Mawu mayi kt khaaa mayo Joyce Banda nthawi yanu tinkalandila zotsiyana tsiyana ndipo so zinthu zinali bwino kwambiri ❤km Pano mmmm it's too hard for all Malawian.
Mai,ine I don't like your party ndithu,koma apa mawu amene mwayakhurawa ndi amphamvu kwambiri,mwayakhula kuposa azibambo a ndemvu zawo,I salute may God bless you with your powerful words.
Ndakunyadira kwambiri martha jailoc cifukwa ca comment yako ya boh tili tonse ndi ena nonse amene mumayika ma comment pa nkhani zomwe timakambilana apa.God blss u all we are in this 2gether
Very good masteni 🔥🔥🔥 uku nde kuyakulakotu
Mawu mayi kt khaaa mayo Joyce Banda nthawi yanu tinkalandila zotsiyana tsiyana ndipo so zinthu zinali bwino kwambiri ❤km Pano mmmm it's too hard for all Malawian.
Mayi mukuitha ena pansokhano palibe akukamba zanzeru big up mum
Mai,ine I don't like your party ndithu,koma apa mawu amene mwayakhurawa ndi amphamvu kwambiri,mwayakhula kuposa azibambo a ndemvu zawo,I salute may God bless you with your powerful words.
Zoonadi nanenso chipanichi sichimandiwaza koma apapa wandiyakhulira bwino kwambiri
Very powerful speech. Thanks for sharing the full video, well done!
Iwe uzijambula uko anthu angaone ngat ndilipo ndekha😂😂😂😂😂😂😂😂 Chaka chino tiona zinthu
Koma kuzimba kunali kwanu may mnamnga nyumba zaanthu wokaramba mnali ubwezi ndi ammberwa ❤❤❤
🎉 chakwera achoke ndi oipa ANANENA KUTI adzakhetsa mwazi ndipo mmanja mwake muli magazi panopa zikukwanilitsidwa
Bale mussa mcp yatitopesa, yatikwana cibadwileni canga sindidaonepo mbuzi ya presdent ngati cikangawaci
Zomangowoneka nthawi ya kampenizi zimandinyasa awa analikuti thawi yomseyi 🙇♂️🙇♂️ angonamizila kuzuzula boma koma zawo ndizimozi agalu amene
My Malawi 🇲🇼 ♥️ 😢😢😢😢😢😢 kalembetseni Malawi waunyinji wanu.
Kabanza and mdilidwe wa Abambo, was Joyce Banda revolution,
Ulemu wanu ... Madam Hirda..mtika Banda❤❤
Ndakunyadira kwambiri martha jailoc cifukwa ca comment yako ya boh tili tonse ndi ena nonse amene mumayika ma comment pa nkhani zomwe timakambilana apa.God blss u all we are in this 2gether
Aaaa amai wa mcp uyu
Akukwanisa kulakhula za zeru muthu wa mai ngat uyu wina wangopanila maujen koma kukanika kulakhula ndikuchita za zeru
Amama my vote.
Eeeesh
Tikufuna kuyakhula ngati uku
😮Mai ndimakunyadirani mulamuliro wanu munathetha vuto lamafuta
Haaaa Ambuye alowerere chilungamo chitipeze pa Malawi
Amayi inu ngakhale muli a satanic mwakamba za mzeru, cikangawa afuna atibweletsele nkhondo dziko muno. Cimene cingacitike apa nonse muli apa tikakumane lachitatu ku mademo kuphatikizapo iweo joyce osamangonena pakamwa its time for actions smart matic, mec,Anabelo, Nrb onsewa acoke komanso kalembela ayime cifukwa mcp aszilowetsa cibwana.
🤣🤣🤣 iwey walakhula bwino ase
😂😂😂😂😂 koma anthu mwatopa
Munatilakwisa ndinu ameneso powauza anthu kuti achakwera ndie busa and ale zanu ndi zimodzi
Mmmm amayi muzinamatu bwino ku pulaimale bwanji ana akubwezedwa chifukwa chosapeleka ndalama mmmm polani moto
Mobilise people to Demostrate
Inuyo mama ndi mbambande
Zowona amayi awa akhoza kuchiya umboni ndi nasowangawa
Yapp
Koma kulizinthu eesh ambuye atithandize💔
Aaaaaaaa amayiwa akutipusitsa awa
Awatu asamatipinde kuseli akupanga zina
Chosecho ali pa ubare ndi mcp
Mayi mwawalankhula koma gulu limeneri zoona likufuna libweretse nkhondo
Takumvani amai ,Bola mulinjeze kuchoka pansi pamtima wanu kut mudzachitadi ,anthu akufa ndinjala kudziko lino
Uyuyu atithandiza guys tiyeni timpatse 5yrs
Kkk camera man😂
Koma Joice muma kwana koma vuto simukuoneka pa ndanda oti nanuso mupanga mademo ochosa smatic pamozi ndi Anabel wake
Aaaaa amayi chilungamo, zandisangalasa mene mwayakhulila
Bolanso amai omwewa komadzinazi mmmmmmm
Simmene kulilitu🤣🤣🤣
Kkkkkkkk iwe uzijambura ndimwamba momwe uremu wanu masten
Iwe uzijambula uko
Ndakusokosera nkulunga utanva
Banji iweyo suukukhala nawo pa opposition za mademo pa 13th pano
Kumtumbo kwachakwera konunkhako ndithu
Twapikene mayi,kudomasi tudyaule chakachi.?
Akulitenga dziko ngati la amawo agaluwa chakwela iweyo km iweyo mmm khyaya
mai uyo ndi mcp ndi amoz
Mai mwalakhula yooo muli mfundooo umu osaopa
❤❤❤❤❤
Mayi alangizeni apule apanowa kuti mwina zinthu nkusinthako
Mmmmmm zakuchipatalazo ndakumana nazo ine ati kuti andithandize ndipereke ndalama mmmmm zoopsatu
Yalimba mkandiro nawonso amayi atopa kuti topiii
🎉
Ndizoona kulibe chipatala cha ulule kuno eeee
😮😮😮😮
Nde iweyo ngat mtsogoleri wakale why preaching nkhondo ku anthu? Mpake udaluza pa chisankho cha 2014
Kawauzeni olembao azipanga zachilumo zomwe akupangazi ndiye nkhondoyo
Zoona
Ulemu wanu wanu
Odi uko! amai adutseko
Zoom amayi