Kkkkkk kulila kwa kholo

    • @McanthonyNdau-m4y
      @McanthonyNdau-m4y หลายเดือนก่อน

      Panalibe tsogolo apa anthu 4 kufuna mpando umodzi nde amati onsewo awina

  • @EdwardGeorgeKasabola
    @EdwardGeorgeKasabola หลายเดือนก่อน +1

    Usi chenjera anthu amenewo akufuna akudyere ndi adyera president wachipani Cha UTM ndi Kabambe basi wina afune asafune

  • @catacata13
    @catacata13 หลายเดือนก่อน +2

    Conversation inachitika bac
    Racing owina ndi munthu modzi bac inu lilani mmene mungathere mphavu zachipani zili ndi DR KABAMBE

  • @esthermafaiti3556
    @esthermafaiti3556 หลายเดือนก่อน

    Kabambe sanakhalitae mu chipaniichi
    But he's appointed by God 🙏🙏

  • @HestingsMatenje
    @HestingsMatenje หลายเดือนก่อน

    Zopepela SKC LEGACY MY VOTE

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley หลายเดือนก่อน +2

    analipo okuuzani Koma kosamva

  • @YanilaGondwe-v9y
    @YanilaGondwe-v9y หลายเดือนก่อน

    Kapepeseni kwa usi

  • @BERNARDSIKWESE
    @BERNARDSIKWESE หลายเดือนก่อน

    With or without, kabambe basi

  • @happynyirenda8790
    @happynyirenda8790 หลายเดือนก่อน

    Usi manye!!! zaveka? Iwe kaliyati mix your attention first and love your wins this is long way to go after this!! they will remember you i know malawian and you will get good position

  • @JudithKatungwe
    @JudithKatungwe หลายเดือนก่อน

    Wa lipompo sananame,, Lero ndakhulupilira limpompo

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 หลายเดือนก่อน +2

    Let talk honesty Mayi kaliyati introduced Kabambe before he Asher in as the PRESIDENT of UTM,now we see usi as PRESIDENT while he refused to Contest at The Convention ,My fellow Malawians Chenjerani akakupatsani ndalama idyani vote yanu sungani mtima mwanu what l have discovered now Just wanted to confused MALAWIAN'S while your suffering, no fuel,kwacha ikungwa tsiku ndi tsiku your life is miserable 😉 🙄 Aaaa sad 😮

  • @MalamaMithi
    @MalamaMithi หลายเดือนก่อน

    Anthu amenewa anapitira ndalama ,osati zoti anyanyara

  • @RamzackMphiri
    @RamzackMphiri หลายเดือนก่อน +1

    Amayi awawa agulitsa chipan tonse tikuona ndpo timayamikila lelo ndizimenezo😂😂😅

  • @RefrigeratorElectronicrepa-q4d
    @RefrigeratorElectronicrepa-q4d หลายเดือนก่อน

    Manyaka aathu

  • @VenançioZocueza
    @VenançioZocueza หลายเดือนก่อน +1

    Akaliati vomelezani kuti kabambe ndi wanzeru anthu ambiri lamalawi amadziwa,dzichepetseni.

  • @MaxonVictoria
    @MaxonVictoria หลายเดือนก่อน +4

    Zakukanikani musiyileni Kabambe

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick หลายเดือนก่อน

    Kaliyat abweze ndalama zanzake uja amayendanaye kunaijeliya asathawe wabetsa chipani

  • @JuniorSamalia
    @JuniorSamalia หลายเดือนก่อน

    Pitani mai UTM will be there forever ndi movement iyi

  • @James-v8v8d
    @James-v8v8d หลายเดือนก่อน +2

    He will receive you with the whole heart is a good man you forget everything that is a game of politics so go to Mr Usi he will receive you

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick หลายเดือนก่อน

    Zoona. Ineso ndimamukonda usi

  • @yasitafuphiri-nw2he
    @yasitafuphiri-nw2he หลายเดือนก่อน +1

    Dr usi ndinu 1 kabambe wachepa kutali😂😂

  • @wisdom20mkango49
    @wisdom20mkango49 หลายเดือนก่อน

    i knew ...usi said it kiti wait muziona akabwelako ku convention

  • @PhiriChiyambi
    @PhiriChiyambi หลายเดือนก่อน +3

    Mpikisano ena amawina ena amapezeka oluza

    • @ElizabethNdelemani
      @ElizabethNdelemani หลายเดือนก่อน +1

      Komaso mulungu walolela kuti anthuwa asawine kuti awonekele ng'amba ndi anthu achabe

  • @jykstaan678
    @jykstaan678 หลายเดือนก่อน

    Tikuferanji at its best

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick หลายเดือนก่อน

    Ausi oyeeeeeee

  • @VanessaMunlo
    @VanessaMunlo หลายเดือนก่อน +1

    Kulibe wandale wabwino dyela basi anthuwa kufuna maudindo ndi ndalama. Szngatheke aliynse kukhala msogoleri

  • @ChipiriloKamenya
    @ChipiriloKamenya หลายเดือนก่อน

    Thawi Zina kumadekha ,tikamati simutha ndale athuni ndizimenezi.mtima wakaduka Amalawi.

  • @igienaciokelvinPhiri
    @igienaciokelvinPhiri หลายเดือนก่อน +2

    Koma uphawi umazesa uchitsilu🤞

  • @AngelinaNantima
    @AngelinaNantima หลายเดือนก่อน

    That's the Kaliati I know
    aaaaa, chipongwe 21 votes?

  • @euwarttawakali4320
    @euwarttawakali4320 หลายเดือนก่อน

    Youth governor wopanda vision!
    Nkhani ikhale kufuna Ufa

  • @KambewaKenikeni-bz2se
    @KambewaKenikeni-bz2se หลายเดือนก่อน

    He has no mistake. Akuziwa komwe akupita and that is not a mistake. Ngati analowa akhonzanso kutuluka

  • @vinceynyone6693
    @vinceynyone6693 หลายเดือนก่อน

    Osatila usi always ndi azimai okhaa

  • @MagieJames
    @MagieJames หลายเดือนก่อน +1

    Zoonadi maiwa kusava kwawo anakatenga mpando wa secretary genal maiwa anakapeza mavote kma u president anthu amanamiza

  • @MartinMajola
    @MartinMajola หลายเดือนก่อน +3

    Kambambe oyeee

  • @FelixGambiza-fp7tn
    @FelixGambiza-fp7tn หลายเดือนก่อน +1

    Palibe amakonda dziko lino aliyese amabwera kulisokonezq basi muzakayakha ku mwamba

  • @mchipengule
    @mchipengule หลายเดือนก่อน

    Ai bodza sizinayende bwino wina kungouchoka Uko kudzatenga mpando ndizowawa. Pepani Mai Kalifati its really painfull. Lowerani kwina basi kkkkk.

  • @blessingsmasauko3370
    @blessingsmasauko3370 หลายเดือนก่อน

    Afuna akubele amenewo samala

  • @DaveChinomba
    @DaveChinomba หลายเดือนก่อน

    Mai kaliyati ndi winiko ndianthu amisala ndipo anthu awa anatembeleredwa pamene anangochoka ku Dpp pano mizimu yawanthu ikudzudzika chifukwa cha iwowa anapangira chakwera kampeni lero ndiizi tili pamoto walawilawi😭😭😭

  • @CrispineBetha
    @CrispineBetha หลายเดือนก่อน +1

    Kaliati wayituluka UTM hamayo ineso musandiwelengele 😂😂😂

  • @LissahNyasulu-u4l
    @LissahNyasulu-u4l หลายเดือนก่อน

    Nkhani ndi njala osati kulondola chipani Cha utm

  • @KestherMkandawire
    @KestherMkandawire หลายเดือนก่อน

    Welcome to chipani cha fuko❤❤akupusitsani a DPP,kabambe ndiwa DPP

  • @RobertMagombo-i6e
    @RobertMagombo-i6e หลายเดือนก่อน

    Ndiye muziti kuli njala kuvina kwake kumeneku

  • @DanielMkwaila-t3g
    @DanielMkwaila-t3g หลายเดือนก่อน

    Muziyendako m'ma Midzi anthu akuvutika, misika mumayenda inja muziyendaso midzi mu otsakhala m'ma Town monkha bwana utsi

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick หลายเดือนก่อน

    Kaliyati anapha chilima kupusa

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 หลายเดือนก่อน +3

    Achita bwino kutuluka akalamba ndale zamasiku ano zikufunika achinyamqtq opanda mantha komaso akhale ophunzila ngati achina Denis ndi kamangila

  • @josephinemisomali6840
    @josephinemisomali6840 หลายเดือนก่อน +1

    Mai Kaliati kumbali yanga ngati munthu ndikukumvetsani Koma musanyanyale ndimmene zimakhalira owina amakhala mmodzi kumbukilani mau omwe mumayakhula kt yemwe awine tigwilana manja ifeyo timakunyadilani kwambiri imanaoni a kabambe Ndipo mukatero muonetsa umodzi pa chipani cha UTM mwachoka nacho kutali

  • @LenadiMthandi
    @LenadiMthandi หลายเดือนก่อน

    Akape inu

  • @ChiyembekezoJohn-v8o
    @ChiyembekezoJohn-v8o หลายเดือนก่อน

    Aaaaa akufuna u mp uyu Kwa mkando akuona kuti samaka ndi utm bola abwerere ku dpp

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu หลายเดือนก่อน

    Amayi chonde musatuluke mu utm please.

  • @VenançioZocueza
    @VenançioZocueza หลายเดือนก่อน

    Michael usi utsogoleri ayi nzeru zanu ndizachibwana.simungachotse malawi pamavuto.

  • @DennisMhango-nl3gl
    @DennisMhango-nl3gl หลายเดือนก่อน +1

    Kulalata nde amatha but she's not mature enough pa ndale nde amakakamira u president kuti chan sono