Enanu we know already kuti mukudya za mcp watulukira ung'onoung'ono mwayamba kale kutsekula mimba jealousy down ufumu ubwerere kwaini ake ngati tikufuna Malawi asinthe apo bi kayaa...
Tiuzeni zanzeru apaa osat munenazo ai amalawi simungawapusitse ai kuli 50 pls 1 ufuna unene chani plan yanu taiziwa inu ndi pp mufuna mugawe ma vote cholinga zipani zina zisawine muli ku MCP l know your plan
Achinyamata satatipusitse Ali ndi mcp ameneyu Why akupanga chibwibwi? ....that shows he is hiding something to us ..... Atupele sungaputse Amalawi chisadziwa anayaimbira mfiti manja Unfunse kalindo
Salary simuzalandila , iwe ndi Abambo ako tagwelani uko akuba inu... You are leopard you can't change your behavior... poorest education than ever during your Father time
To me welcome back Mr muluzi we know ur dad was a Hero in politics be like him atupele my vote
Kodi Atupere akuthawathawa bwanji akafunsidwa za a Chakwera
I think he might be the right candidate
Sakundigwira mtimabe ine, nkhani ya economy sakuyifotokoza momveka
My vote 🗳
We need alliance please 🙏🙏🙏😭😭
Let's work together as one Chikangawa asowe basi
We love you ❤boss
Please vote for him
Booom atupere muluzi❤❤❤❤
My vote...
tamaliza kutengerana maiko apasi. mutitengera ku space😂
My vote
Interigent Man 🔥
Uyu ndiolephera sayankha futso😊
amayankha mwanzeru,
Mmene Chilima adayendera 2019, ndikukhulupirira kuti adaphunzira pamene paja and ayenda mmidzi😂😂😂😂😂😂
Enanu we know already kuti mukudya za mcp watulukira ung'onoung'ono mwayamba kale kutsekula mimba jealousy down ufumu ubwerere kwaini ake ngati tikufuna Malawi asinthe apo bi kayaa...
Boma ❤❤❤❤ tupele
Ngati adzaphatikizane ndi MCP adzapita yekha waona kale ma supporter ake waakana kale achikangawa awa pamenepo aganize bwino kwambiri..
Ndale zaku Malawi ndizamchibanja ndipo zongomazungulira ndipakamwa ndikumalemeletsa mtundu umodzi modzi omwewo. A Malawi tatopa ndi mabodza tikufuna change ngati yomwe anabweretsa a Bambo ake A Tupele.
Don't go for alliance we want GNU
I think this guy needs chance
Atupere akuthawathawa Nkhani ya MCP ndukuuzan akulu akulu uyuyu sindikumuona bwino mayakhidwe Ake Koma abambo Ake Mmmmm sanayakheso molondola Koma tiva. Akayesela Ku lowa Ku MCP ndukuuzan ndithu apitako okha chipani achisiya. Sirius
Atupele you can't be a president on this country because yo are too young on compain
M'malawi muno timaluza azisogoleli abwino chifukwa cha kuzikonda kwaoyambisa zipani,,, kunena chilungamoh bwanawa ndale anazisiya,, chimene abwelelaso ndichyn please
Palibe cha nzeru wakambapo apa.
Vuto lakula ndi dyera..UDF payokha singawine chisankho.mavuto amene tili nawo m'dziko muno, pamafunika atapanga m,ngwirizano..UDF,,,DPP.. Afford ...UTM ..apo biiiiii..mudzawerengenso comment yangayi next year ..MCP idzawina ..
Kodi za dennis mahata zilipat yanthu vote ikaonongekere konko
Wina mwa andale opanda mbili yonyansa pa ndale mfana uyuyu,frankly speaking.
@@SamuelThanganyika that's true my bro
Kukanika kupeleka % ya mzanke kungot 1/10 nzovutaso izi? Kapena sakuzzsata zinthuzi, naye wakanika basi sangatenge boma npake amafuna mcp yibwere ku convention banzi lamvuta uyu
😂😂😂 mumafuna amene chani ngati timamva akayankhula???
Ukuyambire campaign yanu kukadyetsa anthu akumachinga please
Sangawine payekha tikapusa mcp akhoza kuzawina,chikufunika ndi alliance basi
Bingu anayimalidza UDF singazawineso mdziko muno pawokhaa
@@kennethnasteve4721 udf ndi malemu achipan
Chaka Cha mawa amene akufuna kuwina alimbikile kugawa chakudya kuti anthu tipulumuke ku mulili wa njala
Takhara tikunena pano kuti andare ndiamodzi ndipo amangosiyana maina chabe, koma pari anthu ambiri zikuwoneka kuti ndarezi tazidziwa pompano ndiye sitimadziwa chomwe tikurankhura koma kuthamangira kutukwana basi.
Ndimunthu wanzeru kulankhula modekha ndamunyadila,ndikanakonda pakhale alliance ndizipani zina
Interview yavuta pang'ono bwana.... Muuzeni Chakwera sanayendese bwino dziko
Atupele wadyadi ndalama za chakwela akilephela. Bwanji kuyankha pa funso la chakwela
Tiuzeni zanzeru apaa osat munenazo ai amalawi simungawapusitse ai kuli 50 pls 1 ufuna unene chani plan yanu taiziwa inu ndi pp mufuna mugawe ma vote cholinga zipani zina zisawine muli ku MCP l know your plan
Achinyamata satatipusitse Ali ndi mcp ameneyu
Why akupanga chibwibwi? ....that shows he is hiding something to us .....
Atupele sungaputse Amalawi chisadziwa anayaimbira mfiti manja
Unfunse kalindo
Musapange matama atupere apa inu ndichipani chani simugakhale pasogolo na ikakhala ya 50+1 bcz chipani chanu n chaching'ono
Guys speech ya UDF siyolimbisa mtima ai UDF tisazayivotere ukufuna MCP to come again in government I can see their plan
Awa utsogoleli mulibe thandizilani MCP poti ndalama mwatenga kale
Mbuzi abambo ako woyamba ananamiza kuti agulira sapato aliyese zilikuti?
Mmmm zamumtima nzawekha choona chili muntima mwawomo
Atupelle wanena zoona amalawi alibe chikondi ndiadyela
Akuluwa tawayezeka, kumenya kugwesa 😅
❤❤❤❤ Boma
Koma inuyo simukukalowa ku wusataniki bwinotu mwina mwalandra kale za magazi
Komatikuyeseni bwana
He is not answering questions
Agulitsa chipani awa ku congress
Atupere timayembekeza kut mutiwuza zanzeru koma mmm mwawoneka kt ndinu nthambi ya MCP 😭
one thing I like about this guy, samapanga nawo politics yonyozana....ndi mfana wa look sharp
Koma akuopsa sakuyakhula moveka olo kudzudzurako bomali mwaphavu ayi
Tupele ndi munthu oganiza za patsogolo
@@MjombaMoosa l am with you big man
Atupere ndiosalimba mtima amafuna zokuphaipha
Ndinayiwala paka munaunikira kuti tizankhe molondola chifukwa enawa azalowa m'boma pofuna kuti abe mwakwijo munatiunikiradi
Akuti upereke malikisi iwe ukuyankha zako mmmm uyu wabisala mmasamba zipita kuchikangawa partyko kutha kwa UDF
😂😂 Mantha poyankha atupele.
Very simple futso hw marks amene mungawapatse achakwera?.
Yankho dololo😂😂
Koma ndipo 😅
Funsoyi ayilephera kuyamkha akudodoma dodoma
Awunope tunyakule
Onyoza makolo ake afe ndithu......Bingu adaba u president wa udf Mulungu adzabweza
Inunso ndi mbuli yophunzila
Komaso awa iye amafuna kuwonetsa ntchito zake payekha osati adzilamulidwa ndi anthu
Ali ndi utsogoleri
Akuthawa fuso lachakwera
Akuzembatu mayankho atupele
Akulephera kuyankha bwino bwino mafunso......uyutu akuzapanga mgwirizano ndi Congress
Atupele sakulephela kuyankha zacha chakwela, koma musaiwale kuti atupele safuna ndale zonyozana koma ifeyo ovota ndiomwe tione muthu omuvotela
Ndipo kwambili thawi zambili samenya kampen onyoza
Yankhani funso atupele
Ndalama muchoka nazo kuti ndi bambo wako mbava
Teroni
Cadet wa mcp iwe atupele muluzi
Atupele amayankhula zogwila mtima koma bwanji sapasidwa mpata kuti alamule?
Amalawi kuyankhula bwino sikulamulira dziko
weyi ndilunga anemeyi sitingamusape upule
Ndazikonda izi
..
Mantha ake ameneo mungalamulire dziko inu ngakhale Mulungu amafuna munthu odziwa mchimene ali kulephera kuyankha funso lophweka
Salary simuzalandila , iwe ndi Abambo ako tagwelani uko akuba inu... You are leopard you can't change your behavior... poorest education than ever during your Father time
Sakuyankha funso
Lolani mwanayu alamure
Awa mfundo alibe adzingopita kumakadya ndalama zomwe anaba bambo ake
IWEO UKANDAKHAL ULINDIFUNDO BWENZ UKUVUTIK CHOCHO NO PAIN NO GAIN
Iwe ndi nfundo zakozo bwanji osakamuchotda chikangawa ukalamulire meina anthu adiye kudya chitedze .?
@@cjaylucky munthu ovutika samakhala ku Singapore, I'm enjoying in Singapore 🇸🇬 bro
Aaaaaah opusa iwe anthu amavutika ku 🇺🇸 ukufuna utiuze chani in life
@@mcsellahntv6896 ine ndi dolo siine kape ngati atupele muluzi
My vote atupere muluzi
Akunama awa. Atumidwa kuti agawe ma vote akummwera kuno nkuona akukana alliance. Akufuna athandize chipani china kuti chidutse.
Chakwela 0/10