Boma Bola Libwelele Ku UDF kusiyana Ndi DPP - Mr Abdull

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 24 ก.ย. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Mr. Abdull states that if Malawians decide to change the government, it would be better for power to return to the United Democratic Front (UDF) rather than the Democratic Progressive Party (DPP). Tune in to find out why.
    Ku Nyasa VoiceBox, a Abdull akuti ngati Amalawi angaganize zosintha boma, kuli bwino mphamvu zibwerere ku United Democratic Front (UDF) osati Democratic Progressive Party (DPP). Yang'anani kuti mudziwe chifukwa chake.
    #malawi

ความคิดเห็น • 14

  • @AliyoniBwanaisa
    @AliyoniBwanaisa 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Thank you brother Pamauomalizawa zokuza ku gaza chakwera anenebwino

  • @ibrahimmeemzy9754
    @ibrahimmeemzy9754 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Atupele muluzi my vote ❤❤

  • @FrankRabson-q6j
    @FrankRabson-q6j 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tanenan zoti tive osatite osati tigawikane

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Wa chamba iwe Abdul

  • @AfredMbeta-pk1cn
    @AfredMbeta-pk1cn 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    If we hate Atupele muluzi we lost our direction

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chilungamo ngati madzi ine wa mcp ,

  • @AliyoniBwanaisa
    @AliyoniBwanaisa 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Wabazaiwe naweso walandila etiiiii

  • @jummahswaleyi7744
    @jummahswaleyi7744 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Walankhula zomveka koma kongophatikizana ndi mcp mudziwe kuti sitidzakondwa komanso musakhale chete tupere adzuke ngati nthawi ya bingu ija

  • @lungsTug
    @lungsTug 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Atupele mphamvu zachepa mwina akhale vice president wa Peter then azakhala president......2030

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Atupele sangawine bwanji akuyitana mcp inu simungawine timaziwa kuti atupele ndi wa mcp amangopanga manyazi chifukwa cha bambo ake ndiye inu musatinyase mutu wanu

  • @StellaMichael-s4d
    @StellaMichael-s4d 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kupusa chani khondo imeneyi mungaikwanise nokha? Mwakhuta eti

  • @MasegoModukanele-xg2hj
    @MasegoModukanele-xg2hj 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Inendi kuyakhapo udf ngati atupele amuzuza adpp ngati awufuna gwilozano addp alole kuti mtsogoleli

    • @MasegoModukanele-xg2hj
      @MasegoModukanele-xg2hj 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Dpp yazuza muluzi yagwilitsa ychito atupere kukhala wapambuyo wa piter panopa ngati akufuma mgwilizano atupele akhale mtsogoleri bas ngati suzitheka palibegwilizano

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kapangeni alayasi ndi mcp inu ndachisilu mukufuna kwapusisa amalawi udf singawine koma apa zawonekela kut inu muli ndi mcp mumuyitana mdani wanu bwanji mukufuna mulowe mboma mungamuyitane amene mukupikisana naye galu iwe usatenge amalawi ngati opusa wamva chitsilu cha munthu