ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Umatsatatu stuff sam🎉
Remember history is the best teacher
Umakwana big man ❤❤❤
Angaphe chakwera ndi ndani munthu oti anatemela mpaka ponyelera 😂😂
Kkkk hamayo ine
Paja anthu aku mapita kwa God papa
Iwe umayenela uchoke pamalo pa mene umakhalapo coz ayamba kukusaka anyamata awa samakondwela anthuwa mukamafukula history chochi
Kaliyati ndi tchito yake yopha atsogoleri mwa matsenga,bingunso anafa ali ndi iyiKoma CHAKWERA sungamuthe kaliyati wachepa Chakwera ndi munthu wa MULUNGU ndipo timamupepherera tsiku ndi tsiku
Mpaka Bingu so Kkkkkk mwayaluka
Mzotheka poti Patricia kaliati adayamba wapha malemu bingu wamuthalika mzimu wao uwunse mumtendere
Wa Bakilimuluziuja aposedwa ndi mkulu ameneyi
❤🎉
Mukudziwa kuti Bingu adafa ali ndi mkazi ndiye mkumadabwa za Kaliyati woti ndimayi wolimba mtima koma poti atolankhani athu ambiri amaoneka kuti ali mbali iyi kuchita kudziwika munthu wlna adanena waMCP wotchani palibe mtolankhani adakafusa wa MCP waphedwa,adalengezanso aChakwera wamwalira muli duu muyika mfiti kumbuyo simudziwa kuti zimayambitsa nkhondo mdziko zimakha zitsiru ngati zimenezi zokanikana
Chakwera wasowa chowamangira anthu
Zaboza izi iyaa
Boma kusowa zochita
Mwati Bingu bwanji?
Kkkkkkkk nanu mwayamba za bakili muluzi zil bh
Bakili Muluzi TV is the best ...sungafanize ndi aliyense
Bingu anayenda bwanji?
Zandare izi palibe chilungamo apa
Kaliyati sizachindo kupha asg mwamasenga binguso zaziwika kuti anapha ndiye
Mmmh choka iwe
Mumatha munthu wamkulu
Fake news it's just a propaganda naimwe
Umatsatatu stuff sam🎉
Remember history is the best teacher
Umakwana big man ❤❤❤
Angaphe chakwera ndi ndani munthu oti anatemela mpaka ponyelera 😂😂
Kkkk hamayo ine
Paja anthu aku mapita kwa God papa
Iwe umayenela uchoke pamalo pa mene umakhalapo coz ayamba kukusaka anyamata awa samakondwela anthuwa mukamafukula history chochi
Kaliyati ndi tchito yake yopha atsogoleri mwa matsenga,bingunso anafa ali ndi iyi
Koma CHAKWERA sungamuthe kaliyati wachepa Chakwera ndi munthu wa MULUNGU ndipo timamupepherera tsiku ndi tsiku