KUYANKHA ZOMWE MA MP ACHIPANI CHA UTM ADAYANKHULA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 509

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 3 หลายเดือนก่อน +46

    Musavutike mulungu ndiye yankho tinkhulupilira bwanji poti uyo kunkuyu ndi wakupha Ali kuti witika😢😢😢

  • @khalilugiftmasala3982
    @khalilugiftmasala3982 3 หลายเดือนก่อน +7

    Ngati adali ma plan anu mosogozedwa ndi president chakwera wallah Allah ayambe pansi pompano kukulangani, koma ngati Simukudziwapo kanthu za miyoyo imeneyi Mulungu atikhulukile this is my duwa Allahu subuhana wataala ndiye mwini zonse komanso mwini wake wa miyoyo ya abale atisiyawa ndithuditu Allah ndiye mwini chilango chachikulu

  • @ColetteMalunga
    @ColetteMalunga 3 หลายเดือนก่อน +11

    Kungoona chibwibwi cha mkulu wa MDF, kuti ndi bodza lokhalokha

  • @charitykalulu
    @charitykalulu 3 หลายเดือนก่อน +29

    Kodi ndiye munadziwa bwanji kuti ili kuchikangawa poti inathawa siginal 10:10???

    • @ShabaniKuswere
      @ShabaniKuswere 3 หลายเดือนก่อน

      Komadi pamenepo, komaso ngati anadziwa Kuti inagwera kuchingawa analephera Pati kukafikako mu nthawi yake

    • @peterBokosi-e8y
      @peterBokosi-e8y 3 หลายเดือนก่อน

      Komadi!

    • @EmilyTembo-zu4zy
      @EmilyTembo-zu4zy 3 หลายเดือนก่อน

      Yes anadziwa bwanji anthu oipa awa inu mulungu akukantheni anyani inu

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 3 หลายเดือนก่อน +4

    A well organised move, started with Sidik Mia, now Chilima

  • @CrissyMapemba
    @CrissyMapemba 3 หลายเดือนก่อน +3

    Mwapha chilima inu ndipo nzimu wake ukusowesani mtendere musandandaule zoti mwataya ndege akugulirani ina chakwera

  • @FranciscoKamange
    @FranciscoKamange 3 หลายเดือนก่อน +7

    Muzilankhulanso mchizungu kuti Bodza lo anzathu akunja azimvera kunama kwanuko......Muziona Mwakula Mwatha

    • @joycekanzule9123
      @joycekanzule9123 3 หลายเดือนก่อน

      dont work English translator will do the needful

  • @SophieKamanga
    @SophieKamanga 3 หลายเดือนก่อน +7

    Mukuchita kuoneka kt mwampha munthu ndinu mukuchita kusowa choyankhula km ambuye akulangani nonse mwachita zimenezo

  • @mkhulukinyata5198
    @mkhulukinyata5198 3 หลายเดือนก่อน +7

    Ambuye Mulungu ", Inu ndamene muli ndi mphamvu pachilichonsecho , Kuposa ena aliwonsewo .Ambuye Mulungu ana a ISRAEL tu anadzavutitsidwatu ndi farao kwanthawi yayitali ,Koma kudzera muthandidzo ndi mphamvu zanu' Farao tu munamulanga ndi Imfa yowawa kwabasi ,Nafenso munthawi yino tikukulilirani kuti mupereke chilango kuposa chomwe munampasa Farao mmadzi muja' Kwa munthu wina aliyense yemwe watengapo gawo pachiwembu chimenechi..Atidzimureni Ambuye kuridzimula kwamphamvu kuja .

  • @Thembokatuli
    @Thembokatuli 3 หลายเดือนก่อน +7

    Osangomuuza kuti simuimira bwanji koma mpaka kuchotsa miyoyo ya anthu zidyani magazi achilima mulungu akuonani zomwe mwachitazo

    • @Concerned320
      @Concerned320 3 หลายเดือนก่อน

      Eti koma mpaka kumutero munthu osalakwa the only hope Malawians had...evil people

  • @innocentmusuli7380
    @innocentmusuli7380 3 หลายเดือนก่อน +9

    Chisokonezo mwachiyamba nokha simunati mizimu ya anthu amenewa ikunyapulani mpaka muyaluka mwayamba zinthu zomwe simukwanisa kumaliza

    • @PegoEinstein
      @PegoEinstein 3 หลายเดือนก่อน

      Sorry and shame Mr Commander

  • @PatrickKhutuliwa
    @PatrickKhutuliwa 3 หลายเดือนก่อน +9

    Chikumbu mtima chiluphani nonse amene mwachita zimenezo

  • @LuciusMowa
    @LuciusMowa 3 หลายเดือนก่อน +3

    Musalole kafukufuku ameneyo sakhala ndi osatila owoona chifukwa tikudziwa kuti chilungamo sichituluka pafunika anthu amayiko akunja abwere azafufuze zoona zenizeni chifukwa abomawa amakondelana kubakilana chipani cha MCP ndi cahakupha achoke anenewa atimaliza

  • @NOELMKWANDA-fc7ss
    @NOELMKWANDA-fc7ss 3 หลายเดือนก่อน +2

    When giving your report be minded that Malawians are alert.😢

  • @DansaYamikani
    @DansaYamikani 3 หลายเดือนก่อน +2

    Kwasala tchile moto uli konko
    Dothi kwa Dothi phulutsa kwa phulutsa tikuyenela kulimbikila kupemphera chifukwa wina aliyese azalawa ifa komanso cholengedwa China chiliyotse chimayendela MA seconds ndimene adalembela mulungu sogodzani mulungu osati munthu Amen 🤲🙏

  • @arthurprincenkhoma355
    @arthurprincenkhoma355 3 หลายเดือนก่อน

    I'm happy that Mngelo wa Mulungu anali Ku chikangawa to see everything chimene chikuchitika......So Palibe chinsinsi pansi pa Thambo God has seen everything ndipo Mwazu wa anthu osalakwawa udzafunsidwa mdzanja la wina wake Be watchful mukhoza kuoha thupi lero koma simunaphe Mzimu.RIP Klaus aka Mfana oganiza bho heavy & the other eight died in Chikangawa. & Chikangawa idzakhala mboni pa ngozi imeneyi

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 3 หลายเดือนก่อน +4

    Watching live from Canada

  • @arthurprincenkhoma355
    @arthurprincenkhoma355 3 หลายเดือนก่อน

    The bible says: "Tsoka Kwa iye obweretsa chokhumudwitsa"

  • @TamaraWalaza
    @TamaraWalaza 3 หลายเดือนก่อน

    Ubwino wake Mulungu amayika zonse poyera mweeee,ziwoneka

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 3 หลายเดือนก่อน

    Sanathe kutipha .Apha ambiri kuphatikitiza tonse amene tikipereka maganizo owaloza dzala anthu amene achita chiwembu chimenechi .

  • @brunotembo1543
    @brunotembo1543 3 หลายเดือนก่อน +2

    if i was to name this movie. it would have been named as "1000 yrs of primitivity." the president is dull to have planned that move.

  • @CrissyMapemba
    @CrissyMapemba 3 หลายเดือนก่อน +1

    Muyaluka agalu inu mizimu yonsei mwachotsai

  • @duncainjimmy
    @duncainjimmy 3 หลายเดือนก่อน +7

    I can see kuti Kunkuyu ndi dolo podziwa kufotokoza ndipo amadziwa kuzemba chilungamo .
    Komabe pallbe angakwanitse kuzemba chilungamo kwamuyaya .
    Rest in Peace Dr Saulos Klaus Chilima ,,

    • @cathykabvina3216
      @cathykabvina3216 3 หลายเดือนก่อน

      Zintchito zoipa anazizolowela

  • @shadrackdrums3536
    @shadrackdrums3536 3 หลายเดือนก่อน +4

    Khani iyi sikusiyana ndi ya president wakuyilani thawizambili adani akafuna kugwetsa ndege amasokoneza signal first nde osapusitsika ngati ana open your signal inasokonezedwa chilima was tageted amalawi akanakhala wina anapulumuka bwezi atafokoza momveka bwino iyi sigozi koma imfa.

  • @petermposa6288
    @petermposa6288 3 หลายเดือนก่อน +1

    Aircraft crash is not the same as bicycle or canoe my fellow people. Let's see this crash as a normal accident which anyone can get involved into. If a plane lose a signal its very very difficult to trace it. Also the pace at which an aircraft engage is very higher than other things. Iran President died on a plane crash and even Kenyan CDF also died on a plane crash. How did their countries took or considered those accidents???? Ku Malawi the problem is that political affiliation is that has made all these doubts. Amene amadziwa ndege sangakhale apart kupanga blame a President. Just imagine the plane didn't only carried the VP it carried many people including even MDF officers who were in charge of the flight. Can someone know kuti ndegeyo anthu atchera kuti ikagwe do you think the other on board were stupid to accept accompanying the VP kukwera mundegeyo??? Panoso the families have given chances kusankha which experts can conduct postmortem on the bodies and upon their satisfaction that's why avomeleza kukayika mmanda azibale awo. If those experts could raise doubts they couldn't accept. Nde zinazi a Malawi anzanga tiziganiza polankhula if you haven't done any research do not just talk senseless things just because of politics. Let's say the President was the one on board and the plane crashed, could we suspect the VP to have plotted the crash????? Be wise. Ndudziwa ina munyoza mmene ndalankhuliramu koma bear it in your minds am not a politician and I don't support any party. 😊

    • @KelvinPhiri750
      @KelvinPhiri750 3 หลายเดือนก่อน

      few understand this, simply because they forget that there's death, and the mentality that leaders are immortal, that death can't touch them, it's pathetic that we are still stuck in the past

  • @EmilyTembo-zu4zy
    @EmilyTembo-zu4zy 3 หลายเดือนก่อน

    Ayankha chani chanzeru pakuti anadya kale ndalama kuti asayelekeze kuthamangirako akamva zangozi😢😢😢😢

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 3 หลายเดือนก่อน +1

    The Government is shedding crocodile tears l believe .

  • @WilsonMatenda
    @WilsonMatenda 3 หลายเดือนก่อน +13

    What was the cause of loss of that signal?

  • @RhodrickKambale
    @RhodrickKambale 3 หลายเดือนก่อน +12

    Useless MDF, nkhope zamanyazi anthuwa

  • @VictorKachulu-y3n
    @VictorKachulu-y3n 3 หลายเดือนก่อน +3

    Mukamati tichotsa 2025 muchotsa chiyani palibe munthu amene angakupangileni zofuna zanu koposa yesu or mutavotera wina mavuto sanathe because we're in the last days so most of the things must be fulfilled including economic crisis James 5 the whole chapter lanu likubwera tsiku mudzafanso tiwuzeni ngati mukudziwa momwe ifa yanu mudzafere mwina ndinu mulungu work Up time is almost finished Jesus Christ is coming soon musachedwe ndi kuloza wina lozani mtima wanu usinthekaganizidwe kanu pajatu tidzaweruzidwa ndizolankhula zomwe samalani kaya inu mumamutenga chilima ngati ndani koma mwini moyo walanda or chilima sakanayendetsa dziko mokomera nonse because ma chalanges ndi ambili omwe akuchitika because nthawi yatha siyani ndale siyani makhalidwe oipa tiyeni tiwone Kwa yesu kimbukilani ku Sodom 😢ndipo sodomu wanu akubwera mwadzidzidzi mu njila ya ifa komaso pamene yesu akabwera modzidzimutsa Ngati ifa kodi akafika adzapeza mitima yathu itadzanza za ndale kapena chikondi pa wina ndi mzake ndi ngozi basi vomerezani si Mulungu chilima kuti sangafe ayi koma kuti wafa motani pamaso pa mulungu kapena nayeso mudzadza za ndale mumtima mwake ukafatu basi pomwepo chiweruzilo palibenso zomupempherera wakufa kuti akhululukidwe machimo pamene mwini wakeyo sanalape before death zija zoti mumulandile mbale wathuyo apite ku moyo wosatha ayi ndithu ndi zabodza nthawi imene uli ndi moyo ndiyo nthawi yomwe tingapemphe chisomo kuti yesuyo ayipatse mphamvu kuti tikathe kugonjetsa ntchimo kupanda kutero no second chance after death to be forgiven God bless you all this is very important that death

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 3 หลายเดือนก่อน

      Amen izi ndigwirizana nazo anthu timayila kuti aliyese azafa imfa yake tose sitingafe imfa imodzi kaya mapitidwe ndiwosiyana nkhani ndiyokoxa mitima yathu titengelepo phuziro pa imfazi kuti malingalilo amulungu ifeyo sitingawadziwe even nthawi imene ngozi yimachitika sikuti mulungu anachoka ayi amasamala komandimumene anakozela mwini wake mapitidwe a bale athuwa rip 😢 ambuye otonthoza atonthoze ziko lathu pamene timuzovutazi tikuyenela kuganizilaso za moyo wa wathu ambuye khuzani mitima yathu

    • @VictorKachulu-y3n
      @VictorKachulu-y3n 3 หลายเดือนก่อน

      @@NancyNyirenda-v9o thanks so much for your w

    • @MarthaJafali
      @MarthaJafali 3 หลายเดือนก่อน

      Ameeen

    • @VictorKachulu-y3n
      @VictorKachulu-y3n 3 หลายเดือนก่อน

      @@MarthaJafali thanks so much God bless you

  • @BrotherPaul-ln2ld
    @BrotherPaul-ln2ld 3 หลายเดือนก่อน +3

    MDF commander akuwoneka wamantha ndinso manyazi tu koma

  • @Isaiahphiri38
    @Isaiahphiri38 3 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂commander kulrphela kutankhula.
    Why not use parachute when they knew kuti ndenge insli ndi vuto as a defense force airplane.lol😂😂😂

  • @HawaSadiki-r6e
    @HawaSadiki-r6e 3 หลายเดือนก่อน

    😢unapha witika iwe relo udzitinamiza apa mesa galu nzakoyo anakutulusa Kuti udzaphenso chilima tifa amalawi tikachita zibwana achoke chakwera

  • @LewisKanyinji
    @LewisKanyinji 3 หลายเดือนก่อน +9

    A commander yankhulani zomveka ku dziko ngati wamkulu mwauzidwa kuti ndege yagwa mma 10 am inu kudikira ma communication ama Airport Ena bodza lose mukunenalo

  • @davidkayangemakala7957
    @davidkayangemakala7957 3 หลายเดือนก่อน +1

    Muziwe Kuti kuli azelu kuposa Inu kuzikokuno nde musatipusise likhala ndi udindo sikutathauza Kuti ndinuo wazelu ayi

  • @princekaponda
    @princekaponda 22 วันที่ผ่านมา

    Dear 265 ...repost this report ...athu sachedwa kuyiwala akumbukile kuti MDF inayakhula chani za ndenge yawooo
    Anachita kuphadi muthu uja ....akati akayisaka saka.koma simapezeka ..... responder inatha ma battery kalekale nde ankati ayipeza bwanji

  • @FelixKaminjolo
    @FelixKaminjolo 3 หลายเดือนก่อน

    Moses kumkuyu ....I loved and respected you but I have totally lost confidence and trust in you...WATCH OUT DUDE!!!

  • @Vwalavwata
    @Vwalavwata 3 หลายเดือนก่อน

    Zigawenga zimenezo maka chimene mukuti chinkulu cha asilikalicho😡😡

  • @HannockMesiwni
    @HannockMesiwni 3 หลายเดือนก่อน

    Nkhani zonse zomwe mungatiuze ndizaboza chifukwa apa palikhani yokhuza ndi kuthesa mugwirizano or muli inuyo mungavese ndi momwe ziliri apa

  • @AustinSaidi
    @AustinSaidi 3 หลายเดือนก่อน +1

    4hr fuel ⛽️... pompo mkudzaimitsa search operation..... ayi zikomo

  • @CarlosNdlalani
    @CarlosNdlalani 3 หลายเดือนก่อน +1

    Vuto nsilikali wa pa Nyasa wandikhumudwitsa tikati ntsilikali mwake ndi muthchire awopa bwanji kulowa mutchire ntsilikali sanganenevkuti kwada aaaa olo kutada tochi sangalephere adalima thatha chiani ndiwawolosa akamphunzire pa Mozambique aluta kontunuwa oviou !!!

  • @wilsonnoahkadyamaliro1358
    @wilsonnoahkadyamaliro1358 3 หลายเดือนก่อน +2

    amakapanga Service on an Already Serviced Ndege ?
    ife si ana

  • @AndrewDanger-ec5ns
    @AndrewDanger-ec5ns 3 หลายเดือนก่อน

    Ife kuno ndye tikulira sitikudziwa kt atitothoze ndani😂😂😂

  • @GreysonChilongo
    @GreysonChilongo 3 หลายเดือนก่อน

    Not ngozi chazona muchiziwa imwe a MCP,😭😭💔💔

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 3 หลายเดือนก่อน

    The target was Chilima all the others are pawns of the plot to cover up this croked act .

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 3 หลายเดือนก่อน

    Koma inuyo mulibe manyazi mwawa pheranji wanthuwa mulibe mantha ndi kuopa Mulungu, wamkulu wa Asirikari ndi Chakwera mutenge mitemboyo muita nfune,mukhute mulibe manyazi Wanthu woipa inu mwamu pheranji chilima kuda ndi mtima womwe, Wana a ziwanda Satana muona ziti ziku chitikireni Ku Malawi ko msogoomu mumawona ngati Wanthu saziwa mwabisala koma nsana waonekera

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani 3 หลายเดือนก่อน

    Kunkuyu ndiwe udaphanso Witika lero wapha Chilima ndi adzimzake zomse watiuza mulonda

  • @CharlesTambala-zn2bd
    @CharlesTambala-zn2bd 3 หลายเดือนก่อน +9

    Zitsiru zeni zeni...mudzafa imfa zowawa

  • @EllahEllah-hu7hi
    @EllahEllah-hu7hi 3 หลายเดือนก่อน

    God iz watching dem,no matter wat,dey will face their music soon

  • @SolokingChimzy-yt7dj
    @SolokingChimzy-yt7dj 3 หลายเดือนก่อน

    I'm here reading the comments....zikuoneka kut Malawi yense saliso kumbuyo kwa Boma

  • @Sugerman-tw4do
    @Sugerman-tw4do 3 หลายเดือนก่อน

    Mwai wangasindinalamulilidwepo ndi malawi ai ndi chifukwa ndimadana ndi kumeneko ziko likuwawa chifukwa chamunthu mozi wanga anali bakili muluzi oganizila anthu ake osati iwe abusa odalila kulandila chambale angathandize anthu munaganiza bwanji amalawi abale ao amai anga ndi bambo anga inetu ndimathawa usiluwake umeneo

  • @Sugerman-tw4do
    @Sugerman-tw4do 3 หลายเดือนก่อน

    Zaboza zimenezo oipa khope iwe ukunama zandege panyopako ndalama zizakuphanawe iwe ndindani uziyang'ane kumasoko sikutha kumeneko Ufa nawe uku namiza amalawi zichani zimenezo mkongo wamai ako opusa iwe galu ukumuikila kumbuyo mfitiyo kunali azako amapanga zimenezo osati iwe

  • @Ella13400
    @Ella13400 3 หลายเดือนก่อน +1

    Akuoneka kuti akuopatu mkulu wa asilikali

  • @CrissyMapemba
    @CrissyMapemba 3 หลายเดือนก่อน

    Sitikufuna kumva za kuziwa za experience ya ogwira ncthito khani ndi yoti mwapha achilima

  • @EmilyTembo-zu4zy
    @EmilyTembo-zu4zy 3 หลายเดือนก่อน

    Musaone ngati sitikudziwa kanthu zonse tikudziwa a commender akun'kuyu achakwera mwazi wa saulos chilima uli pamutu panu agalu anthu inu ndipo chaka cha 2024 sichitha nonse m'mwalira agalu inu

  • @giftbanda7690
    @giftbanda7690 3 หลายเดือนก่อน

    Kwasala ntchile ndikomwe moto umapita ....Allah akuziwa zose ..Taluza miyoyo ya abale anthu ..Allah alipo ndipo zizaziwika

  • @IsaacTsinde
    @IsaacTsinde 3 หลายเดือนก่อน +2

    Ma phone onse atengedwatu mumvele limpopo fm with comrade Nthanyiwa..

    • @IsmailKhulela
      @IsmailKhulela 3 หลายเดือนก่อน

      Tipeza bwanji

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 3 หลายเดือนก่อน

    Izi si zoonayi matupi amayenera kuunikidwa ndi madokotala pamalo pomwe panachitikira ngozi osati kukaikakaye ku motchale akaonapo chani poti matupi akhala atauma ndi ma ayesi? Mbuzi zawanthu,anthu akupha, komanso kafukufuku samayenera kuchita a malawi defernce for anafunika mabuungwe chiwembu achita ndiomweo apangabwanji kafukufuku ayini ake achiwembu mukuonangati chirungamo chidxiwika ? Apa akunamiza mtundu wa amakawi iyaaaaaa

  • @julietbanda5203
    @julietbanda5203 3 หลายเดือนก่อน

    MCP yakupha, president of malawi chakwera,with his team,they are both killers

  • @KereeditseMotsetse
    @KereeditseMotsetse 3 หลายเดือนก่อน

    Nthawi zambili ntchentche yojijilika inaphinjidwa ndi mchimba mbubzi ikakondwa ogula amakhala pafupi sichachilendo ukamakumba nzenje kuti wina agwelemo mulungu amakugweselamo wekha tiphunzile kukhala wabwino kwa anzanthu

  • @ShabaniKuswere
    @ShabaniKuswere 3 หลายเดือนก่อน

    Tamuyang'anitsitseni wamkulu wa asilikaliyu akuchita kuonetseratu Kuti akukamba bodza,mukamunvetsera statement yakoyo mkatimo,akuti VP amapita ku maliro a Ruph Kasambala yemwe anali nzao aaa akuluakulu chirungamo palibe apa

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er 3 หลายเดือนก่อน

    Akumkuyu undisamale,iweyo ndiye wakupha ndi mzako zikhale ng'omayo komanso chitsiru chimzanu chichakweracho muzafa imfa yowawa agalu inu

  • @alexmkolongo3089
    @alexmkolongo3089 3 หลายเดือนก่อน

    Munakanika kafukufuku wa Martha chizuma nde zitheka bwanji wa chilima

  • @Thesevengp
    @Thesevengp 3 หลายเดือนก่อน

    Bla bla bla bla. Just wait, the truth will out!

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 3 หลายเดือนก่อน +1

    Nkhope zofuwa ngati mwachezera kukachasu

  • @CharlesTambala-zn2bd
    @CharlesTambala-zn2bd 3 หลายเดือนก่อน

    Kafukuku..ameneyo.... sakufunika ... just go straight on point

  • @HestingsZiba-d6k
    @HestingsZiba-d6k 3 หลายเดือนก่อน

    Kunkuyu anapha witika galuyu anthu oyipa kwambili ndipo a kuyankhula ngati zilizowona koma opha azawo ndi wowo

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 3 หลายเดือนก่อน

    Kunkuyu akuona ngati anthu akhala chete pa imfa ya vp mene anakhalira chete atapha Allan witika apapokha nkhanga zaona sitikumva za usiruzanuzo agalu kwabasi

  • @MPHATSOKALUWA-lm2uy
    @MPHATSOKALUWA-lm2uy 3 หลายเดือนก่อน +2

    Nde fuel wambrmbr bwanj sinayake yitagwa bodza limnelo

  • @Dee01papa
    @Dee01papa 3 หลายเดือนก่อน +3

    Fuel okwana ma hours 4? Funso limenelo simunakambilane komwe mumauzanako and you didn't see it coming. Fuel ma hours 4? Hahahaa

  • @Sugerman-tw4do
    @Sugerman-tw4do 3 หลายเดือนก่อน

    DC tokotani osaopa galu ameneyo chakwelayo bon kalindo timakudalila tili Bali yako osaopa ai usamagone nyumba imozi galuyo akusakasaka umaimilila Malawian osaoopa chakwela panyopako

  • @anifoiuene6301
    @anifoiuene6301 3 หลายเดือนก่อน

    Iwe mkulu wa nkhondo machende abambo ako plus iwe kunkuyu machende abambo ako inu ndi omwe mwapha Chilima

  • @kestenlemucha8316
    @kestenlemucha8316 3 หลายเดือนก่อน

    We dont need uto recture us about pilot or assistant earoengineer they are just innocent too. U must answer the relevant questions

  • @StazioChitsulo
    @StazioChitsulo 3 หลายเดือนก่อน

    Anthu oyipa inu khope zanu zikuchita kuonesa kt mukukamba boza lenireni mitsonkho yamalawi mpaka kuphelanilana chilungamo chiziwika mpopano

  • @AnorldJohn
    @AnorldJohn 3 หลายเดือนก่อน

    Kodi kumalawiko kuli chitetezo asilikali aku Israeli ndi Rwanda amafunanji mudzikomo

  • @CharityChirwa-t1e
    @CharityChirwa-t1e 3 หลายเดือนก่อน

    Kulibeino kusiya kutibwelesela manyqka anuwa zomwe mafuna zatheka koma tchitoyi mwangoyamba koma towone momwe muthele athu owoneka ngati khosa koma mulibng'ona zachabe chabe witika munampha miya munampha kasambala mwamumpha chilima mwamumpha ana ayini osalakwa mwawampha kuwopa mawumboni koma umboni wayamba kutuluka mizina layesu chilima amaphela muchowonadi ndipo kolona anafanaye mmanja uja ndiamene atakusawuseni fiti zachabe chabe

  • @chewejeali1059
    @chewejeali1059 3 หลายเดือนก่อน

    Commander kuyipa nkhope mpaka mtima chimodzimodzi

  • @CarlosNdlalani
    @CarlosNdlalani 3 หลายเดือนก่อน +1

    Am Mozambiquean we will teach you how sojars doing guys

    • @lakatkat_lakat5250
      @lakatkat_lakat5250 3 หลายเดือนก่อน

      Just maintain peace in your country before you poke nose other countries stuff.... This is accident stop pointing fingers

  • @ChrissKaswaya
    @ChrissKaswaya 3 หลายเดือนก่อน

    Aliyese anaba ndalama m bomam anthu kuvutika kukwela kwazithu mulungu wayamba ku yankha and ubwino wake aliyese azamfa koma kusiyana mayendedwe

  • @AnorldJohn
    @AnorldJohn 3 หลายเดือนก่อน

    Patsikuli ndenge zonse zomwe zinauluka kapena kudutsa mudzikoli zikuoneka bwino bwino bwanji sizinataye signal kukataya yomweyi kodi akupatsani ndalama eti

  • @mphatsosadiki4983
    @mphatsosadiki4983 3 หลายเดือนก่อน

    Misozi ya Malawi singangopita in vain,tikwera phiri ndipo pemphero tiswa ndithu Mulungu amva pemphero lathu...Tatopa

  • @christinagmkumbwa7230
    @christinagmkumbwa7230 3 หลายเดือนก่อน

    You government... what we are questioning is your poor response... vp and others in the mountains .....4 hours.... inu munabereka... musadzapweteketsa mtundu wanu...

  • @TiwongeLuwe
    @TiwongeLuwe 3 หลายเดือนก่อน +1

    Munthu akamayankhula bodza or nkhope yimachita kuonekerathu ambuye akuoneni RIP our Malawian😢

  • @isaacthawani5442
    @isaacthawani5442 3 หลายเดือนก่อน

    Munthu oipa uyuuuuu oipatu koma azafaso Naye ndipo azayakha wakupha uyuuuuu

  • @ThokoMalele
    @ThokoMalele 3 หลายเดือนก่อน

    kodi nthawi yakusowa kwa ndegeku kunalibe kafukufuku wa ma herocopter kuti aziona zapansi ndima GPs kusiyana ndi magalimotowa?

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w 3 หลายเดือนก่อน

    Iweyo walandira nawo ndalama eeeit galu commander opanda nzeru

  • @mafukenimasangwi5487
    @mafukenimasangwi5487 3 หลายเดือนก่อน

    MDF yogwilisidwa nchito ndi andale koma ku Malawi

  • @ShabaniKuswere
    @ShabaniKuswere 3 หลายเดือนก่อน +1

    Zoona mkulu wa asilikali kumachita kuwerenga moonetsera kuti wachita kulemberedwa ndianthu ena cholinga akwanitse kunena bodza

  • @MadalitsoBitton
    @MadalitsoBitton 3 หลายเดือนก่อน

    Zabhoza zimenezo tiuzeni zowona soja ayi maboza😡

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 3 หลายเดือนก่อน

    Mizimu ya anthu onse amene amwalira wa ikusowetseni mtendere nonse amene mwapanga zimene😭😭😭😭😭😭😭

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 3 หลายเดือนก่อน

    Kunkuyu akuziwapo Kathu pa imfa ya Chilima

  • @SPEARSTOSUCCESS-mv4ct
    @SPEARSTOSUCCESS-mv4ct 3 หลายเดือนก่อน

    Aaaaa ndiyengat ndege. Ya asikikari ma palatute anali kut! Mswwii

  • @BehindThecamera-xo1qg
    @BehindThecamera-xo1qg 3 หลายเดือนก่อน

    Anthu akungowopa kuwamanga basi zomwe mukunena apazi si zoona

  • @eliasmhone-cy1dn
    @eliasmhone-cy1dn 3 หลายเดือนก่อน

    May comfort us.we are together even as Zambian s

  • @AnthonyHalale-gp3md
    @AnthonyHalale-gp3md 3 หลายเดือนก่อน

    Mwina sindikunva bwino bwino pa ma hours amene inayenda kuchokera ku mzuzu kupita ku lilongwe komanso kubwerera ku mzuzu.ndiye amayenda masiku angati?.coz 24 hours make a day,so 3000 plus ulendo wake omwewo

  • @OretarbadrBwanali
    @OretarbadrBwanali 3 หลายเดือนก่อน

    Munthu amene amaziwa kut mulungu adalenga imfa sazamuloza chala munthu wina aliense chifukwa cha moyo chilichonse chizalawa imfa

  • @JoyceBanda-k8t
    @JoyceBanda-k8t 3 หลายเดือนก่อน

    Iwe kumkuyu umazolowera kupha anthu allan witika ali kuti lero mwafuma kupha chilima kumkuyu chikumbu mtima chikugwire ukuona ngati iwe udzakhala wamuyaya

  • @charleskazembe5728
    @charleskazembe5728 3 หลายเดือนก่อน

    Longosolani mene mungachitile Ambuye akumva bas kamaso waona

  • @PatrickKeneth
    @PatrickKeneth 3 หลายเดือนก่อน

    Komamso ndimmene ndikumvela number ya ndege imene ankwela ndi imene inapezeka kuchikangawa ma number ndikuwona ngati akusiyana bwanji?

  • @Mphatso-jr1fb
    @Mphatso-jr1fb 3 หลายเดือนก่อน +3

    Koma mukawaone Akuoneka comfortable akamalakhula? Ine sdikuwaona bwino kulakhula ndikhawa

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 3 หลายเดือนก่อน +1

      Nkhope zamanyazi ndipo zafuwa ngati achezera kulira uli ufiti💔💔💔

    • @inessmsiyambiri8517
      @inessmsiyambiri8517 3 หลายเดือนก่อน

      Kuyalukati