ZOMWE AYANKHULIDWA A MICHAEL USI KUTI ANTHU AKU RUMPHI AWACHITIRE

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 50

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 2 หลายเดือนก่อน +8

    Apule mwandisangalatsa ndinu osadzikonda mwakumbukila amai amene mumagwira nao ntchito kt khalan apa wina kukhala pa bwino sangapange zimenezo kutengela udindo umene muli God bless you ndi zimene Mulungu amafuna

  • @josephmunthali2526
    @josephmunthali2526 2 หลายเดือนก่อน

    God bless you Dr Michael Usi, for remembering the people who you worked with, when God changes your story, it's always Good to remember where you are coming from.

  • @victorkachepa3515
    @victorkachepa3515 2 หลายเดือนก่อน +3

    All hospitals have the same problems. The approach should be targeting the general problem not individuals.

  • @AlfaKatula
    @AlfaKatula 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mwa ma drama momwemo zikutheka bas😂 Nice

  • @frankkhanja750
    @frankkhanja750 2 หลายเดือนก่อน

    Well done Mr Kingsley Phariyao

  • @louisgolden
    @louisgolden 2 หลายเดือนก่อน +2

    Kodi mukuti awa ndi apurezident a UTM nanga bwanji sakupita kukaona Malo womwe anapangika Ngozi kuwuzana ndi kwantere nzakeyo ? Amalawi khalani ndi nzeru awawa ndi afiti

  • @GiftSalijeni
    @GiftSalijeni 2 หลายเดือนก่อน

    Mr kingsly phaliyao kuyakhula kwabwino with confidence that's wat we want to the youths

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll หลายเดือนก่อน

    Well done a VP

  • @samchibenene4458
    @samchibenene4458 2 หลายเดือนก่อน

    Am happy mr president sumaona mutundu God bless you

  • @edwinsambo3691
    @edwinsambo3691 2 หลายเดือนก่อน +1

    VP visit Mitundu hospital, the situation is pathetic

  • @chikuchimbatata3169
    @chikuchimbatata3169 2 หลายเดือนก่อน

    a VP mukuyesetsa being humble

  • @NigatuUmuro-wh8wi
    @NigatuUmuro-wh8wi 2 หลายเดือนก่อน

    Mai wathuyo wawerengeratu pamenepo..ndiye osangobwerera mma jokes

  • @SiphamandlaNcaphayi
    @SiphamandlaNcaphayi หลายเดือนก่อน

    Bwana usi akanena zinthu zimasintha ndipo zichitika

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh 2 หลายเดือนก่อน +2

    Mwachedwa zedi nthawi mulibe mwaiseweletsa nokha,busy kusula ma plan ophera anzanu basi.

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk 2 หลายเดือนก่อน

    Bwana mukamaliza u vp mupite ku ubusa bac missionary

  • @JustinChiwale
    @JustinChiwale 2 หลายเดือนก่อน

    Kkkk ichi ndicha drama ndithu eeee mai mulipo KKK

  • @WilliamMwendera
    @WilliamMwendera 2 หลายเดือนก่อน

    VP visit agriculture offices especially the EPA'S

  • @qhwireless961
    @qhwireless961 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mr kingsly ndakuonani

  • @CathrineKumwenda
    @CathrineKumwenda 2 หลายเดือนก่อน

    Thank Mr VP focus on

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 2 หลายเดือนก่อน

    Bwana ndani yr mad akupha ameneyo kafuse chilima 😢😢

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 2 หลายเดือนก่อน

    Kukhala vice president ndikwabwino, mpaka usi wayamba kunenepa

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 หลายเดือนก่อน

    Kuyendera zipatala ndi kumeneko koma mankhwala mulibe so zosowekera ndi zambiri mbiri

  • @ntombiunice8637
    @ntombiunice8637 2 หลายเดือนก่อน

    Zopempha zachuluka 😂😂😂

  • @franciscomalola92
    @franciscomalola92 2 หลายเดือนก่อน

    munthu angoyenda inu kungoona kt ndi vice president zopempha mbwee koma palibe chimene chikuchitika zopusa bc

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kumayamika usi tchito akuyigwira big up bwana VP

  • @louisgolden
    @louisgolden 2 หลายเดือนก่อน

    Angonena zinthu zosathandiza anthu tikufuna pa galaundi

  • @EllahEllah-hu7hi
    @EllahEllah-hu7hi 2 หลายเดือนก่อน

    Mwachedwa mutalawila mudakapanga zimenezi dzana,,koma ma plan anu akupha tiyeni uko

    • @ronaldordinga6537
      @ronaldordinga6537 2 หลายเดือนก่อน

      Ndipo wachedweratu,,, olo apange motani chomwe ndikuziwa ine choti akuziwapo kanthu pa imfa ya CHILIMA😢

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 2 หลายเดือนก่อน

    My vote vice president

  • @ChrissySalimu
    @ChrissySalimu 2 หลายเดือนก่อน

    Mmmmmm anapha nawo chilima ameneyo ukoooo

    • @SarahGolden-rp1pu
      @SarahGolden-rp1pu 2 หลายเดือนก่อน

      Ukuchedwa ndikumunena manganya musiyeni muthu agwile tchito yake

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 2 หลายเดือนก่อน

    Aaaaaaaaaa kuononga ndalamako malo mogula mankhwala kuika muzipatalamo alibizy kujoya zazii

  • @ChimtamboWiliam
    @ChimtamboWiliam 2 หลายเดือนก่อน

    Kodi mukamati bwana president akhala liti?

  • @ChimtamboWiliam
    @ChimtamboWiliam 2 หลายเดือนก่อน

    And ma president alipo angati ku mbomako?

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 หลายเดือนก่อน

    Usi ndi wachibwana achedwa ndipo anthu akuziwa zonse

  • @GiftHaward
    @GiftHaward 2 หลายเดือนก่อน

    Zoona Pena kumayamika usi akuyesa ku mbali yake

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er 2 หลายเดือนก่อน

    Zandale zimenezo anthu akumiduma amenewo

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 หลายเดือนก่อน

    Mukupempha manganya uyu akusangala ndingongole angoyenda yenda opanda manyazi mankhwala kuzipatala mlibe basi kungofusa mumayamba liti ntchito abwana ali kuti pambuyo mumva ngongole zafika aliyese alandila pano ali ku nkhota kota akubwera kunu.
    Bwanji ndalama zimene akuyenda yenda ndi muchimwene wake kuti agule mankhwala

  • @FWhite-w3l
    @FWhite-w3l 2 หลายเดือนก่อน

    kodi anthu enanu mukuti usi ntchito akuigwila kodi ntchito yake iti poti sitikuiona Amalawi muzikhala ndi nzeru because usi akungoyendayenda kumupangila Kampen chakwera this is nonsense

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 2 หลายเดือนก่อน

    Yowoyani akulu wane, kwithu ku mpoto

  • @joyahmedjoma4615
    @joyahmedjoma4615 2 หลายเดือนก่อน

    Nanga ife ameneo?

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk 2 หลายเดือนก่อน

    Mukukwanira

  • @GreyMwanyimbo
    @GreyMwanyimbo 2 หลายเดือนก่อน +1

    Usi ntchito akugwira

    • @joyahmedjoma4615
      @joyahmedjoma4615 2 หลายเดือนก่อน

      Akugwira kuti kapena akuyenda yenda ndikuvesera mavoto wabwelesa chikangawa?

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 2 หลายเดือนก่อน

      ​@@joyahmedjoma4615iweyo ndiwe gulukunyinda umafuna azivera PA phone zimenezo mutuwo uzigwira tchito si za sale izi ndizopititsa mtsongolomoyo WA athu osati zachibwanazo zogwetsa ulesi athuzo uzipanga pakhomo Palo wava

  • @Andule-v4n
    @Andule-v4n 2 หลายเดือนก่อน

    God bless

  • @CharlesGremu
    @CharlesGremu 2 หลายเดือนก่อน

    MA kuipatsa moto

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 2 หลายเดือนก่อน

    Usi munthu wachitemwa chiuta wakhale namwe

  • @ChisomoMsiska-oi2vg
    @ChisomoMsiska-oi2vg 2 หลายเดือนก่อน

    Usi ndimunthu ofunikadi kukhala president ndimunthu ozichepesa komaso oziwa nchito yake