Our last hope kut dzikoli lichoke mu gahena amene takhala tikudutsamoyi ndi inuyo bwa Atupele. Ndiposo na ngat ndifundo zake izi I believe in Allah we will pass Insha Allah. Allah akutsogoleleni paulendo wa mu 2025 Insha Allah be a president
I'm sure that you did worn chakwera chigawenga cha ku chikangawa in 2019 that you don't know what is the meaning of the president but people was thinking that you are lie today they witness it
Alliance ndi MCP masapota anu akukanilani ndiye mwaganiza zoti mugawe mavoti kuti mudzaoneke ofunikira pa rerun. Mudzakhumudwa ndi zotsatira. Chikuni chachikulu osachipweketsa. You will be surprised.
Good Manifest, thanks atupele act as Burkina Faso leader Pls May Allah bless you
a very good speech , well and detailed.
chikungolankhula osawonela...chili pheeeeee
❤❤❤❤❤May Allah protect u until 2025 Nd be came apresident of Republic of Malawi Nd change our can try us u say,God bless you all the times
Masha Allah wishing you all the best 👍
Moto to Atupure 1 please God help us Atupure must be one of the Riders of Malawias
Please God help him please 😢😢😢😢
MashaAllah Allah bless you and
Before ruling Malawian muyambe mwakafusa kaye nzeru kwa Ibrahim Traore 😅
Ine ndi wa MCP koma uyu ndi munthu wothandiza kudziko la Malawi!!!
Exactly
Indeed he is a President to be in 2025
Number one Atupele muluzi ❤❤ 💪💪💪💪
❤❤❤❤Beautiful occasion
All the way from kk.ooooh what a young future president
Bea and speech from atupeleee😊😊
Tiyeni timuyese Atupele ngati mtsogoleri Kodi pakuvuta ndipati a Malawi🔥💪
Mvuto ndilakuti anthu akumalawi kusakhana mitundu chifukwa ziko lanthu silikupita pasogolo malo moti tisakhe asogoleri anthu atukule dziko lipite chisogolo timakaika zimbalangondo chifukwa chosakhana mitundu
Malawian let's us try young blood, we're tired of these elders 😢
Apatu amanganya atha kulowa ka 20 pa Atupele
Long live honorable AA Muluzi all power is belong to God
No matter what atupele my vote
UDF BOMA🔥💪
Ambuye azikudalisa atupele❤❤
May Allah bless you tupsy
My favorite president 🎉
Mashaa Allah good speech
Excellent speech Sir Atupele
He knows our struggle
Good I dear
Ndilipambuyopo ❤❤❤❤
Atupele ur my vote 🗳 ❤
Tatiyen tipatse mwanayu mpata guys mwina akhoza kutukula malawi uja
Last hope of malawian leadership ❤
Atupele my vote
My vote
My❤️❤️❤️❤️❤️
Good speech and my vote belongs to you Atupele
My vote ❤❤🎉🎉
Our last hope kut dzikoli lichoke mu gahena amene takhala tikudutsamoyi ndi inuyo bwa Atupele. Ndiposo na ngat ndifundo zake izi I believe in Allah we will pass Insha Allah. Allah akutsogoleleni paulendo wa mu 2025 Insha Allah be a president
Akukula mundale zokhala kumbuyo kwa winazi zimapusisa koma pali vuto ndi apa poti chipani cha bambo angapa
Allihamdhullillah Allah akbar mwainuyo Allah balibe cholepheretsa mwainuyo tikupepha mwainu Allah kuti mwanayu inshallah zamupasen mwai wakupeza kukhala utsogoleri mudziko lathu
Atupele nzeru ngati abambo ako amatidyesa
Vote yanga UDF, GOD bless you in every situations you can pass through, amen
Yah Allah yathaljaral Wal ikram make this guy to be president in Malawi 2025 to you we ask and to you only we worship
My vote 🗳 💜
Bolanikon gulu ili ndikanakhala ku Malawi ndikanampasa vote
Nzeru zilimo ndithu
❤❤❤❤boma ilooo
Onebhead can not carry a roof yemweyo 😂😂
Zikom ❤
I see ibrahim traore in you Atupere Muluzi
Atupeli pangani zinthu zothekela UDF ndiimene inabwelesa ufulu pano tikunyadila ziko lathu si tikulipila musonkho nyambalu zakuphazi tatopa nazo
Marsha allah zofunika
Kungovotela atupere muluzi yemwewu basi
No matter what UDF yomweyo
I'm sure that you did worn chakwera chigawenga cha ku chikangawa in 2019 that you don't know what is the meaning of the president but people was thinking that you are lie today they witness it
Abuye mulungu lowelelaniponi uyuyu alowe moba
Congratulations 🎉🎉 my president we are with you ❤❤🎉🎉
Akuluwa ali ndikuthekela kukoza zinthu osati ena akungokhalira chikangawa e chikangawa osanena zonwe adzachite pokuza mavuto omwe tilinawo
Ife ma sports a udf tafuna kunena kuti ngati atupele ukupita ku udf vote yathu singaitenge tikapasa utm
Kuyankhula Kwa bwino atupele ndili pamboyopo ndimvoti Yanga
Mnyamata wathu sopano voti Yanga 💪💪💪
Ine ndwa mcp km my vote is atupele😂
Kuyakhula mu Chizungu kufuna kusangalasa asamunda 😢Zopanda pake
Sudaname m bale
Mwayankhula zamzelu kwambiri koma mumatifowoketsa mumangowoneka nthawi ya kampeni itayandikila
Awa ndimunthu wa nzeru koma ife amalawi tili ndi vuto jerous too much
Democracy ndi mpikisano wa mbava kukaba boma,ndiye aliyense akafuna kukalowa amayenera kudzichemelera kuti iye akathetsa mavuto,koma akapatsidwa mpata uja phwanso lokuba limayamba pompo.
Andale ali ngati mamuna ponyenga mkazi,amanama ndi cholinga avomeledwe basi.Zonse zimene amalonjeza amazitaya uko,akangolowa m'boma.
Zoonadi timavutika mpaka timathawila kwaweniwake timamangidwa kwa chisawawa
Guys womuvotera uja koma uyu❤❤❤
Ndipo Live ❤
Boma ilooooo
Atupele very confident 😅😅 this is a good move, though the party was destroyed by Bingu
UDF imakhala ndi moral nthawi zonse.Come election amapezeka aluza
Koma payekha sangawine Koma Ali ndi fundo zabwino
Tiyeni tonse A DPP timpange sapoti A Tupele Muludzi Kuti awine A Dad akula chonde
Atupele uja nd sheikh komans m, busa osamuphweketsa
Atupele muluzi, ndi boma kale 2025@
Dpp ikunva kuwawa😂
Ifeso as mcp timenya kampeni and tiwina
Mumakwanila abr
Kkkkkkk wosaiwara sumfumu uwu bambo ndi mwana zazi
❤
Gys timuyese mwanai akulu akulu tawayesakale nkutheka mwamwanai muliusogoreri
Mwava inu a DPP wakukanani Atupele muluzi hoyeee
540 Arvel Prairie
mumakwana
Calm man
Mathews 5v9 Quran 49v13
Uyu ndiye omuvotera uja uyu
Akamuna atulukilano ndi mau amphanvu
Azanuso amkatelo koma pano mmm 😀😀
Ishaallah ngatimu. Mulungu akutiongolela
Maloto amulimi ngati vula ingagwe bwino chaka chino chaka cha mawa ndimanga nyumba.
Ikapanda kugwa bwino uzamanga chani?
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Chi vote changa 2025
apa ndapeza omumvotela osati zomangokanganazi aliyese tamuesa wasala ndi mr atupele wa tiyenaeni
Ndipo straight
Nthawi yanu inatha ngat momwe inathera ya d.p.p
Osaitchula dpp ikuotcha aseh
Thomas Jennifer Thomas Dorothy Lee Sharon
Ife ndi a UDF basi kkkk
UDF boma atupele woyeee
Alliance ndi MCP masapota anu akukanilani ndiye mwaganiza zoti mugawe mavoti kuti mudzaoneke ofunikira pa rerun. Mudzakhumudwa ndi zotsatira. Chikuni chachikulu osachipweketsa. You will be surprised.
😂😂😂 lirani mokweza
😂😂😂😂😂😂😂Ndipo@@adamashrafi5875
U d f bomamo
Alakwisa kuyika English kwambiri. A Malawi omwe ndi omwe akufunika kumva izi. Or apeze omasulira ngati kamuzu
Atupele kut moto buuu
Atupele nyamulani boma anthu chizana waphe chiteze chomwe chikudyedwachi
Awa amagona awa azuka lelo zapagalawundi sakuziziwa okha sangawine
Iyayi sanagone ndindale izi bale wanga munthu wanzeru sanganene pa convetion kuti tipanga gwilizano never uwona kutsogoloko