Akaliatu ...inu ndi ife a malawi tidanapo...ndege sinagwe .. anachita kuikola...ndi ndege zingat zimayenda kumwambaku tsiku limene lija....innnuuu ...mutisamale ...Chilima was brutally slaughtered ...how csn a ndege be involved in vulling the vp's jacket,trouser as well as shirt????????????????? How
Komatu kwinaku ndikupembeza mafano...Chulimatu sakumva kanthu...munthu akafa samamva.....khalani ndinzeru.... We are together koma tizilankhula what is sensible
Chihana now you came with a full force than any party, udf and dpp I don't know why they are sleeping, utm aford and small parties let's join osati mapate adalamura kale akumabwelezanso khalidwe lomwe linja we need new system now
Please UTM and AFORD make an Alliance now now!!!!!!
Bravo Enock...
Wonderful speach... ❤
Akaliatu ...inu ndi ife a malawi tidanapo...ndege sinagwe .. anachita kuikola...ndi ndege zingat zimayenda kumwambaku tsiku limene lija....innnuuu ...mutisamale ...Chilima was brutally slaughtered ...how csn a ndege be involved in vulling the vp's jacket,trouser as well as shirt?????????????????
How
Eishiiiiiiii imfa iyi yatisiira mabala osowa otitsuka Ambuye tithandidzeni 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
We need to wake up amalawi please chakwela machende Ake
Eya machende ake
UTM for ever osaopa osafooka
Imfayi ya pweteka kwambili chifukwa Cha lipoti lomwe silikutuluka ndi anthu Ali okwiya
Pakufunika opposition yose ipange alliance
Ndipo kwambiri tu
Ndipo zoona galu awa achoke awononga dzikoli kumangoba ndi kupha anthu.. 💔💔
Chilima mzimu wao uuse mmutende SK
Pangani mungwirizano UTM and Aford pls
I love utm
Amen amen and amen
May His Soul continue to Rest In Peace
SKC 🇲🇼
Komatu kwinaku ndikupembeza mafano...Chulimatu sakumva kanthu...munthu akafa samamva.....khalani ndinzeru....
We are together koma tizilankhula what is sensible
Iwe amene umapembedza mkazi wakowe, ndiye kuti umapembedza fano! Komaso SKC si fano Komaso mapazi ako.
Pajaso tisayiwale kuti anthufe tli ndi zikhulupiliro zosiyana komaso zipembezo zosiyana weather we want or not
@@petertaulo8014 akowo
@@petertaulo8014 nde adzuketu abwere amuombe chikangawa makofi🤣🤣🤣
Exactly. Ndipo anthuwa sakudziwa kuti zonsezi zili ndi tanthauzo lalikulu kwambili kuposa mmene akuganizira
UTM Mulungu akutsogoleleni
More fire UTM 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤❤
Under whose directives? Tilikulira basi
Tapangani alliance inu
Chihana now you came with a full force than any party, udf and dpp I don't know why they are sleeping, utm aford and small parties let's join osati mapate adalamura kale akumabwelezanso khalidwe lomwe linja we need new system now
Kkkkk afford yotha kaleyi
Ndipo we need new party
Please tipangeko kuno Kwa bvumbwe please ndimewomba
Pangani alliance inu tizakuvotereni
Infa Yosaiwarika mmm
Ameen ameen
Mmmm zopwetekatu
Ife tili komweko komano chakwela asiye kuchosa malikuru mmaboma ena kumapititsa kulilongwe Ngati ali dolo apange chitukuko chatsopano komwe akusamutsila maukuruwo
UTM. and. Afford creat an alliance please
❤
Osafoka makosana kungatalike bwanji kuyera kunja
Please
Zoon koma
Mulibo amayi
Mahule inu
Hahahahahah chizeleza iwe ,,
Pathako pake uyo
Waiwala uhule wakwanu wakumtundu , amanuso muwauze zauhulezo
@@MzadziWanga simulowa mu boma mungoyendela yomweyo yamakandulu.
Ma ARV'S amene ukumwawo Mesa unatenga ku uhule komko!
Uthenga wanga ndiwakut a utm ngat mungapange alliance ndichipani china musankhe mosamala osati zimfiti ayi zikuphani zikomo