Nici say ntili mmasiku osiliza olo atabwera wina things will never change mwana wa malungu ali pafupi kudzaa ndipo zizindikiro zikwanitsidwaa sitinatiiiiiii
😂😂😂😂 aaaa kma zinazi nzochimwitsa, he has a hand of help when did he start helping others ever since he was a minister n now as the VP?? Angonena kt anaona kukagwesedwa, tamufuse kt ngt sanakapange nao convention ndi angt amene wawapasa ndalama kt athandizikire??? Akumusaukitsira Dala Malawi kenak mzigawa tima change tanu muzioneka ngt msamaliya kwinak mukunyoza kt amalawi anazolowera zolandira
Mkuluyu wazungulira mutu 😂 inu inetu nde i understand kuti Him and Chakwera onsewa they re insane 😅 cos palibe chanzeru chomwe akumanena ,,,,, anatengana zitsiru
Nici say ntili mmasiku osiliza olo atabwera wina things will never change mwana wa malungu ali pafupi kudzaa ndipo zizindikiro zikwanitsidwaa sitinatiiiiiii
Ndipo tsitinatidi kuli kulira
Ndizoonadi olo abwele wina ndichimodzimodzi masiku osiliza awa
Zimenezo mwadziwa lero? Chakwera ndolephera akagwere
May God bless you Dr Micheal Usi. You got a heart of help... Mulungu azikhala nanu
😂😂😂😂 aaaa kma zinazi nzochimwitsa, he has a hand of help when did he start helping others ever since he was a minister n now as the VP?? Angonena kt anaona kukagwesedwa, tamufuse kt ngt sanakapange nao convention ndi angt amene wawapasa ndalama kt athandizikire??? Akumusaukitsira Dala Malawi kenak mzigawa tima change tanu muzioneka ngt msamaliya kwinak mukunyoza kt amalawi anazolowera zolandira
Opusa ameneyu fiti
Opusayu akudya mane anapita ku school inu ochenjeranu mukutani?😊
Tikufa😅😢
Mkuluyu wazungulira mutu 😂 inu inetu nde i understand kuti Him and Chakwera onsewa they re insane 😅 cos palibe chanzeru chomwe akumanena ,,,,, anatengana zitsiru
Koma uyu mukuti chairman ligomekayi nchitsilu ndipo andisamare asanwereso pa nsikapa ndimugaza why akukamba za Lazaro ndi zakeyi
Manganya wasowa kolowela ndale ndi zomwe zimakudyesa ndiye ukunena chani apa
Ndikusowa chinena chifukwa palibe ali mbali ya Usi apa
Biggup from ur prodigal sons who flew from their motherland 'cause of starvation,si'sonkeeee!
Mxieew odi mgone apa
Ausi u khala kuti simunali mu UTM mukanafika apa muliri mwatha nzeru
Anthutu mumkanena kuti ngoumila akuopa 20milion ndakhulupilila😂
😅😅😅
Kkkkkk kumbwambwqna kokhakokha or simunapeke 20 million chani chimene mukuchota kuntundu wa malawi kupatula kuvina ndi azimayi mma bonamu ,chilima munammpanganilayo akukankhani ndithu
Km kugura oyimba anthu akuzuzika ndie za bwino eti??
Awa ndi amisaladi ndaona ndiye kukalima nawo kumunda zithandiza chani uyambe wamuthandiza make sikono uja mumsikamo akuvutika mayi umakhala naye uja
Awa sizandale. 😅
Kkkkk ndiwe chitsiru kwambiri manganya
Ngati ausi mukudziwa kuti zikuchitikazi ndi za mmalemba ndiye mukuchita chiyani osasiya ndale mukufuma mukwaniritse mudzisiye dzakuvutani mudziwawuza amalawi zimenezo uchitsiru sagawana inu ndichitsiru chamunthu.
Ndiye maw amenewooo❤❤
Ndye ngat mukuziwa kut athu akuvutika mukuchitapo chan kupatula kumangoyakhula pasokhano
Kuzolowera u running mate wa ulere uyu
@@FrancisViola-x2n ongovemcha olowa ndichamutu
Matendatu awa...kumangophatikiza nkhani apa
Alibe zokamba uyu mtima ukuwawa. You were not utm usi simple
Akulu awawa ndi amzeru kwambir
Magazi amunthu ndioopsa kwambiri.
Kkkk manganya amaziwa kupempha akakupemphelani ku ADRA
Nsanje anthu mulungu anakupatsan mpandowo bwana malizan nthawi yanu
Zikuwoneka kuti zopanda sogolo kungowola apakachasu kkkk
Anthu akuchita nanu nsanje a usi, timakukondani
Nane ndipo ndimanva nao bwino
Kulankhula mopusa neef sitilandira Kma kubwereka mr president ndikukonzen pamenepo.nde osamatchula kuti enaso alandire
Usi pano amangondibowa ine
Koditu usi or kwawo sanawinepo u MP anadziwa kuti or apite kopisasana sanakawina
Zavuta ndale apa
U president uja wathapo basi, mpaka kuvala za MBC?🙆🙆🙆😂😂😂 Kenako tidzaona za wodya zake za zakeyo😂
😂😂😂😂😂😂😂
Tikuthokoza chifukwa chazitukuko zomwe mukuchita. Nkhuku yanjiru siiswa
😂😂😂😂😂 ausi mwangundikatu
Nuala sikhalapo..anthu alhala ndi ndalama..inu a usi mutu suyenda bwino..mwalephera kulamula dzikoli ..Pano munamiza a malawi
Inu mungodzivuta sangakupatseni ndalama awa, katiyeni tikangulimbikirani maganyu athuwa basi
Anati munthu abale chabwino mufuna atani mmh
Galu iwe usi kape iwe ukumudelera kabambe iwe uzipta kwanu ku Zimbabwe
Awa ndiwovundadi!!
Manganya ndi oumilatu uyo😂😂😂
Komatu batile Ili palibe nzeru 😂😂😂
Mmmmmmmh
😅😅😅😅😅cholibe ndalama icho azako 20million sikanthu
😂😂😂Ndalama Ali nawo koma kuumira😂😂😂😂
Much love usi .... you have a heart of gold....may God continue blessings you
Lelo zakhala bwino osamagwilitsa ntchito makaka a utm ndipotso ukanangolengeza kuti walowa ku mcp basi
Mzimu woyera utiyo kupemphera ndi Chippewa mmutu
Manganya lelo ndimutukwanene aaaa fiti iyi ndithu
Mumuwuze Chakwera zimenezo kuti azikonda athu
Osati tsiku Lina ingonenani pa 16 september .2025 .NDI MCP yanuyo.mukuchoka nonse
Sungawine koveshoni iwe
Campaign mode
😂😂😂😂 Pali chanzelutu kkkkkkk
Apa palibe cha nzeru..
The short Lucifer himself
Ndi vp was dziko osati chipani apikene
SiZakale izi tazipatsa za new plz madata
Kambani za chitukuko.
Ndalama uzitenga kuti za sola kape iwe
chitdiru chopanda mzeru yudasi ms phwala ake
Ine uyu ndinamutulika
Koma dziko la malawi😅😅😅
Akakupempherani manganyayo amakapempha
Mukungomikisa khani
Achitsiru awa ausi
Stinge maiko usi
❤❤❤❤❤
Osamugenda bwanji ameneyu
Garu wa muthu kusowa fundo
Aaa km mkulu uyuu alibe mzeru kwambr, shame on you
Anthuwo sakukodwa
Kodi akuti chani
Galu iwe
Fundoless
Khala chete
Bava izziii
Munthu oyipa manganya
Manyi
Kufupikako
Aaaaaa
Km azimay Zimay eeeemumaipasa moto mawa kukafka wina mumutamandnso
Anthuwo sakukodwa