ความคิดเห็น •

  • @wedumaulidi1199
    @wedumaulidi1199 ปีที่แล้ว

    Mvuto madzuzitsa Ana dekhani kambilanani sizingatheke kumangokangana rest of life waluma ndiwadzelu

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 ปีที่แล้ว

    Iwe dt uzipeleka m'pata kwa abusa osamangolongolola

  • @enittachimombo3314
    @enittachimombo3314 ปีที่แล้ว

    Kunena zoona, Chachikulu chufunika ndi maso auzimu ndinthu coz mabanja ambiri nde muli mavuto, Pali ena amakhala mmavuto mommo kupemphera mkutopa Koma zithu osasitha, ena mpaka akufa ndinthu nkhani yake banja, mpofunika kusamalitsa Moyo ndi mpamba, kulipo kumakakamira pompo mkuludza Moyo coz nkhaza mmabanja nde zilimodi, Ambuye atithandidze Koma,

  • @jjgrobler704
    @jjgrobler704 ปีที่แล้ว

    Sellina umamuikira DT kumbuyo Awalumawo angokhala oupeza cos zaubusazo ndi zaku church 😏😏

  • @ezekielwakudyanaye8294
    @ezekielwakudyanaye8294 ปีที่แล้ว

    Sellina, mudzikhala pakati pa DT ndi Waruma because one day adzagwirana pakhosi. kkkkkkkk

    • @ezekielwakudyanaye8294
      @ezekielwakudyanaye8294 ปีที่แล้ว +1

      In each and every family muli mavuto, koma tikamalangizana in family, tidzimvaerana msanga kuopa mavuto kwa ife ndi ana. Ankhoswe athandizenso mwa changu in this family. Koma kwa kukulu eni awirinu, mum mumvane mwansanga kuopa divorce avoid selfishness in marriages.

  • @marietdaniellukhere1475
    @marietdaniellukhere1475 ปีที่แล้ว

    Tikuphunzira ndithu