Aaah iweo Joab ndinanena kale za iwe and zodiac sindimamvela koma munthu amene amandisangalasa kwambili ndi iweo basi makamaka ku program imenei umatha to be honest.
Koma mwa band yonse awo azimaiwo akumveka mopelewera akusiyana ndiamene anaimba amamveka pa real song pomwe Loyd komanso azida akumveka pure popanda chosinthika Ndie chonde ma vocals pa live adzimveka mmene akalewo amamvekera that's why there is practice of voices
You did a good project for us Lloyd may the good Lord continue using you
Aaah iweo Joab ndinanena kale za iwe and zodiac sindimamvela koma munthu amene amandisangalasa kwambili ndi iweo basi makamaka ku program imenei umatha to be honest.
Amen! Sachedwa safulumira amachita muthawi yoyenera Ambuye, ndipo akachita umakhala ndi mathu wa umboni❤❤❤
Zilibwino brother and God bless your ministry
Nyimbo Za Mr Phiri and the happiness voices muli kuzodza
Kwambiri
I like the song sachedwa safulumira ❤
🎉🎉 Ulemu wanu guys we are still enjoying your music
Great job 💃💃🎹🎷🎺🎸🪕🎻🎤
Lloyd's music has been my favourite since way back...Joab umatha
Owoooo yesssss 🙏🙏🙏🔥🔥 pemphelo silinama mwalimbikitsa moyo wanga
Ajoab mumakwana you stand for us
Live ngat cd,,,amatha Lloyd and the happiness
Joab know his work professionally,he loves his job
nice songs watching from Zambia
❤love it so much
Beautiful
Great🎉 amatitsitsimutsa
That's powerful may God continue to bless you all in Jesus name.
Congratulations 💐
Good work Joab
❤❤ I like this song Omkana yesu sakalowa
So nice ❤❤
Joab respect you bro
Nice ❤❤
So nice
Umatha joab bravo
Mwandikumbutsa kale pa franch culture center. Muli bhoooo
Ndipo inu kale lokoma😊
Inu nanu waulura chani, zaka 9 ndimwana kwambiri wangokhala kuti alindi memory yabwino..kukakamula nkhani bwanji hiyaaa
Koma Joab umatha
Nyimbo za ziwanda izi
Ichichi mukwapula malume❤
Nice Joab
Koma Joab eish ndiogulugusha
Joab 🎉🎉🎉
Sasha joab, amatha kucheza
Komatu eeee loyd phiri your still strong kuduphako kundiposa ine obadwa 1998 yo kkkkkk
Koma umatiimilira lyd
Excellent watching from Johannesburg Mr Phiri is very honest person amaziyika pa mbalambanda
Inunso mumalemba khani sosiyana ,kuulura ndekuti chani ,Munthu akunena za uchimwana wake kuti anasuta chamba kuti apenge ali wachichepere,inu mukuti waurura ndechani,zauusiru basi
Ndpo chilungamo
Akuti amafuna akope anthu mcholinga akhale ndimacomment or ma viewers ambiri
Koma mwa band yonse awo azimaiwo akumveka mopelewera akusiyana ndiamene anaimba amamveka pa real song pomwe Loyd komanso azida akumveka pure popanda chosinthika Ndie chonde ma vocals pa live adzimveka mmene akalewo amamvekera that's why there is practice of voices
@@StatesmanPartsonkkkkkkkkk
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Nyimbo zosafwifwa izi
❤❤❤
Powerful 💪🔥
Zosangalatsa izi,msilikali wadziko kuimbira Mulungu😅😅😅
Munthu amene anakupatsa five hundred kwacha sukumukumbukila a u serious dude
Koma mlaka nde number 1 kusuta chamba pa oimba palibe angamake🙄🤣🤣🤣
Mmmm❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Amkatiyendetsadi mmidzi kwambiri ndipo timakhala gulu
Amen
Kma chakhaza eshiii
Kod aku user et?, .akufiila.mutu okha😁😁😁🙌 kapena ndinjalai kut yandiseka maso
Mumatha guys
❤❤❤🎉😂
Koma joab umakwana iweyo 😂😂😂😂
😂😂😂😂 ajabu kuvina kumeneko kapene kugong'ola😂😂😂😂
Creator your own content
Yaaa, kukubwelaku tiyamba. Tingopeza katundu ojambulira basi
Amen
❤❤❤
Amen
❤❤
❤❤❤❤❤❤❤
❤❤❤❤❤
❤❤❤❤
❤❤❤❤
❤❤❤