Watching from Durban location clairwood On point mkaziyo love yake ili pa ndalama akuitanisaz tea wake khat sugar yoo anagula ndiyeyo KKK mami ndinu akt
Kma Adzimai tadziona dzithu zokt mudziononger ndalama 500Pin ndi ndalama yambiri yokt muntha kuyambir Business kupanga improve pa family yanu kma zoona ndalama mukather kumutu zokt mutha kungoonona future ya family yan sheeemu
Watching from Durban location clairwood On point mkaziyo love yake ili pa ndalama akuitanisaz tea wake khat sugar yoo anagula ndiyeyo KKK mami ndinu akt
Watching from Johannesburg, South Africa 🇿🇦🔥
Ine Jack kunu ku Mozambique ngati alindindalama zambili abambo apeleke koma kulopo kupeleka ufa palibe pali mzeru?
Boom that guy amadziwa chomwe akufuna, Amuna anzeru akusowa
Mkazi ameneyi makolo Ake Ali nawo?.
Celine you are so serious on your part every time. keeping up
Komaso mkaziyi mutu wake sukugwira nkhan yake imeneyo paka amulande tea ☕
Nsena nzanga Selina Dumbula, umatha ase
Abambowo mwina Ali ndi chibwezi ndee ndalamazo zimathera kumeneko ndikuwona Kuti zimayiyo chiganizocho adachipanga kalekale
Mo fire magaye 🔥 🔥
Kod ndalama yochuluka ngati akukana kupitiliza maphuzilo bwanji wosangoyamba business
Ine ndinapanga download app ya MIBAWA kanena mmanja koma ikumakanika kusayina
Uyu mkazi ali ndivuto lofunika ku hospital
Mayi ameneyu ndi opanda nzeru
Sizoona 500k weave amaio sali serious ndi banja,
Ineyo ndakondwera mmene wayankhira bamboyo, bamboyo ndi munthu wa nzeru
Koma mkazi ameneyi alibe tsongolo.
Nkazi ameneyu ndi galu komaso wawonesa kukonda ndalama zabanja ameneyu mulibemo
Ndalama yoseyo aaaaaaa
Ndalama zachuluka
😢
Uyu kashana uyu nikawalala
Mr waluma your are right
Mayi opusa ameneyi ngati mtima wa chakwera ndithu
Kma Adzimai tadziona dzithu zokt mudziononger ndalama 500Pin ndi ndalama yambiri yokt muntha kuyambir Business kupanga improve pa family yanu kma zoona ndalama mukather kumutu zokt mutha kungoonona future ya family yan sheeemu
K500,000 zachamba eti bwanji ndikapatse Mai anga
500pin yakumutu kokha 😂😂😂
Azimayi polani moto kunjaku sikulibwino
Kodi 50Kg ya chimanga chili pazingati pano?😅😅😅😅
Banja limeneli likonetsa kt abambowo sawulula zandalama mmene apezera kapena mmene amapezera komanso sapanga maprogramme apanyumbapo limodzi bcz mkaziyo sakanatha kuphempha ndalama yonseyo , pakhomopo maprogramme kapena maplan amapanga ndi abambo okha,that's y zili choncho
Kutheka mwina abambowa mwapeza yomwe wapepha mkaziyo kuchepa
😢😢😢😢