A Chakwera Ndi A Chilima Ntchito Yanu Yatha - Billy Banda
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 19 พ.ค. 2024
- On Nyasa VoiceBox, Billy Banda says that time is up for His Excellency Dr Lazarus Chakwera and his Vice President Dr Saulos Chilima becuase they have failed to govern the country.
Pa Nyasa VoiceBox, Billy Banda wati nthawi yatha kwa Olemekezeka Dr Lazarus Chakwera ndi wachiwiri wawo Dr Saulos Chilima chifukwa alephera kulamulira dziko.
#malawi
Dzikoli likufunika ma Demo....ngini zinakwera mitengo monyasa.anthu akuvutika heavy..
Palibe chomwe tingaloze kuchiyenda.
Achoke amenewa awononga Malawi wokoma uja Lero mavuto okhaokha zawavuta basi
Kumanga bakili mluzi tv Malawi azayaka moto
We need people like you not those people on times,zbs,mbc onse alikumbuto kwa boma lakuba ilili
Big up boss,atikwana
From today, Commander atenge ulamuliro mpaka tsiku lachisankho. Chakwera out
NO PAIN NO GAIN INSHA ALLAH WAKUVA WAVA AKUT SIYAN NCHITO MWALEPHEL PLEASE GOOOOO
Let's put everything to our God almighty. God is watching
good message Mr banda
big up brother that kind of citizen needed in our country than those people the get bribe and appreciate nonsense from chakwera and chilima mulungu akupaseni mphavu ndi kuima pa chilungamo
Tikulira ife a Malawi apa tithawira kuti dziko lathu lamvunda kwacha yagwaso zithu zakweraso 😢😢😢 MCP Chakwera ndi UTM Chilima vote yanga ikundimvutisaso malawi ineeeee 😢😢😢
We need more of you zithu zikhare bwino bwino
Rev Chakwera kms Chilima kunena zoona zinthu zawakanika ndipo achikhala athu amzeru anakasiya pansi Udindo koma pakuti ndi agalu akakamirabe ubwino wake 2025 ndipompano..
Yes we are very disappointed ndi wulamuliro wathu amenewo
Very strong message.
Mumatiimilila Mr Banda mulungu akupatsen zabwino
God message
AChakwera usogoleri mwa inu mulibe kwanu ndikuononga ziko amalawi ndiwokwiya
Chakwera achoke basi enough is enough
2025 saiphuranso chifukwa zinthu sizilibwino, life now we struggles.
Chakwera ndi chirima Maso ngati Kazizi nchito yanu yathaaaaa. Tulukanimoni nyumbazathu zaboma . Palibenso chifukwa chokusungirani mmaudindo choncho ngati mukufuna ntendere muzipatse ulemu Nokha popular pansi maudindo and koma ngati mukufuna kuyaluka pokakamira maudindo amalawi azakutulutsamoni ndi Manama, mateche ndi zikoti kapena chakwera ndi chirima tayesani Zidane mumuwone mmalawi akakwiya.
Munthu oipa ameneyo chakwera azipita watipha amalawi
Zoona zache azipita basi ndithu
Ine kumangolankhula kt tsiyan udindo sizimandpasa sense iliyonse coz olankhula ndi ambili Koma zaka zikupitabe
Exactly these is true All it's about Allah and let's ask our Almighty Allah to guide us and to help as to take out these mbava zimene zikuonga boma lathuli kumaba ndalama zathu zamisokho
Ndizona achoke akuba awa
Achoke galu ameneyu
Kuyakhula kwabwino
👏👏👏🙏
Mbuzi zalephela zimenezo zichoke we don't want them useless president in Malawian history zitsiru zeni zeni za anthu
Tipita liti tikamupakilitse h failed us ,cement nt evn a year kukakwera kawiri eeee ai zikomo, we are nt tired
Ambuye lithandizeni ziko lathu la malawi tikhululukireni zochimwa zathu ngati mwatikwiira bwezani nkhwiyo wanu
My vote belongs to the dc booon kalindo
One more kachasu from me, kkkk
Chakwela akufuna ataimanso koma mulungu akukana
Anthu opanda nzeru amayankhula zopusa ngati zimenezi. Ngati akuganiza kuti DPP ilowanso m'boma ndiye bodza. Chilima sanayendetse nawo dziko. Amene akukutumani a Banda tazingodyani ndalamazo. Iwe ndiwe wapangapo chiyani?.
Zoonadi ,dziko ili achoke a chakwela ndi a chilima
Ndenge zikugwaso nza ku Iran zakuno ai
agalu amenewa atizuza ndithu
Apandiku ona mosi akusapota mbusi chakwera achokekumen sisilu sawandu andichilima panopa akuspota chakwera mbusiya kape
Ndakaika ngati zingatheke kaya mwina. Ndiye zikalepheleka kuti gologolo wakakamila zitani in that scenario 9
😢 😂 andiliza awa
Akufuna Kuti abwereyo adza pezengongore adzi dzatiso ramuka Nika apume bas
Dziko lamalawi likufunikila mademo akathithi ziko lapansi lidziwe
Munthu oipa chakwera watipha azipita
Good message ❤
Akumangani
Kkkkkkk
Kkkkkkkk auzeeeee!
Brother my respect to u.inever been in any Malawi since multiparty system came in Malawi.but Chakwera is worsest and rubish president in the world
Chakwera waononga dziko kuposa ma president onse
Zawakanika
Komatu a Malawi ufulu kuchuluka aliyense kungodzuka anyozepo chakwera koma izi tipita nazo kuti kodi ana athuwa adzakhala potani ufulu umenewu boma likugona olo Bingu samkaselera zopusazi
Kkkkkk Zina ndi ziwanda. Mudzionongera nazo izi ndi uchitsiru wanuwo. Nsanje ikuphani baba
True some of these ndi mademoni awa a billy bwanji ? speak peace and unity ..
Ndiwe opusa kwambiri mmene anthu tikuvutikira ungamaikire cakwera kumbuyo zoona
Mcp yakupa ndipo yangasa chakwera andi chilima alepela ose mbusi sawandu mbava sa kuba
Chakwela acoke sakufunika
Kodi anthu amenewa mfundo zawo kampeni wachakachino angamveledwe boza zisiluzo kunama bs
Kagwere iwe ndiwe ndani chitsiru usatibowe ukuti ifeyo wina kuphatikiza ndani poti ukuyankhula wekha pomwe ulipo ndi milomo ya yothethekayo galu
Iwenso ndi wanyawu eti?
Kapena ukudyanawo a MCP kwanu ndikutiko iwe?
Chitsiru iweyo galu uyu ukunena zoona ufunse uladi pa kk kuti panali bwanji
Zulo aziona uladi musa amanyozedwa akuva pa chigumula
Ngati mwadya nawo a mcp khalani chete,anthu akuvutika
Ndiye iweyo ukati chakwera ndi chilima maso ngati kadzidzi nanga peter uja afanana ndichiyani kuphatikiza iweyo ufuse athu akuuza mene ukuonekera.kodi iwe billy banda umadziwa malamulo ?uchoke ndiwe kaya mbuzi yotheratu cadet.
Peter munthalika sungayelekezele mbuzi ziwili zikutchilidwa apazi,
Uchisilu abillywo ali nkuchikamwa ngati adya zowawa tiyeni wauko ndinu achisilu galu amalawi ake ati chimbwe
Mbolo yako iwe
Mademo ayambaliti
Galu wachabechabe president yuti adakwanisapo zokhumba za anthu onse
You are a full
Chilima amayendetsa boma lake lambuyako? Zoti anamuimitsa ntchito for the past 2 years iwe sukudziwa? Kapena amagwira nyumba mwako? Leave chilima alone pliz wadutsa kale muzambiri
How can a fully grown up man Billy speak lik this ...u may have something to say but the way u present it its very poor . Go back to the drawing board
Judge wakumalawi akulankhula atakhuta ndalama za DPP mukuva km kkkkkkk akt sakuona magetsi kusaxima, at mukumukaniza kukateng
Mafut ku mela at sakuona HSA akulembedwa iyeyo a police akulembedwa ntchito akuvek ndithu
Magetsi anthu akumidzi samadya aise,ndipo kumaganiza poyankhula osayankha phala apa ngati munthu amadya msewu,munthu amadya magets,shame
Zazii zenzeni chitsilu chamunthu zolskhula zako zosabveka mbuzi yamunthu shupit
Motherless squirt
Mbuzi iwe
Inu achitsilu kwanu.kut .ndibwere ndikudinde
Muchoka nbomamu
Good is good: no black out but prices of 3Fs, foods, fertilizer and Fuel eshiiiiiiiiiiiiiiiiii