the dc mulibwanji.ku malawi kuli ma president awiri ,president chakwera ndi president Bon kalindo,amuna .bwanji poyembekezera kuti tioneko president wa amphawi tiyeseko president wamphawiyu.
Kma a opposition azakukumbukira how? Mesa you also fought for the sitting govt? We are the victims of greed. If we continue to live in the jaws of Crocs, and if we continue to die, it is the 2020 decision that Malawians made themselves. If any opposition leader fails to take the mantle, they will still survive because they can still be bribed to sell us.
Bon Kalindo Zi Anthu Izi nzoipa Zakumidima Mulunguwawo ndi Ndalama , pano Let's Unite Tikane Chitsulo Cho Anapangakale Zakumbali pano aziti Ndichabwino ayi Inu Chipani cholamula Kugagula chimachine pachokha aaaaaaa Ife Si opusa we are Malawians eni dzikonso ngati owow app ayi Sitilola, ama Church ambili Za Yes ndipodyera Akusiya Zavuzimu Akuka panga za ndalevL mmmm Satana wadesa masovA azibusa ndi achinyengo Zedi
Kalero nthawi imene ma BISHOP amayankhula yo ndiye ndalama zowagulira kunalibe? Ma Bishop tu nawonso ndi anthu sikuti ndi ma robot ayi. Amaona kuti zambiri zikunenedwa ndi zipani zotsutsazi ndizoona kapena ndizidani chabe? Akaona kuti wakula ndi udani ma Bishop salowerera. Alekeni anthu a mulungu.
This guy is very genius
Mulungu anatumiza anthu awa, kalindo, Ntanyiwa, bakili muluzi tv ..Thank you Jesus
Always chomwe utakambe mbuyanga .....zimakhala zoonadi.....ndipo ine ndima kukhulupilirani.......❤
Koma mtunda uwuwu palibenso the DC Boooon Kalindo president wa aphawi 🔥🔥🔥🔥💪 you're a strong man 💯
Kmatu Adah awawa sometimes amakamba ma facts
Ndagwila mau oti tisadalile andale, koma tizilimbikile tokha. Zikomo
Thanks to you Mr kalindo,mtanyiwa,bakili muluzi
mr bon kalindo malawi future president ....... god willing..... u got my vote from london,,,,
Adzukulu tikuva watching from salima 😂
Dpp woooooyeee!!!!!!!
the dc mulibwanji.ku malawi kuli ma president awiri ,president chakwera ndi president Bon kalindo,amuna .bwanji poyembekezera kuti tioneko president wa amphawi tiyeseko president wamphawiyu.
Nane andgule changa 1 million
Iwe udzingobwebweta basi boma ndilomweli stikusintha
Ma bishop ake ati amulunguwo..okonda kunyengawa kumanamisila dzina Lamulungu
Kunena zoona thawi imeneo ijah mcp payokha sikanapanga ma demo koma inkalimba mtima ndi iweyo kalindo, mtambo,chilima after kuukila DPP ndi mabungwe ndifukwa mcp inalimba mtima suree, inuyo panopa mukungoyakhula osamema anthu kupita nawo panseu bwanji ngati momwe munkachitira thawi ijah 2019 mukatero muona otsutsa akutsatani osamangobwera tsiku lina lilironse kumangolubwalubwa nkhani imodzimodzi aaa
Mumakwa boss,
Nde inuyo mukutani inuyo osapangapo kanthu
This guy is malawians gift from God
Onetsani action Akalindo musamangoti koma opposition ikugonai zonsezi ndiinu ndi gulu lanu
Iye siwandale
APM wooooyeeee!!!¡!
Àzibusa ena ndi mbuzi zenizeni.Zoona kulola Smart Matic zisilu za abusa
MEC ndi NRB amenyetsa nkhwangwa pamwala kuti Malawi ayake basi 😭😭
Komatu ndiye Malawi ayakadi 🔥🔥 ndipo tiwona zinthu!!
Mwalowa libolonje UTM.
UTM siyomvetsa Chisoni inu koma MCP Ikufunisisa kutsokoneza UTM ....
Kalindo president wa anthu osauka ..timakukondani chifukwa cholimba mtima
Church ndi anthu andale ,anayamba bwanji, history speaks by itself Church ndi ndale
inuyo mudali limodzi ku ma demo ndiye lero akuthilani mphula mmaso kodi?
Akalindo itanisani mademo mwachangu
Ndakhala ndikumatsatira zonene za Brn k,(DC)musawalimbikitse anthu za zionesero.Inu ndi amene munapanga pamozi ndi mtambo komanso chilima lero inu nomwe kazichotseni tsete zonse zomwe zili pa mipando ulamuliro onunkha ulipowo.
Tatulutsani ndodo yomwe mumayikamba yinja akalindo,
Kodi a MEC akuopa audit chifukwa chani? Asanamize anthu za security mbuyomu taona MEC ikupangidwa audit.
Ulemu wanu bwana dc
Azipani akugona kwambili dpp udf aford utm pdp lef onse ali mtulo zomvesa chisoni chonde Apm Atupele Achihana Akabambe Nankhumwa Ambewe chonde aganizilen amalawi muli pamene chifukwa cha amalawi
Bon kalindo ndiwe mwana oyipa kwambiri that's y a dpp amakumenya mpaka magazi fafafa
Kma a opposition azakukumbukira how? Mesa you also fought for the sitting govt? We are the victims of greed. If we continue to live in the jaws of Crocs, and if we continue to die, it is the 2020 decision that Malawians made themselves. If any opposition leader fails to take the mantle, they will still survive because they can still be bribed to sell us.
😂😂😂😂 ma vote aja nd NPK
chipani cha UTM chatha back ku DPP
Boni wasowa masupporter tele wayamba kulira. Anthu amakuziwani komaso sazakusatilani. Chifukwa ndinu wopusa ifeyo timalima ndikuzidalira thokha. Sitimadya mademo zipitani ndi azanu opusa, aulesi chifukwa ifeyo tikudusa mofewa.
Mwaziwa litlo kuti mumalima achitsilu
Ine bola ndizingokhala zovota ine ai
Komat kumalawi Kuno Andale atitola. Bwanji
Munthu wamkulu born kalindo mumakwana boss
Norman chisare ndiwakuba kwambiri
Koma Bonnie kalindo yekha 🙄😁
Bravo❤
Ndine odandaula kwàmbiri dziko lá Malawi latha basi.Peter Muthalika ,Atupele ,Chihana,ndi Joyce Banda what are you men?
si akangoti Monday boma lili ndi zochita basi mwanya ma demo alephekanso one party
state Tiyeni tivomeleze basi
The D.......C.......
Do manually full stop
Bon Kalindo Zi Anthu Izi nzoipa Zakumidima Mulunguwawo ndi Ndalama , pano Let's Unite Tikane Chitsulo Cho Anapangakale Zakumbali pano aziti Ndichabwino ayi
Inu Chipani cholamula Kugagula chimachine pachokha aaaaaaa Ife Si opusa we are Malawians eni dzikonso ngati owow app ayi Sitilola, ama Church ambili Za Yes ndipodyera Akusiya Zavuzimu Akuka panga za ndalevL mmmm Satana wadesa masovA azibusa ndi achinyengo Zedi
Koma Bishop ali muchinyengo kufuna ndarama basitu
Ndipo ma mfumu mmmm ndianthu ovesa chisoni
The Dc mwana yopsa kwabasi
😂😂😂😂😂kalindo sudzathekaso
Kalindi ndiwe galu kwabasi moti sungayamike miseu imeneyi moti galu iwe Malawi afamangapo mseu ndindalama zao mesa zimakhaka zochoka kunja ndiwe mbuli zedi moti parliament ija adamanga ma china tinene kuti Bingu sadapange chitukuko galu iwe ukungofuna kusokoneza anthu ulibe zeru
Ndi kanakwanitsa ndikanapha chipani cha MCP chandikwana 😢
Inuyo amwe tiyeni kusewuko
🙄chikuchita ku boma ngati ng'ombe chi Bonnie kalindo chili "Booooooooooon kali do 💩💩💩💩💩🙌🤔kumlanje nako kuli dzinthu ndipo tsikudzatheka 🤣🤣🤣🤣🤣🤣😁
Eee kalindo ndiwe katundu omanga nd mawaya
amalawi tisalole sumati matiki tiwerenge pa manja
Wamisala anaona nkhondo
Ndipo zoona zamanetizo zili kuno kuchigumula neti npaka kujambula Cha nzika
Koma malawi ambuye inuyo mulipo please bwerani musathese dziko ili
Kalero nthawi imene ma BISHOP amayankhula yo ndiye ndalama zowagulira kunalibe? Ma Bishop tu nawonso ndi anthu sikuti ndi ma robot ayi. Amaona kuti zambiri zikunenedwa ndi zipani zotsutsazi ndizoona kapena ndizidani chabe? Akaona kuti wakula ndi udani ma Bishop salowerera. Alekeni anthu a mulungu.
Amboni tangonyamukani nthawi
Mfana woooopsya kwambiri
Zoon boos mn
Zowonad boss man
Uncle
Koma dzikoli silidzatekaso Malawi
Ndalama yawonga zithu pamalawi 2025 kulibe chabwino
The DC
mademo anali kale
Kkkkkkkkkkkk
Inu ndi freedom fighter tengan action iwo aonere inuyo
Chitsilu chamunthu uyu kamabodzaa daily kubweretsa nkhani zopusa zopanda phindu
What are you doing men
Dzipani dzimene dzikudziwa kuti ngakhale chinsankho chitapangika lero , sizingawine monga UDF ya a Atupere Muluzi dzayamba kale kuchemerera dongosolo lakavotedwe kuti lilibe bvuto . Kwathu kuno kulibe opposition . Tidalakwitsa koopsya kubwereza chipani chakuphachi .
Pepaniii
MCP iyi guys awa akufuna ife Kaya tipange bwanji mabusa onyenga awa
Musovaa
What are doing men
Kd inuyo mukanika kukapangitsa mademo bwanji
Iwetu ulira zeni zeni,,, DPP yakoyo sidzabweraso, iweyo bwanji osakapanga ma demo ukuopa chani
Kodi iweyo uli mbali it ?
Ngt Mulungu amakhal kwanu DPP sdzalamula koma ngt Mulungu amakhal paliponse DPP ikuwina zingodyan ndlama za Chakwerazo
Aaaaa kodi mavutowa akukhuza opposition yokha kani???
❤❤❤❤❤❤❤😂
❤❤❤❤❤❤❤❤
❤❤❤❤❤
koma guys chomwe akufuna a mcp ndichan ndidzikoli
Kukayamba nkhondo, tizawadula mitu
This guy's is very genius
❤❤❤❤
❤❤❤❤❤