I love kwagwanji special...... 💪 Uyu wadzidziyu amakhala ndi katsabola kabwino..... Big up TTV big up kwagwanji team .... timakunyadirani TTV ndi #1 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 ng'alulayzation.....💪
We are always proud of you gentlemen. Talking the truth where things go wrong is what we need to do as a country. In this country, no one is above the Law. Everyone needs to observe or obey the Law regardless the position we are holding in our respective parties or institutions .
Ndyee mwatii maudindowa tisamansokedxe nawo mabanja awa2 etiii Kod alipoo wina akupanga etii kma program ya kwangwanji ayiií idabwraaa nd2 welcome, welcome Brian Band n friends kumenekooo
Iweyo amene ukuti Brian ndi Ndevu za Mwai apange chao chipani ndiwe wa tsoka ndipo ndiwe mfiti do u think what MCP mchipaniso pano kapena weapon of killing
Koma mwangaluka Akulu akulu More fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 we all love you guys well done ✅👍 chawonamuzako chapita mawachilipaiwe Anayiwala kuti malamulo amaphamwenewowapanga lero siyizi zafika kwawo ku MCP , more 🔥🔥🔥🔥🔥🔥😊
MCP is not Malawian. Why do you expect them to behave like Malawian servants. They're Western Servants. Mabwana awo ndi Azungu, osati Amalawi. Wake Up...!!!
Kukondera kwa times. A mcp kuwaitanira legal expert kuti amasulire malamulo koma akakhala a utm ndi dpp ayi? Anthu amadalira inu ku bvetsa ndi kuphunzitsa zandondomeko ndimalamulo adziko to bring about peace in the country Ndite zomakhala apa kuseka a utm mukudziwa kuti kuli malamulo amene akuyenera ku tsatidwa mmalomwake mukungowaseka ndikumapanga ma programme omangowaseka ndikuonkhetsera moto to split the followers. Ndebvu zamwai fears mcp, aggression yake yonse imatha. He is good at blocking mcp questions fro brian. Brian is chairing this programme, but ndebvu has taken over to prevent brian from asking his usual questions. He was even trying to control the direction for the legal expert. Pankuku sapanga za biaszo ai.
Penso a Ching'oma ndi a Kezzie Msukwa mukutichitsa manyazi mpaka mukaderere court? Kodi Vitumbiko Mumba akukuopsyani chani? Musokonezatu chipani I tell you
This program is very powerful and sensitive if the president can watch this we can build a better malawi❤
We missed you mr Brian Banda welcome back mumativetsa kukoma, much love to you guys you are really son's of the soil
Ose amene akanidwa angotuluka MCP akalowe chipani chamakandulo
I love kwagwanji special...... 💪 Uyu wadzidziyu amakhala ndi katsabola kabwino..... Big up TTV big up kwagwanji team .... timakunyadirani TTV ndi #1 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 ng'alulayzation.....💪
We are always proud of you gentlemen. Talking the truth where things go wrong is what we need to do as a country. In this country, no one is above the Law. Everyone needs to observe or obey the Law regardless the position we are holding in our respective parties or institutions .
We are proud of you Brian with this program hope Malawian will open there eyes it shows that next term will be worse than this if people vote for amcp
I admire the freedom of speech that Malawians portray on media. The democratic principle at work.
😂😂😂😂 ànyàmàta ínuyo ulému wanu ndimkàonà ngat mwadyà chibanzi koma ayi ndipo chilungàmo mwalankhula apàchi chikhozà kukonza malawiyo sure ❤❤❤
I really appreciate Mr brian banda you're doing a fantastic job ❤
Nkhani zanu zimakoma chifukwa mulibe bodza koma zoona zokha zokha I like watching you guys keep on doing the good job...
MCp singayendese Dziko, Anthu awa kwawo ndi kumpha kuba ndi kuwononga
Mwachidule satana
Ntchito za Lucifer zimenezo
Nkomwe nkomwe asatana a ndevu ndi azikazawo achina jezebel 😅
Osanyengelela powayankhula anthuwa we love you guy's keep it on
I salute you guys... keep it up saying the truth...kung'alulara basi...
Very nice guys kuyakhula kosaoa🎉
Ndimakutsatila banda kwamafuso athu amalephera kuyankha maka wochokera kuma yudas skaliot mcp
YuDAS AZIMANGA YEKHA
Powerful guys....its democracy keep going
Zikomo atate Chifukwa m'maona mizodzi Yathu
Palibe woposa lnu namalenga m'maona chichichonse 🙏🙏🙏🙏
Kkkkkkkkkkkk kma BRIAN ukhalikeee mpaka SHYAAAAA udamchedzaaa nayoooo BUSHIRII kkkkk. Umatha
Abundantly exceeding grace my legends🤗
Ndyee mwatii maudindowa tisamansokedxe nawo mabanja awa2 etiii Kod alipoo wina akupanga etii kma program ya kwangwanji ayiií idabwraaa nd2 welcome, welcome Brian Band n friends kumenekooo
Very unfortunate indeed .These people rush into conclusions before proper grounds. They always think they are above the law.
AMBUYE AKUTIYANKHA MAPHEMPHERO ATTHU KUKHALA KUUNDUMUKA KWA MCP
The same MCP used Nankhumwa to confused DPP but DPP respected all courts judgements until time came for Nankhumwa to be expelled.
Eee Mr Msiska ,, true talk ,, well done
A Chakwera alibe mawu oti angamveke mchipani cha mcp. Iwonso was hand-picked
Rules and laws of the country must be respected at all cost
Great Brian
Uthenga wanga kwa MCP. Tisamve kuti mwamusowetsatu Bandayu. Chigamulo apeleka ndi aCourt. Tikukuonanitu
Mubwereso ndi ya report ya ngozi ya ndege kuchikangawa kuja ma guys
Brain Banda and the entire team keep it up. You are teaching politicians so that in the future if God allows things will work. Be blessed
TTV is the best in Malawi. Sanyengelera
Iweyo amene ukuti Brian ndi Ndevu za Mwai apange chao chipani ndiwe wa tsoka ndipo ndiwe mfiti do u think what MCP mchipaniso pano kapena weapon of killing
Anapha chilima ndikupanga kidnap DIrector of public prostitution
Ilike you guys mumadzuwa kusanthula bwino a Malawi ambiri tili mumdima
Mwazi wambuye yesu ndio and this song mbuye msalore pamene tayasa nyali Santana sazimisenso
Lets go & demonstrate u will c to it that people no longer need the party
Mr Banda 😂😂😂😂akuti kafungo kaja sikanathe ka congelesi😂😂
A Abanda ng'alulani mcp more fire
Program akapanga host ndi Brian Banda ma viewers amachuluka pamenepo a TIMES mudzifuse😂😂
Koma mwangaluka
Akulu akulu
More fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 we all love you guys well done ✅👍 chawonamuzako chapita mawachilipaiwe
Anayiwala kuti malamulo amaphamwenewowapanga lero siyizi zafika kwawo ku MCP , more 🔥🔥🔥🔥🔥🔥😊
Zopanda ukulemba kupanga attack brian ndi nzake mzimu wa SKC ukudzuzani anthu akupha inusimkanakhala mmboma opanda SKC RIP
Wisdom guys...bravo!!
God bless you Gays 🎉
Well done 👏 guys
Koma a MCP mwapase thawi azazipha okhatu awa akaluza chipani chifukwa matama akupangawa tsiku Lina azapanga ena
Lero kuvuta ,,kuphatikiza pa a Msiska ,,pabwera Brian
Mwana amene amathamanga kukanena sikuti amakhala osalakwa 70% amakhala ndi omwe alakwa 😂😂😂😂 koma chikangawa team mukhale serious
Pajaa pule anati chilichonse chomwe akuchita achipani iwonso akuchita nawo
Mumatha kucheza ❤
Zoona ndevuzamwai amalankhura bwino akakhara side yauku,
Koma mwati enawa anali oshota 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Congrats
Mbuzi za MCP zimatengera malamulo kumanja mwagwanayo fotsek!
Kkkkkkkkk chikangawa team mlimbuli zokhazokha
The President has no say ku chipani cha MCP nchifukwa chake sakutha kudzudzulapo zomwe zikuchitikazi. 😏
MCP is not Malawian. Why do you expect them to behave like Malawian servants. They're Western Servants. Mabwana awo ndi Azungu, osati Amalawi. Wake Up...!!!
Kukondera kwa times. A mcp kuwaitanira legal expert kuti amasulire malamulo koma akakhala a utm ndi dpp ayi? Anthu amadalira inu ku bvetsa ndi kuphunzitsa zandondomeko ndimalamulo adziko to bring about peace in the country Ndite zomakhala apa kuseka a utm mukudziwa kuti kuli malamulo amene akuyenera ku tsatidwa mmalomwake mukungowaseka ndikumapanga ma programme omangowaseka ndikuonkhetsera moto to split the followers. Ndebvu zamwai fears mcp, aggression yake yonse imatha. He is good at blocking mcp questions fro brian. Brian is chairing this programme, but ndebvu has taken over to prevent brian from asking his usual questions. He was even trying to control the direction for the legal expert. Pankuku sapanga za biaszo ai.
MCP ikuyenda ndi mwazi 😢
Mumakwana guys M c p yikutengachirichose ngati chawo ndiye agwanayotu
Achakwera akudalira kumbera ma vote
Penso a Ching'oma ndi a Kezzie Msukwa mukutichitsa manyazi mpaka mukaderere court? Kodi Vitumbiko Mumba akukuopsyani chani? Musokonezatu chipani I tell you
Okay
Onse olimbana ndi MCP ngati chipani amatha okha nkhani ndi ngodya zinayi zija anapanga,taonako magulu osiyanasiyana koma pano akuchita kubweranso ngati alendo,nkhani kusasunga ngodya zinayi
Go deeper Mr msiska ,,ndazikonda .akumbutseni nao anangochoka ku mpingo nkuka gwera kuchipani ,,,mwina aiwala
MCP gule kwawo ng'ona zosekelela zikuchoka mboma
Chikangawa president sangapange decision why osewo akupanga zimozi RIP SKC Tikudikila report la ndege
Report will never come until mcp is in opposition...shuwa
Ngati boma likukhuzidwa kulibe zoti mumvako zosatila never
Siska,kuyankhula kwabwino auzeni andale athu eish!!!!!!!!
End of mcp
Achina yodasi awonekera ng,amba , kupha kuba ndiku wononga
MIZIMU ija imapengetsatu ikakukakamila
But guys chonde pitiliza kuteteza Malawi chonde musagulise Malawi agalu a mcp atiwonesela kuti mwana wanjoka ndinjoka yomwe Kodi azikhale anali ndani mmene mwakambila kuti achakwela anali kuti sikuti anali abusa koma Malawi
This pple are still in darkness 😂
I lv you all
Anyamata inu mumakwana
Anthuwa salemekeza malamulo
Mumata kusantula, pitirizani kutsegula mitu kapena kusinta maganizo a Amalawi ena nkusata chofunika kuti dziko lipite patsogolo.
Brian please don't eat baz please tikudalira inu kumeneko
It's true that
The down fall of mcp
Kumalawi kulibe Ufulu wachibadwidwe
prof
Izi ndiye nkhani zanj kod amalawi?
iwe ukuona kut ndi nkhani yanji?
Go deepest
Akufumba asokoneze. Malawi nchifukwa afuna aziditha mavotedwe opusa Kwa basi nkhani akufuna azabele sichina please tatopa ndikuvutika aMalawi😠
ziko lathu limapangisa manyazi ngati Lina zaza ndi mbuli chosecho ai ndithu.
Tisamafinyike dziko ndilathu anthu MCP zigawenga
Ya Haman Tchayani kkkkk koma Brian mumayitha
We are just watching waiting for the vote that's all we are tired with this
Ikomo andevu zamwai mwayakhula bwino 1:05:23 😊
Koma panopa ndie kwagwanji mbuzi zinazi zinali zama 1sawu pano eee
Chifukwa chani anthu 20 akuwaletsa kuti asaimire chonsecho ndi aMCP?
Brian Banda ndazanu a ndevu zamwayi tapangan chanu chipan Brian Banda president ndevu zamwayi vc, kutokota mpaka thukuta mkamwa, ndiye zakuvutan
Malawi
Mcp ose ndiopusatu ndiye mkana akuyakhula zopanda mutu
🔥🔥🔥🔥
Mawu aphavu kwambili andevu zamwai
No MCP in 2025 no more
Anthu wopondereza akuwona ngat nthawi ya kamuzu inu, kunja kunacha dzukani ngat mukanagona
Tili mbuyomo kukusatilan ulemu wanu pitilizan kukhoza dziko lathuli zaonjedza izi
Asaiwale analowa mboma ndi 1 pin ya Chilima pano kulibenso imeneyo
Guys mmatimilira kundimvesatu kukoma inuyo
❤❤
Vuto amalawi sitisiyanitsa politics ndi government
Mbwitix mwati😂😂😂