- 186
- 1 206 173
Malawi Lero🇲🇼
South Africa
เข้าร่วมเมื่อ 16 ม.ค. 2021
Welcome to Malawi Today! Dive into the pulse of Malawi with our channel, where we bring you the latest trends, hot topics, and vibrant stories from across the country. Whether it’s breaking news, cultural highlights, or exciting local events, we cover it all with insightful commentary and up-to-date information. Subscribe and stay informed about what’s trending in Malawi today!
วีดีโอ
KOMATU UYUYU PENAPAKE CHILUNGAMO CHIMAPUPWETEKA!
มุมมอง 3442 ชั่วโมงที่ผ่านมา
#politics #africa #trending #malawi #memes #remix
DZULO NDINAITEMBENUZA GAME! KALINDO LERO
มุมมอง 2.8K2 ชั่วโมงที่ผ่านมา
#politics #africa #trending #malawi #memes #remix #throwback
UKUKU TIMVA ZINTHU! WINA AMUKHAPA🙌🙌🙌
มุมมอง 1.4K2 ชั่วโมงที่ผ่านมา
#politics #africa #trending #malawi
KOMATU KULILONGWE! MADEMO ALIPO?
มุมมอง 4.5K2 ชั่วโมงที่ผ่านมา
#politics #africa #trending #Mademo #Chakwera #chilima
Uthenga wa mademo ochokera kwa NAMIWA
มุมมอง 2K4 ชั่วโมงที่ผ่านมา
#politics #africa #trending #malawi #memes #remix #throwback #musica #chill
IZIZIDI NDI ZOMVETSA CHISONI KWAMBIRI KU UTM.!
มุมมอง 1K4 ชั่วโมงที่ผ่านมา
#politics #africa #trending #malawi #memes #remix
KOMA NAMIWA AMWENE! 🤣🤣
มุมมอง 1.4K4 ชั่วโมงที่ผ่านมา
#politics #africa #trending #malawi #memes #remix
ANTHU AKU NDIRANDE KUWAUZA IZIZI ANANGOTI OHO! 😂
มุมมอง 29K7 ชั่วโมงที่ผ่านมา
#politics #africa #trending #malawi #memes #remix #throwback
IZIZI ZAFIKA POMVETSA CHISONI!
มุมมอง 4.3K7 ชั่วโมงที่ผ่านมา
#politics #africa #trending #malawi #memes #remix #throwback #musica #chill
KUNKUYU AKUTI KUULULA OMWE AMUGENDA! NKHANI ZONSE ZOMWE ZINACHITIKA PA TIMES.
มุมมอง 18K9 ชั่วโมงที่ผ่านมา
#politics #africa #trending #malawi #remix #throwback
NDE MICHAEL USI KU NDIRANDENSO WATANI?
มุมมอง 36K9 ชั่วโมงที่ผ่านมา
NDE MICHAEL USI KU NDIRANDENSO WATANI?
ANTHU AKU NDIRANDENSOTU EEEH MPAKA KUGENDA NDUNA?
มุมมอง 34K9 ชั่วโมงที่ผ่านมา
ANTHU AKU NDIRANDENSOTU EEEH MPAKA KUGENDA NDUNA?
PETER MUTHARIKA KODI ZINTHU ZAKE AMAZIYENDETSA BWANJI? KASONGO!
มุมมอง 46K12 ชั่วโมงที่ผ่านมา
PETER MUTHARIKA KODI ZINTHU ZAKE AMAZIYENDETSA BWANJI? KASONGO!
ATUPELE AKUZIZIRA KWAMBIRI NGATI ALI MU BARBERSHOP
มุมมอง 3K12 ชั่วโมงที่ผ่านมา
ATUPELE AKUZIZIRA KWAMBIRI NGATI ALI MU BARBERSHOP
ZINSINSI ZAMBIRI WAITULUTSA POYERA KALINDO!
มุมมอง 81314 ชั่วโมงที่ผ่านมา
ZINSINSI ZAMBIRI WAITULUTSA POYERA KALINDO!
BWALO LA MILANDU AKANA KUTHETSA MILANDU YA CHISALE. NKHANI PA TIMES
มุมมอง 2.1K14 ชั่วโมงที่ผ่านมา
BWALO LA MILANDU AKANA KUTHETSA MILANDU YA CHISALE. NKHANI PA TIMES
ZIPANI ZOTSUTSA ZIKAMVA IZI ZIKUTIPO CHANI?
มุมมอง 3.6K14 ชั่วโมงที่ผ่านมา
ZIPANI ZOTSUTSA ZIKAMVA IZI ZIKUTIPO CHANI?
ZOCHISONI! MPAKA COMRADE NTANYIWA MSONZI MBWEE
มุมมอง 10K16 ชั่วโมงที่ผ่านมา
ZOCHISONI! MPAKA COMRADE NTANYIWA MSONZI MBWEE
MANGANYA WADABWITSA ALIYENSE! KOMA IZI ZIKUCHITIKADI?
มุมมอง 3.1K16 ชั่วโมงที่ผ่านมา
MANGANYA WADABWITSA ALIYENSE! KOMA IZI ZIKUCHITIKADI?
IZIZI NDIZOMWE ADAPANGA KABAMBE KUTI AWINE! MAFIA!
มุมมอง 31K19 ชั่วโมงที่ผ่านมา
IZIZI NDIZOMWE ADAPANGA KABAMBE KUTI AWINE! MAFIA!
MGAWO LA CHIWIRI LA MAUDINDIDO NDI ILI OKUGWA AYAMBA KUGWA! MPAKA MWAGWETSA MASANGWI!
มุมมอง 1.1K21 ชั่วโมงที่ผ่านมา
MGAWO LA CHIWIRI LA MAUDINDIDO NDI ILI OKUGWA AYAMBA KUGWA! MPAKA MWAGWETSA MASANGWI!
UKUKU BOLA MA DELIGATES ASACHAPANEKO!
มุมมอง 17K21 ชั่วโมงที่ผ่านมา
UKUKU BOLA MA DELIGATES ASACHAPANEKO!
KWAVUTA KWAMBIRI KU CONVENTION YA UTM ALIYENSE KUZIGULIRA MALO
มุมมอง 16K21 ชั่วโมงที่ผ่านมา
KWAVUTA KWAMBIRI KU CONVENTION YA UTM ALIYENSE KUZIGULIRA MALO
KU AFORD KUNALOWA ANTHU APHUMA KAYA MUMATI NTAMBO! ABUSA KUULULA CHINSINSI CHA ZISANKHO ZA 2025
มุมมอง 5Kวันที่ผ่านมา
KU AFORD KUNALOWA ANTHU APHUMA KAYA MUMATI NTAMBO! ABUSA KUULULA CHINSINSI CHA ZISANKHO ZA 2025
Analikuti uyu thawi ya UDF chitedze ndikalongonda tinadya umpama ife uyualilut2001 Mufuna akuveni ndani? Malawi unakhalako opanda njala? Inesiwachipani tangodzudzulani zomwe mungathe!! Inumunena mademo azimayi anagwiriridwa kwasunjwe ndekuno tizisekelela mutivulileso Azimayathu? Kagoneni uko Mudikile azanu achiteko pitala anapita ndimisewu yomwe 😂😂
Anyamata amcp awa
This Police man the don't they not qualified be a police man Alephera kunhwira nchito yawo
Awa ndi achitsiru mnzeru alibe mmalo momakamba za mnzeru busy kulimbana ndi munthu zaziii Dr Kabambe my vote
Ndirande mumatiimilira, keep up the pase, adziwe kuti akutizunza, mukamaliza miyalayo muiwunjike tigenderenso WINA akabwera 🤣🤣🤣🤣🤣
Kma zoona izi
Kunkuyu ndi chisiru cha munthu!!!
Ine ndi wa DPP basi boma ndi lomwelo
Choka iwe siwa Dpp kagwere uko!!!
😢😅😂
Mwati
Amuchita bwino galu ameneyo
Koma MCP aaaaaaa A kalindo mwaitha❤
Ndi belo ameneyo umo ndimongodutsira anthu akufuna Chakwera amuonetse zokuda asayerekeze kuyenda wapansi kuno
Umanyi umeneyo uzalila uzalila kusogolo agalu
Crocodile ndi mbuzi yamuthu koma nyengo ndi thawi ikwana
Moti amutanyiwa mkuganiza kuti your opinion will be someone's opinion? Noooooo tiyeni tizipemphelera zanzeru abaleee Moti inu mkubisala pa imfa kuti muzinyoza anthu? Aaaaaaa pepani pangani zanu osamalimbana ndi Ena kapena nanuso mkufuna mgule plot mubomamu? Ayi amalawi tiyeni tizilimbikila zoti zingatithandize😢😢
Achewa aulesiwa kholozao, kupatula ozindikilawa
Munthu owopa MULUNGU ndi ameneyu not mbava ija komanso WAKUPHA uja Chikangawa APM my future my vote ❤🎉❤❤❤❤
Koma inuso mmmm usi Siwa UTM 😂😂😂😂
Chakwela ndi terrorist,amene akugwilitsa, ntchito zigawenga zomwe zalanda dela lina la Mozambique malile ndi Tanzania.ngati, amalawi sitiganiza bwino,tidzibvuladzidwa kapena kuphedwa ngati agalu.lero,ndikunenetsa mcp izipha,ndi kukhapa, anthu aku Lilongwe koko mcp isapedzeke ku mwela kuno malile ndi dedza koma,ntcheu yonse mpaka mulanje mcp isapedzeke,ma office awo achoke kapena thilani,moto.mcp, isapedzeke.
Ine kuva kukomatu
Ine ndi wa MCP komano yisazawinenso basi chonde timafuna ife si izii ayi karembeseni tichose MCP yangayi chonde chonde guys
Asakupusitseni uyu nyimboyi wangoiyikapo, adayimba ndi ma kadet m'mbuyomu pa msonkhano wa DPP.
P
Umaitha bro
Ndipo akuchita bwino iwe akanakupha ndithuu
Ngati sitikusamala a Malawi zimene zikuchitikazi zotsatira zake ndi zija tinali nazo ku Mzuzu nthawi ya Bingu. Dikirani muone zimene zichitike ku Malawi kuno. Mkuziona ngati masewera koma kumene zikupitaku dikirani. Nkhani ndiyoti Chakwera mwaononga zinthu if mukupanga sponser ndalama kwa gulu limene likuopsedza anthu mind that Lilongwe is not a government it'self bra wait and see kuti muma boma enawa muchitike zotani. Be cool.
Akalindo,musamauze otsusa kuti ngati simuchitapo kanthu,mukutanthauza chani?adadtu alibe vuto vuto ndinu amene munamenya nkhondo kuti adad achoke pampando,ndiye inuyo ndianzanu antambo,tipulumuseni basi,
Anthuwa ndioputsa akulu akulu akwa nsundwe mukuputsa a chakwera ndi nduna zawo zitavuta azathawa koma inuyo mulibe ndalama mudzakhala momuno mudzadzunzika kwambiri mugwire mawu angawa.
Misala yakubvutanitu, Inu za Michael Usi zakubvutani pati?
May sangalala ndi abwana anu musakwiye mabwana awakaya zazi tamukwezala i malipilo muthu
May sangalala ndi abwana anu musakwiye mabwana awakaya zazi tamukwezala i malipilo muthu
Ndilsnde silora zopusa azikapanga ku lingwe konko Kunkuyu ndichigawenga
Kunkuyu akumawatenga anthu kanga zitsilu kod zinthu zazipolowezi ku central region zapangika angat? Nanga inuyo ngat boma munachitapo chiyani? Even nd M'modzi emwe mpaka panopa palibe omangidwa. Kod boma limatha bwanji kumanga anthu amene apwetekana pachibale or M'banja koma mukukanika kumanga anthu azikwanje? What you should know is ngat kholo ukamakondela mwana M'modzi ngat kholo ukuganiza kut enawo akhoza kunva bwanji? Chakwera abwele poyela ngat president wadziko
Mulungu akutetedzeleni mu chiwembu chomwe chakwera wachikonza.
😂😂😂😂😂😂 koma a Kamgwadira,, inuyo miyala ikuvumba mungamayende pang'ono pang'ono?
😂😂😂😂😂 ngat amulozw
Opusa kunkuyuu
Mademo zopusa zaziii
Kod Zipan zilipo zingat kumalawi ko yilipo DPP yokha iweyo chisilu kwambili
Kunkuyu machende ako ziko silako ovota si iweyo iyayi
Usi ndiwe dolo taona anthu aja adziwa kupemphera tsopano
Omenyera ufulu pang'ono ndi pang'ono mbali zawo zayamba kuoneka
Chakwela ziko lakukulila ndipo palibe ukupanga chomwe umaziwa iwe ndikupha anthu kuchikangawa
Aaaa mwayambapo sichoncho
Ayi zkm km ziliko
Esime chombo esime chombo ndakuyitana kangati mayi oyipa
basi dziko mukuliona ngati la achewa okha okha chakwera munthu opanda umunthu mpando umenewo analiposo ena koma anausiya ndipo ali momuno koma chakwera uzathawa dziko lokhala lako
Azikwanjewa tiwaphumzitse
OSafooka osatop
Kabambeyotu Ali ready nkhondo muziona manjawo wapilinga kale zibagela