Amagwetsa mvula ndi chakwera wabodza iwe usadzabwereso ku church kulalikila ngati ndiwe munthu ayi sungawine ndi chakwera iwe wachepa ukufuna udindo wakubawo DK wabodza
Chakwera kudalira kubera sangawine akukaksmira zamachine bwanji tizavota pa manual tizaone ngati chakwera wanuyo angawine ku sapota za ziii mukuvutika kugagada pansi no mafuta chakudya mankhwala koma chakwera yemweyo shame on you school ndiyofunikadi kufera 2,000 ukagula chani sinthani dziko ili likupita kuphompho think twice chakwera akusangalala ndi ana ake nanga iwe.
following you DR DK but please upgrade your microphone
Big up big man
My vote to Dr kabambe
Nice
Thanks my president
koma kumwelako muphanatu😂😂😂😂😂😂
@@wisdom20mkango49 why....??
Dk❤❤
My vote utm 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
❤❤❤❤DK
Zowona zimenezo bwana chakwera kumtumbo kwake konunkhako namachende opanda nzeru
Our president
We want promises not descriptions
Viva dk
Come on Kambabe
Kunotu amtumbuka akasuma musalimbane ndi MCP zilimbanani nokhanokha kuno achakwera akupanga chitukuko or fertilizer atamachita 1tambala anthu akumwera sangalime musanamizepo anthu apo
Chitukuko chilikuti
Zoonadi chokudya chili paliponse ndalama zambir mafuta agalimoto ngabwingabwi ndipo dziko likuenda bwino
Abakasuma zake izo nanga mfundo zikhale zokuti chilima anali nzanga hahahahhaha
Citukuko cake citi kape iwe
Mmutu mwangozaza gule basi mungakambe zanzeru mutazola manyi anu nkumati chitukuko
Kabambe president wa UTM nayenso wayambapo inu Zanu Zada basi
Maulemu bwana kabambe ozaopa
Amagwetsa mvula ndi chakwera wabodza iwe usadzabwereso ku church kulalikila ngati ndiwe munthu ayi sungawine ndi chakwera iwe wachepa ukufuna udindo wakubawo DK wabodza
Kamweni panado
Koma ndeamwe ochulukirapo .. athe kupenya kkk
Zoti magwebwe a mvula kuyambila chaka chatha ndi chaka chino avuta akulu inu mukudziwa koma?? A Chakwera 2025 boma bas
Koma Kabambe pls be on your own man osagulitsa chipani ku DPP
Too late bro 😂😂😂
Machende anu aUtm kabambe ndikape saziwa kuyakhula chitsiru cz chilima anali dolo Mcp tiana iti poti amcp ndinuso makape mulephera kuwina masakho cz makape amenewa inuso ndiye zitukwi za anthu bobobo akuvutani chimwendo ndiye munthu osokoneza basi chotseni
Thyolo iphana pakat pa nkhalamba ndi nyamata koma ndi kathyali atasankhe ndani pamene paja chakwera kudusa moyera
Chakwera kudalira kubera sangawine akukaksmira zamachine bwanji tizavota pa manual tizaone ngati chakwera wanuyo angawine ku sapota za ziii mukuvutika kugagada pansi no mafuta chakudya mankhwala koma chakwera yemweyo shame on you school ndiyofunikadi kufera 2,000 ukagula chani sinthani dziko ili likupita kuphompho think twice chakwera akusangalala ndi ana ake nanga iwe.
Big kabambe osaopa umakwana
2025 boma
Inu simukumva mukati mfundo zimenezo nkhani yayikulu ndi Chakudya
Unkalindanji moyo
Koma ngati mukufuna boma 2025 a kabambe uzani anthu anuwa tizipita kumsewu smart matic icosedwe kupanda apo zotenga boma muyiwale
Kabambe yemweyo
Nde njala wabweletsa nichakwe mayesa nivuto lavula machende ako
Nawemso ako
kabambe ndiwe mbuz
naweso ndiwe mbuzi or garu anthu akumpha inu kumpha anthu chifukwa chandare zazii
Kabambe ndiwe amene wagwesa ndalama, unaba ndalama ku reserve bank
😂😂😂kuchikamwa kwako
Mmmmm manyazi mulibe koma
@@DavidPhiri-o6w zinazi kumayankhula muli ndi umboni mutu ngat finye mxiii