The song is way too old but because it was a hidden to us that this song will one day be a emergency. Isn't easy to accept that the man is no more 😢😢😢😢😢😢
Mark my words...Dziko lakumidima lipanga chothekela kupha onse omwe ali ndi maso mphenya ulamulila dziko la Malawi kufikila Anyamata a illuminate mosogodzedwa ndi prophet wao atalitenga Dziko...If You know you know
I feel bad like i am the one of Malawi people but i am Zambia anyway only God knows Rip 😭😭😭😭😭😭😭😭 we are one people namvera kuyipa😭😭😭😭😭
Even here in sensheke,people are in sombre mood coz of this.Am a malawian.
Imagine am a Malawian, the way I am feeling, this is too much, Chilima has gone just like that eish😭😭😭😭😭😭
These are the times that will tell you that we are one. This is painful
Your speach was always about wishing better for the Malawians...
Rest well our HR. Dr SKS💔💔💔🕊️🕊️🕯️🕯️🕯️
Misozi sikutha mmaso mwanga😭😭😭😭😭..... tsoka iwe ozetsa chokhumudwitsa hi😭💔💔💔
Imfa yowawa kwambiri misozi yosaxhoka mmaso mwanga ndamulira ngati m,bale wanga 😢😢😢😢😢
It wl take a lot of time and years to come to myself,this painful death wl be in our hearts forever,,May His Soul Rest in internal power
this song makes multiple streams of tears
It reminds me of Dr Kwame Mkuruma he survived four assassin's may the soul of SKC rest in peace
Anthu talira enough is enough mulungu akadzuka papando wake wachiyerunzo iwe amene ukulilitsa anthu samala he's supreme God magastrate, superlative
Mzimu waChilima ndi onse omwe adali mundege yomwe yatenga abale athu enanso- iuse mumtendere ❤
Wafa infa yowawitsa kwambiri 😭😭. Rest in peace VP, Shanil, Daniel and six others 😭😭😭😭
Ngati maloto kt chilima kulibe😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
😭😭😭😭😭💔💔💔💔
Sinaswekepo mtima ngati ifa iyi abale ndalephera kuchinga misozi yanga😢 ndamulilira chilima ndi mtima wanga onse
Imfa yawawa iyi, munthu kufa mowawa chochi😭😭😭😭 Ambuye akuona zonsezi😭😭
Kma Chilima akanadziwa kut anthu ambiri timayang'anira pa iye sakanatithawa chonchi😭😭😭😭
Tizatonthola Koma mochedwa,,,😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
A very beautiful tribute ever.. Rip Dr SKC till we meet in the Glory of God 😭
Ine ndudikira ya Nkasa
Mene anaimba nyimboyi Evance ngati kuti ankadziwa zizachitike💔😓
May God grant him internal peace in his sleep, heartbreaking 💔 😢 . Tonse tidzapita komweko ndithu
I can't stop crying Lord! I have no strength anymore! Heal my country Lord 💔😭
😭😭😭😭😭💔💔💔💔💔 my president,I feel like am in a continuous dream eish, we live in a wicked world.
Rest in peace Mr Chilima ndi anthu onse mwamwalilira limodzi 😢
Mulungu mudzilemekeze nokha paifa ya klaus saulos chilima amene waika maganizo ndikuthandizira kuti lero vice president amwalire mulungu muwakathe ndikhwiyo wanu zimu wake uuse mumtendere zoona wafera mbendera yadziko lanthanu kutimenyera mtendere koma osaupeza❤ chauta achita koposa
Amen😭😭😭
Abale this is so touching 😢😢
Indeed 😢he was the great pillar of Malawi but wicked people killed him 😢when are we going to be free sure 😢why we don't want development sure 😢
Tizazindikira bwino pasogolo
RIP SKC🙏🙏😭😭😭😭💔💔💔
Mhuuuuuuuuu sk puma mtendele
The song is way too old but because it was a hidden to us that this song will one day be a emergency. Isn't easy to accept that the man is no more 😢😢😢😢😢😢
Rest in Peace Dr Chilima.. The Catholic Church will forever miss you.. Kumwamba ko Mulungu akuona zonse.
For sure tizazindikiladi bwino pa tsogolo 😭😭😭😭
Km2 meleka nyimboyi waimba bho penaso amwene mumatiimilira ulemu wani😮😮😮😮
If am dreaming, please wake me up from this terrible dream😢💔😭
No more chilima ngt boza😢
😭😭😭😭😭💔💔💔💔
😭💔😭😭😭 dziko lodzadza ndi anthu oipa
Ambuye mudziwa ndinu😭😭😭😭😭
Big up Evance Meleka....RIP Bwana Chilima
Kodi oimbawa osang{sonkhana pamodzi ndikuimbila limodzi bwanji zikhale ya 2 hours timvela
koma mesa nyimboi ndiyakale
Ambuye akuona zonse😭😭
Big up mwana wa meleka
Zomvesa chisoni
Very sorry Malawi anzathu mulibemwai chilima anali kufuna kupulumusa ziko 😭😭💔💔
SKC you will always be remembered
Thanks Evance meleka and let tell all Malawians that 2025 to be united and choose the best leaders
Wafera chilungamo ndikunvesesa ndikufewa ntimawa kwake ndpo masiku ano chilungamo tizichiwopa ndithu
Wachilungamo sakondedwa
@@user-fq7gb8gm3qeeh izo nde ndi zoona
I still remember this political rally, It was very emotional. The man is no more 😭😭😭💔 life is unpredictable
Am real African and I love all African s people sorry for all people.
Nice song, poor vedio camera
He was our hope I it wl take time to forget
Amen mzimu wanu uusa mtendele achilima ndi onse amene anatisiya
I had,we had the hope........Chilima you have left us in DESPAIR....R.I.P
Be comforted. Have Faith in God! He never fails 😮
😭😭😭😭😭
Ndimaona ngati mudzandiuza kuti boza ali moyo😢😢😢
I love you saulos clous chilima
This death has dealt us a heavy blow
😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢 kufela dziko ndipo wandiwawa ngati ndiwe mubale wanga chilima mayo mayo ine imfa kuwawa mweee
Amen RIP Chilima will never forget only God knows
INNA LILLAH WAINA ILAIHI RAJIUNA 😢😢😢😢😢
Nyimbo iyiy ndinaivelako pena ikumakhala ngat ikalotedzela ifa ya Tate wathu wa utm 😭😭😭😭😭😭😭
U had version words... Rest well Dr SKC 😭 the president
😭😭😭😭😭 Zoonadi wafera mbendera ya Malawi chilima eish
Ya apa wayifera
Ngati ndikulota, ndizidzimuseni Ambuye💔😭
Big up bro 💪
Mwapha chiyembekezo cha AMALAWI 😭😭😭😭😭😭😭😭
Eish chilima wapitadi osadwa koma ndipemphero langa kwa mulungu kuti achitepo kanthu kwa onse okhudzidwa za imfai
Pita mukapume mumtendele
Eish mr chakwera muliko mulungu akuzindikilitseni mwina muli mu nyengo ya marko 8 ves 32 muzazindikira choonadi ndipo choonadi chizakumasulani
Inna lillah waina ilayih rajiuna
Misodzi mumaso mwanga to my president😢😢😭😭
Ndizoonadi tidzanena nthano
So sad 😭rest well our vice president Mr Chilima, oh my God 😭😭😭😭😭😭😭
Nyimboyi ndiyakaletu
😭😭😭😭😭 koma imfaa iyii yopweteka
This song make cry again
Ndipo sitikuopa😢
Mr Meleka mwandiimilira ndithu
🙏 may God continue be with Chilima🙏😭😭
Only God knows muwuse mutendele Dr chilima
Mulungu akudziwa zonse
Ndipondi mafelandi ndembela Dr Chilima
Rest in Peace Dr SKC
😢😢 rest well my vice president ndale sizikomanso
Ndilire bwanji ine 😢😢
Hallelujah God pls may these people rest in peace 😭😭😭😭
Only God knows 💔
😭😭😭😭😭 zosayenda
Zengerezu anayenda kwawu kwawuu
Tidzakhalabe pambuyo pa utm osafooka
Zosayenda 😢😢😢
Mark my words...Dziko lakumidima lipanga chothekela kupha onse omwe ali ndi maso mphenya ulamulila dziko la Malawi kufikila Anyamata a illuminate mosogodzedwa ndi prophet wao atalitenga Dziko...If You know you know
evance meleka big up
Chifunga a day will come for you
Oh! My God!!!
I wish there was a second chance for him to leave
Leave ????? ?
Live
Oimba akumalawi kumagoimba ma tribute mmalo mothandidza amalawi Kut tinkhale pa mtendere ayi mmmmm
He waz my Hero
Mmmmm koma oyipayo anakamvera nyimboyi 😢,😭
Wandilitsa Evence😭😭😭😭
R,I,P. My president zowawa 😭😭
nice song kutidekhetsa
Inu nyimbo ya kale iyi
Oyenda ndi lupanga azaphedwanso ndi lupanga muyeso omwe umuyesa nawo nzako omwewo uzayesedwa nawo galu wankota sakandira pachabe
Chakwera afune asafune 2025 ma vote sazawina ndipo ngati azawina akanifunse or pompano anifunse
Good Messnge