ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Kkkk abale mukuniwaza selina kumuzi sikukumukhala zimakovuta ndizo basi, ngakhale ndinakuonelanipo ndikale koma eee aye
First to coment Malawi lets support our fellow Malawian's
Selina amandisangalasa ndipo ndimamkonda ngakhale sakundiziwa . Malo amenemumayikawo mumuchosepo mukundibowa kwambili , mukuzuza mahop anga😢😢😢😢😢😢😢
Kkkkkk 😂😂😂
Tadala umudziwe yesu ndi ophunzira Ake 12.lino ndi dziko osamala mzake samadziwika
When shooting make sure that the mic shouldn't appear in a scene coz there are two scenes where it has appeared ma camera muzionesesa km big up uli mwala iyi😍😍😍😍😍
😂😂😂 koma gyz zikubeba keep it up 🔥 kma madam Charles nde inawachemera, Dunken kukanisa x kukhala pa khonde 😂😂😂😂
Nice mukutimvetsa kukoma tiphunzira zambili never give up
😂😂😂, koma Sandra gululu ndi bambo ake a chirles
Keet it up guys ❤
A Bima yotolera ma botolo yomweyo😂😂😂😂😂😂
Koma tadala amandiwaza 😂😂 akamamatuma ngat sakunva chocho aaaa😂😂
My favourite comedy following from Pretoria south osasiya guys keep on
Nkhani ndi ya akulu akulu ana palibepo😂😂😂
Hahaha akut amutchula iyeyi nde ungakhale umbon woti wapereka mimba
Koma ankolo akwa berthia nawonso vibe😂😂😂😂😂
Very nice
Tadala kuzunza nzake😂
Tadala ati soya peace's angaphike anthu awiri🤣🤣🤣🤣🤣
Great!!
Great guyz
Azi Ankolo Ali umu akundisangalasa bwanji 😂
Xxxxx
XxxxXxxx
Guys mumandivetsa kukoma Mozambique tete 🔥🔥🔥🔥
Bambo a Charles kkkk ayi zikomo ati njara yakura 😂
😅Soyapisesi angaphike anthu awiri😂
Km maio abwera bho mumatha heavy😅😂
Kusauka mmachimo ndithu bambo a Charles mwalalatatu apa
😂😂km Tadala anabwera
Kumabwela mwachangu komaso mukufupikitsa kwambili gayz esetsani timamva kukoma
Eeeeeh apongoz bwanji kod 😂😂😂😂
Kodi iyiyi abweleza ya last week?
Steve wabwela 🎉🎉
Achibwezi a hanah azivala ngati alipakhomo not like akuchoka
Nde ali ndi step yakayendedwe😂😂😂😂
Abambo a Charles kumeneko kulalata😂😂😂
Ngati anamukonzekera🤣🤣
Bima acting amatha👍👍👍👍
Breakdown
Motoo Kuti buuu ,,,,nice Guys ❤❤❤❤
Kanyimboko munaika kabwino
DUNCAN NGO😂😂😂😂😂😂
Koma tadikiraeeeee ayi tamayesesan kupanga changu like yoyamba ija please
Ndipo I was wondering ndayambira kupanga check ndati kapena anasitha tsiku iiiii
Kkkkkkkkkk😂 wometa mbarimbari
🤣🤣🤣🤣🤣🤣 iyiyi ndiye ndimwalatu guys
Ma hana asamayan,gane camera
Koma Duncan eish
Zibwini heanvy
Mukutimvesa kukoma inuyo
Daken kukhaulisa ma x
tivomereze kut Steve si actor
Danken kuyankhulitsa iiiii
Boring act

Xxxx