A DPP Munagwetsa Ndege Kuti Muwonenge Mbiri Ya Chakwera - Akutero A Mayi Awa

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 24 ก.ย. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, a woman states that the DPP has been busy trying to assassinate President Chakwera’s character with various schemes, including deliberately crashing Vice President Saulos Chilima’s plane. However, President Chakwera is anointed by God, and their attempts to tarnish his image will ultimately lead to their downfall as a party.
    Pa Nyasa VoiceBox, mayi wina wati chipani cha DPP chili kalikiliki kufuna kuonoga mbiriya mtsogoleri wa dziko lino a Chakwera ndi ziwembu zosiyanasiyana, kuphatikizapo kugwetsa dala ndege ya Vice President Saulos Chilima. Komabe President Chakwera ndi wodzozedwa ndi Mulungu, ndipo zofuna kuipitsa mbiri yake zipangitsa kuti chipani chawo chigwe.
    #malawi

ความคิดเห็น • 74