CHAKWERA CHINYENGO CHAKO SICHITHEKA ULENDO UNO NZIKA INA YA TCHALENJA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 17 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 78

  • @RitaKainga
    @RitaKainga 2 หลายเดือนก่อน

    Anthu mukuyankhula zoona zokha zokha, keep it up

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn 2 หลายเดือนก่อน +1

    I love you my guy Billy Banda, my brother don't retreat or surrender

  • @mbonilekisebe2286
    @mbonilekisebe2286 2 หลายเดือนก่อน +8

    Abusa akumidima.... Olo nkhope ikuchita kuwoneka... Kuba kupha ndi kuononga ndi zomwe amadziwa

  • @Fanzo-h2l
    @Fanzo-h2l 2 หลายเดือนก่อน +2

    Amayamikira nsi billy malata uyu ndi Billy Banda mwaonanso kusiyana kwake kkkk billy malata ndaika ka small b nda kasmall m koma akamunawa ndaika ma capital letters kkkkk Mr Billy Banda moto kuti🔥🔥

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 หลายเดือนก่อน +4

    Ndipo chakwela akutikhazika ngati dziko lino sikwathum,fumu iliyose yoipa isowe m tendele ndipo chakwela athu tikumudandaule daily ndipo kanyama kotchedwa kachakwelaka mulungu azachigwetsa chimuthu chakupha chakuba chigawenga ndipo mulungu achite naye ndithu muthu otembeleledwa chakwela

  • @lyiemax
    @lyiemax 2 หลายเดือนก่อน

    Powerful talking ❤❤❤

  • @TheboZilinde-tq1gf
    @TheboZilinde-tq1gf 2 หลายเดือนก่อน

    Bwana andiyankhulira bwino ✊

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko 2 หลายเดือนก่อน +4

    Ndimangopemphera mulungu kuti apitirize kusunga miyoyo ya anthu amene akutiyankhurira ntanyiwa, wa bakili muluzi,bon kalindo ndiena onse akufunira zabwino ziko last malawi kuti mulungu aziwatetezera kwa oipawo

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 2 หลายเดือนก่อน

    Kaya mukuti ndinu a billy banda zikuoneka kuti mwadya ndalama za mbili koma pa chakwela athu alemelelapo kwambili koma plz mutsamuyike mulungu pa machimo anu plz a billy banda

  • @watsonmhango8794
    @watsonmhango8794 2 หลายเดือนก่อน

    Amen

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 2 หลายเดือนก่อน +2

    Chakwera wationongera Mother Malawi....Akuti kaya abusa....😂😂

  • @daltonjafali3856
    @daltonjafali3856 2 หลายเดือนก่อน

    Even brother Banda you are a patriot ever

  • @emmanueljelemani4203
    @emmanueljelemani4203 2 หลายเดือนก่อน

    God's judgement is coming...

  • @Fridayasani
    @Fridayasani 2 หลายเดือนก่อน

    Ameen please mulungu watu timenyeleni ngontho kwasatanayu chakwela😭😭😭😭😭😭 amen

  • @LottiAffati
    @LottiAffati 2 หลายเดือนก่อน

    10 million percent biggy awuzen amenewa agalu a mcp

  • @EddenKamanga
    @EddenKamanga 2 หลายเดือนก่อน

    Boza libero baba😊

  • @AishaLeman
    @AishaLeman 2 หลายเดือนก่อน

    ❤❤❤

  • @FloridaMakwinja-eq2ek
    @FloridaMakwinja-eq2ek 2 หลายเดือนก่อน +2

    Chakwera nkhope ndi maso kuchita kunyansa chifukwa chakuba ndi kupha

  • @EfeloYovita
    @EfeloYovita 2 หลายเดือนก่อน

    kodi malawi deffence force sakuona zikuchitikazi? zikutiwawa ife anthu kumangoyang,ana pomwe boma likungoononga ndalama pomwe anthu akuvutika

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂 chakwera sakumva uyu

  • @Mahamudu-q6b
    @Mahamudu-q6b 2 หลายเดือนก่อน

    Yes😢😢

  • @crytoniegrantliffa2431
    @crytoniegrantliffa2431 2 หลายเดือนก่อน

    A bambo inu tisiyeni .........mwatipha kwambiri

  • @ClydeNyasulu-tk6fj
    @ClydeNyasulu-tk6fj 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo kwabas chakwera ndiwakupha

  • @DoricaGoweka
    @DoricaGoweka 2 หลายเดือนก่อน

    Ulemu wanu broo Mulungu atithandize ndithu. Ndipo ine mtima wanga ukundiwawa kwambiri mene Lazaro akuyendetsera dziko.Akutitenga ngati dziko lonse lamalawi ndife anthu akutchalitchi kwake kumatiumilira.

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 2 หลายเดือนก่อน

    Fundo yanu siyinanveke a billy banda

  • @CourageSydney
    @CourageSydney 2 หลายเดือนก่อน +1

    Nice voice ❤

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 2 หลายเดือนก่อน

    Koma nkhopeyi ikuoneka kuti ndi hellodi.chakwera mnthu woyipa iwe uchoke utuluke muboma....

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj 2 หลายเดือนก่อน

    Bille banda ulemu wanuw mulungu adalise inuyyo nkwamasinku osse tiutseni soona

  • @sharifujoe7633
    @sharifujoe7633 2 หลายเดือนก่อน

    Strong word big long life Billy Banda.........

  • @williamyusuf259
    @williamyusuf259 2 หลายเดือนก่อน +1

    Insha'Allah

  • @ChiefJustin-cl8jl
    @ChiefJustin-cl8jl 2 หลายเดือนก่อน

    Ndi anthu ife tomwe tikufunika kumuchosa mkulu ameneyu asanamalize kwasalaku

  • @BeatriceMawala
    @BeatriceMawala 2 หลายเดือนก่อน +2

    Amen mulungu wathu atimenyera nkhondo

  • @johnlameck8366
    @johnlameck8366 2 หลายเดือนก่อน

    Koma zinthu ndiye zikudulabe mmmm tisaname

  • @GeraldMkwewu-gd5eb
    @GeraldMkwewu-gd5eb 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zoona chikangawa mulungu amukanthe fiti satanic ziko lanthu likuramuridwa ndi zigewenga km hule lamec liture pasi udindo osafika nxt year plz azayambisa nazo nkhondo or lyeyo tizamupha ndigalu kwabasi

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zoona zimenezo bro mulungu atithandiza pa chilichonse

  • @FunnyKatchenga
    @FunnyKatchenga 2 หลายเดือนก่อน

    Amen.

  • @EfeloYovita
    @EfeloYovita 2 หลายเดือนก่อน

    a timothy mtambo mu 2019 munasogolela ma demo koma zotsatila zake zinatheka koma mutaona kuti tonse llience sikupanga zomwe mumayembekezela munatuluka allience pano ndizimenezi zavuta tsogolelaniso mademo achoke amenewa mdikanakhala kuti ndili kumeneko kumalawi ndikanadzathamanga nawo zatikwana 2025 ndikutali akangosiila pompa azikadya ndalama abazo amalawi akuvutika

  • @SovietMzungu
    @SovietMzungu 2 หลายเดือนก่อน

    Maiko ambiri avutika pa chuma inu nkhwizi chabe mulinazo mukunyoza chabe msogoleri taonani kachithuzi mukuika kakale contribution yanu it's bias....

  • @LUCIAChambote
    @LUCIAChambote 2 หลายเดือนก่อน

    Mwatilimbikitsa ndipo ambuye atimenyeredi nkhondo

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 2 หลายเดือนก่อน

    Inu chibanzi chakupwetekani koma mudziwe Kuti chibanzi chimene mwatenga kwa a DPP UDF ndi Atupele muluzi zina zimene mumanena zikuonekelathu Kuti chibanzi chakupwetekani

  • @YusufAjiruh-c5q
    @YusufAjiruh-c5q 2 หลายเดือนก่อน

    Za ubusa zinatha awa achikanģawa awa munthu okupha

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi 2 หลายเดือนก่อน

    Ndipo amalawi nthawi yakwana

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 2 หลายเดือนก่อน

    Zoona zake big awa ndanyani aathu

  • @JessicaManda-zm1ug
    @JessicaManda-zm1ug 2 หลายเดือนก่อน

    Amen sure 🙏

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 2 หลายเดือนก่อน

    Guys akazangowinaso chakwera tizangogawanapo ma president basi

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 2 หลายเดือนก่อน

    You always make me happy my brother

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere 2 หลายเดือนก่อน

    Amen Amen

  • @MerryMphande
    @MerryMphande 2 หลายเดือนก่อน

    Ndipo sizithekha ife zatitopetsa

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 2 หลายเดือนก่อน

    Koma tatopa panopa ndi ma cadet zowona kungokhalira kunyoza boma bwanji mumawu anuwo muziyikamu zabwino zimene boma likupanga koma bwinotu mawa mungazagwide ndi bp chakwera akawinaso tatopa nanu samalani banja lanu bambo ngati mwasowa zochita

    • @TrizaGeorge-q8w
      @TrizaGeorge-q8w 2 หลายเดือนก่อน

      @@SlindiryLoveness taona boma ife m,buku lamboni zaziii Kodi bwanji mumaimbila m,fiti m, manja athu akupha asatana mulungu akuoneni nose

  • @allahslave7177
    @allahslave7177 2 หลายเดือนก่อน

    You still calling that guy abusa ??? Really 😮

  • @EliasKawuwa
    @EliasKawuwa 2 หลายเดือนก่อน

    Malawi will never develop chifukwa Cha dyera,nsanje, komaso kaduka, mumafuna munakalanda dzikoli ndi inuyo? Anthu a Nsanje inu,Chakwerayo nde si Malawi? Onse achina Bakili,Peter,ndi ena onsewo sanakhareko ma president mu mudziko muno? Anakakupatsani mipando ndikumadya nawo ndalama bwezi mukubwebweta inu, anthu oipa kwambiri,amene sanabadwire kuno nde ndani? Kalindo, nde naye Anayamba zobwebwebweta chifukwa sanampatse mpando,kuti azidya nawo ,nthawi imene anali mu UTM,ataona zake Chimwendo kuti ku MCP anamuganizira, lero angobwebweta basi,anthu oipa kwambiri inu,mutenge ndi inu dzikoli muyendetse ndi inuyo,mudzikadya ndi inu ndalamazo,tione ngatiudzidzayankhura zanuzo? Mulungu musiyeni akhare Mulungu basi, anthu ankhwidzi inu, one thing you should know, whatever happens on this Earth, God is the one who allows it, Mulungu samva mapemphero anthu ankhwidzi ngati inu

  • @spademwale2952
    @spademwale2952 2 หลายเดือนก่อน

    Dpp inalowera pa window noma lidali la UDF.
    Muli mmadzi. Zopanda pake izi.

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 2 หลายเดือนก่อน

    Chokani inu ndinu alomwe mukuthandizila peter ndi a dpp kut azawine koma ife ayi stikuvotelani ndinu asankho zitsiru za wanthu inu

    • @AlgentChilanga
      @AlgentChilanga 2 หลายเดือนก่อน

      Zabwino ndizimene akuchita chakwera wakoyo ?mwana wopusa iwe

  • @shanlaljith5389
    @shanlaljith5389 2 หลายเดือนก่อน

    Be blessed brother

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 2 หลายเดือนก่อน

    A banda mwanatsowatu ndimskunyadilani MCP yatikwana iyi kuwinatso awa tabwelelatso chipani chimodzi apa tabwelela kale koma bolani pano akangowina 2025 TIDZAKHALA kuti MCP tamvumela kuti Atiphe ndi kumanga padzifukwa DZIIIIII koma mulungu asatisiya nthoka

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 หลายเดือนก่อน

    Kodi abile banda alipobe 😂😂😂😂😂😂😂😂 ndiona gati anawalia nanga

  • @RichardLuciano-x6j
    @RichardLuciano-x6j 2 หลายเดือนก่อน

    Live boss

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 หลายเดือนก่อน

    Yes that's 100percent😢

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 หลายเดือนก่อน

    achakwera ayiwale awa zowina

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 หลายเดือนก่อน

    Awa ndachisilu alibe zelu munthu ozelezeka uyu chidzete chisilu chamunthu

    • @AlfredNazombe-me2ly
      @AlfredNazombe-me2ly 2 หลายเดือนก่อน

      Iwenso mbudzi yamunthu opaka manyi kumaso ulibenso kanthu kom chipongwee thooo kungopasidwa data bs udya data yomweyo mwanapwaa iwetiii

  • @EllenNamulu
    @EllenNamulu 2 หลายเดือนก่อน

    Mau chakwera ali ndimagaz manja

  • @JamesSaidi-rw6ek
    @JamesSaidi-rw6ek 2 หลายเดือนก่อน

    Mau mau , mulungu atimenyere this war

  • @AugustineMwamadi
    @AugustineMwamadi 2 หลายเดือนก่อน

    Billy zimene ukupanga ngakhale munthu amene anayamba wapengapo sangachite dzana wamuyamikira chakwera lero watembenukanso

    • @TrizaGeorge-q8w
      @TrizaGeorge-q8w 2 หลายเดือนก่อน +1

      Inu tamakondani dziko lanu chonde

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi 2 หลายเดือนก่อน

      😢

  • @JonathanMtambo-w6e
    @JonathanMtambo-w6e 2 หลายเดือนก่อน

    You are biased you have. left E nock Atupele is. doing nothing

  • @AggiePhiri-n1i
    @AggiePhiri-n1i 2 หลายเดือนก่อน

    Amen

  • @THOCCOChimbali
    @THOCCOChimbali 2 หลายเดือนก่อน

    Amen

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 2 หลายเดือนก่อน

    Amen

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 2 หลายเดือนก่อน

    Amen