I wish you well Atupele Muluzi ❤ all we need its a better cos things are really bad in Malawi , malangizo anga kwainu boss ; Avoid kuyang'anira zinthu pandale the action that u always say izichitika❤❤❤
Ine ndudabwa ndizochitika za Atuple... khala ngati sakhazikika mu zisankho zomwe amapanga...mzokaikisa kt atha kukhala president odalilika .sangatsogolere aMalawi molongosoka...
I have always wanted Atupele to be a president
I wish you well Atupele Muluzi ❤ all we need its a better cos things are really bad in Malawi , malangizo anga kwainu boss ; Avoid kuyang'anira zinthu pandale the action that u always say izichitika❤❤❤
Uyuyu NDI dolo koma athu sadziwa that's why wanena kuti mpando mukumawapasA athu okuba😢😢 mulungu chonde Mwini thakayi Tipaseni ameneyi ulendo uno
Atupele Muluzi 2025🇲🇼
Atupele wagulidwa ndi mcp
Atupele mwana wa mudzi takurandirani... Kuno... Ku Bunda.. Mitundu. Dikison. Malingunde.. TA. Chadza.. Wanthu mwana.. TA.. Malili wanthu.. TA.. Chiseka.. TA.. Masumba nkhunda.. Wanthu mwana.. TA.. Masula, 💪💪💪💪.. TA.. Tsambago... TA.kalubu.. ❤❤❤❤Lilongwe ndi yako... Osaopa takurandirani.. Obwana
Atupele utimphesa kwamilango
Bambo ake anagulisa ma company ndye ife a UDF ndlama sinkhani compain ikubwerayi ai tilandra ma laptop
Ine ndudabwa ndizochitika za Atuple... khala ngati sakhazikika mu zisankho zomwe amapanga...mzokaikisa kt atha kukhala president odalilika .sangatsogolere aMalawi molongosoka...
Koma kusiyana NDI zimene zili panoziiitu
@@ThembaniJikah kkkkkkk izi ndi worse
U disappoint your people,u escape when things are bad and u appear when it's calm.
Ngati mumawakonda a Malawi why are you failing to assist those who r suffering ku machinga ndi njala before kutenga boma??
Better
Atupere kuyankhula mumatha koma kumaka pa ground ndye simumatha mpira mpaground bwana koma mkufuna T shirt basi
Onse amalankhula choncho akalowa m'boma totally opposite.