Jealous down , this guy is doing wonders and may God continue blessing him Komansotu Mr Chakhaza mmabhebhetsa interview lol !! Ayi taphunzirapo ziwiri,zitatu 👌
Pakutha pa zaka 10 chiswe chizasowatu zikungofunika zowetazo kumazipanga multiply basi otherwise the other side will be affected monga ine okonda kudya dothi lachiswe 😂😂😂😂
Unbelievable a longosi. Zoona mungapite motero? It's like I am having a bad dream that I will wake up to discover that it was just a nightmare. The great news is that in the 2 years you went back home, you have made a great impact in many lives, not only at home, but even here in the USA. We mourn with the family for your untimely demise. Your legacy will live forever a longosi. I am 💔
Kuphunzira ndiye kumeneku munthu akupanga zake uyu akudyereratu big up Mr sapemba
Sleep well brother Matthews, till that resurrection morning on that beautiful shore,when the dead in christ shall rise from their graves.
Chamba ndi mowa sizoipa... I like the boldness in articulating in the things he believes in.
Thats nice interview
Dr Mathews Sapemba
Ndakunyadilani kwambiri Mulungu anakutumani inu
Pitilizani kuthandiza osowa
Jealous down , this guy is doing wonders and may God continue blessing him
Komansotu Mr Chakhaza mmabhebhetsa interview lol !!
Ayi taphunzirapo ziwiri,zitatu 👌
"ndimadana ndi umphawi" ndagwa nawo mchikondi mawu amenewa.Mr Msulira ndinu anzeru............
Number one cruise 5 of the year 2023
Patriotic getto boy, I have learnt a lot from u, naneso ndikutsakula ka poultry kanga for a start
This is a very very great man, I salute you big man
I enjoyed watching this interview.✌️
Apa sizinayende, imfa kutenga anthu oganiza bwino anzeru.... Rest in peace sir
How I wish RIP means "Return If Possible"💔rest easy uncle 😭😭😭😭
And he smokes weed ..nzeru😂👍
Smoke weed yes
Ndi Pupa 😂😂
Mwina amachilimanso yekha😂
Pa chambapo moto kuti buuu 😅😅😅🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼
😅😅😅😅😅😅
Zachisoni kuti mkulu ameneyu watisiya dzulo pangozi ya galimoto 😢😢
Ndipo ndakhumbila ,ndnkhumbolanga kuphuzira zinthu izi,ndpo ndne osilira
Ahhhh komanso imfa ilibe luso. Matthew Sapemba RIP
Wow eeeeeeee awawa ndi adolotu mpaka kuweta ntchentche
Zbirimbiri mmalawi.mino timati black soldier fly
Rest in peace my teacher at Kaphaizi primary school
😢😢😢😢
Akatunduu!!
Joab l love your voice and freedom man 😂😂❤❤🔥🔥
So sad, may his soul rest in peace
Rest in peace boss matheslws
Koma sopano ajambulayo nsimayo sikumukhuza?
Pakutha pa zaka 10 chiswe chizasowatu zikungofunika zowetazo kumazipanga multiply basi otherwise the other side will be affected monga ine okonda kudya dothi lachiswe 😂😂😂😂
Mzimu wake uwuse ndimtendele,tizasowa luso lake
Koma mmene mukutchulira kumudzi kwathu ku Kapiri
Sizinayende,RIP sir ..😢
Ichi nde chipembedzo chathu chenicheni chachikukda munthu sunganene kuti ndiwe opephera uko ukunyoza chikhalidwe chako zimayendera limodzi muzimu ya makolo athu igone bwino
Rest well brother till that day
Mr Chakhadza help me to link up with this aspiring man if possible please
We have lost and heaven has gained.RIP
Sleep in power alamu you will be greatly missed
May his soul rest in eternal peace
kuzala mitengo, kenako kuzala mitengo, kenako boom wakwatila mchinese
legend
Macheza wanu aluyenda bwino zedi dala 😂
Cruise 5on fire🔥
Wow zopasa chindwi
Regassy ndiyofunika
May his soul rest in peace
may ur soul rest well Mr sapemba
Kuchita manyazi ndi chakudya......?
Joab at kod inuso mudya nawo mesa kuno mkwanu
Nice
Kwathu sipadziko, rest in peace.
Iiiiiiii Koma mwadya chi Malawi Kusilila
Unbelievable a longosi. Zoona mungapite motero? It's like I am having a bad dream that I will wake up to discover that it was just a nightmare.
The great news is that in the 2 years you went back home, you have made a great impact in many lives, not only at home, but even here in the USA.
We mourn with the family for your untimely demise. Your legacy will live forever a longosi.
I am 💔
Kungoti ukangojhalitsa kunja, kenako nkupanga zobwelela kumudzi kudzakhala, just Kno that kumanda kwayandika..
Just stay there,
Rip Dad 😭😭😭💔
Kodi ndiye mukuti mkulu ufunikilayu zakhalanso bwanji koma guys noooo 😂
Rest in peace uncle
Zokomatu izii
Massive 🎉
Ine ndasangarara nazo koma ndingakumane nawo bwanji plz help me to meet this gay
Gay ???
Rest in peace mr sapemba
Koma Joab ahahaha..mutu wake unathawa...😅😅
Eeshii koma Joab ayayayaya
apapa mwasangalala
RIP Bambo sapemba
Uzimu mumpingo wa Aaron
How can I get the number of Mr sapemba
Beautiful
Sopano ukudya wekha nanga camera man yo
So nice
Ati chikondi chake chinayambila kumitengo
Dzizili ndichani ?
Kwawo Kwa agogo Anga uku mayi amayi Anga 😂😂😂😂
Kodi uli ndi contact ya mmodzi wa gulu limeneli
RiP #Mathews Sapemba
😂😂😂Koma ajoab chakhaza inuyo anakonza aaa
Anakulira pa farmer
Koma camera man mwamumana
Rest in peace
Ndazikonda
So sad kumva kuti Mr sapemba is no more.mmmmmmm
Cruise 5
AKuti kubwera pano padziko lapansi
Rip Sir
This man is a Rasta
Kodi joab nyimbo ili yose umayiziwa ??
Rest in peace. Mathews Sapemba
Anamwalira?
Imfanso inu mmmmm
Muli nzeru
Mmmmm ajoab kugupulirakkkkkkkkkk
Dolo
Game tembenu
It's weed for me...
😂😂😂😂 km joab athu umakumana nawo iwe
Tidye zinziri basi
Asset
😂😂😂😂
@Joab Frank Chakhadza
please connect me to this new sense
Game tembenu