Mulungu akudaliseni chifukwa cha cha umboni wamphavu. Mu u bomboni wanu ndarimbikiskika mu zambiri. Zimozi mwa izo pa zimene mulungu anakuwoneskani. Naneso zina ananiwoneskapo. Nthawi za mbiri nimakayika kuti. Zoona izi ambuye mundikhululukire pokayika. Amen ambuye akhare nanu mai mawindo pa zonse 🙏
I heard this from my mother. When I was young I use to attend Glory to God ministry, lords willing one of the faithful days wants to return their once again. Hearing from UAE Dubai❤

Very powerful testimony
I heard this from my mother. When I was young I use to attend Glory to God ministry, lords willing one of the faithful days wants to return their once again. Hearing from UAE Dubai❤
Tipstseniko manambala a Mai maeindo chinde
Mulungu akudalitsen mai cfukwa cha umboni wamphamvuwu ndipo ndkuona anthu ochuluka akupulumusidwa cfukwa cha umboni uwu. Zikomo A mbuye YESU
Tilape ndithu kuti ambuye atikhululukire
Zonama mukunenazo mai simungandiopsezeso
Ku mwamba kulemekezeke
Amen
Umboni umenewu wasitha moyo wanga
Umbon umeneyo wapangisa kut ndidziwa zambiri Ambuye aremekedzeke
Ndiomboni umenewu mtima wanga ufunafuna nkhope ya Ambuye Yesu nthawi zose.
Nanga mkukupezani bwanji kuti tifuse zambiri zonkhudza umboni umenewu
Chonde anthu tiyeni tilapedi kuti tisakapezeke ku gehena Malo amazuzo.
Umboni uwu wasuntha moyo wanga Ambuye alemekezeke
Amen!! God help me
Ambuye aleme kezeke
Zikomo kwambiri abusa chifukwa cha uthenga wanu.
Amayi mumandidalitsa kwambili
Ambuye andichitile chifundo