Inetu ndigwirizana ndi zomwe dj munyanane wanena anthu sakungo lowa mwa kufuna kwawo koma mphavu za akumidima ndalama yomwe ikugawidwa ku mcp ili ndi chikoka chakumidima
Ndi bodza ilo kuti oyimba anagulidwa, nthawi ija Dan Lu anali ku DPP tinganene kuti dpp inamugula? , munthu ali ndi ufulu wolowa ndi kutuluka, ndikudabwa kuti anthu mumangoti a Malawi adabwa zoti mwakuti, aaaaa.
O imba omwe Ali bize kuimba zo yamikila chakwera ameneyo ndi kalu obanda uzimu ma udasi nonse ukuyamikira chakwera chikangawa busa unyenga sikaliyoti okuba anthu osalakwa nonse afiti
Dziko la malawi ndi la democracy, chovuta ndi chiyani oimba kugwira ntchito ndi boma lolamula? Zaipa lero chifukwa anthuwa akutumikira boma, koma mmbuyo monsemu analipo oimba amene amayamikira DPP, PP, UTM vuto lanu ndi chiyani?
Grace Chinga bwera udzawone kuno zijazi😢
Ndipotu adaulula zija ndi zimenez
Inetu ndigwirizana ndi zomwe dj munyanane wanena anthu sakungo lowa mwa kufuna kwawo koma mphavu za akumidima ndalama yomwe ikugawidwa ku mcp ili ndi chikoka chakumidima
Ndiwe opusa kwambili ndichi fukwa chani zipani zimakhala ndi director of recruitment kapena simumadziwa tanthauzo lake
Or onse oyimbawa atapita ku mcp ife ku mpoto sitikuopa chifukwa tikudziwa kuti chakwera sakudziwa kuyendesa dziko
Big up boys
Boma ndi lomweli, zoona, a Malawi chimene tikufuna si president wina koma chitukuko basi , let us work with Chakwera, wonani pa ground
Boma ndi lomweli
Galu iwe kagwileni uko mboloyako ndi MCP yakoyo
Zaziii president panda mnzeru ngati uyu ine chibdwire changa sindinamuonepo
Ngati kwalembedwa kuti pita awine azawina
Tamutulukabeeeeeeeeeee
❤ umakwana iweyo
Athu akusatako ndalama koma ife MCP ayi taikana
🎉❤
Ndi okha okha a illuminate awa pitani ku masamba awo antchezo mupeza kuti ndi apasi panyanja pompo
Grace mulungu akudariseni mnaunikira amalawi kom kusava kwa2 zizindikiro zaoneks mot mavuto ndiambili
Zonsedzi dza temporary
Ukunama aise legacy yavaya.azikufira ndi a mcp akowo aise watha basi in music industry in malawi believe you me.
Ine ndili pano kuvetsela mwa tchelu 😊
😅😅😅
Just take this note.....OIMBA SANGAWINITSE CHIPANI.......🎉🎉
Kkkkk MCP kulibe anthu ambiri oti akhoza kuwavotela mpaka kuwawinisa
❤❤❤❤❤
Oimba alingati opanga sewerotu achina manganya umaona ngat muli limodzi kumapeto umazangomva odya zake alibe mulandu🤣🤣🤣🤣🤣
Rip Grace Chinga😢
Ndi bodza ilo kuti oyimba anagulidwa, nthawi ija Dan Lu anali ku DPP tinganene kuti dpp inamugula? , munthu ali ndi ufulu wolowa ndi kutuluka, ndikudabwa kuti anthu mumangoti a Malawi adabwa zoti mwakuti, aaaaa.
😂😂😅😅 oimba abalilalika ,
Mdyeleni chakwera 😂😂 azalila munthuyu kwabasi,
Zachamba izi ma artist wose alowa mcp athela pompa .
komano boma ili kuli ndalama osati zochedZ
Koma nanga amavota ndioimba kod 😂
Akuti unali mgwilizanotu ndi oimbawa ndiye ndi ndani safuna moyo kkkk
Onsewo akugulidwa ndi Mcp, zambia, Nigeria, south Africa and Malawi
Kkkkk koma ndalama ziphesa anthu
Akalowa ku dpp ndekuti sana gulidwe koma mcp agulidwa eti nanunso mukhoza kumagula palibe akukulesani
Or chakwera azawine or ayiii koma yemwe wawinayo azakhalabe Apure anthu basi mlungu tiyendereni😊
falling down of bab lone
Adaga ndalama daniyo
Mr chikangawa wagwa bsi or atagula oyimba sangawinise zisankho
Hi what language are you speaking
Azigula oyimbawo aziwe kt akuluza ma followadzi oyimba ofuna ndalama osati kuganizila amalawi akukhutitsa mimba zawo.anthu akudya chiteze mamizimu ena mango athira juwisi.
Iweso orengenzawe bhori yako watumidwa
Iweso ndiwa mcp eeet
azamuvotela garu oyimba omwewo
Bwino lake ndi oyimba lokoni atatenga ose oyimba Malawi munu sangawine
Peter sangasiye kuwina chifukwa cha woyimba onse awagule ife tili pambuyo pa dpp
🤕🤕🤕
Tamutukabe ameneyo
Sazabwelelaso tiziwona bola osapepesa
Iwetu ukufuna kuti anthu akutame😊 boma ndilomweli man
Grace uja munaphela zoonadi
Kodi oyimbawa mukufuna azilowa DPP poti ndichipani chakubanja kwanu,akalowa MCP aguridwa Mesa DPP yalamulirako dziko lino 14 years kusinthana pachibare ngati ufumu oyimba makuyimbirani aja mumagura nde mulibe ndalama zogurira ngati mumachikonda chipani chakubanja kwa muntharika athandizeni muwagurire oyimba akunja
Zikuthanthawuza kut Giboh adawuza Nkasa kuti ku Mcp ndalama yapweka ayi zikomo... basi ife tizidya chitezechi achuke iwowo😭
Nanu a sam muyaluka ndi channel chanu chomangopanga za wanthu
Kodi iwe zandale siziyeni uzingopanga za oyimba
Mwina wakula ndi umphawi koma oimba sayenera kuonetsa mbali choncho,,zimatsitsa carrier yawo ngat oimba
Oimba sangawinise
ndiye vuto mchani
Kugulidwa sikhani ndiokavotayo😅
Ku MCP kuli ndalamah zochuluka kadyeni km never MCP sikuwina,,, inukadyeni zabooka
Oyimba ambiri pano alibe ndalama ndiye akufuna ndalama.
Anthu ngati mukufuna kupitiriza kudya chitedze zanu zimenezo
Basi people are after money, leave them
Giboh nyimbo xako timazisatila koma walowako ayi
Asikefa nde tataya kare muona mukatulusa nyimbozo ine pheeee kumastand
Atenge oyimba onse tilibe nazo ntchito ife
O imba omwe Ali bize kuimba zo yamikila chakwera ameneyo ndi kalu obanda uzimu ma udasi nonse ukuyamikira chakwera chikangawa busa unyenga sikaliyoti okuba anthu osalakwa nonse afiti
Ulendo uno zisinthe come 2025 adzakhale komweko ku mcp koz definitely ikuzakhala pa bench mcp yo ena achilendo atakhala pa driver's seat.
Eeee zilikotu
Koma abare aziagura athuwo koma vot sazayiwona 2025
Ndiye nanga giboh akupezekamo bwanji
Dziko la malawi ndi la democracy, chovuta ndi chiyani oimba kugwira ntchito ndi boma lolamula? Zaipa lero chifukwa anthuwa akutumikira boma, koma mmbuyo monsemu analipo oimba amene amayamikira DPP, PP, UTM vuto lanu ndi chiyani?
Agulidwa poti ndi MCP ndi DPP adangolowa ndale zaku Malawi zimenezo mtima wajerasi okhaokha basi
Ziko lapasa
Koma ghibo ufuse anthu akutulukidwatu oooo wakura watha
PETER MUNTHULIKA AKAWINA NEXT YEAR PLEASE STAY AT MCP ....
Paja osewatu anachulidwapo ndi mayi gres chinga ndiye ndi zosadabwisa anthuwa ndi satanic ndintu mosakaika chifukwa zonse zaonekela poyela
kupusa ma muscian akumalawi
Mwina zipani sizimadziwa ntchito ya director of recruitment.... Ndikukopa anthu kuti aloee chipani timagwiritsa ntchito xipangizo zonse zomwe tilinaxo kukopa anthu ngati inuyo mulibe shauli yako
Ma chendeyake Dan lu ndi gibo matumbi nose pa ntumbo panu
MMAWA
Asiyeni oyimba akalowe ife sitikupitako popano tiwagwesela limozi
Ntaba yakoyija. Uwabaye chijakeseni anawa akuziwe
Nanuso zigulani anu oyimbawo
Iweso wadziwabwanji kit wasataniki kod aliposo atsogoleri abwino aaaa iwe samala wava
Mcp ikundigirigisha anthu akuthawa dpp chifukwa cha kalindo
Koma agalu oyiimba shaaaa satikonda ifeee amalawi tooonse ambiri oimba aiiiiiiiii niaagule zitsiru apite pamenepo oimba ambiri ukuopa kufa ni satanic money from galu bushiri
Boma ndilomweli koma pd tkusitha
Ubwino wake sitimadya nyimbo
guys music industry Nd ya. Bushiri mkuziwa nose. Nde bushiriyo Ndi chikangawa alilimodzi msadabwe. Oyimba , amene salowa MCP Ndi ulendo
Shinkangawaw satanic yinkuphangsa simeneso serious
😂😂😂😂😂😂😂
Bodza si dziko lonse mwanama
Ineyo wakupoto usamat Ifé kupoto ngat unatifusa ai iweyo ndiye wadpp.osat.kupoto ngat tonse ai pangazako
Ndizaurura ananena
Ndie Pali vuto kod??, opposition ikulephera kuwagula bwanji
𝐀𝐤𝐚𝐧𝐚𝐤𝐡𝐚𝐥𝐚 𝐤𝐮𝐭𝐢 𝐚𝐥𝐢 𝐩𝐚 𝐦𝐭𝐞𝐧𝐝𝐞𝐫𝐞 𝐬𝐢𝐛𝐰𝐞𝐳𝐢 𝐚𝐤𝐮𝐩𝐚𝐧𝐠𝐚 𝐢𝐳𝐢 𝐦𝐚𝐯𝐮𝐭𝐨 𝐤𝐨𝐦𝐚𝐬𝐨 𝐳𝐢𝐤𝐮𝐤𝐰𝐚𝐧𝐢𝐥𝐢𝐬𝐢𝐝𝐰𝐚 𝐧𝐝𝐢𝐳𝐨𝐦𝐰𝐞 𝐚𝐤𝐮𝐜𝐡𝐢𝐭𝐚𝐳𝐢 𝐜𝐡𝐨𝐦𝐰𝐞 𝐮𝐝𝐳𝐢𝐰𝐞 𝐦𝐜𝐡𝐚𝐤𝐮𝐭𝐢 𝐦𝐮𝐭𝐡𝐚𝐰𝐢 𝐲𝐚 𝐁𝐢𝐧𝐠𝐮 𝐤𝐨𝐦𝐚𝐬𝐨 𝐉𝐨𝐢𝐜𝐞 𝐁𝐚𝐧𝐝𝐚 𝐦𝐮𝐭𝐡𝐚𝐰𝐢𝐬𝐨 𝐲𝐚 𝐏𝐞𝐭𝐞𝐫 𝐢𝐳𝐢 𝐤𝐮𝐧𝐚𝐥𝐢𝐛𝐞 𝐤𝐨𝐦𝐚 𝐜𝐡𝐢𝐟𝐮𝐤𝐰𝐚 𝐜𝐡𝐚𝐤𝐮𝐤𝐰𝐚𝐧𝐢𝐥𝐢𝐬𝐢𝐝𝐰𝐚 𝐤𝐰𝐚 𝐦𝐚𝐥𝐞𝐦𝐛𝐚 𝐭𝐢𝐲𝐞𝐧𝐢 𝐭𝐢𝐳𝐢𝐩𝐞𝐩𝐡𝐞𝐫𝐚 𝐦𝐨𝐨𝐧𝐚 𝐦𝐭𝐢𝐦𝐚 𝐦𝐮𝐥𝐮𝐧𝐠𝐮 𝐚𝐭𝐢𝐜𝐡𝐢𝐭𝐢𝐥𝐞 𝐜𝐡𝐢𝐟𝐮𝐧𝐝𝐨 𝐜𝐡𝐢𝐟𝐮𝐤𝐰𝐚 𝐢𝐳𝐢𝐳𝐢 𝐬𝐢𝐳𝐨𝐨𝐧𝐚 𝐦𝐮𝐥𝐮𝐧𝐠𝐮 𝐚𝐭𝐢𝐤𝐡𝐮𝐥𝐮𝐥𝐮𝐤𝐢𝐥𝐞 𝐛𝐚𝐬𝐢
Akagwele UKo amenewo akufuna angodya ndalama zaphweka ku mcp km zikatha abwelela
Zowona
Komaye mau kukhalangat ugalamule iweyo adzawineyo ndameneadzlamuletu bas
Ndilamulo laku satanic onse oyimba akulambila chakwera ili ndi lamulo la bushiri
Ali ndiufulu olowa chipani chilichonse
Ndipo satanic yafikapo ku Malawi kkkkkkkkkkk
Asiyeni 2025 boma Dpp
This is a bad development of the music industry our own artists should differenciate between arts and science
Dpp iiiiiii yilibe nkhalidwe
Koma dan lu iwe ndimuyawo ineso ndimuyawo petoga ryenu bwanawe wamvatu
zilibe ntchito zimenezi