MBC EXCLUSIVE KUCHEZA NDI BROTHER WA PETER MUTHARIKA - THOM MUTHARIKA. ANTHU ATUTUMUKA NAZO

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 19 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 124

  • @GlazoMw
    @GlazoMw 27 นาทีที่ผ่านมา +1

    Doctor Lazarus McCarthy Kachero, hiii Chakwera 😅😅😅😅

  • @henryibrahimsailes4638
    @henryibrahimsailes4638 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    😂😂😂 madala awa apitira limodzi ndi chikanawa crocodile 🐊 party dyera mpaka kuzikokera chibale ndipo iwe alinafe ndichitsiru kwambiri exclusive yake itiyo

  • @thesocietynews3181
    @thesocietynews3181 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mwayamba program yatsopano yofufuza zibale?

  • @thesocietynews3181
    @thesocietynews3181 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Komanso ndi cousin wake osati brother.

  • @BlessingsMasakala
    @BlessingsMasakala 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Ngakhale nditakhala ine peter muthalika sungadzaionenso khobidi yanga ndi betrayal mkului ndimpake peter anamuona mpaka kukalowa ku mcp cholinga amve kuwawa peter simulibho madala

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Km ku MBC kwangodzadza mbuzi zosowa zochita 😂😂😂

  • @Ayanali-cr4vy
    @Ayanali-cr4vy 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Atupele Muluzi my Vote

  • @Noel-y6t
    @Noel-y6t ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma akuluakulu tayang'anisitsa mphunozo?Sakufana ndi PM eti?

  • @ChaonekaSande
    @ChaonekaSande 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    😂😂😂 palibe chanzeru chanenedwa apa

  • @ChiyembekezoPhiri-sv8nw
    @ChiyembekezoPhiri-sv8nw 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kodi madalawa amatuluka nthawi yazisankho why, komanso ameneu mnagadyera

  • @IssacNduna
    @IssacNduna 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    😂😅😅😅 dalai ndi mfiti angathe kudziwapo zakufa kwa chilima

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Chibale sakokera, inu a MCP ndi Nankhumwa muthandizeni munthuyo- koma zomwe akupanga iyeyozo sizimuthandiza.

  • @Imtiyazkalikodole
    @Imtiyazkalikodole 45 นาทีที่ผ่านมา

    Uphawi siwabwino uyu wakalamba alibe Kathu 😂😂😂😂

  • @BlessingsMasakala
    @BlessingsMasakala 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Vuto mulungu anabisa tsogolo lamunthu simunadziwe kut bingu ndi peter adzakhala madolo lelo mukukumba chibale waona do ur own thing izi zikuchedwesan madala

  • @EmmanuelGodfreynkhoma
    @EmmanuelGodfreynkhoma 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Uyu ndi mbuzi yamuthu alipo ammutuma nthawi yoseyi anali kuti this is the end of MCP😂😂

  • @RitaMwale-m2p
    @RitaMwale-m2p 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Makape a MBC,you think ife tisintha maganizo okavotela APM just because of this nonsense,by the way mdalayunso alibe sure zomwe akuyankhula

  • @mishecknkhumbwa832
    @mishecknkhumbwa832 24 นาทีที่ผ่านมา

    Kodi MBC ndichani kwenikweni😂😂

  • @GlazoMw
    @GlazoMw 21 นาทีที่ผ่านมา +1

    Komatu dzimaudzo dzufanana😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @andrewkalukho
    @andrewkalukho 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zitipindurira chani izi? Inu mumathandiza abale Anu onse?MBC inatha inali kale kaya mwatolo kuti ameneyo mpatsa Neef

  • @BoydMuyaba-h7k
    @BoydMuyaba-h7k 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Mphamvu yamaluzi. Masikuwosewa unalikutiko?

  • @BlessingsBanda-w1s
    @BlessingsBanda-w1s 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Aaaaaaaaa zanziiiiiiiii, nde pamenepo mukuti mwaaphunzitsa chani a Malawi? Mdala ya chingambweyo zaka zonsezi yaona kuti ikumbe chibale pano? Migogo ya chakwera iyi.

  • @RennieSomba-xt9zk
    @RennieSomba-xt9zk 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mbc bring us program yopasa hope zinthu mu dziko muno sizikuenda.
    Akungooneka ngat Habakkuk apa. Size imeneyo bas chinkhoswe

    • @BlessingsBanda-w1s
      @BlessingsBanda-w1s 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@RennieSomba-xt9zk kkkkkkk ndipooooo, uyutu ndi brother wake wa habakuku

  • @DuncanKambewa
    @DuncanKambewa 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kape momwe anzako amaphunzira mpaka kumapeza professor unali kuti?

  • @EmmanuelGodfreynkhoma
    @EmmanuelGodfreynkhoma 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndiye A chakwera akhala m,bale wanu inu ndi opusa bambo mutu wanu sugwira

  • @GiftGowelo
    @GiftGowelo 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kma mene wakulila uyu naye kumanama

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mwapita ku mcp chifukwa cha thandizo osakhala mtima okonda mcp

  • @CardoJustin-l7m
    @CardoJustin-l7m 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Madala iwe ngati uli umphawi kalapeni ndithu

  • @PeterChikoti-f6w
    @PeterChikoti-f6w 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zosamveka kufotokoza zachibale sungakhale jenkha kuganizila zoyankha

  • @duncanKingsly
    @duncanKingsly ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂Mukuona ngati akupasa gawo lako

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ife kuthundu kwathu Muthu sangalowe mcp

  • @ulemumuthala4693
    @ulemumuthala4693 55 นาทีที่ผ่านมา

    Mwasowa zochita mpakana kuyamba kufufuza zibale za eni ake😂

  • @ChikondiBannet
    @ChikondiBannet 58 นาทีที่ผ่านมา

    Iweo umakana kupita kusukulu anzakoyooo analimbikiraa so lero ukufuna chan ?

  • @HopeMasache
    @HopeMasache 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    God should help us for removing the spirit of poverty

    • @ChangeLive-w7t
      @ChangeLive-w7t 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Yes that's what's we e need in our country let change guys uyu palibe wakanika basi the don't know nothing totally

  • @MariaJaya-s9b
    @MariaJaya-s9b 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zazii anthu mukusowa zochita

  • @KondwaniHarawa-eb3pv
    @KondwaniHarawa-eb3pv 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Uwona mmene chakwera akupasire njomba

  • @CassimCawanga
    @CassimCawanga ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pamtumbo panu nonse a MBC ndi mkulu wa chimutuyo

  • @AfunikaMafotetsa
    @AfunikaMafotetsa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Alowa bwanji chipani poti iye siwandale? Izi nzamabodza ndithu akanangopempha kuti a MCP awathandize basi

  • @ShukuCassimu-m7g
    @ShukuCassimu-m7g 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Km Khan ndiyoti thawi yoseyi anali kuti nakha zachibale zafika paka apapa

  • @CHARLESCHIPOYA-y2f
    @CHARLESCHIPOYA-y2f 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mapwala ake ameneyo

  • @ChikondiChingana
    @ChikondiChingana ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zomvetsa chisoni kut ngakhale azigogo akupereka dziko kwa anthu ankhaza ngat sakudziwa history ya Malawi

  • @jomochirwa
    @jomochirwa 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Koma mdalayotu ndiwodziwa kulankhulatu.

  • @LesterSydrick
    @LesterSydrick ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mfiti uyu ,akudziwapo kanthu za imfa ya bingu

  • @ShareefKalima
    @ShareefKalima 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkk M.C.P yatha ndi mizimu 9 ija ku chikangawa Peter sagwesa ndege ngat akupasa ndalama yidyan koma vote Peter

  • @DigleDafter
    @DigleDafter 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mcp n DPD muthandizene mfiti yu chibale sakokela thawi yonseyi analikuti akufana ndi chikangawa osati muthalika family ayi😂😂😂

  • @BrownMatonyola-xi3lb
    @BrownMatonyola-xi3lb 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nde chopangira program ndichani inu ambc

  • @amoschisisi2070
    @amoschisisi2070 17 นาทีที่ผ่านมา

    MBC ndinu a galu

  • @AtuswegheKabango
    @AtuswegheKabango 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    One nation..izi zauchisilu

  • @SidreckRashid
    @SidreckRashid 21 นาทีที่ผ่านมา

    A hule tamafunsani zomveka....tikudziwa ndinu Mr chikangawa first eleven..ndipo pagolo pali kamajekete...

  • @hendreson
    @hendreson 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kusauka sizinthu

  • @LastonMmanga-r2u
    @LastonMmanga-r2u ชั่วโมงที่ผ่านมา

    A bwera ku MCP kuti awone kuwala pomwe so wandale😂Komatu umphawi ndi kanyama koyipa kwambiri eti??? Mmmmmmm😂

  • @LipengaPhillip-u5l
    @LipengaPhillip-u5l 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndiye ife zikutikhuza chani zapachibale panuzo

  • @SamukLungu
    @SamukLungu 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akape mwasowa program ngati zabanja mwaziroweska ku M BC uyosi mutarika ayi

  • @thesocietynews3181
    @thesocietynews3181 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Vuto lanu ndi chani kodi inu a MCP? Mutengeni akhale m bale wanu chabwino. Mukufuna Peter atani? Inuyo kwanuko mumalera abale anu onse? Zopusa basi

  • @blessingssaiti
    @blessingssaiti 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Inu akunama akulu awa nthawi yonseyi anali kuti nthawi ya Bingu Muthalika Ali pampando

  • @CharlesBande-yr1yb
    @CharlesBande-yr1yb 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Munthu oipa mbava imeneyo mmangeni ameneyo komanso atumidwatu ameneyo

  • @martinkasamba1576
    @martinkasamba1576 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mkulu wopusa kwabasi.
    Chibale amakumba?

  • @SamuelKupeta
    @SamuelKupeta 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Booshit!!!!

  • @NoahLingson
    @NoahLingson 52 นาทีที่ผ่านมา

    Akufuna adyeko tindalama tachipani cha mcp kkk

  • @Elizabethmanda-es7se
    @Elizabethmanda-es7se 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    MCP IKULIMBANA NDI PETER Muthalika.... asiyeni chibale kaya chibale or sichibale akudziwa okha.

  • @AliNtolera
    @AliNtolera 26 นาทีที่ผ่านมา

    Kkkkkkkkkkk umphawi ndi ufiti ndichifukwa akumukana

  • @ModesterNyakwawa
    @ModesterNyakwawa 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma ku MBC anthu mukupusako kwabas

  • @Tophillpvtsecondary-x7l
    @Tophillpvtsecondary-x7l 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nanu MBC mwasowa chochita takonzani dziko osati zanuzo ayi

  • @moffatchauluma171
    @moffatchauluma171 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Habakkuk part 2

  • @RodgersNtambalika
    @RodgersNtambalika 5 นาทีที่ผ่านมา

    Koma agaru inu muli ndi vuto Kodi nkhani ya pachibale mkubwera mayo pa air umphawi sizinthu MCP mupangadi chilichonse kuti muipise anthu

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiye bale wanu akhale chakwela osakhala peter Mesa muliku mcp

  • @g2foods
    @g2foods 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mmmmmmmmm za ziiiii mukuona ngati mungathandizidwe moyowanuonse? Bakalimani kumudzi..........MBC chomwe chukukhunzani ndi chani? Abale a APM alipheeeee uko

  • @JohnPetro-vv3er
    @JohnPetro-vv3er 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Gwape uyu

  • @CassimCawanga
    @CassimCawanga ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uyu ndi mkulu wake wa chimwendo Banda muziona chimutucho dowa dowa iyi

  • @MuhaShaibu-x5x
    @MuhaShaibu-x5x 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Aaa kkkkkk mbuz za anthu mwasowa ma program et 😅😅 kod ndi wa MCP so aaaa...

  • @blessingssaiti
    @blessingssaiti 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Sindikufuna kunyoza Munthu wamkulu ngat amenei koma azinvere chisoni

  • @HystonMlungu
    @HystonMlungu 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwati ndinu wa mcp

  • @ZavutaSimeonKamanga
    @ZavutaSimeonKamanga 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    That's politics

  • @blazembiza1952
    @blazembiza1952 43 นาทีที่ผ่านมา

    Palibe icho ndanvapo chanzeru

  • @MagieJames
    @MagieJames 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ntwi yonseyi anali kt watumidwa nd chikangawa kt aziyankhula zopusa

  • @ShareefKalima
    @ShareefKalima 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Musayipise Mbili ya Peter ayi. Anthu akufuna Peter fetetrizer, chimanga, Mafuta zonse zakwela tikufuna zinthu zichipe osat zakupha Anthu ku chikangawa. Komanso Ngat Munadana ndi peter Muthalika ku mudzi kwanuko iffe tilibe nazo ntchito zimenezo nkhan ndi yot M.C.P yalephela kuyendesa ziko zawavuta

  • @jomochirwa
    @jomochirwa 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Achinyamata tiyeni tichepetse mnyozo ,bambowu ndi achikulili ndiye kuwanyoza sibwino.izi ndi ndale ,anthuwo ubale wawo tisaulowele akudziwana wokha.

  • @ulemumuthala4693
    @ulemumuthala4693 52 นาทีที่ผ่านมา

    Mpakana kukwatira ka chitatu, kkkkk

  • @HarounRatib
    @HarounRatib 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kaya ndichibale kaya sichibale zawozimenezo ife tikuchosa basi,,,,,,,, mwachiziwikile mukuwopa

  • @jameslweya-eo1uj
    @jameslweya-eo1uj 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    MBC kusowa zochita, be creative please

  • @Tophillpvtsecondary-x7l
    @Tophillpvtsecondary-x7l 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mdala Onama uyu , Mutharika odziwika Ali Ku Luchenza amayendera magalimoto odula and sagwira ntchito kma he is a rich inu anakusiyani pati?? Iwe ndi Wa MCP ukhale mkulu wao Wa Chakwera 😝😝

  • @petermtembenuzeni2508
    @petermtembenuzeni2508 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chibale sakakamiza

  • @dennismkombe7193
    @dennismkombe7193 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Khalamba yopanda zeru and whole ABC 😂

  • @ajasikalonga3210
    @ajasikalonga3210 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iwe chitsiru kwambiri 😂😂😂😂😂😂

  • @Trustmkanya-qrt
    @Trustmkanya-qrt 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    But it make sense munthu sungakane m'baliwako even if ndiosauka vuto Peter munthalika khalidwe mulibe angokula mutu osakhalaso ndi mano nkamwa chitsilu

  • @JamesIngeni-ku3qj
    @JamesIngeni-ku3qj 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nde ngat alibalewanu nde ife titani

  • @kingSoko-wf4pe
    @kingSoko-wf4pe 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Limbikirani kulima madala Nanu mupange zanu anzanuwo analimbikira sukulu

  • @mzeewandembonyirongo2972
    @mzeewandembonyirongo2972 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    But what is the intention 😢. Koma akufanana ndithu athuwa😂

    • @IsabelLuka-i8f
      @IsabelLuka-i8f 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Mmmmmm sakufanana😂😂😂😂😂

    • @mzeewandembonyirongo2972
      @mzeewandembonyirongo2972 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      ​@IsabelLuka-i8f uyu kungoti alibe ndrama koma akufanana

  • @WisdomKapawo
    @WisdomKapawo 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Palibe umbale yapa 😂😂😂

  • @WillyNjinje
    @WillyNjinje 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndi wa bodza ameneyu anali. Kuti nthawi yotseyi .Anachita bwino kumukana .apite kwa abale ake ku mcp ko

  • @patricktaibu4874
    @patricktaibu4874 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zaziii kutumidwaet

  • @GivenKitha
    @GivenKitha 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zazi zopanda muchere komanso palibe chomwe munganamize Amalawi,malawi yinaseguka

  • @HopeMasache
    @HopeMasache 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    MBC PEZANI ZINA ZOCHITA BWANJI?

  • @SimonMochede
    @SimonMochede 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nzopusa izi

  • @EmmanuelGodfreynkhoma
    @EmmanuelGodfreynkhoma 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂 power of poverty MCP ikupita basi

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Komatu MCP zomwe mukufuna sizitheka thawi yoseyi munali kutiko

  • @ChikondiMasebo
    @ChikondiMasebo 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Wakuba ameneyo kwathu mulibe mbava imeneyo, wakutumayo akupweteketsa.

  • @CardoJustin-l7m
    @CardoJustin-l7m 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Madala wabwera ndi planne yophemphatu zaka zonsezo unali kuti

  • @harrygobede7693
    @harrygobede7693 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Inu a Mbc mufuna mukonze ubale wa a muthalika?kkkkkkk

  • @ReubenMuhuwa
    @ReubenMuhuwa 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Cheap propaganda uyu si bale wake wa muntharika a mcp muntharika uyu

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zonama basi zikuchita kuoneka kuti zotumidwa