Ulemelero wa malawi unachoka basi ....Bingu was q blessing and special gift to us malawians koma tinali mu m'dima.May forgive our country and give us someone like him😮
Good speech that people with good confidence will follow it forever, he died for body only but spirit for him still alive. Your body rest in peace almighty name of Jesus Christ Amen 🕊📖.............✍
ndine wa mcp koma pa bingu hmmm zinali nkhani zina mpaka 2009 mutu wanga unapenga bingu ngati anatumidwa ndi ambuye kudzatilamulira moti pazoipa zake zimene anthu amanena ine ndimaziika m'manja mwa mulungu coz satana anakwanitsa gawo lake kutitseka maso ndikumadana ndi utsogoleri wangilo
koma osati zinazi kungoonjezela kuipitsa mbili yake koma sindikukhulupira kudzaonaso tsogoleri ngati ameneyu ngakhale kamuzu sangafike pamzelu zake rest in piece baba
Anthu abwino sakhalisa paxiko I remember you Bingu Mtharika I miss your voice and incouge
ZIMANGOONA KUVUTA BUT THIS MAN USED TO INSPIRE ME A LOT
MAY YOUR SOUL CONTINUE RESTING IN PEACE
WISE TALKING
This was a real man to govern Malawi
Ulemelero wa malawi unachoka basi ....Bingu was q blessing and special gift to us malawians koma tinali mu m'dima.May forgive our country and give us someone like him😮
He was best President ever in our loved country Malawi
0
O
0
0
O
The best president ever in Malawi, continue resting in peace Pro Bingu Wa Munthali. It's my prayer that God should give us a wise n strong president
M'dima sumadziwa kut kuwala kuli pomwepo.
This man, anali muongoli wa dziko lino la malawi.
Koma dziko silinadziwe.
We lost such a great and visionary leader in him. May you still continue resting well Pro Bingu Wa Muthalika
I'm one of a Malawian who was inspired by Bingu,
May his soul continue to rest in peace
I will mourn and celebrate Bingu Wa Mutharika for the rest of my life he was a good and wise president..RIP MY PRESIDENT.
We're still crying for you late Genius Bingu
True leader we miss u
Kuno chomwe amadziwa atolankhani ndikufalitsa zoipa zokhazokha osati zabwino kkkkkkk apapa am glad kuti Bingu anawatsukuluza hvy
And ichi ndichidziwitso chimodzi kuti atolankhaniso nawo ali patsogolo pakubwezeretsa chitukuko cha dziko lino pa mmbuyo.
mutha kudabwa inu kwaona atolankhani omwewo lero akumutamanda Bingu kuti anali mtsogoleri wabwino
We had a true leader. Honest and caring character.
great leader ever n ever
A leader with fatherly heart and love. Keep resting easy ngwazi
Ndinadziwa how great he was atamwalira. You the best president we ever had
l proud of speeches of this formar president.Rest in peace boss.
We miss our best president ever In Malawi 🇲🇼
That was the best advice from bingu
We had genius
But God love him most
Keep on resting well our hero
God choose the best
This dude was genius indeed
Good speech that people with good confidence will follow it forever, he died for body only but spirit for him still alive. Your body rest in peace almighty name of Jesus Christ Amen
🕊📖.............✍
We really miss him now
Amalawi Amapangirana Nsanje Mpaka zaka Zino, Ndimaopa Kupanga Associate Ndi Amalawi Anzanga.
Amalawi Ndinu anthu oipa kwambili
I miss this president and we've never had a president like Bingu wa Mutharika and we'll never have a president like Dr Bingu wa Mutharika in Malawi
Awa ndiwo mawu amawi amalawi kaduka basi chomwe timadziwa😁😁👍
We lost such a great Leader
Marvelous
Abingu muwuse muntendele 😭😭😭😭
Inu aBakili News Channel mukuamva malangizowo?
Rest well Mr bingu
wow ine kumva kukoma
Only the one and the best president in our country anaphuladi dziko pamoto may continue rest in peace 😭😭😭
Wiseman
We will never to forget sir🙏🙏🙏🙏🙏💔
On point
Kodi jelouse mupita nayo kit?
❤❤❤❤❤
We loss ...RIP Father Muthalika
RIP
Zinali Mbubzi za aKAZITAPE.
Munthuyu amaona kut akumutaisa nthawi 😂😂
Sunga yelekeze ndi manyi ali lelowa.awa anali wakulu
Takutoperani a MCP
Tavelani malangidzo
@@elufedavid3788 ndipo ugalu wakesotu nde winawina nanga zugwirizana bwanji ndi MCP apa? Uchimidzi
Madala kuyionera patali game
Inuyo Munali Tate weniweni, Rest in peace
Anali tate wa nfuko
Mzimu wake uziusa mumtendere osatha munthu oyipa uyu mafuta atavuta mkumati kagone pamsewu. Aaah kunapita mfiti
Am dying 😂🤣
Awa adali am'dala bambo
Wa dpp iwe hiyaaa
I like Donald Trump's stand on CNN, He calls them fake news kkkkk
🤣🤣🤣🤣
ndine wa mcp koma pa bingu hmmm zinali nkhani zina mpaka 2009 mutu wanga unapenga bingu ngati anatumidwa ndi ambuye kudzatilamulira moti pazoipa zake zimene anthu amanena ine ndimaziika m'manja mwa mulungu coz satana anakwanitsa gawo lake kutitseka maso ndikumadana ndi utsogoleri wangilo
koma osati zinazi kungoonjezela kuipitsa mbili yake koma sindikukhulupira kudzaonaso tsogoleri ngati ameneyu ngakhale kamuzu sangafike pamzelu zake rest in piece baba
Tulukani Mcp man mutaya nthawi
Zooonadi zokhazokha satana ndiwochenjera koma pomaliza💔💔
Wiseman
Nthito za manja ake ndio nkhani lero Anasiya zonse phazi ndi mulomo Mzimu wake ukuusa ndi mtendere