Bravooo professor Peter . Mwalankhura bwino kwambiri. You are endeed a professor sir. Long live Peter. Ife tinavotera chakwera chifukwa cha chilima. Chakwera bashopu yamba kupakira a landrord aku statehouse a kubwera anyani inu
ngati wina anabwera kumene anaputa ku mozaqui ndikupitirira ku zumbabwe ngatu wunafika chaka cha mawa wumaka wundiyankhe mwana wa hure iwe wukupita basi ku opozichino

I love the verse and the interpretation: ufumu wagawidwa between DPP, UTM, PP, AFORD
@@TheAttorney-j9w DPP, UTM, UDF, AFORD
Fight against evil rulling, MY VOTE ADADIE
My vote🎉🎉🎉🎉
Speech yokoma kwabasi🙏💓❤️💯%
❤ kukoma kwake kulipo kale wakhaka
Dpp boma ❤❤💙✊💙
UTM my vote
Big Man🥰
Bomaaaa iloooo
Zooona adad
Mau akulu akoma akagonela.
Powerful
Apapa ndiye pamoyo
Amen
Fight against evil ruling
Mbambande speech
Please ngati uli wa MCP ma comment opusa sitikuwafuna pano. Asiyeni a Daddy agwile ncthito yawo mwadongosolo.!!!!!
@@JamesManjawira-yz4ji ndakomoka ndichani chomwe angabweretse chachirendo
Piter kung'alula lero.
Akut chani awa agogo akulimbana ndimuthu Oti salimbana nawo
Tikawina kuchedwa adadi
I like the statement, 2025 kuli nkhondo yayikulu, ndipo he's surely aware kuti mtunda umenewo sangaukwere.....
Ine ndati masalimo 83 ititsogolera popeza ndi namalenga watero
Muthu wakulu kwambiri
Mmakwana fada😂😂
ngati wina anabwera kumene anaputa ku mozaqui ndikupitirira ku zumbabwe ngatu wunafika chaka cha mawa wumaka wundiyankhe mwana wa hure iwe wukupita basi ku opozichino
Lee Michelle Thompson Kevin Allen Michelle
Munthalika party
mmm fundo alibe
Manyaka eni eni,kwao ndikuba ma votes sangawinenso or atapangila campaing imfa ya Chilima.
UDF Ngati ingapange gwirizano ndi DPP ndye Kuti Mitu Yao sikugwira ntchito ayi ndi anthu oyipa kwambiri
Hahaha 🤣 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Ndi chani chomwe angabweretse chachirendo aaaaa
@@ZephMbeleswa kubwezeresa momwe zinalili
😅zoona ndithu presetent alipokoma tsogoleri tilibe
😂😂😂😂😂😂
Old wood
Gagaini iuzeni mau ikonze Kodi amuyika chinjoka mkamwamo?
Ife sitikufuna oziwa kuyakhulawa akumatigenda kutimenya bolani adad
Sitimadya slang ife
Iwe chimene ukuona ndikusantha kuyakhula?
Palibe chomwe ukuyakhul sungawine iwe
Even drunk ambuye mtengeni palibe kuona vote yanga😂
Taonani kuvura chipewa ngat robot 🤖😂😂