The problem with Comrade Timothy Mtambo is that He's after Money so He has nothing to do with the development of this Country. He started as an Activist while His aim was to benefit something.
I also don't trust Timothy but if I overthink about the dearth of SKC makes me think that maybe Timothy lost direction because of the ruling gvnt. His mouth was shut by other elites who takes Malawi to their own hands
God, how many times have we consulted God? How come that God fearless countries are more progressive than Malawi? Do you think we really survive death to claim heaven?
Pempho langa ndilakut ngat chilima anaphedwa ndi anthu ndikut mzimu wake uwakathe ndipo asowe mtendere mpaka kare uwakathe
Imfa ya chilima mpaka lero ikumandivetsa mutu 😢Rip legend
😢😢😢😢😢
Nanenso
I still don't believe
The problem with Comrade Timothy Mtambo is that He's after Money so He has nothing to do with the development of this Country. He started as an Activist while His aim was to benefit something.
I also don't trust Timothy but if I overthink about the dearth of SKC makes me think that maybe Timothy lost direction because of the ruling gvnt. His mouth was shut by other elites who takes Malawi to their own hands
Ndi galu kwabasi ameneyi Timothy Mtambo
Timothy mtambo is a betray cos he was betrayed the who malawians some years ago I really don't like this gu
I love this brother but dyela
Zikomo mtambo
THE best way is you to prepare yourself with God. So that you are right with God.
God, how many times have we consulted God? How come that God fearless countries are more progressive than Malawi? Do you think we really survive death to claim heaven?
For the first time I agree with Mtambo .Sitimayenela kusangalala 6th July. Palibe chikukoma
We're still crawling to get there!! Rest in peace Dr SKC, UTM is a movement
That's too bad,and it's evident kuti chilima anachita kuphedwa,it just needs the youth to clean up this mess
Khala chete God knows ungatenge tsoka😂😂
Mtambo thanks for the vital words.
We now needs actions against these idiots in the government
powerful words Mr Mtambo
Only stupid people with commend the selfish and greedy Timothy Mtambo
Antambo 😂😂😂 ndikukutengeni ngati ndinu amene mudasongezera dzikuni dzamoto kuti tipse Malawi muno ndiwe galu kwabasi
Very true 😢😢
Very true
Ndipo Inu alibe umuthu uyu za ziiii mesa iye emweyi ndiamene anapangitsa kuti tilowe mudima akuonapanowo galu zedi
No matter how long you have gone the wrong road, turn back.
Turning back isn't an offence
Amtambo...ngat mukufuna kut ife tikukhululukireni ...pitani ku mademo mutibwenzere dziko lathu...anthu akuopa mademo chifukwa alibe support...mabungwe onse chakwera adasiya abale ake mmaudindo
Exactly
DPP could have finished us . He did the right thing to rescue some of us from DPP. It was oppressing us
😂😂😂
@@ancientnkhata1137 oooooh ...May the curse of Almighty befall who is a lier...and make them the wood of hell fire
Mtambo mseu wa Rumphi Nyika Chitipa munawukana mesa munkaguba nkumaphwanya zinthu kuti musinthe utsogoleri
SKC forever in our hearts 💔🔥 powerful words Comrade Mtambo Osafooka kms Osaopa Dziko ndi lanthu ife kuno Ku Ntcheu tili mbali yanu...
We quote more political speeches than prayers. This was not a political rally
Ntambo is not a pastor.... Just watch pastor's preaching time...
Ndikakumbukila ifa yaathu amenewa mtima umawawa
Kwambiritu
Mtanbo akuyakhula za ndale zikugwilizana bwanji ndi mwambowu
Ndipo inu
Sometimes I wish Bakili Muluzi to come back again....
Ligongo apano indu yayi itupile Draft kwabasi. 😅😅 Yangajenda Ata panondi
The voice of a lion always brings confusions
Apm my vote ✊
Wakuba mtambo akutiona ngati amalawi ndife galu anthu mwa sandutsa ndale ndi maliro a Dr saulos chilima 😂😂😂
Man ife amalawi tikufuna dpp enawa abodza ngati iweyo Timothy anakuchosa ku mcp chifukwa cha katangale
Keep morefire mr tman
He has got nothing to give malawians never
Idol worship
I totally agree with you
Ndipo live i agree with you big time 👍👍👍
And they don't realize it, they blindly do it💔
Usaweluze pakuti kuweluza ndikwake namalenga
Take it if it was your DAD.... 😔 Bwez iliso Idol worshipping
Mtambo ndi kape
Thanks so much 🙏 keep it up please we need people like 👍 u
Chitsiru ichi, ndiponso uku sikumapemphero
mtambo walankhula za mzeru kuposa namachende chakwera
😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂
😅😅😅
Well spoken, comrade Mtambo.
He has missed the trail. Uyu watha. Ndipo akamati ngati wina amawona ngati wayimisa agenda, atanthawuza kuti munthu wina anachita kuphedwa? Kulankhula kopanda nzeru
Nanga munthu angati anyamata oganiza bwino akumanena wena Lwarwa aaaah guys Mtambo anaganiza bwanji?
Koma ndipo poletsa kupepherapo ndie nduchitsiludi,mobwereza amene amaletsa kupepherayo nchitsiru
Well spoken comrade mtambo criticism singalephere as Malawian we were born like that, keep it up comrade
Watching live from Salima, Khombedza
That's true they is nothing to celebrate 60 years, it's like we help chakwera, kumkuyu ndi zikhale ng'oma kudya mitsonkho yanthu. Ayi momwemo 😂
A Mtambo ikani za mapemphero kuti mzimu wa skc uuse mumtendere
More fire mtambo chakwera machende ako😂
You will gain nothing bro potukwana munthu wankulu, matsoka agwa pakutu panu
Watan😅
I'm getting confused, he is the man who mobilized people to fight a government that was to me far much better than the this one he helped to form.
Zikomo Inu nonse amene mwalimbabe mtima kupanga mwambo uwu though asatana akutchinga,Mulungu wathu ndwabwino,sanalepherepo,imfa iyi ndyovuta kuiiwala
More fire bro ,love from ccter namtambo cp
Kapolo uyu guyz akulubwa chani, mesa udapanganso ufitiwo at dat time kape
LUWALA ANGASINTHE CHANI MBAVA YA MNTHU
Vote yanga yikupita kwa afford
Give your life to Jesus.The owner of your soul is Jesus
Ndipo ngati chilima anachita kuphedwa ndi anthu adzakhala osowa ntendere mpaka Ndipo ngati mizimu imakantha yakanthe anthu amenewa
Amalawi please! Let's pray to God forgive us and punish those who mudder saulos chilima
Viva mtambo Viva🔥👏👏
Mpava iyi atidye bawo bwanji Sumatuluka uli nduna pano abakuchosa ukufuna kodwela amalawi timaiwala
A ndale ndabodza kumene. Ndi chifukwa chake olo akuba ndalama zambiri-mbiri akavala amangokhala ngati avala chithumba chaku chigayo
😂😂😂😂😂😂😂
Big mtambo timakunyadiran
Koma tizikukhulupirirani ndithu a Timothy???
My question too 😢😢
Osaoopa ai......ku Malawi kulibe president
Only God is our rest not this politicians. God help Malawi
Good Messnge Mr Mutambo
Malawi timakhala ngati tili pa stage tupanga drama kma ayi ndithu ndi action
The biggest problem mtamboyu
Akulesa bwanji ma pephelo akuopa chani tiyeni nazo pephelo ndi chida
Antambo vuto chinthu chimozi mumafuna ndalama Chonde muzikhala ngati Born Kalindo chifukwa amati pavute pasavute asayimira amalawi ndipo akuti imila amangidwa amangidwanso pomwe enanu mumatifuna pomwe zakuvutani tikukukuwerenganitu INEYO NDIKUCHALENJA zoti wina aliyese aime payekha kuyambira Apita. Tupele. Raz. Nankhumwa. Shahana. Osati Chakwera Amayi Joyce banda ndi phulezdent Kalindo. Ndiye tikavote masankho mawa mwachilungamo mopanda kubela angawine ndi Kalindo chifukwa ndi amene akuoneka kuti angatithandize osati Ena inu 😁😁😁😁😁😁😁😁😁
Inuyo
Kalindo ndiolimba mtima, ofunika kumuvotera. 😂
@@user-ww4ei5fb7d zoonadi sister osati enawa akuoneka ngati akuti konda koma mmitima mulibe chikondi
Exactly Andale akale achoke boma achinyamata alamulire dziko nkhalamba ndi mfiti komaso ndiankhaza
Atambo ,Ulibe Zelu unaphetsa Athu Ambili
Mtambo 💥💥💥💥
Ada awawa bwenz Ali MUNTHU wapamwamba kwambir kma Anapanga zausiru ngat akufuna timukhulukire ayambise mademo
Mtambo ndamene anapangitsa zonse izi palibe chomwe angayankhule Mutu wake sumayenda bwino ameneyo chifukwa anamuchotsa unduna wagwa nayo Mbuzi iyi
More fire comrade
What's the reason of kuwaletsa anthu ku phiri. Kiphiri kuli chani?
Dziko la Malawi likuyenda cham'mbuyo
Apm my vote
Mzimu wa chilima awasowetse mtendere anthuwa mpaka anfe amene anapha chilima.
Uku ngat kunari kumapemphelo ngat uyu anari compain amtambowatu safuna Bata Malawi koma kusokoneza
Chomwe mkukanikila kutiyimilira ndichan boss wanga
chilima wakuba ngati amwalira sangakhale wabwino Ife tonse tikuziwa zimenezo aphana pa gwilozano wawo
❤❤❤ Exactly
Good Messnge
We're heart broken 💔 SKC still remains in our hearts 😢😢😢
Rest in peace 🕊️ chilima anagwira chito yaikulu DPP mu
2014 ikanafela giya komano chilima anapanga zotheka kuti Peter akhale tsogoleri muchomwechotso mu 2020 wayigwira ntchito yathangata kumuyika Crazy Chakwera akulamulila koma njilu ndikupanga mission plane yakumupha yooohhh Chakwera ngoyipa
God is our side nthawi zonse
Ndipo takonzeka kuchotsa masewerawa
Only chilima not you mtambo RIP CHILIMA
Rest in peace, my president .. we are still fighting
God still be my vote
Unatinamiza ndiwe tuu kut MCP 2019
❤❤❤
Imfa yachilima ine sinfidzaiwala mpaka pano ndikulirabe ngati kuti anali bambo wanga amene anabereka ine koma sichoncho Ndipo mzimu wachilima ukuyendayendabe pakati pathu mzimu wachilima ambuye muulandire kumpando wanu wakumparadise
Mpira amauona ndi akunja big bolani osaiwala zimene mukuyankhulazi antambo
Anali momwemo mu galawundi bwanji zinamukanika
Andale inu musamatiwawitsemutu muma gofuna ndalama agalu inu
Viva mtambo
Viva mtambo
Amtambo naye ine ndinakhumudwa naye ndipo ndinataya chikhulupiriro mwaino mwatulukirano nthawi yonseyi munali momwemotu mu Timbaland wakudayo ndiye pano mukutinamizaso chani apaa iyaaa😊
It's not over until it's over. We shall shut up when we will be satisfied.
Munayambira kukonaza dziko mudzamaliza liti komanso palibe chimasintha mumaona ngati umphawi wamalawi ndiye podyera panu komanso polemerera panu palibe chanzeru chkmwe wayankhula mtambo apa
Iwenso ndi mfiti chifukwa ukupanga za ndale mtambo
A Minister of National Unity aja
Achinyamata ake ati angavele iweyo pathako Pako iweyo unakakhala wa mzelu unakakana undunaaa
The problem with us is that we are the ones that took evil to lead us
Mtambo mbuzi ya munthu
Akutitu ndi afana osata ngini mwana wapa Chitipa .moooooo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
inetu ndimangokuveran anyamata a mcp ndimaziwa kt simunakumane nazo uyo mtambo ngat ndinu madolo kkkkk
Serious reverse gear ineed
Vuto athu kumalawi safuna kumenyela athu ovutika kom mimba zawo zomwe akuyakhula uyu ntambo ngati Ali ndi nzeru chonsecho momwe anali nduna samayakhula PAno anamuchotsa wayamba kuwalalatila athu omwe anawasiya a kugwila ntchito mbuzi ya muthu uyu ndipo ndipo ndiyemwe anapangitsa kut athu azivutika mpaka lelo
Mumatipangisa ndinu omwe muli ndikuthekela kolamula dzikoli koma chonsecho simutithandiza and iwee ntambo uli nkuyankhula koma osakwanilisa mxiii unduna uja unali pheeeee ife tikuvutika pano fukwa cha nzerru zomwe unatilimbikisa ife kuti tikavotere mcp yet lero ukuti usintha ziko mub 2025 yet wakanika zaziii
Anthu ambiri osutsa pano ndi a MCP
Zoona mpaka kuwaopseza amipingo,a MCP mwafikapotu
Imfa yachilima imandidwalisa Bp daily😢
Timothy ugwilizire utm please za u vuce uzisiye
Mtambo is the man