HON JOSEPH MWANAMVEKA A DPP LERO ATAMANDILA VP MICHAEL USI POGAWA CHIMANGA KU CHIRADZULU

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 28 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 7

  • @jomochirwa
    @jomochirwa 11 วันที่ผ่านมา

    Thank mr mwanamveka inu mwawonetsa ubuthu,ndipo apa zawonetselatu kutu mwa inu muli sukulu.msaka,mwanamveka my faivorite dpp readers .wosati readership yomangotukwana ayi .😊

  • @GanizaniMavuto
    @GanizaniMavuto 11 วันที่ผ่านมา

    Wapusatu iwe😂😂😂😂😂

  • @FrancisChisuse-dc9ok
    @FrancisChisuse-dc9ok 10 วันที่ผ่านมา

    Ndiye January fertilizer sanabwere akamupeza kuti VP wo

  • @Thabiso09
    @Thabiso09 11 วันที่ผ่านมา

    It's fair on Mwanaveka to appreciate the good work done by Their Excellencies Bakili and JB
    APM arrogantly rejected the call by the State president Chakwera to assist in rehabilitation of all structures in the wake of the hurricane destruction your party leader nurses petty issues discarding matters that are at heart of the whole nation

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 11 วันที่ผ่านมา

    Kodi chimanga chomwe akupeleka kumeneko ngati ndi cha Michael usi ndi chamabugwetu aliyese atha kulandila zicha mcp chimanga chinapelekedwa kwamabugwe otandisidwa ndi dziko lamalawi

  • @Noel-y6t
    @Noel-y6t 11 วันที่ผ่านมา

    Eish policewoman yo zomuyeneratu

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 11 วันที่ผ่านมา +1

    Mayi Joyce Banda ndi Ambassador woyimira l think ku Africa nde Anapepha Chimanga ku Ukraine 🇺🇦 nde President wa Ku Ukraine Zelesicky adapereka ku Boma la Malawi chitafika Aboma adagokhala chete kuchikhalira kikikiikiki Plus Hahaha 😆 😂 osawa uza Mayi Joyce Banda 😆 koma Mayi Joyce Banda atauzidwa l think ndi President waku Ukraine kuti tinatumiza Chimanga ,Mayi Joyce Banda adalengeza pa nsokhano kuti Chimanga chopepha ine koma osandiuza kuti chabwera Eyetu ,muyang'ane minsokhano yambuyomo maybe amonth ago Kenako ndi m'mene Aboma amayamba kugawa Zilipa TH-cam pompa kikikiikiki koma YEAH koma BOMA ILIiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii SAD 😔 😟 🙁