Munthu wabodza uyu, akulimbikitsa anthu kusiya manyumba awo, ntchito zawo ndi achibale awo kumapita Malo ena kumakazunzikako. Kodi iweyo Twaibuwe ukuuza anthu kuti azikakhalao ku tchire, nanga iweyo bwanji sukumakakhala nawo ku tchireko? Inu amene muzitchera makutu Anu nkumatsatira za munthu uyu mungopusitsidwa chabe , mudzapanga regret. Mitu yanu izigwira ntchito how can life exist on Saturn .. ?
@hastingsbreak3545 iweyo ndamene udzapange regret together with this false prophet. By the Twaibu shud tell me what is LCD?, why did you called your device as LCD? why teaching people things that are not practically happening? And why you people just following things you don't have evidence why? Did the Bible say you shud get out of your homes and leave in shrums for sarvation? You people why can't you use your ears,eyes and all your senses right?
@@KondwaniNyalugwe-w4c Don't waste your time my dear Anthu onse akupanga comment zomuyamikila amatumidwa ndiiyeyo so that aziwonekangati ali ndi ma followers but the truth is this guy hi has mental health problems because it doesn't even make sense that ukuwawuzaanthu kuti ndiwe X satanist but u are still giving out information yazimene zikuchitika kusatanikeko so why are u calling your self × yet you are still communicating with your fellow satanic people it means you are still interested . uzinamiza makape azako omwewo
Ana amulungu tikuyenera tiimebe pamaso pa mulungu chifukwa chilichose chimene chinalembedwa mu buku la moyo chikuchitika tipemphere zolimba kuti pamene msautso ukubwera mulungu azakhale thandizo lathu amen
To be honest this man he change my life coz everything what he's saying is a true
Ine tu kumvera izi sizindiopseza, palibe uthenga wina oposa uthenga wabwino wa Christu Yesu ndiwo chipulumutso chathu.
It's a God messenger I always listening to each and every audio
Tidziwitsen mtumiki Twaibu. Tithandizeni kupanga chisankho podziwa zomwe mdyerekezi wakonza pofuna kuononga ana a Mulungu mmasiku otsiliza ano
Utumiki wanu umandigwila ntima kwambiri
Ndisitheni. Ndidzawone ufumuwanu
Mamuna uyu aaa alemekezeke yehova kwaife amalawi ndidalitso LA mulungu yehova mupatseni mtumiki you moyo wawutali pali moyo yochuluka you ipulumuke kaamba ka maumboni ogwira mtima amtumikiyu
Continue sharing the audios pliz muli mphamvu
Pemphero langa ndi lakuti Yehova Mulungu wa Kumwamba adzidalitsa ndi kutetezela mtumiki Twaibu nthawi zonse.
kodi mmesa munasiya usatanic nanga ukuonabe bwanji
Mulungu adzikudalisani nthawi zonse.mulungu wakumwamba titezeni ife ana anu kumikango yolusa oti Amen
Praise God for your blessings
Ndinaseguka maso
Amen mtumwi God bless you
A mr twaibu mulungu anakusinthani ndicholinga ambuye azikutetezerani
Si mphamvu si nkhondo koma mzimu wa ambuye
😢ziko silimmene tikuonera
Mulungu azimudalitsa ndi kumutetezera Nthawi zonse mpakana mission yomwe anamutuma idzakwanilitsidwe,ndipo chilichonse chomwe wakhara akunena zikufanana ndi zomwe brother Enigma yemwe wadzukanso kuno ku dziko la South Africa ndipo zikumachita kukhara ngati wakunoyi akutanthauzira zomwe ananena Mtumiki Twaibu.Nthawi yatha tieni titembenukire Kwa Mulungu
Mmm God hv mercy on us
Atwaibu ndinali ndifuso loti kod zibwezizomwe achinyamata amasiku anofe ndizololedwa
Very inspiring Amen
Wakuva ave osava akhale
kumwamba kulemekezeke chifukwa tikuva zambili kuchokela Kwa Mr twaidu yaweh aziwatsongolela nthawi zose
Tiyamike Yehova Mulungu wathu chifukwa tili nawo mwati wakumva nawo Izi mu chiyankhulo chathu
Tisadzaname kt sitimamve mtumiki Mulungu apitilize kukutetezani limodzi ndi banja lonse🙏
😊😊
Thank you for sharing
Ndipemphe kwa ATwaibu,mudzafotokoze satanesatane wa ma Aliens
Mr twaibu mumausutha moyo wanga
is this true?
Munasowatu brother twaibu
Ambuye atichitile chifundo
Ambuye atithandize😢😢
Ambuye tithandizeni paife tokha sitikwanitsa
Kwathu kuno kukumabwera anthu akumagawa ma phone komanso ndalama za ulere zikutanthauzanji zimenezi?
mr twaidu mudakambako za zayoni kod zaoni ndichiyani kod ndiuchimo
It's all the truth
Amen
Kodi zimene anthu akukambiranazo bwanji osayika audio ya zinthu zomwe zikunenedwazo kuti anthu amve zomwe zikunenedwazo?
Amen 🙏
Musamasowe mr timatolamo ndithu
Sakukuonani?? Zithekabwanji eeeee tixiwenawo zikuophyanso koma tikusegukanso maso auzimu😢
Eee km abale mulungu atithandize
Kod mukuti zikukhala bwanji
Masiku akusadziwa mulungu analekelera inu amene mmadana ndi twaib bwanji osapeza Zina zopanga follow nanga amachita kukuuzani ????? Twaib akumalalikira zokakhala kutchire kapena munthu ekha akamva uthenga wabwino akumapanga chisankho???? Ifeyo tisiyeni tidzimvera inuyo follow zomwe mwakonda zapadziko lino lapansi mukumbukire Paul atatembenuka kuti anapanga chani inuyo basungani zomwe mwakakamilazo nde musamakhale busy kumvetsera ngati zimakubowani
❤
😢
Munthu wabodza uyu, akulimbikitsa anthu kusiya manyumba awo, ntchito zawo ndi achibale awo kumapita Malo ena kumakazunzikako. Kodi iweyo Twaibuwe ukuuza anthu kuti azikakhalao ku tchire, nanga iweyo bwanji sukumakakhala nawo ku tchireko? Inu amene muzitchera makutu Anu nkumatsatira za munthu uyu mungopusitsidwa chabe , mudzapanga regret. Mitu yanu izigwira ntchito how can life exist on Saturn .. ?
Kodi Kani your still far with what the world is soon it's you who will regret mkondo zikafika pa chimake
You're blind, you don't understand things of spiritual realm
@@hastingsbreak3545 ndipo ndizoona amakhala ku tchire
@hastingsbreak3545 iweyo ndamene udzapange regret together with this false prophet. By the Twaibu shud tell me what is LCD?, why did you called your device as LCD? why teaching people things that are not practically happening? And why you people just following things you don't have evidence why? Did the Bible say you shud get out of your homes and leave in shrums for sarvation? You people why can't you use your ears,eyes and all your senses right?
@@KondwaniNyalugwe-w4c
Don't waste your time my dear
Anthu onse akupanga comment zomuyamikila amatumidwa ndiiyeyo so that aziwonekangati ali ndi ma followers but the truth is this guy hi has mental health problems because it doesn't even make sense that ukuwawuzaanthu kuti ndiwe X satanist but u are still giving out information yazimene zikuchitika kusatanikeko so why are u calling your self × yet you are still communicating with your fellow satanic people it means you are still interested . uzinamiza makape azako omwewo
Eeeee
Amen
mr twaidu mudakambako za zayoni kod zaoni ndichiyani kod ndiuchimo