The Earth and universe will remain but the creation will be vanished anthu chomwe akufuna sdzambiri fertilizer mtengo wabwino mafuta adzipezeka katundu ma groceries akomere anthu osauka maka maka okalamba akumidzi sdzambri
@@GeshoMwakitwile ndpo sakupita kulikonse ndpo akufera Malawi momun leave it or take it kupusa kwa Amalawi mkumeneko mwaona bwanji maiko adzanu odzindikira amwenye ndi azungu ndi amene atukula maiko awo tikhalira yomweyo koma sakuchoka
Iwe ndi chitsiru komaso muthu wasakho iyeyo ndi malawi anabadwira kumalawi, za umbuli basi, a zungu ali ku South Africa inganene kuti azipita kwao kutiko, umbuli basi kusayenda, kuzolowera kukhala pa miyendo pa makolo anu abasi
My Vote Goes to Professor Peter Munthalika ❤🎉❤ VOTE 🗳 😀 👍 👏 💙 😊 🗳 😀 👍.
Koma ada awa amandiwaza sure 💃💃
Osaopa osatopa osafooka comrade
Allah give us a good leadership in our country
APM my vote
Chakwera president amene azakhara history mupaka kalekale atizuza amalawi president wosamva mavuto ya anthu amangomva mavuto ya chimwendo
DPP My vote
Chilungamo ndi mwano 😂😂😂
😂😂 president wa wadowado anali opelekela ma tope ..amakugwila ntchito Kuchipiku😂😂😂
Mbusa wachinyengo crocodile muthu oyipa kwambili ngati idya amin koma thawi yake yasara pang'ono
The Earth and universe will remain but the creation will be vanished anthu chomwe akufuna sdzambiri fertilizer mtengo wabwino mafuta adzipezeka katundu ma groceries akomere anthu osauka maka maka okalamba akumidzi sdzambri
Yomweyo tikuna fertilize wubwerere basi tikufuna kudya nsima mango sichakudya chogonera sure 💃💃💃💙💙
Kodi Sameer suleman upita lit kwanu ku India usatisokosere kwathu kuno
@@GeshoMwakitwile ndpo sakupita kulikonse ndpo akufera Malawi momun leave it or take it kupusa kwa Amalawi mkumeneko mwaona bwanji maiko adzanu odzindikira amwenye ndi azungu ndi amene atukula maiko awo tikhalira yomweyo koma sakuchoka
Iwe ndi chitsiru komaso muthu wasakho iyeyo ndi malawi anabadwira kumalawi, za umbuli basi, a zungu ali ku South Africa inganene kuti azipita kwao kutiko, umbuli basi kusayenda, kuzolowera kukhala pa miyendo pa makolo anu abasi
Mchilawako mbuzi iwe.
iwee kwanu nkuti?
iwetu kutukwanidwa wachita kufuna fundo ndi loti nthawi anayamba ma games smpila bwanji sunkanena kuti skapange kwao ku infia mbuzi iwe