Olo Anthu A Ku Kasiya MCP Sakuyifuna - Comrade Ntanyiwa
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 7 ก.ค. 2024
- Comrade Ntanyiwa, speaking on Nyasa VoiceBox, suggests that the MCP is becoming so unpopular that even his kinsmen in Kasiya, Lilongwe, are prepared to vote him out.
Comrade Ntanyiwa polankhula pa Nyasa VoiceBox akusonyeza kuti chipani cha MCP chayamba kusatchuka moti ngakhale abale ake aku Kasiya mu mzinda wa Lilongwe ali okonzeka kumuvotera.
God is able Mr comred❤ 🔥 we are the winers
Bakili Muluzi amayenda yekha wopanda Asirikari nkuma wumba zidina, uyu chakwera m'busa wonyenga wakupha anzake ayende yekha tiwone Kodi kampeni akachitira Kuti?
Ruto and chakwera mulibwanji
May Allah guide and protect all the real freedom fighters from evil people
Tadzuka bwino ka inu comrade ntanyiwa, mdzenjemo agweramodi okha, adzimangiliranso ngt yudas chifukwa mizimu ya anthu omwe anawapha aja idakayendabe pa dziko pano may the almighty God continue to protect comred you wherever you will go❤
Amen Mr my god protect you
May God keep you safe comrade no weapon formed against you shall prosper
Good Messnge Chakwela you mast go
Our gentle men comrade umatiimalira panakati pakhale anthu 20 a Malawi Malawi sibwezi chakwera akutitola ngati akutitolelamu
That's the great Original Mntanyiwa ❤🎉
Amen 🙏 mulungu amene ndimampelela ine alindimoyo.
Okay takumvani kuti simukupezeka pa FB
Comrade mumatiyimila❤
God bless you 🙏🙏🙏🙏🙏
Alo akanachoka mpompano mcp ndiyakupha we don't need mcp any more 😢😢 😭 we are tired if this manyi yeniyeni
Mau akulu big Allah protect like always
Angafune ndani machende machende ameneyo uja
Emen Mr comlade
Our freedom fighter 💪 🙏
More fire Ntanyiwa❤❤❤
More fire ntanyiwa
Mutima mmalo ife a Malawi tili nga nga nga pambuyo panu, asiyeni nasatana awa
Yet akunka nagwetsa kwacha koma anthu oyipa ngati awa mmmmm timangokunva kuti mcp ndi yoyipa its true aaaaa yalanga anthu kotheratu
Aaaaa wabodza momwe tagulitsira fodya kuno ku kasiya tingakane chakwera akulu inu bodza mudzafa nalo
Amen
More fire 🔥
BODZA ILO 😂😂😂😂😂😂😂😂
Komaso atanyiwah Kuno ku balaka akungo tinamiza aid kulibe ndine Muhammad'yasin
Za ma lD zo polembetsa ma vote ai. Kunonso anthu ambiri Sitinalembetse ku CK
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa God bless you sir
Yr days r numberd ulibe ntendere ukuyenda mojowajowa
Fire 🔥 🔥 comrede
Zoona zooona
From Malawi
Good msg ❤❤❤
Ndipo ntanyiwa 2025 azakhala pompo kumaonelela mcp ikuluza, God bles you ntanyiwa
Chilungamo chiyende ngat madzi
Chilungamo zibthu sizilibwino pa Malawi, a Chakwera ndi MCP yake paulendo 2025.
Ndipo auzeni amve , dzenje limenero ndilao a MCP agalu achabechabe mulungu sangakutae mtanyiwa ndipo mulungu azikutetezani
Comred inuyo ndinu mmalawidi chifukwa kenakalikonse ukukaziwa ndimakhulupililakuti inuyo mwatumidwandithu ndinzimu wothandizila kulilakwa amalawi
Zoona pension akutizuza nayo.Ikambe ñthawi zonse
Ndipo sitikuchifunadi ndipo tikuona kutalika 2025
😊
Ndipo agwelemo okha muzina la yesu athu oipa asatana
Mumafunini kumakakhara ku malawi koko ngat bon kakalindo zikakharabwino mukuyakhura nose mulilimozi kumeneko chokani
And we will never and support UTm akufuna aputsitse anthu. Ife ndi a dpp, komaso udf. Sitizakujhulupilirani Mai kaliyati zokhazija munayankhula ku maliro a soja lusius banda, we will never trust you again mama. Andale ndioopsa.
Chakwera akanakhala wa nzelu za umunthu akanangopanga resign chifukwa wether he likes or not walephela kuyendetsa dziko waba pakwana
Achakwera siyani yimeneyo simbariyanu utsogoreri wakuvutani zanu zada apa kalapeni m'charichi kutimunalakwira kumwamba basi
Ma pension anthu Sakupatsidwa
Chakwela a choke atikwana palibe chimene akuchita zamanyi
Chikungondithela bundle yanga chitsiru ichi
Zazii zenizeni kusowa zochita dzinamizanani chotcho mukhumudwa 2025 chakwela sakuchoka
Chakwera must go
Its true
❤❤
Chakwela must go we don't want you
zoonad ationjeza azipita
Auze amvemvemve
Achakwela mwadzka bwanj
Chakwela mbudzi ya munthu
Auzen
Mcp yakupa yangasa
see
Mcp yatha
😂😂😂😂😂😂😂
Ine ndi waku kasiya koma chakwera ndimamukonda koopsya Inu kasiya yake mukunena ya kwa Goliati kapena
Choka iwe wanyawu kangwele uko ndi buzi limodzi ndi changwera wakoyo
😢
Inunso ndiomvetsa chison ingokhalan chete
Who cares?
You're a big liar. Konseko kufuna kukokera mavotii kkkkk