A KABAMBE NDIOMWE ABETCHA NDALAMA YOPOSA ALIYESE POGULA POTRAIT YA SKC KU UTM FUNDRAISING DINNER

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 17 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 104

  • @beatsbymcstevens
    @beatsbymcstevens หลายเดือนก่อน +14

    The spirit of SKC was really moving around the room, what a very organized happy home. Chonde after convention zipitilire♥️

  • @isaacchipatala1618
    @isaacchipatala1618 หลายเดือนก่อน +3

    UTM forever ❤❤❤❤

  • @HildaMbizi
    @HildaMbizi หลายเดือนก่อน +6

    Tawonga chipani chilipo viva UTM Kabambe mweneyuyo

  • @felistassumani
    @felistassumani หลายเดือนก่อน +2

    Let love lead in remembrance of Dr Chilima. We love you our leaders. UTM my vote.

  • @HildaMbizi
    @HildaMbizi หลายเดือนก่อน +6

    Kabambe sanatumidwe ndi dpp iyayi musiyeni naye wachikonda chipani Cha UTM khomo ndiloseguka osamatsekela anthu kunja

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 หลายเดือนก่อน +4

    Dinner ya Classic🎉. Koma wa 2pin yo munakamulandira ndiyambiri. Kanjawala mkachabe😂😂😂😂 i love you man

  • @DennmichSimb
    @DennmichSimb หลายเดือนก่อน

    Utm family yonse thanks nice fundraising. Youthful leaders, God should guide you all,so that you have to lead our country to prosperity please,Malawians are tired of poverty for more than 60yrs.

  • @JasonMailos
    @JasonMailos หลายเดือนก่อน +3

    UTM my vote ❤❤

  • @ramseymavuto3546
    @ramseymavuto3546 หลายเดือนก่อน

    I love the confidence and determination of fellie njawalam..
    Team builder... Keep on support kabambe

  • @JosephShadrech-o3q
    @JosephShadrech-o3q หลายเดือนก่อน +2

    For real I hv seen the spirite of SKS moving in the room.cz the way it was going on more than the way u think what a lovely dinner found rising ❤❤🎉🎉🎉UTM

  • @EmmanuelkpPraise
    @EmmanuelkpPraise หลายเดือนก่อน

    You guys from UTM you are very inteligent,am saying this becoz you fo things publicary that no one can say where do you get the money keep it up SKC 💪💪💪💪

  • @EdwardBilly-p8t
    @EdwardBilly-p8t หลายเดือนก่อน +12

    Koma ali ndi makhobidi agalu amenewa, akamalankhula ngat tikuvutikira limodzitu😅😅😅

    • @PatrickFicklem
      @PatrickFicklem หลายเดือนก่อน

      kkkk eti kumatipusitsa kuti tiziti tikuvutikila limodzi koma kwinaku akunya ndalama zochukuka mmakomo mwawo

    • @PartsonMdeza
      @PartsonMdeza หลายเดือนก่อน

      eeeh anthu wa dollar nde alinazod eeeh

    • @FelistasNkasalaMakumbo
      @FelistasNkasalaMakumbo หลายเดือนก่อน

      Galu ndiwe kkkkk Uline kanthu

    • @kingsleyChisenga-i8g
      @kingsleyChisenga-i8g หลายเดือนก่อน

      Andale ndi mbava Inu akabambe anaba izi

    • @MikeLodzi
      @MikeLodzi หลายเดือนก่อน

      kkkkkkkkkkk ndiye mwati agalu

  • @AbdulrahmanKachere
    @AbdulrahmanKachere หลายเดือนก่อน +1

    My friend politicians do not think of the needy instead think of themselves

  • @SandraChibaka
    @SandraChibaka หลายเดือนก่อน

    Njawala 🔥🔥🔥🔥 you are such amazing guy 🎉🎉🎉

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate หลายเดือนก่อน +2

    Kabambe ❤❤❤❤

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 หลายเดือนก่อน +3

    Za china Kambala nza simple mmaonekedwe koma ndi zopata,ndi a mapwepwete osazionesera

    • @MikeLodzi
      @MikeLodzi หลายเดือนก่อน

      ndipo anthu ali ndi dolla mmmmmm

    • @LLOYDMWANDIRA
      @LLOYDMWANDIRA หลายเดือนก่อน

      I can confirm that SKC has just disappeared from our naked eyes, but his spirit is leading the party 🎉🎉🎉

  • @EliSMpuka
    @EliSMpuka หลายเดือนก่อน +3

    Musabweletse maganizo osalana aliyense ali muno ndi wa Utm kabambe analowa UTM ndi mtima wake onse osayankhulapo zanu zosankhanazo ndipo za chuma munthuyo amazidziwa kwambiri ku dpp sanamupatse mpata kuti akapikitsane a Peter munthalika

    • @LinlyMatheweKufakwina
      @LinlyMatheweKufakwina หลายเดือนก่อน +2

      Zoona zake inenso koyamba ndinali odana naye but as of now munthuyu anabwera ndi mtima onse ndithu ambuye alowelerepo

  • @BlessingsCperumal
    @BlessingsCperumal หลายเดือนก่อน +1

    Njawala may God bless you

  • @miltonkanyamula9486
    @miltonkanyamula9486 หลายเดือนก่อน +3

    This is party fund raising... So no gradges...

  • @GiftBanda-fn6si
    @GiftBanda-fn6si หลายเดือนก่อน +2

    Kod usi ali ku chikangawa ?

  • @emmaculatemenzeiwa
    @emmaculatemenzeiwa หลายเดือนก่อน

    Utm is not dead. Thanks SKC

  • @tiyamikelatson4908
    @tiyamikelatson4908 หลายเดือนก่อน

    Zachamba kwambiri izii

  • @TsArKhaii
    @TsArKhaii หลายเดือนก่อน +1

    Kabambe❤

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 หลายเดือนก่อน

    This is nice and cute. This is the party

  • @DoniasKamwana-l7r
    @DoniasKamwana-l7r หลายเดือนก่อน +1

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ very btf celemony

  • @RuthMkangala
    @RuthMkangala หลายเดือนก่อน +2

    Dk woye asafuna akakolope munyanja

  • @Josephiriillovo
    @Josephiriillovo หลายเดือนก่อน +3

    Chonsecho cho potrait cha chifanifani cha ambuye yesu sichingagulidwetu pa ndalama yonseyo 😂😂😂😂😂 eehh koma dziko ndi anthu ake. Nde mwati azikatani nacho? 😂😂😂😂

    • @gersonkaka9528
      @gersonkaka9528 หลายเดือนก่อน

      Amene mulibe ndalama ingowombelani manja 😂😂😂😂😂

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde หลายเดือนก่อน

      Ndipo zoonadi kkkk nanga akafanizile ndi yesu zoona anamuonako yesu ndindan pot yesu ndi mzimu inuyo mulipo yesu munamukana kare chifukwa mumkaduka yesu amakana​@@gersonkaka9528

    • @mikeyakobe-j2l
      @mikeyakobe-j2l หลายเดือนก่อน +1

      Inu amene uja sichifanifani cha yesu weni weni pomwe ichi ndichifanifanj cha ke chenicheni cha SKC komaso amapikisanawo ndi ana ake nde Inu muti chani

    • @Josephiriillovo
      @Josephiriillovo หลายเดือนก่อน

      @mikeyakobe-j2l ukanyere kutali bwa

    • @Josephiriillovo
      @Josephiriillovo หลายเดือนก่อน

      @mikeyakobe-j2l hahahahahaha ATI amapikisanawo ndi Ana ake koma bwanji ukuganiza mwa mamina ngati chakwera hahahahahaha mbuzi sure iwe chitosi

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os หลายเดือนก่อน +3

    A President a Michael Ussi ali kuti sakuwonekapo apa

  • @elizabethlizi-w5h
    @elizabethlizi-w5h หลายเดือนก่อน

    tingagule pa bwanji ngati mungapange print zina

  • @Medal-f6u
    @Medal-f6u หลายเดือนก่อน

    This party has very creative ppo

  • @keeganvanloggerenberg3029
    @keeganvanloggerenberg3029 หลายเดือนก่อน

    Iyi timati fundraising or ku tchalichi timapangaso ndiye chisawawe apa (no nthuka)

  • @YusufJimmy-v1o
    @YusufJimmy-v1o หลายเดือนก่อน +3

    Good ❤..kuthandiza chipani

  • @chifunirokachingwe2627
    @chifunirokachingwe2627 หลายเดือนก่อน

    Njawala is a vibe 😂😂

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 หลายเดือนก่อน

    P0funikadi kuchenjera nayedi nkulu ameneyu .Kabambeyu ali ndi ka DPP mmaganizo ake koma bola asamaiwale SkC anakanidwa ku DPP ngati Nankhumwa amanena zoona

  • @RuthMkangala
    @RuthMkangala หลายเดือนก่อน

    Maganizo obwezera zithu pa mbuyo munenawa kufunika ndalama zochuluka ku convention

  • @MacfelsonMunthali
    @MacfelsonMunthali หลายเดือนก่อน +1

    Anaba zambiri ku reserve Bank

    • @amosiabdulallh7965
      @amosiabdulallh7965 หลายเดือนก่อน +1

      Ngati Mwafunse kale pitani nae kupolisi

    • @BlessingsCperumal
      @BlessingsCperumal หลายเดือนก่อน

      ​@@amosiabdulallh7965ndipo anthu tilibe pabwino

    • @MlecheFatch
      @MlecheFatch หลายเดือนก่อน +1

      Kamumangeni

    • @ChixomoPeter
      @ChixomoPeter หลายเดือนก่อน +1

      Eeeeeish km amalawi ndife anthu osazindikila sure

  • @FebbyPhiri-n7j
    @FebbyPhiri-n7j หลายเดือนก่อน

    Koma mdalama muli nazo anthu inu ayi dzikomo

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile หลายเดือนก่อน

    Kabambe ndiwakuba ndiposo anaba zambiri anthuwa panopa zinthu zikuvuta kamba ka awa a dpp ,asabwereso awa

    • @ancientnkhata1137
      @ancientnkhata1137 หลายเดือนก่อน

      Ndipo kwambiri

    • @symoldicky
      @symoldicky หลายเดือนก่อน

      Poor mentality ,zinthu lero zikuvuta lero cuz of poor management cuz u can agree with me kut Malawi misonkho akudula daily plus ngongo nde zungobweledweso where all this money going ? DPP ikumabwerabe kuzaba ngat nkubako? Am just a citizen sinnavotepo koma ndibwino kumanena zoona anthu akuzuzika

  • @adsonphiri6497
    @adsonphiri6497 หลายเดือนก่อน +2

    Kabambe uyu anatumidwa ndi Mthalika kt azatenge chipani kuchipitisa ku DPP,personally i dont trust this guy

    • @TsArKhaii
      @TsArKhaii หลายเดือนก่อน +1

      Umboni wanu uli kuti?

    • @HeerahJohn
      @HeerahJohn หลายเดือนก่อน +1

      Mesa UTM inachoka ku DPP mwaiwala? 😂😂😂 Muchila

    • @ancientnkhata1137
      @ancientnkhata1137 หลายเดือนก่อน

      THIS IS VERY TRUE BUT HE WONT MAKE IT

    • @MlecheFatch
      @MlecheFatch หลายเดือนก่อน

      Imwani panado

  • @ShillahChisi
    @ShillahChisi หลายเดือนก่อน

    Where is kaliati

  • @StevenMagalasi-y6i
    @StevenMagalasi-y6i หลายเดือนก่อน

    Anphawinu mukuti chani

  • @macfordjames7803
    @macfordjames7803 หลายเดือนก่อน

    Anthu adzachita mayere padzinalanga,bwanji osapeza njiraina guys?

    • @Trendingbag
      @Trendingbag หลายเดือนก่อน

      its a fundraising dinner remember? imagine having that potrait in your house. iwe iwe

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde หลายเดือนก่อน

      ​@@Trendingbagkomasotu akungoyenera coz sck ndi founder wa utm

  • @hanleckbunnet
    @hanleckbunnet หลายเดือนก่อน

    Ndale zathu zikanakhala zokomela anthu bwenzi pano tili patali♥️♥️♥️♥️♥️♥️♥️♥️♥️💪💪💪💪💪💪💪🙏🙏🙏🙏🙏

  • @RuthMkangala
    @RuthMkangala หลายเดือนก่อน

    Akuthandiza chipani Inu vuto lanu chani

  • @atupelemwangomba206
    @atupelemwangomba206 หลายเดือนก่อน

    MPAKA 1 MITA?

  • @PraiseWisdomson
    @PraiseWisdomson หลายเดือนก่อน +2

    Why not assisting the needy with your money?

    • @chifundomatumula1652
      @chifundomatumula1652 หลายเดือนก่อน +3

      Ndie convention ndalama zake akazitenga kuti

    • @JoshuaJuwawo
      @JoshuaJuwawo หลายเดือนก่อน +1

      It's for Fundraising of the convention zoti ma delegates akadye

    • @nokosemakolija-xe9do
      @nokosemakolija-xe9do หลายเดือนก่อน +2

      Tapangani ndalama zanu muthandize ma needy wo osamachulukila nzeru thukuta laeni

    • @beatsbymcstevens
      @beatsbymcstevens หลายเดือนก่อน

      @@PraiseWisdomson they're raising money for their convention ase sikuti akuseweretsa ai

    • @petertaulo8014
      @petertaulo8014 หลายเดือนก่อน +1

      Vuto la umphawi wanu musapangitse kuti anthu ena alephele kuchita zinthu zawo

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo หลายเดือนก่อน +3

    Akugula chipani inu simukudziwa anatumidwa ndi DPP Kuti azathtese UTM

    • @BonMatemba
      @BonMatemba หลายเดือนก่อน +3

      Kulakhula kopasula uku

    • @yassinn5634
      @yassinn5634 หลายเดือนก่อน

      Akachigulitsanso kwina

    • @chifundomatumula1652
      @chifundomatumula1652 หลายเดือนก่อน

      Utm inachokera ku dpp komkotu

    • @BlessingsCperumal
      @BlessingsCperumal หลายเดือนก่อน

      ​@@chifundomatumula1652ndipo

    • @MlecheFatch
      @MlecheFatch หลายเดือนก่อน

      Better than ng'ona party

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f หลายเดือนก่อน

    Wayambapo kubweza zomwe amaba zija. Kkkk

  • @shotsfired588
    @shotsfired588 หลายเดือนก่อน +1

    Nde he paid 20 million for presidency and 27 million for a picture and he’s telling us how much he loves the country and people are suffering, what does he know about suffering. How much does he have left in his account.

    • @ancientnkhata1137
      @ancientnkhata1137 หลายเดือนก่อน

      He is just useless

    • @Sofi-p1v
      @Sofi-p1v หลายเดือนก่อน +2

      Pamenepo

    • @nzotakilango9578
      @nzotakilango9578 หลายเดือนก่อน +1

      Pamenepo ndipamene pakudabwitsa

    • @StarfordKAMOTO
      @StarfordKAMOTO หลายเดือนก่อน +2

      Don't trust politician, they are doing business

    • @GibsonMithi-n4y
      @GibsonMithi-n4y หลายเดือนก่อน

      Kkkkkkkk my friend mind your business