U have more common sense🎉🎉 where were u all this tym we r suffering 😢😢😢...may God continue protect you so that you may succeed in your wisdom❤❤❤ much encourage to u ❤❤❤bravo young man don't let anyone to stop u .
You are blessed, Mulungu akuze malire ako,ukutilankhulira ife amphawi,anjala ofinyika ndipo mose to inayambira kulira Mai athu sanveka,bolaso mau amunthu wakhungu uja ankati Yesu mwana wa David ndifuna mundichitire chifundo,ndipo Yesu anamuchiritsadi Koma Ife sikukunveka kulira kwathu I hope pakufunika chinkuza mawu, Lord have mercy on amphawife
Let's find ways to make u president of Malawi. Your ideology is like that of Bukina Faso president, YOUNG BUT MATURE. MAY ALMIGHTY GOD BLESS YOU AND THE PLANS THAT YOU HAVE FOR MOTHER MALAWI.🎉🎉
Mtolankhaniyu ndi mwana pa kafunsidwe coz had little understanding than attacking. I know time was limited so @Denis Mahata find time to articulate these to the youth who are ready to stand with you on this mission for it is clear and live saving move Malawi nation seeks. Bible saya mphonje imodzi sichedwa kuduka poyelekeza ndi zambili so the vision will still grow in many lives and it wont be killed ndi anthu adyela osakonda dziko lao
Pakufunika civic education yamphamvu kuti munthu ayambe kukumvani zomwe mukunena Ntolankhani uyu sakukumvani zomwe mukunena Maganizidwe anu ndi abwino chifukwa ndimaganizidwe monga anthu aku mmawa I support you 100%
Denis iweyo ndiwe David wanthu nthawi ikwana uzatimenyera nkhondo afilisiti achina goliat tikuwaona wa ulibe ma boardgurd ulibe chitetezo chilichonse koma osapa osatopa osafooka board gurd ulinayo ndiye mwadzi wa yesu ndikulengeza protection from above mulungu akusamalire mphamvu iliyonse yakumidima isapambane pa iwe, ndiwe udzapulumuse ana anthu ngati si ife
Ine ndikupemphera kuti amene adzango bwera mmaganizo okoza zoti aphe munthu wathu uyuyu, Kungo yamba mkukhala ndi ganizo loipalo...nthawi yomweyo mnkuntho wa YEHOVA ukupeze kaya ndi mzungu kaya wakuda...usayesele kutiphera munthu wathu....mzungu ndi satana
Izi apule anthu sakuziziwa olo moti akamamva izi akudabwa nawo mwana uyu muyitaneni akumphumzitseni simutsika value school siintha komanso ana amakono alindi mzeru osawaderera musamapange zakale this is new generation yesani kusintha malumulo a 1964 bweresani ena ndi nyengo mmene ilili plz
I am with you ..A servant .And also, Franklin, you are becoming a very wonderful Journalist.
We need all small energy big boys like him my loya don't forget Mr Kamangila
Finaly i met my like minded ..thank you sir i keep in touch
U have more common sense🎉🎉 where were u all this tym we r suffering 😢😢😢...may God continue protect you so that you may succeed in your wisdom❤❤❤ much encourage to u ❤❤❤bravo young man don't let anyone to stop u .
Mnyamataa! Wachepa nazo....Dziko ili likudana ndi anthu abwino,likufuna asatana okhaokha,omabisa choonadi ndikumaombela m'manja chilichonse kamba kamantha......Akafansiyanjife tiyeni tiwasiile eni ake omwe sadzafa....
Ooooooh what wonderful statements! Continue the way you started, I just love it
Malawi protect this young man he will help Africa, Solomon Mwanza Zambia.
𝑰 𝒍𝒊𝒌𝒆 𝒕𝒉𝒊𝒔 𝒈𝒖𝒚 𝒉𝒆 𝒊𝒔 𝑹𝒊𝒈𝒉𝒕
Osaopa,osatopa,osafooka generation
I like this guy let's support him
You are blessed, Mulungu akuze malire ako,ukutilankhulira ife amphawi,anjala ofinyika ndipo mose to inayambira kulira Mai athu sanveka,bolaso mau amunthu wakhungu uja ankati Yesu mwana wa David ndifuna mundichitire chifundo,ndipo Yesu anamuchiritsadi Koma Ife sikukunveka kulira kwathu I hope pakufunika chinkuza mawu, Lord have mercy on amphawife
Munthu uyuyu wandisangalatsa kwabasi and I like pa mfundo zomwe akunena ndizogwila mtima
This guy mmmmm. Ndiwanzeru zakuya eshii
Let's find ways to make u president of Malawi. Your ideology is like that of Bukina Faso president, YOUNG BUT MATURE. MAY ALMIGHTY GOD BLESS YOU AND THE PLANS THAT YOU HAVE FOR MOTHER MALAWI.🎉🎉
This guy is very brave like Traole, keep it up God is with you.
The very chi best man thank u may God azikudalitsani pa nzeru thanks again
I like this guy, he is very fine
And it's true
May God multiply kind of these pipo
Mtolankhaniyu ndi mwana pa kafunsidwe coz had little understanding than attacking.
I know time was limited so @Denis Mahata find time to articulate these to the youth who are ready to stand with you on this mission for it is clear and live saving move Malawi nation seeks. Bible saya mphonje imodzi sichedwa kuduka poyelekeza ndi zambili so the vision will still grow in many lives and it wont be killed ndi anthu adyela osakonda dziko lao
Man don't let anyone to corrupt yourself, stand a great man like a pillar no shaking 😊
Times exclusive should plan , Brian Banda, to talk with Denis Mahata,
We are waiting anxiously.
Uyu can be a good leader like Ibrahim Traoore
We need a person like this to be a president in this our country, a brave man.
We all need to see things like this guy. He needs support
Mmm I like this guy ndiozama mmaganizidwe ❤
Chilungamo chimamasula
😢 that's it kulimba mtima nde kofunika aliyese azafa palichbwino Pali chowawa keep it up mahata
May God bless you fro what your doing 🙏🙏🙏
Let's support him...
Much love ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Fantastic man very good
Good coming man❤
This is Genius ❤
I like this guy, let's support him
This guy is Malawian indeed let's support him
This guy is a genius
Big 2 Mahata and kamangila GOD protect you guys
Mahata is a saviour of our time
My vote 🎉
May God protect this soul at anycost
That's very sharp minded person
Bro long life 😊 ukuchita explain momveka heavy,,,, being age mate umakwanira keep it up dude
Big boy i like yr answers. Nyamata wa mzelu kwambiri
Am supporting him.keep it up.
NEW G . Z LET SPORTING HIM 🎉🎉🎉🎉
Thanks zodiac chifukwa chopanga expose this guy,he is indeed very intelligent
Ndipo tikuipwasula constitution yonse ija and start afresh!
More love 💕 my brother mtanyiwa boni kalindo bakili TV mukupuzinsa ana kulimba mtima
Osaopa bro pitilizani mpaka cholinga chako chizakwanilisedwe Allah akuzikutetezani sangalole muphedwe ngt mmene akuganiziramo keep up bro
We need people like him let's support 💙
Mahata you are our God sent.....be our president
Kamangila come here
Mr Mahata, you are very intelligent. Please, lembani bukhu mu zilankhulo zathu kuti Malawi isukusule. What you are saying is very helpful.
Mahata my vote
Ndikadakala kuti tikusiwani bwesi ndikujoina fudoom imeneso umuthu ndiumenewo ❤mulungu akudalisene moyo wanu
I like it I would like to join this movement
Pakufunika civic education yamphamvu kuti munthu ayambe kukumvani zomwe mukunena
Ntolankhani uyu sakukumvani zomwe mukunena
Maganizidwe anu ndi abwino chifukwa ndimaganizidwe monga anthu aku mmawa
I support you 100%
Great ✊
Chilungamo ichi💯
Uyu ndiye pongolini wathu palibe amene angamake pa Mr mahata ndili pa mbuyo pako
Bingu is still alive
Munthuyoo ndiwoganiza guyz mwanva
I'll join this guy soon
❤❤❤❤❤Malawi iri ndi anthu azelu kwambiri
Munthu akufa kuchipatala chifufwa chosowa LA wa 2000 , pamene iwo akumupatsa T-shirt ya 5000, akumuona munthu ngati vote😭😭😭😭😭
This guy, Atupele and DK can transform Malawi
Nanu Atupele ngopepela uja same as Chakwera, bola enawa.
Your the best wabwela iweyo pitiliza bro ndipo uli bho❤❤
Great minds
I like this guy so much
Ku Malawi tikufunikila anthu ngati Mahata, pitiliza kuphunzitsa a Malawi, ndipo mulungu akupatse nzeru .
Umatha mulungu akudze malire ako zigawengaz zisakusokoneze mu dzina mbuye kristu wamoyo
Mahata is Malawi's Traore
Koma tikuona zinthu mkuzigwirakomwe😂🙌🙌😆
My vote basi
Tell them reality you think like what am thinking brother ❤❤
Denis iweyo ndiwe David wanthu nthawi ikwana uzatimenyera nkhondo afilisiti achina goliat tikuwaona wa ulibe ma boardgurd ulibe chitetezo chilichonse koma osapa osatopa osafooka board gurd ulinayo ndiye mwadzi wa yesu ndikulengeza protection from above mulungu akusamalire mphamvu iliyonse yakumidima isapambane pa iwe, ndiwe udzapulumuse ana anthu ngati si ife
Good interview
Osaiwala kut mahata a abwera kudzakhala 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Ur the best
U deserve to be president of my country 🇲🇼 remove makepe
Awawa ndi afana aganiza bhoo, thinking machine
Kabambe
Kamangila
Mahata
These are Malawians that can change things. Komabe tili mmasiku osilixa zambiri zipitilirabe kuipa
Uyuyu ndi machine mmmmm
Dr mahata muli mwala inuyo
Big up... Kuyankha/kuyankhula mosabalalika
Bingu he back again
More 🔥 ma guys
Nice Man Wake up Upitilize ziribwino
Ine ndikupemphera kuti amene adzango bwera mmaganizo okoza zoti aphe munthu wathu uyuyu, Kungo yamba mkukhala ndi ganizo loipalo...nthawi yomweyo mnkuntho wa YEHOVA ukupeze kaya ndi mzungu kaya wakuda...usayesele kutiphera munthu wathu....mzungu ndi satana
Citizen yamphamvu imeyo ayise🎉🎉🎉
Koma musatiphele mwanayu pls
First sentence yachita kuonetsa kt mulizinthu 🔥
Mwana wa nzeru osati chitsiru phwala chakwera
This guy is very intelligent
Mwana,,,,uyu,,,ndamukonda kwabasi,,,,zolankhula zake zimandpatsa tsebwe!@@@@
Koma awa ndi boss
Great Man
He sounds like Obwande
Am interested with this man
Anthu omwe akufunika ndi oti agwire nawo ntchito, ma comment alibe nawo ntchito , osaopa , osatopa , ndiye khani zake .
Izi apule anthu sakuziziwa olo moti akamamva izi akudabwa nawo mwana uyu muyitaneni akumphumzitseni simutsika value school siintha komanso ana amakono alindi mzeru osawaderera musamapange zakale this is new generation yesani kusintha malumulo a 1964 bweresani ena ndi nyengo mmene ilili plz
Thinking outside the Box
Genius man
The unjust law is no law at all. It must be disobeyed.
Fumu Solomon mahata
Ulibwino mulungu akusunge ndi moyo