Ineyo koma ndimaganiza kuti, ngati nkotheka, bwanji pakanakhala debate ya atsogoleri a ma institutions ndi a ma systems amene mkulyu akunena, kuti timvetsetse bwino bwino mbali imeneyi. The academia should come out and provide guidance on the pro and cons of his phylosophies if possible. So that dziko lisamuone ngati wosokoneza. Pemphotu iriii. Otherwise continued silence on his advocacy by these groups of people will mean either we are agreeing with him, we don't understand him since the issues are so complex, or there is fear of unknown and or maybe we are feeling good and we are not concerned with the affairs of the nation. Zodiak can you please arrange this debate or whatever name you may call it.
Tipange tokha osati zodiak mmene akuchitira mahata. Za chitika pa kenya pompa nkhani ngati zimenezi. Ntsogoleri ndiyemweyi musasokoneze po bweretsa ma media andale.
Chilima still lives here in Malawi in people like this one, we need leaders who are selfless and loves loving Malawi to see her getting developed and start doing her own things and decisions as an independent nation.
Allah 🙏 muteteze mahata ku chilitchotse chimene chingathe kuwononga moyo wake, mcholinga maganizo ake ofuna kuwombola malawi apitilile ngt akuyangula kutchoka pasi patina wake. Allah musalole satana awononge moyo wake 🙏🙏 Allah ndkupempha kwa inu kt munthu atiwombole ku mavuto omwe tikukumana nawo 🧎🧎🙏🙏🙏🙏😭😭😭😭😭
Where were u brother,this is true pan Africanist,leaders we need in this times,how I which to meet u,to gain some knowledge.i l really like u.u will have true followers.mark my words
Man we're tired of voting for same political ideas with only tribe difference for sure. When saying different parties it means there is different ideas but all the parties running around now have same scamming ideas instead of coming with new political theories
Mutiuze kuti Ndikusaphuzira Kwathuku, tingagwire nanu Ntchito motani?,malo anji?, nanga likhale liti?,ine monga m'modzi mwa achinyamata okhudzidwa mutiyike mugulu la anthu omwe alibe kalikonse kodetsa nkhawa kuti tingaluze pogwira ntchito imeneyi,tiribe kanthu ndikale, ngakhale moyo wanga ulibe mantha ndi ifa .coz rght now Its same like we are dead already. Let malawi of torrow be bright Through our pain... Zaka zochuluka zatha tikumati tili pa ufulu ,koma Ufulu palibe.ziri ngati Kuti,, Brother Denis akutiwuza kuti tisiye kumwa ma ARVs ,tiyambe kumwa mankhwala othetsa Hiv and Aids it is the same.. Mpaka liti tikhale tikuvotera atsogoleri oti sakubwera kudzathetsa mavuto anthu koma kuzaonjezera.Pakali pano amalawi tiyeni tigwirane manja kuti nyali inene yayaka pa malawi tiyinyamule kuti kuwala kwake kufikire anthu onse omwe ali mudziko la malawi .osati kuivundikira nyaliyi mu mbiya kuti tizivutikabe no no no!. Fundo izizi zikusonyeza kudzipereka, kulimba mtima, komaso kuzindikira ndiso umunthu. Ine chibadwire sindikhuzidwa ndi za ndale chifukwa ndinali ndisanaveko fundo ndi ndondomeko zogwirika ngati izi.kuchokera munthawi ya Kamuzu kufika pano. Ndikoyamba pamalawi .ino ndithawi yoti chiphona chomwe chinaimikidwa panjira yopita ku ulamuliro wantendere chomwe chimatchedwa kuti ''Mantha,''chichotsedwe, tiyeni tiyimene pamodzi ndikuchichotsa kuti tilimbane ndi chilombo chopondereza maiko kt mibado ikubwerai idzakhale ndi ufulu weweni.chonde amalawi tiyeni Tiwapemphe anthu onse omwe adzipereka kutibweretsera nkhani yachirendoyi kuti, asatikhumudwitse ntundu wa amalawi ,poyamba zithu zoti sangazikwanitse .komaso ndibwino kuti anthu avutike,ngakhale kufa kumene pazinthu zoti zipereka ntendere kwa mibadwo yotsala osati ifa zomangotenga anthu azeru koma dziko osasitha ayiii. Muthe kuwaunikiraso ,anthu za chinthuchi ,kuti pamene chikuyamba ndimavuto ati, omwe tikhale tikukumana nao tisanafike pokwanitsa khumbo lanthu.pasi pakuti ululu komaso kulira sikulephera pamene munthu akufinyidwa chithuswa ,kuit nguma/ mutu uturuke sizophweka .ngati amalawi ataunikilidwa zonsezi tidzayenda tikuva ululu, tikulira koma tiri ndi chiyembekezo chapmphavu komaso chokhalitsa. Ine sine otumidwa. koma odzipereka kukhala munthu okonda dziko lake kuposa moyo wake .. Morris Natulu from Ntcheu. But rght now am in (SA Durban.) Respect to all Malawian who listen..to this intrvw & u write a comment which can take malawi to other side.lets follow it with care...
I've been following your public lectures & am no longer the same person but a different one in view of this i render my support to you on what ever the cost may be.i can sense well fair system which can benefit everyone one in the country
Apatu pakufunika achinyamata olimba mtima timupange support Denis.
Tiyeni tikhale naye mnyamata zathu abale
This guy needs support, ndi genius
Kwambiritu 😮
@DennnisGogoda
Kodi iwe ukupezekera kuti? Ulipo?
This guy is a good.Lets support him
Ineyo koma ndimaganiza kuti, ngati nkotheka, bwanji pakanakhala debate ya atsogoleri a ma institutions ndi a ma systems amene mkulyu akunena, kuti timvetsetse bwino bwino mbali imeneyi. The academia should come out and provide guidance on the pro and cons of his phylosophies if possible. So that dziko lisamuone ngati wosokoneza. Pemphotu iriii.
Otherwise continued silence on his advocacy by these groups of people will mean either we are agreeing with him, we don't understand him since the issues are so complex, or there is fear of unknown and or maybe we are feeling good and we are not concerned with the affairs of the nation.
Zodiak can you please arrange this debate or whatever name you may call it.
This is a great request to Zodiak
Agreed 💯
I am with you
Tipange tokha osati zodiak mmene akuchitira mahata. Za chitika pa kenya pompa nkhani ngati zimenezi. Ntsogoleri ndiyemweyi musasokoneze po bweretsa ma media andale.
This system thrives in veil of silence and is never questioned in open debates.
Thanks Lord for allowing me to listen to this best of the best interview in 2024
The kind of President I've been looking for is finally found , you have my full Support
Ndipo yangaso uyu ndizamupasa.
This guy is full of wisdom and intelligence 💯🙌🏾🙌🏾💯
Mbewu iyi ndiyabwino let's support mr Malata kulibeso mpulumusi wina kuposa uyu
Mesiya
Uyuyu ndikatundu akufunika sapot
I think we need to support this guy.
U have my support brother...this country needs people like u
Muli nzeru this young man needs support.
i knew a day like this will come, i have been following his public lectures on economy
We need these kind of people in Malawi Mr mahata your are a leader
He is another level this person,i can say thanks God, bless Malawi with another chilima.My fellow Malawians lets support this person please.
Chilima still lives here in Malawi in people like this one, we need leaders who are selfless and loves loving Malawi to see her getting developed and start doing her own things and decisions as an independent nation.
Uyuyu mau ake akuonetsa kt angatukule Malawi exactly he need our all supports 🎉❤
He needs support
This guy💪🇲🇼🇲🇼 abudula memo wagulu 2025 .tatopa ndi ma recycled politicians omwe cholinga chawo ndi kukhutitsa zimimba zawo
Mbambande! So refreshing! Nzeru zokhazokha.
Me is number one 1️⃣ to give him support ❤❤❤
Is better kuvotera uyu than kutaya vote yanga kuzipani zangot mbweezi😢😢
We need anthu ngati awa mmalawi you carry my vote Dennis
There is light in u, just imagine IMF afraid of u eeee.u have gain a follower in me
This man has come out as a fighter, very intelligent man. We suport you
Tikupangani support Denis❤❤❤❤❤❤
Denis ndikugwilizana nawe maganizo ako koma zikufunika machawi chifukwa uyatsa Munda uwu suzatha ngati tingachedwe ndilinawe muzimenezi❤
Clear and direct this is what we need
My President 👉💪 Mahata God Bless You 🙏
Bravo Mahata we need Joabu Chakhaza to interview you
Allah 🙏 muteteze mahata ku chilitchotse chimene chingathe kuwononga moyo wake, mcholinga maganizo ake ofuna kuwombola malawi apitilile ngt akuyangula kutchoka pasi patina wake. Allah musalole satana awononge moyo wake 🙏🙏 Allah ndkupempha kwa inu kt munthu atiwombole ku mavuto omwe tikukumana nawo 🧎🧎🙏🙏🙏🙏😭😭😭😭😭
Awawa ndi atate 🔥🔥
Anabwera kudzakhala
Denis please don’t give up 💪🏽🇲🇼
Iyiyi ndi brain 🔥🔥🔥🔥
I like this kind of thinking especially on dealing with IMF
Give me the lists of the books you just mentioned
Chilima sanafeletu anasiya mbeu this guy akufunika chitetezo apo biiii tiluzaso ngati momwe tinaluxira mfana oganiza bho uja
This one I can vote million times if possible
This guy needs our support
Akufunika akumaneso nd Brian Banda uyu ma intelligent okhaokha
Eish this man anthu ampatse support
Kodi anthu awa sitingawapase mpata,am very impresive with this man let's stand on his shows
Denis Mahata is right and needs support!
Tafika apapa ndithuuu!!!
That's great deal God bless you and guide to full fill your plans
Where were u brother,this is true pan Africanist,leaders we need in this times,how I which to meet u,to gain some knowledge.i l really like u.u will have true followers.mark my words
Big up brother matata am on your side let's develop Malawi 🇲🇼
Mnyamata uyu Chiuta wakoleko. Keep it up, am also behind you.
Ziko ili likufunika fresh brud kuti ritsogoreredwe tiyeni tigwile tchito tisinthe ziko lathu please achinyamatha tiyeni tizuke timange malawi watu zukani zukani tikuponderezedwa kwambiri tiyeni tigwire tchito lomanga malawi weniweni achinyamatha tisamangoyang'anira zindu zikuonongeka tiyeni tizuke 46:24
Ku Malawi kunadalitsidwa ndimafana othinka bho we lost one but one also raised God bless Malawi and be with that guy
43:45 ati ndabwela kuzathesa michitidwe yopusa😅. This guy wandiwaza
God bless you my brother am with you am coming home to vote you
Denis to the world
Man we're tired of voting for same political ideas with only tribe difference for sure. When saying different parties it means there is different ideas but all the parties running around now have same scamming ideas instead of coming with new political theories
brilliant Ideas, this guy needs support
Homie you my support, I am interested in your philosophy and I am joining, my personal issue that has been bothering me is our education system
We really need to change and improve our education system.
❤❤❤❤❤❤ koma munthu uyu tikumuchedwetselanji kuti izi aziyambe mmoyo uno uyu amanena zowona ndithu
Interview iyi a Host achepa. Mahata uyu akufunika Brian Banda.
Brian banda wachepaso kwambiri
Abwanawa aku ziwa zimene aku lankhula. Awa akufunika ntolankhani wozitsata
Mwina akakambirane ni kabambe@@NelsonMd-x5h
Iwe ndye wabwera iwe, Host uyu akuchepera kwabasi
The host doesn't even know,, he is asking rubbish as if he has been sent by chakwera 😂
😂😂😂😂
Hope he goes far and takes on our rotten systems.
Tikaona ngat Bingu anafa koma uyuyu ndie ndi ndimoto wamalasha
This is the only man I can vote for
This man is God sent
Ine am ready to support this man💪
Unfortunate thing such wise people won't test power
I like this Man very much
Malawi is blessed with this brilliant next president Mr Denis Nthanthwe Khang'a Mahata
Very impressive and profound
I like this guy let us make him the president of Africa
Traore your brother is here in Malawi
Let's support this guy
One of the most intelligent Malawian
We need people like Mr mahata for malawi to change
The devoted citizen of Malawi am with you
This Man is very intelligent he speaks as if he is reading a book.
My president Dennis thatwe
ali nd zinthu za BHO kwamb mkuluy km very complicated zofunika munthu ovesa kwamb.
ndiwe wa vision osasitha vision piliziii 🙏🙏🙏🙏🙏
Until our scales fall from our eyes and waxes melt from our ears we may see and understand that this guy is right, let's support him
Gteat
Let's support Denis mahata,change is loading not these old politians ,we are tired of them
I was waiting for
Koma uyu allah amupatse moyo wawutali azakwanitsa kusintha zinthu ndithu
the people who are chosen to be leaders one of them is this guy
I like this guy Moro fire bro
Ndikava zomwe akuyankhura mahata ndimadziona ngati wayamba kale kutilamulira dzukuli sugar ndukugula k13.99 kwacha ninty tambala😮
This guy is very genius, another Bingu and Chilima in our time. Youth lets wake up
Best interview ❤
Uyuyu akufunika support yanga by default. We share quite a huge chunk of ideas on how we can liberate this country
We need people like him as a nation
Katundu uyu akufunika support.
I know this guy he was once the president of NRC campus student union if am not mistaken....he is a natural born leader
Ifeyo ndiy telowamo tipatsen link yo tipanga support now
Abwana awawa simunthu wamba guys
Mkulu uyu ndi amene akufunika I'm impressed if he means what he is saying
U will rule this country n ur the Chosen one Malawians are waiting for.
This philosophy is great and need support
Well said brother
Uyu ndi Alexious kamangira dziko lilongosoka bas
Tingopanga za emweyu basi. Enawa atipha😂
Bakili muluzi tv Denis more fire
Big up brother, sukulu siyitha aphunzise komanso awunikile kuti achoke mu mdima
Denis for president 💪💪
14:30 point
Pangolin winaso uyu ❤
Kumamvelako izizi.
Umumu muli nzeru!!!
This guy is brilliant.
Mutiuze kuti
Ndikusaphuzira
Kwathuku, tingagwire nanu
Ntchito motani?,malo anji?, nanga likhale liti?,ine monga m'modzi mwa achinyamata okhudzidwa mutiyike mugulu la anthu omwe alibe kalikonse kodetsa nkhawa kuti tingaluze pogwira ntchito imeneyi,tiribe kanthu ndikale, ngakhale moyo wanga ulibe mantha ndi ifa .coz rght now
Its same like we are dead already.
Let malawi of torrow be bright
Through our pain...
Zaka zochuluka zatha tikumati tili pa ufulu ,koma
Ufulu palibe.ziri ngati
Kuti,, Brother Denis akutiwuza kuti tisiye kumwa ma
ARVs ,tiyambe kumwa mankhwala othetsa Hiv and Aids it is the same..
Mpaka liti tikhale tikuvotera atsogoleri oti sakubwera kudzathetsa mavuto anthu koma kuzaonjezera.Pakali pano amalawi tiyeni tigwirane manja kuti nyali inene yayaka pa malawi tiyinyamule kuti kuwala kwake kufikire anthu onse omwe ali mudziko la malawi .osati kuivundikira nyaliyi mu mbiya kuti tizivutikabe no no no!. Fundo izizi zikusonyeza kudzipereka, kulimba mtima, komaso kuzindikira ndiso umunthu.
Ine chibadwire sindikhuzidwa ndi za ndale chifukwa ndinali ndisanaveko fundo ndi ndondomeko zogwirika ngati izi.kuchokera munthawi ya Kamuzu kufika pano. Ndikoyamba pamalawi
.ino ndithawi yoti chiphona chomwe chinaimikidwa panjira yopita ku ulamuliro wantendere chomwe chimatchedwa kuti ''Mantha,''chichotsedwe, tiyeni tiyimene pamodzi ndikuchichotsa kuti tilimbane ndi chilombo chopondereza maiko kt mibado ikubwerai idzakhale ndi ufulu weweni.chonde amalawi tiyeni
Tiwapemphe anthu onse omwe adzipereka kutibweretsera nkhani yachirendoyi kuti, asatikhumudwitse ntundu wa amalawi ,poyamba zithu zoti sangazikwanitse .komaso ndibwino kuti anthu avutike,ngakhale kufa kumene pazinthu zoti zipereka ntendere kwa mibadwo yotsala osati ifa zomangotenga anthu azeru koma dziko osasitha ayiii.
Muthe kuwaunikiraso ,anthu za chinthuchi ,kuti pamene chikuyamba ndimavuto ati, omwe tikhale tikukumana nao tisanafike pokwanitsa khumbo lanthu.pasi pakuti ululu komaso kulira sikulephera pamene munthu akufinyidwa chithuswa ,kuit nguma/ mutu uturuke sizophweka .ngati amalawi ataunikilidwa zonsezi tidzayenda tikuva ululu, tikulira koma tiri ndi chiyembekezo chapmphavu komaso chokhalitsa.
Ine sine otumidwa.
koma odzipereka kukhala munthu okonda dziko lake kuposa moyo wake ..
Morris Natulu from Ntcheu.
But rght now am in (SA Durban.)
Respect to all Malawian who listen..to this intrvw & u write a comment which can take malawi to other side.lets follow it with care...
I've been following your public lectures & am no longer the same person but a different one in view of this i render my support to you on what ever the cost may be.i can sense well fair system which can benefit everyone one in the country