ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Onsewa ndi madoloPalibe woopsa kuposa mzakeI enjoy them both...koma anamenya mental yomwe analowela Bee Jay ndi katswiri
Amene tafila Ace jizzy let's gather here
Mwalowesa chibwana ku hip hop iyi nde ndi miss
Timavovera ace or tisanavere verse yake🎉
Acee ndidolo
@@kappascofie9131 Ace Jizzy sikunthu wamba
Odii! Kuno skill yochta kugogodela💥💥💯
Eeeeeee😂😂😂😂 kuti umvetsetse zomwe akukamba bee Jay ukuyenera kuyionera kangapo ase 😂😂😂✨✨big gee
Beat Selection Bee yampweteka..Jizzy Waigwira pakhosi, my opinion 👍
Verse kulemba mpaka mwezi koma verse ya Week (weak)BARS🔥🔥🔥🔥🔥
Ace Jizzy ndikatakwe
Ineyo ndi mkango/Ineyo ndi nkango-tii/Ndinu madolo koma ndinangozii-Ndikira/Kuti munangotchuka mwangozii mboba/Mukadya mango, mangozii-popa ( Mangoes)//😂😂
Ace waipha no cap
First time I thought Beejay 🔥🔥koma Ace jizzy uja ndwachabe eee
Skill ya odi ea kunoYocita kugogodera 💪😍😍😍
Who's here to support Bee Jay & Ace Jizzy! 🙋🇲🇼
Jizzy amaganiza modabwitsa🎉
Ku L city kuli ine , udolo ndi bello shirt 😂🎉🎉
Km jizzy ndidolo ka 100😂❤❤❤
Bee jay ma bars ofunika munthu olingalira kwambiri eee🙌🔥🔥
Straight takes a couple of listens to get what he is saying..dolo ka 7 ngati Namani.. 😩
Tikufunika ma dictionary
@@realonedon9604dolo osamba ka 7 ngati naman
Koma viwana iviii mmm 💥💥💥😂🙌🙌
Jizzy uja ulemu wake guyz🎉 your flower bro🎉🎉
Kudya legend, legend in the making, legend opuma nditcheni bataza engonga
Ace jizzy ndi chidolo kwabasi ase 😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤
Bee jay and ace jizzy fire🥰🥰🥰🥰🥰🥰 ma burz awawa Ali super glue kkķkkkkkkk
Those who say bee Jay killed it gather here we had a conference tomorrow
bee jay ndiakatundu adah eeh
Ndabalalikatu boss, conference yo inachitika kale kapena ichitika mawa?
Eeh all the best for had it tomorrow 😂
Ineso zikundidabwisatu ...we had a conference tomorrow??? Akuti chani Kodi lol 😂😂😂😂
Ace munvele mopanda mantha man jizzy killed it
Bee Jay -" kudya legend, legend in the making, legend opuma nditchen Balthaza 🤣😂😅"
Akulu awa amwene hahaha
Awawa amaimba zomwe amafuna wow ❤❤
Nyimbo zamadolo awawa umafunika unvele modekha, mopananda wina kusokoneza, Tinvela ngat tikayankha mayeso ndithu 🌹🔥🔥❣️
Ace jizzy ndikapolo hvy guys 😢🎉
Kom uyu ndi moto🔥🔥🔥luso la cream cream❤
OMG 😳🔥There is no Bee jay without Ace jizzy so stop comparing these dude they all contribute to each🔥🔥
Ulindi skill yo chita kugogodela😂😂😂🔥🔥💪
Bee jay kuyinjanjisa beat osazamutola😅😅😅👈👈🔥🔥
Eeeeh koma kaya ma dolowa amaganiza bwanji za hip hop,ndie momwe aipwetekela beat shaaah!!!🔥🔥🔥🔥🔥
Underrated chabe Koma izi ndiziphe mumativetsa kukoma 💥💥🇲🇼💪 fan wankulu 23🇲🇼
Bee jay ma Bars a hard ngat ukupeleka ma mbama kwa anawa😃😃💥💥👋
Jizzy ndiwachabe 🤣🤣🤣🤣 chapha ma guyz
ACE JIZZY ndoopsa ❤️🤞🏼💀
😂😂😂ikupita kwandan iney 😮😮 achin 😂😂😂😂
Ndipokwambili ase
Ndipo live
Zitsiru za ana inu. Kuimba ukuku ambiri akukuopani 😂😂😂😂💯💯💯
Eti man aaahh Satha kuimba away😂😂😂
Honestly Bee Jay has bars pomwe ace anapanga major mu flow💯🤝🏼
Sangadye ghatta ,ndimwana wachabé
Bee🔥🔥 kuyambila beat selection 🔥🔥🔥 ma bars eeh
Sungatipange cancel ase sungatikhasule 🔥🔥🔥🔥
Kma anyamata mumayenda mwamatama Move yot kape sangayende nanu😂
Tonse a L~city lets gather here n support our heroes, anyone who will like my comment i will come back and watch this again n again
Tili mtika😂😂😂
L city in the building aise
@@PrincePgwadada Ndpo tkuva kukoma nd ana amenewa eeeeeee
@@LebiamMthunzi-hm1ek Ndpo tkuva kukoma nd ana amenewa mmmmmm
Ma rivals anga ndye navana nawo tinagwiriza ndiwaike gulu la anawo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Eeeee koma ma Guyz mumakhala ndi nthawi yoganiza🔥🔥🔥
Koma zoti spe watenga best hip hop artist mukuziwa mukuyimba mphala ma guy
Ndye mwati kudya ma legend opuma et,😀😂 mwanotu, anthu akatha muzitero
Even Zambia is not ready for this new style🎉❤🇿🇲🇲🇼🤔
Guys who is this one......can somebody ask where he was?😢🎼🎶🔈🎙
Barz on barz ...🔥🇲🇼💯
Bee Jay anadya atangomuuza azimise bulb last 31 December I was told the same koma sinadye lero lero ndli koko kazimisa bulb asanandiuze
Phe kudikila verse ya A Nyasulu.... Komabe Gattah Ndi 1 🔥🔥💥😝
Ace Jeezy ndi dolo🙌
Km bee jay mmmm Madala kwambri 😂😂
Mmmh mmmh ayi😂🔥🔥🔥🔥
Bee and Jay amapheratu 💪💪💪
Mawu ndilibe😂❤🔥🙌🏾🤝🏾
Bee Jay kuzavina ngati Kendrick Ramar pamenepaja🫰😂
Listen 👂 👂... ndangofuna KT ndikukhau listen... Mene ndima followerer ndikufilisen ...listen 👂masowa ndikufilisen ..makapewa asama kudandaulisen 😴🫡🫡🫡
Ai Ndithu.....Pa PRAIB Palibe "S" Koma Lero We Making "Space For The Ace"🔥🔥🔥🔥Munangobwera Kudza🗣🗣🗣🙌
Wordplay ya madolo wa aziyiphunzitsa sukulu za ukachenjede🙌🔥💯
Those days ku seminary tinkagona around 3am chifukwa chonvela ma tracks a Ace Jizzy and Bee Jay 🔥🔥 Big up guys
Eeeee koma anawa 🔥💪🔥💪💪🔥 Hip-hop ilibe kwawo koma Rhumba imashala ku BT 🙌🙌
Nyasulu more 🔥🔥🔥🔥🔥
❤❤❤❤ma nigaz awa amandibhebhera bwanj
Ndinu madolo🔥🔥🔥🔥🔥
Udzititchula dzina ase😎😎😎😎
Udolo Nd Belo sheet 🔥💯
kuseka kokhako ndi punch payokha😅🔥
Wagulu onse pansi barz on baraz lit 🔥 🔥
A bee chabwino mwawina🙌🏾🙌🏾🙌🏾
Izi ndi zomwe ife timaziwa 🔥🔥🔥🔥
Wayiphweteka bro🔥🔥🔥🔥
Ma guys awawa ndi madolo,Koma Bee Jay ndi Dolo kwambiri akanakhala amayimba dancehall, pamene Ace Jizzy ndiwa hip-hop kwambiri❤
Aaaaa Mdubs or Gwamba amafila kah🔥🔥🔥🔥🔥
Zirombo eeeee mwala 📌📌
Koma nde kuli Zima style Bee jay & Ace jizzy 👍👍🔥🔥✊
Ace Jizzy si kape 🔥
The dynamic duo 🙌🔥🔥🔥
Tikanaimba za nzelu km munatasa kwambir 🔥
Odi eya yochita kugogodera😂😂😂😂
Anthu ambiri zizatitengera nthawi kuti tizazindikire zoti Ace Jizzy ndi Bee Jay ndi madolo
Iwe verse umalemba mwezi koma verse ya week 😂Bars🔥
Palibe winner yathela 1_1 mashasha inuo munabwela gyz🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Madolo kasauzande🔥🔥
Barz on 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Siinu Madolo Koma Zilombo Kahanded😂🙌🔥🔥
I think we are not ready indeed mmmh Bee.🔥🔥🔥🔥
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 koma ndaseka.
Eeeeee udolo munamaliza inuyo 🔥🔥🔥🔥 kulibeso
Ya China bee & jize inuyo ndmadolo🔥🔥🔥
Madolo 🔥🔥🔥
Kkkkkkk koma gyz ..... Esh ....... Chaka chi mwatimalizra bwino gyz
Mukadya mwango m’mangozipopa 😂😂😂Next
Koma awawa eeh baddest duo 🔥💯
Kkk tatopa ndizot muzizembera... Tangovayan direct apa aaaa😂😂😂
Eeee kmatu ma guys awawa iiii 🔥🔥🔥 We are not ready kkkk
Ma shasha a Hip-hop pa Nyasaland 🇲🇼
Ichii mumati chi Bee jay 🙌🙌
Barz ON barz Uzinditchula dzina aseh🎼🔊🔊🔊
Koma jizzy eeesh umandifikapo
Amene ma bars akutivuta kumva let's gather here😂🥱
Nyasulu apapa nde wabwera aise😂
Onsewa ndi madolo
Palibe woopsa kuposa mzake
I enjoy them both...
koma anamenya mental yomwe analowela Bee Jay ndi katswiri
Amene tafila Ace jizzy let's gather here
Mwalowesa chibwana ku hip hop iyi nde ndi miss
Timavovera ace or tisanavere verse yake🎉
Acee ndidolo
@@kappascofie9131 Ace Jizzy sikunthu wamba
Odii! Kuno skill yochta kugogodela💥💥💯
Eeeeeee😂😂😂😂 kuti umvetsetse zomwe akukamba bee Jay ukuyenera kuyionera kangapo ase 😂😂😂✨✨big gee
Beat Selection Bee yampweteka..Jizzy Waigwira pakhosi, my opinion 👍
Verse kulemba mpaka mwezi koma verse ya Week (weak)
BARS🔥🔥🔥🔥🔥
Ace Jizzy ndikatakwe
Ineyo ndi mkango/
Ineyo ndi nkango-tii/
Ndinu madolo koma ndinangozii-Ndikira/
Kuti munangotchuka mwangozii mboba/
Mukadya mango, mangozii-popa ( Mangoes)//
😂😂
Ace waipha no cap
First time I thought Beejay 🔥🔥koma Ace jizzy uja ndwachabe eee
Skill ya odi ea kuno
Yocita kugogodera 💪😍😍😍
Who's here to support Bee Jay & Ace Jizzy! 🙋🇲🇼
Jizzy amaganiza modabwitsa🎉
Ku L city kuli ine , udolo ndi bello shirt 😂🎉🎉
Km jizzy ndidolo ka 100😂❤❤❤
Bee jay ma bars ofunika munthu olingalira kwambiri eee🙌🔥🔥
Straight takes a couple of listens to get what he is saying..dolo ka 7 ngati Namani.. 😩
Tikufunika ma dictionary
@@realonedon9604dolo osamba ka 7 ngati naman
Koma viwana iviii mmm 💥💥💥😂🙌🙌
Jizzy uja ulemu wake guyz🎉 your flower bro🎉🎉
Kudya legend, legend in the making, legend opuma nditcheni bataza engonga
Ace jizzy ndi chidolo kwabasi ase 😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤
Bee jay and ace jizzy fire🥰🥰🥰🥰🥰🥰 ma burz awawa Ali super glue kkķkkkkkkk
Those who say bee Jay killed it gather here we had a conference tomorrow
bee jay ndiakatundu adah eeh
Ndabalalikatu boss, conference yo inachitika kale kapena ichitika mawa?
Eeh all the best for had it tomorrow 😂
Ineso zikundidabwisatu ...we had a conference tomorrow??? Akuti chani Kodi lol 😂😂😂😂
Ace munvele mopanda mantha man jizzy killed it
Bee Jay -" kudya legend, legend in the making, legend opuma nditchen Balthaza 🤣😂😅"
Akulu awa amwene hahaha
Awawa amaimba zomwe amafuna wow ❤❤
Nyimbo zamadolo awawa umafunika unvele modekha, mopananda wina kusokoneza,
Tinvela ngat tikayankha mayeso ndithu 🌹🔥🔥❣️
Ace jizzy ndikapolo hvy guys 😢🎉
Kom uyu ndi moto🔥🔥🔥luso la cream cream❤
OMG 😳🔥
There is no Bee jay without Ace jizzy so stop comparing these dude they all contribute to each🔥🔥
Ulindi skill yo chita kugogodela😂😂😂🔥🔥💪
Bee jay kuyinjanjisa beat osazamutola😅😅😅👈👈🔥🔥
Eeeeh koma kaya ma dolowa amaganiza bwanji za hip hop,ndie momwe aipwetekela beat shaaah!!!🔥🔥🔥🔥🔥
Underrated chabe Koma izi ndiziphe mumativetsa kukoma 💥💥🇲🇼💪 fan wankulu 23🇲🇼
Bee jay ma Bars a hard ngat ukupeleka ma mbama kwa anawa😃😃💥💥👋
Jizzy ndiwachabe 🤣🤣🤣🤣 chapha ma guyz
ACE JIZZY ndoopsa ❤️🤞🏼💀
😂😂😂ikupita kwandan iney 😮😮 achin 😂😂😂😂
Ndipokwambili ase
Ndipo live
Zitsiru za ana inu. Kuimba ukuku ambiri akukuopani 😂😂😂😂💯💯💯
Eti man aaahh Satha kuimba away😂😂😂
Honestly Bee Jay has bars pomwe ace anapanga major mu flow💯🤝🏼
Sangadye ghatta ,ndimwana wachabé
Bee🔥🔥 kuyambila beat selection 🔥🔥🔥 ma bars eeh
Sungatipange cancel ase sungatikhasule 🔥🔥🔥🔥
Kma anyamata mumayenda mwamatama
Move yot kape sangayende nanu😂
Tonse a L~city lets gather here n support our heroes, anyone who will like my comment i will come back and watch this again n again
Tili mtika😂😂😂
L city in the building aise
@@PrincePgwadada Ndpo tkuva kukoma nd ana amenewa eeeeeee
@@LebiamMthunzi-hm1ek Ndpo tkuva kukoma nd ana amenewa mmmmmm
Ma rivals anga ndye navana nawo tinagwiriza ndiwaike gulu la anawo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Eeeee koma ma Guyz mumakhala ndi nthawi yoganiza🔥🔥🔥
Koma zoti spe watenga best hip hop artist mukuziwa mukuyimba mphala ma guy
Ndye mwati kudya ma legend opuma et,😀😂 mwanotu, anthu akatha muzitero
Even Zambia is not ready for this new style🎉❤🇿🇲🇲🇼🤔
Guys who is this one......can somebody ask where he was?😢🎼🎶🔈🎙
Barz on barz ...🔥🇲🇼💯
Bee Jay anadya atangomuuza azimise bulb last 31 December I was told the same koma sinadye lero lero ndli koko kazimisa bulb asanandiuze
Phe kudikila verse ya A Nyasulu.... Komabe Gattah Ndi 1 🔥🔥💥😝
Ace Jeezy ndi dolo🙌
Km bee jay mmmm Madala kwambri 😂😂
Mmmh mmmh ayi😂🔥🔥🔥🔥
Bee and Jay amapheratu 💪💪💪
Mawu ndilibe😂❤🔥🙌🏾🤝🏾
Bee Jay kuzavina ngati Kendrick Ramar pamenepaja🫰😂
Listen 👂 👂... ndangofuna KT ndikukhau listen... Mene ndima followerer ndikufilisen ...listen 👂masowa ndikufilisen ..makapewa asama kudandaulisen 😴🫡🫡🫡
Ai Ndithu.....Pa PRAIB Palibe "S" Koma Lero We Making "Space For The Ace"🔥🔥🔥🔥
Munangobwera Kudza🗣🗣🗣🙌
Wordplay ya madolo wa aziyiphunzitsa sukulu za ukachenjede🙌🔥💯
Those days ku seminary tinkagona around 3am chifukwa chonvela ma tracks a Ace Jizzy and Bee Jay 🔥🔥 Big up guys
Eeeee koma anawa 🔥💪🔥💪💪🔥
Hip-hop ilibe kwawo koma Rhumba imashala ku BT 🙌🙌
Nyasulu more 🔥🔥🔥🔥🔥
❤❤❤❤ma nigaz awa amandibhebhera bwanj
Ndinu madolo🔥🔥🔥🔥🔥
Udzititchula dzina ase😎😎😎😎
Udolo Nd Belo sheet 🔥💯
kuseka kokhako ndi punch payokha😅🔥
Wagulu onse pansi barz on baraz lit 🔥 🔥
A bee chabwino mwawina🙌🏾🙌🏾🙌🏾
Izi ndi zomwe ife timaziwa 🔥🔥🔥🔥
Wayiphweteka bro🔥🔥🔥🔥
Ma guys awawa ndi madolo,
Koma Bee Jay ndi Dolo kwambiri akanakhala amayimba dancehall, pamene Ace Jizzy ndiwa hip-hop kwambiri❤
Aaaaa Mdubs or Gwamba amafila kah🔥🔥🔥🔥🔥
Zirombo eeeee mwala 📌📌
Koma nde kuli Zima style Bee jay & Ace jizzy 👍👍🔥🔥✊
Ace Jizzy si kape 🔥
The dynamic duo 🙌🔥🔥🔥
Tikanaimba za nzelu km munatasa kwambir 🔥
Odi eya yochita kugogodera😂😂😂😂
Anthu ambiri zizatitengera nthawi kuti tizazindikire zoti Ace Jizzy ndi Bee Jay ndi madolo
Iwe verse umalemba mwezi koma verse ya week 😂
Bars🔥
Palibe winner yathela 1_1 mashasha inuo munabwela gyz🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Madolo kasauzande🔥🔥
Barz on 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Siinu Madolo
Koma Zilombo Kahanded😂🙌🔥🔥
I think we are not ready indeed mmmh Bee.🔥🔥🔥🔥
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 koma ndaseka.
Eeeeee udolo munamaliza inuyo 🔥🔥🔥🔥 kulibeso
Ya China bee & jize inuyo ndmadolo🔥🔥🔥
Madolo 🔥🔥🔥
Kkkkkkk koma gyz ..... Esh ....... Chaka chi mwatimalizra bwino gyz
Mukadya mwango m’mangozipopa 😂😂😂
Next
Koma awawa eeh baddest duo 🔥💯
Kkk tatopa ndizot muzizembera... Tangovayan direct apa aaaa😂😂😂
Eeee kmatu ma guys awawa iiii 🔥🔥🔥
We are not ready kkkk
Ma shasha a Hip-hop pa Nyasaland 🇲🇼
Ichii mumati chi Bee jay 🙌🙌
Barz ON barz
Uzinditchula dzina aseh🎼🔊🔊🔊
Koma jizzy eeesh umandifikapo
Amene ma bars akutivuta kumva let's gather here😂🥱
Nyasulu apapa nde wabwera aise😂