Mkufuna udindo Kuti uti udzakhare wa mbuyako wanyanayo kulibe mbuzi Inu kulibe kutinamidza ndipotso Boma ndi lomweri basi kulibe kusintha or mtaphaka matope
Timakusatilani mumalimbisa mtima, koma pali vuto limozi, mumachedwa kulankhula cheninicho cha nkhaniyo timadana ndi mcp, mongoti bomba Koma kuili ziii.
Mukamaliza kunamizanako mupite mukawamange onse ndikumuyika chilima papando kachikena fake munatani atanyiwa kubwela live ndikupeleka mabodza anuwo mutathe ndinu osati mcp Basi mumangonamiza anthu pa social media Basi anthu mkumavelani
Assemblies Of God mumkasungira chigawengatu apa. Zovuta.Pano mukamasankha mtsogoleri wampingo wanuwo mupewe kusankha anthu olowela pa window. Chikangawa ndi ameneyu.
Mumatiimilila antonyiwa. no 1
More fire ntanyiwa
I love u ntanyiwa work hard to succes
Mkulu iwe udzapenga chifukwa zomwe kumanenazi umboni weniweni sukuoneka. Cholinga chako ndikusokineza anthu mdziko muno. Nkhani ya chisoni ngati imeneyi munthu kumanena akuseka,ndiwe munthu omvetsa chisoni ndi opanda nzeru
Mr Ntanyiwa mukamaykhula muzikhala siliyasi tikudalila inu
Tiuzeni time nawoo ??tili limodzi ??
Carry on mr Mtanyiwa tell us the truth. Ipatse motoooo.
A ntanyiwa so ngamwano ati kumanthawaso azikwanje kkkkk
Commolent mutanyiwa please West our time
ndufuna nzaone mathero a anthu opanda pake,mfiti,ana achionongeko,njoka
ndipo mmodzi wa aliyense wa iwo asadzalilidwe maliro awo
always listen limpopo fm more fire
Ipase Moto mtanyiwa
mmm mizimu wa biyeni ndi ena ONSE 8 iziusabe mu ntendele🙏🏻🙏🏻
M'busa Nyilenda Ndi m'busa wapansi panyanja ameneyu .... More fire boss Comrade Mtanyiwa
Walakwa chaninso analakwa kutuluka mu commission kapena
Ndipo inu
I salute Mtanyiwa tell Malawians the truth Chakwela is Stupid together with his cabinet resign
Bwana, Ntanyiwa, do not afraid, God is with you always you talk to Malawians.
Ambuye chonde tionetseleni za imfa ya president wathu wokondedwa Dr Chilima
Mulungu sangatisiye tokha ayi ndipo dzimu wamalem chilima uwuse muntendele mr comrade ♥️
Ntanyiwa tell us the truth don't play with the life Dr chilima
Ingoyambitsani chipani chitsiru chachikulu ndiweyo ukuona ngati tose tingakhale aku mmwera galu iwe.
Overayoso ndi chitsilu ngat iweyo 😂
Amaona ngat akapha chilima adutsa mophweka akunama tili nawonawo olo kubela sizitheka mulungu adakali kumbali ya chilima ndipo tipanga zoti mzimu wake uuse ndi mtendere kutchaya chakwera kugwetsa chaka chake ndi chino
Zaboza izi
Koma aise sumakhala serious pa nkhaniyi umakamba mwachibwana.we need serious pple in this case.
Koma ndikamamuwona chilima moyo wanga umawawa uyu akadzutsa malawi
Ntanyiwa ndi nyatwaaaaaaaa
Anthu opusa amene aja mxeeew akuona ngat miximu 9 ndimasewera
Anthu awa amangidwe life prison ndi kulandidwa katundu yense anyani akupha a MCP awa akafele Koko ku ndende
Zoonadi mwanenazo indeeee alandidwe katundu kuphatikizapo ma business awo ndi misonkho ya a Malawi imeneyo.
Asasiiridwe Chiri chonse agalu amenewa ndipo asapitenso kundede ai tiziwaona Ife amphawife atabva zikag'a mmakwalalamu agalu oyipa amenewa
Chilima anafa Ngati bonzatu mmmm
Nyansi sizikwililika
Inu
Uyuyu ndizamutukwana one day chifukwa amachulutsa kuyankhula, Malo Moti a bweletse ma Audio akwanenawo timvere 😢
For free and fair Sept 16 polls, let's bring national Solidarity in Malawi.
Iwe ndi wamisala
Audio yokhayoo ndi imene itapange campaign Hahaha
Makwana twanyiwa
You talk too much spices,
Rather just go to points.
You make others to loose interest
Or atakana bwanji sizingamveke black box inabisidwa chifukwa chani?
Ndiye munthu angoseka uvaponji apa km znaz ifa yazanu kumaseretsa zoona
😭😭😭
Mbamband
Tikudikira kumva ma audio amenewo
Ng'alula ave akuona ngat anabisala kom msana ukuoneka
Atakupezani aza pompa ndi magazi Anu omwe kkkkkk
Ngt ndavap audio ine apaaa uyus ND kape bwnj
Antanyiwa am sure azikwanje aja sagona Nanu tulo😊
Ayaluke amenwwa
🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔
nyimbo mukuchulutsa bro ntanyiwa
Ndie mutulusa liti canemayooo
Ing'aluleni aziweso amenewa
Che Nkhukuyu game yagatu.makobili muzidya muli cheucheu
😅 mcp ulendotu ulipo mukanemusakane
Achoke nyani ameneyi Ali ndi mangazi m'manja m'busa oyipa kuposa manyi
Kuposa satana osat manyi😂😂
Ndipo satanayo amachita kudadwa kuti awa beanjiñso mphamvu zimenezi akuzitenga kuti
Muzimuopa mulungu polankhula mandala ndizikoili zikukomela inu koma abaleawo akufuna atava chilugamo so osamasewela ndi khaniija please
Mkufuna udindo Kuti uti udzakhare wa mbuyako wanyanayo kulibe mbuzi Inu kulibe kutinamidza ndipotso Boma ndi lomweri basi kulibe kusintha or mtaphaka matope
Inde boma ndi lomwelidi koma president tikusintha mukanda anthu akupha inu
Mwatero ndinu
Busy kuyamikira za Chipiku ndi Chikangawa government kkkkkkkk
Ukhaula zikwanje zija mukayamba kudulila bango lokozela phasa
Zili pati
Pointless! You have nothing to tell Malawians,,,,,,, Why are you just repeating?
Just wasting my time for nothing kumvera chi clip cha 20 minutes kumangoti pali ma audio ma audio osawayika bwanji dzingosonyeza kuti mulibe
Timakusatilani mumalimbisa mtima, koma pali vuto limozi, mumachedwa kulankhula cheninicho cha nkhaniyo timadana ndi mcp, mongoti bomba Koma kuili ziii.
Zopusa basi awa amangotinamiza
Program yanu Ili bwino koma talking too much, muzipita pa point
Ndie timvele nawo kaya ma audio wooo
Mumankhwanababa Mulungu azikudalisani
Kwaikika kwamunthu kufa kamodzi kenako chiweruzo
Bm
Zili kuti nanga. Be serious
There is no secret under the sun.
Mukamaliza kunamizanako mupite mukawamange onse ndikumuyika chilima papando kachikena fake munatani atanyiwa kubwela live ndikupeleka mabodza anuwo mutathe ndinu osati mcp Basi mumangonamiza anthu pa social media Basi anthu mkumavelani
Zikupwetekani achule Inu muwululika agalu anyani munya muona mumavera ,a Nyanyiwa wathuyu amakutumani chikangawa eti kamuwuzeni anyeredwa Chaka Chino😊
Ndipo amcp ndi agalu kwabasi munthu oti anafa angakhalenso pampando kusayiziwa imfa mene imawawira agalu inu Mulungu akuwoneni mkuchikamwa kwanu komwe mukuyankhulira konyasako
Black box abwelese
Chipani cha MCP chipangidwe ban ku Malawi. Chaonetsa kuti sazasintha fisi ndi fisi
Koma chikangawaa party anatirakwira kwambili kutiphera chilima
Mizimu yakwiya
Munabwera kudzakhala inuyo chaka chake ndi chino 2025
Chilima anafa mopweteka
More fire Comrade Ntanyiwaaa
KUCHOKA PA UBUSA KUKHALA CHIGAWENGA CHOKUPHA
Mungoti chibomba kod chili kut bro
this lacks seriousness
Chakwera chimwendo zikhale ng'oma ndiwena wotero anaphadi chilima chifukwa cha mpando wa Chaka chino 2025 alemba mmadzi achule awelenga.
Ai ndithu
Kumakhala serious nanu,, pasana panu
Pansana Pake ukunenatu pa mako, chitsilu cha mwana
Ma audio umayika atali kwambi zimandibowa sindimasiliza kuvera
M
I'm.
Assemblies Of God mumkasungira chigawengatu apa. Zovuta.Pano mukamasankha mtsogoleri wampingo wanuwo mupewe kusankha anthu olowela pa window. Chikangawa ndi ameneyu.
M
I'm.