UDF ndi DPP Ndizipani Zokhazo Zoti A Malawi Angavotele - Concerned Citizen
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 21 พ.ค. 2024
- On Nyasa VoiceBox, a concerned citizen says, UDF and MCP are the only parties worth their salt in 2025.
Pa Nyasa VoiceBox, nzika yokhudzidwa yati UDF ndi MCP ndi zipani zokha zomwe a Malawi angavotele mu 2025.
#malawi
Apm my vote ❤❤❤❤❤
Atupele muludzi ndi mulosi ameneuja analisela zoona kuti Chakwela sangaendese dziko tiyeni tivotele nsigoleli woonabpatali
Za zii, dziko lidalaka Bakili Muluzi. Kamuzu Banda adasiya china chili chonse chili m'malo, makampani, ndizinthu zambiri koma Bakili Muluzi adadzawononga china chili chonse. Chodabwitsa palibe wina aliyense amene amalankhura za izi kuti Elson Sixpence Bakili Muluzi adawononga dziko lino.
God bless you bro 2025 DPP woyeeee ❤❤❤ tinapanga mistake mulungu atikwiyira chifukwa.chake tiliku bagamoyo
Msonda si munthu ai, hule pa ndale uyu, kulowa uku, kulowa uku, osakhazikika munthu.
Walankhula aise size ndithu😂😂😂😂😂
Powerful
Speaking truth❤
😂😂😂😂 kaliyati joyce banda mahule akuluakulu
Eeeeee ine no comment ❤❤
Thanks munthu wankulu walankhula mwamphamvu
❤❤❤
Tikukonza Malawi osati Zambia ndeno enanu lekani zomayelekeza ndi maiko ena sitikukhala ku Zambia ife ayi.
Amen
Pano chakwera akudya mkazi wa sadick mia😂😂
Power to that 👊
Zina umangoona utaziyamba 😂😂😂😂😂😂😂❤❤
Mumakwana goodness
Big awawa anadziwa kufotokodza
Kuyakhula kwabwino musonda sangayakhule zabwino ndiwodwala ameneyo
Mwalankhula Baba Takumvani
Akwen uzimvere mumtolo😂😂😂😂 zopanda mzeru amalawi tatopa nazo
Apm my vote 2025
Zoonadi Brother tilipambupanu
Don't take him again people like this guy Muthu opanda chipani
Ngakhale inuyo mukunama mukulankhula zambwerera. UDF ndi DPP zidalephera, musanamize wanthu inu, akulonjezani mpando inu. DPP kungakhale quite? Zabodza zimenezo
Opanda nzeru
Inu
Mcp ndi utm zipani zimenezi anthu ana zituluka kale
Ansonda 😂😂😂 osaiwala kuti ansonda akumwa tijati
Mawu omveka bwino ndinthu...
GOD BLESS you malawi 🇲🇼 watha wafika pa Zimbabwe akaliyati uchitsilu atakutha ndalama a mcp kumabwekela ngati dziko likuyenda bwino iiiiii mulungu achite nanu kuyambila chakwela chilima ndiwotse akuyamikila boma ili ndagalu kwabasi uchisilu wanu akaliyati magayile amalawi otse mayi uchiysilu unakumelani ati
Otilangiza, otikonda mulipo ndithu, chonde anthu timve. 2025 is our last hope to solve all these tribulations.
Mwalakhulatu chilungamo apa
Mwamveka ndithu
Inu amene mukumuzuzula Patricia Kalitati mwakoma pati. Chonsechi mukutankhula choncho kuti namwe mudzapeze mpando muzabe bwimo misonkho ya a malawi 2025
Izo ndizowona mavuto achiluka malawi achoke anthu okubawo
Apm boma ilo❤
Kumalawi kuli anthu oganiza kwambili eeesh
Auzeni man osawanyengelera
Awuzen zoona zake asamapuse
Utim is only party to change Malawi,, DPP under Peter, shit up
Auze ase achina nsonda
Komad ❤❤❤❤❤
Atupele anati msogoleri asathawe udindo olo zinthu zitzuta bwanji ndiye chilima athawe ayii
Maganizo anu amenewa
Vuto la UDF kudulana dziwalo mmmmm
Komadi akweni ndi opoila mwano okhaokha
Wokamba moyipa msondayu, osati wokalamba bwino ayi, simukumuona makutu oyima ngati nkhumbawo kkkkkkkkkkk
Munthu wankulu mumadzwa kuyankhula zoona ndithu Komanso chilima wakumananazo ndi ochenjera nzake chakwera amamutola Peter Mutharika samayankhula chifukwa ndi munthu ophunzira kwambili ndi chifukwa samayankha zopusa ndipo Peter Mutharika ndi munthu opamulungu ndi chifukwa anthu amamukonda kwambili
Tikhale ndi maso auzimu ndithu
Muuzeni galu ameneyi.....kamwa yake ngati wizilo
Kodi a msondawa ndi chani kwwni kweni
Muziwa era chisoni amsonda mutu unajama afunika kubox1 ku zomba akasungeko pang'ono mutu ubasrelamo unataya
Mzeru za ansonda zinakalamba
😮😂😅😂❤😅😮😮😅❤❤❤❤❤❤😅🎉
Mau abwino kwambiri zikomo
Auzeni agalu amenewa a chilima zangakhalenso pusident mu dziko la malawi wolo atatani wagwa nayo 😂😂😂😂😂😂
DPP+UDF=Fire Works!!!!!!!!
Asondwa ndi amisala wosamayanga edzi ikuwasunguza mutu
A Nsonda simungawasiyanise ndi mbatata bolanso mbatata ili ndi nzeru!
Kodi boma amayendetsa motani kkkkkķ koma Malawi ufulu
amapha anthu mcp kale bambo ake a chakwela ndi kukuyu mbuzi za wanthu
Adadi ndi atupele amalosela koma amalawi satana anati sekama kumaso pano taonani njala ilili kumalawi
Odi ndiwelenga ma comments ine chonena ndilibe
M'manja mwanu akulu, mau amphamvu.
Ulemu wanu mabwana,, kulankhula moona mosaopa makape amenewa.. agwa nayo amenewa, Olo atayesera kubera aonabe nyekhwe yoopsa.
asonda ingodekhani
Iweyo ukuyala zakaliyatiwe ndikaliyati yemwoyo nonse ndinu zitsilu osatiuza chipani choti tisankhe ayi
Akulu palibe angasithe dziko lapansi penapaliponse zithu zandula pa Zambia soya pieces mk700
Soya pices wake uti ife tikugula 150 bodza silabwino
Asonda ndachisilu nkalamba yopanda zeru
Dpp moto
Chisilu ndi ambuyako osati msonda galu iwe sankho basi
Regionalism koma adah
Chokani adpp mufuna muwa pusitseso a UDF ngati momwe munawa pusitsila muja
Palibe kanthu
Bola zipani zopusazi
Zichoke.
Zoonadi Asoonda ingokalapee mwalandila kale chibanzi
Choka iwe mchawa wasankho muwafuna anthu aku mpoto pompano galu iwe fotsek.
Iwe nawe munyane wa ku mpoto ulije zeru wasankho pakati pa mchawa ndi mchewa wasankho ndikuti? Namwe wakwithu mahala ngakichepa mcp munayamba mwakhala nayo imwe ? Pala ku Malawi kuno kuli mtundu wasankho ndiye mchewa nambala 1 panopo maudindo m'boma almost 90 percent chigawo Cha pakati mchewa Kodi mwabadwa muma 1990s eti?ndipo kuno ku mpoto tisayerekeze kivotere mcp si chipani chimenechi chankhanza chatikomera wanthu wanandi kuno kupoto foseki
Ku malawi aliyense amafuna kukhala wandale, political analyst, judge etc.
Nanga zopusa zikukambidwa apazi ndi chani?
TH-cam yaphweka.
Chilungamo chaku sinanitu akulu
@@mafukenimasangwi5487
Chilungamo chake chiti pamenepa?
Dpp, utm mcp udf
Pp etc being party nothing is wrong but who is leader. Serious kuvotera Peter muthalika albinos killer stupid mbava ndi chisale nepotism galu racist president galu galu zitsilu zomwe vikavotere Peter muthalika galu
😂 udziwe lero boma lililonse limakhetsa mwadzi popanda kukhetsa mwaz boma silingayende ulamulilo wa u president suzozedwa kuchokera kwamulungu Koma satana
And satana ndiamene amawalumbilitsa ena amapha mosaonetsera kuzera munjira zosiyanasiyana nde ngongole zomwe amatenga maiko akunja aja
Kupatsidwa ma billion awulele so dzungu sapeleka chithu chaulele komaso satana sapeleka zithu zaulele kungovomeredza palibe wabwino sir
You are being a tribalist
akula vumbwe otatha patsekela sonda
Munthuyu muli kulankhula mwa usogoleli
Maganizo anu amenewa
NO PAIN NO GAIN IWEI SLM BOY GO BACK 2 SCHOOL GALU