Tamuvani Zikhale ng'oma a MCP anthu awa aphana okha okha

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 18

  • @Sammy-vb1ed
    @Sammy-vb1ed หลายเดือนก่อน +1

    Akukanika kuyankhula nfundo zonveka, apa zikuchita kuonekeratu alephera ndipo ndiolephera komanso tsankho komanso nkhanza kuphatikiza katangale.

  • @Fatima-f5c
    @Fatima-f5c หลายเดือนก่อน +1

    Uyuuu ndi chisilu ndithuu

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi หลายเดือนก่อน +1

    Nazikolamawi likuzuzika anthu ake ndiinu sankhani anyuwani mwina koma Aaaasaa fisi ndi fitsi sangakhale mbuzi😂😂😂😂😂

  • @Sammy-vb1ed
    @Sammy-vb1ed หลายเดือนก่อน +1

    Guys ndalamazo akakupatsani idyani osazikana, koma osamuvotera kape ameneyu.

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz หลายเดือนก่อน

    Kkkkkk Malawi chikangawa party 😂

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus หลายเดือนก่อน

    Kodi ameneyu ndikulumala eti
    Kulankhula kosalana ngkhale kuchipani?he's a fool...nanga ngt akudana okha okha,nanga amalawi....

  • @LiamTennessee
    @LiamTennessee หลายเดือนก่อน

    Ngati mukufuna Kuti aChakwera asavutike ndi campaign this is the plan, Pali nyimbo imene ndidayimba ine Liam Tennessee imene ikukamba Za ubwino wa a chakwera,, inu a MCP tengani nyimboyi when ever you are campaigning muziyiwulusa pa MBC,Times,zodiak etc, aliyense amene angamvetsele nyimboyi ndithu ndithu azavotela MCP,

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm หลายเดือนก่อน

    Km ali ndi mau onyasa kwambiri uyu ndi munthu kapena chilombo

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d หลายเดือนก่อน +1

    Koma khumba iyi

  • @BlessingsNyirenda-ru7ss
    @BlessingsNyirenda-ru7ss หลายเดือนก่อน

    Uziyankhula zoti ife tiziva kut munthu akuyankhulira mukamwa koma ayi ndithu

  • @user-hx6jl2jq9j
    @user-hx6jl2jq9j หลายเดือนก่อน

    Ukulankhula chani kamajekete sizili unveka panyo pako

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo หลายเดือนก่อน

    Galu iweyo

  • @ChristianMtambalika
    @ChristianMtambalika หลายเดือนก่อน

    Km munthuyi mutu wake umagwira zimenezi ndare kapena kusowa zokamba sukulu Yake iti kapena or kukalibu akadameko aaaaaaa takamba mfundo iwe kkkkkkk zowagwira anthu mtima maganizo ndalama bas wandikumbusqtu bukhu Lina lake england wanga go back to school uyunso qbwerere coz undunawu walowera certificate ya 8 kkkkk km kadothi kkkkk

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz หลายเดือนก่อน

    Ah ah nanga chackweratu anachoka ku chipiku ndi assemblies

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p หลายเดือนก่อน

    Zosathekako

  • @MerryWayson
    @MerryWayson หลายเดือนก่อน

    Ziphanani bas nokhankha

  • @Fatima-f5c
    @Fatima-f5c หลายเดือนก่อน

    Uyuuu ndi chisilu ndithuu

  • @ChristianMtambalika
    @ChristianMtambalika หลายเดือนก่อน

    Km munthuyi mutu wake umagwira zimenezi ndare kapena kusowa zokamba sukulu Yake iti kapena or kukalibu akadameko aaaaaaa takamba mfundo iwe kkkkkkk zowagwira anthu mtima maganizo ndalama bas wandikumbusqtu bukhu Lina lake england wanga go back to school uyunso qbwerere coz undunawu walowera certificate ya 8 kkkkk km kadothi kkkkk