ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Ayudasi akaporo akupha usi ndi kafarawo........😅😅😅😅
Mbuzi yachabechabe imeneyi Michael Usi sakudziwa chomwe akufuna
Ndimuthu osokoneza ndimbava uyu muthuwa dyela uyu usi ndimfiti mwachidule😢
Wasowa zokambatu inu khani munayamba bwino mwaisokonedza,UTM MY VOTE
usi ndi yudasi😂km wagwa nawo anamuchosa ku chipani today the party is growing older than ever🔥
This party will be destroyed by kaliyati, let us wait and see
Usi ndi Yudas kamunthu koipitsitsa aka
Bola mukaziwa chomwe kaliati akufuna muyiziwa mbuzi kuti pakati pa usi ndi kaliati mbuzi ndani
Ife tinkadziwa kale khalidwe la manganya ndi ka faraoh no 2
Oonjezera Nkhani iwe
MCP sikutuluka MBOMA nanji ndi DPP inabelamuja sitikuifunaso musamanamizane kumeneko ikadzatopa MCP anthu tidzavotela PDP yanankhumwa basi❤❤❤
Usi ndi nfiti ya ku chikangawa yudasi weni weni
Mwapotozaso nkhani ndinuso opusa eti
Let us want and see
She lost her credibility when she said that it wasn’t her voice in the leaked audio. She is a liar!
Analysis yanu ikuonetsa mbali kwambiri... you can do better...zayamba kuoneka zawamba ngati achina DC
Usi ndi osokoneza,akanakhala wanzelu akanalowa opanda opikisana naye
Za ziiii
Usi ndi ka munthu koipa kwambili
Mayi kaliyati mukuchepa.usi is too powerful pa graund. Usi sakusewela pa graund.inu wanu mayi ndi mwano chabe.
mmmmm moto wake utu wa usi???
Wusi ndale sakuziziwa sitingayelekeze ndi Kaliati.
Kkkk utm singawine payokha sizingatheke kuvotera utm kuvotera kabambe mwavotela dpp
@@FelixKChisale ndiye pali vuto? ddp is coming back aise
Ndiwauku ndi uku usi sakanadana ndi anthu ku UTM amapangisa ndiiyeyoo udindo uli ndi usi uja umaphweteka.
Amafuna kukhala president
Anthu awa ndi andale, komanso ndimadabwa akamati MCP inawina chifukwa cha UTM poti DPP 2019 inabela zisankho kodi anabeledwayo anali ndani popeza UTM inapeza mavoti 1 mita? Mwina inuyo panopa muzingoyesela pa number 2 ngati mayi wanu DPP angakupaseni mpata
Usi ndi kape
Mayikolo dawarf smoke ndi nthira kuwiri munthu oyipa kwambiri ndi amene anakolezera moto kuti chikangawa aphe chilima
Aaaa Mesa mwini wake wakana ku VN sinali yake nde inu mukufuna chani zaziii
Patria kaliyati anakulandani udindo azanuwo a kabambe kugona turo usi ndi wabwino kusiyana iweyo
Udindo analandidwa ndi utsi wakoyo
Usi wakoyo ndi waganyu wa chimwendo, amasenza matumba a chimanga ndi fertiliser.
Ambuye kufuna kwanu kokha kuchidwe monga kumwamba chomwecho pansi pano pa dziko la malawi.
Chomangidwa pa d,Iko la pansi pano mdikumwambanso chamangidwa.
Zavoteleni DPP basi zinazi zitayeni
Usi ndiyudasi
Munthu oyipa manganyera. Akukakamila why
😂 6:50 6:50 6:50 😅😢
Iwe mtolankhani usamanyoze olo kuikira ndemanga sibwino
Mwina iweyo sunavere bwino mene kaliat anayankhala nkhani yonkhudza uthenga omwe athu aamayi ndiwake koma iyeyo anakana ndekaya iweyo ukufuna kulankhula kuti chani kayaa
😂😂😂😂😂😂
Koma zilipo Ku Malawi
Anayankhulapo za chamba pamene paja?
Michael Usi bilimankhwe oipitsitsa
Utsi sufuka opanda Moto
Zopanda nzeru this type of reporting,we need mawu ake enieni not this
Monse muja unali kuti? Interview yakelekale Anthunso mmasowa zolankhura eti
𝑃𝑒𝑛𝑎𝑠𝑜 𝑛𝑎𝑤𝑒 𝑢𝑚𝑎𝑛𝑎𝑚𝑎 𝑝𝑎𝑗𝑎

Monse muja unali kuti? Interview yakelekale
Anthunso mmasowa zolankhura eti
𝑃𝑒𝑛𝑎𝑠𝑜 𝑛𝑎𝑤𝑒 𝑢𝑚𝑎𝑛𝑎𝑚𝑎 𝑝𝑎𝑗𝑎