BRIAN BANDA NDI A PETER MUNTALIKA 21 September 2024

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 20 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 11

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    A Brian musanamepo apa Dausi ananena kale kuti ndinu a DPP. Bwanji Chakwera simunamutsatire msonkhano wake utatha. Mungonena kuti mukuzikonzera malo aku State house Cathy Maulidi angogwiritsidwa ntchito iye sakudziwa cholinga cha Brian Banda

    • @WinerdShadreck
      @WinerdShadreck ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kkkkkkkkkkkkkk

  • @VenançioZocueza
    @VenançioZocueza ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Munthu aliyense alimkufunika Kwake. Kulephera convention sikusonyeza kuti siofunika.

  • @FontesChisale
    @FontesChisale ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nenan kt mumakaphulila sikuti tingakunenen , mwanyanya dyera inu eeee mukwanisa .

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bwanji sanachite condemn zimene zinachitika ku Nsanje pamene magalimoto a pulezident anagendedwa. Bwanji osamufunsa zimenezo?

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kumachita ku nena kumsonkhano waku Phalombe kuti Chakwera kuno asadzabwere inuyo anyapapi a DPP dziko ndilanu lokha kuti anthu azingokusekererani azikuthyolani kumene makosi mukapita kwinakonso. Mwapambana chani inuyo?

  • @ELIOTMUNYAMAPEPAKAZIZWA
    @ELIOTMUNYAMAPEPAKAZIZWA ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Brian ndiwe wadyela komaso wosokoneza

  • @DysonTummiesSajiwa
    @DysonTummiesSajiwa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwawondat a gogo pitala kwakudani ku world 🌎

  • @giftmwale8475
    @giftmwale8475 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Peter muthalika ndi galu weni weni weni 😂

  • @SABITIKAISI
    @SABITIKAISI ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ❤❤❤

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 50 นาทีที่ผ่านมา

    Koma zoti wakulazo bodza taonani akukanika kuyakhula kkkkkkkk aaaaaaa chipanichi da Honda koma madalawa gosokoneza ndithu