As a DPP supporter, I agree with your idea of not fighting those members of Parliament because it's pointless anyway. It's better just to leave them to finish their remaining period and find their replacement peacefully and smartly
@@Chisomo-dh2gq Aise ine siwa MCP ine ndwa UDF kmano timaona chinsogolo nde nd DPP ngakhale ine ndli wa UDF popanda DPP ife a UDF sitingawine ndchifukwa ine ndmadalila DPP kut mwina 2025 ngakhale ndli wa UDF
Bon kalindo simuthu wa bwino pkhani ya ndare chifukwa ndi munthu amene amangofuna zabwino zikhare zake basi alibe fundo zeni zeni zoti ineyo ndi ngavepo or pang'ono
APM my vote sitikufuna achikambelembere ayi APM ❤❤❤❤❤
DPP sikusunga kape or m'modzi
Peter si munthu wamba akuxiwa chomwe akupanga mukuwona ngat nd mcp
Apm my vote
Program ya Gwede-gwede ili very hot Masiku ano🔥🔥 YOHANE 8:32 Coonadi cidzakumasulani..
Kawawa achoke basi APM my vote
ADADI A.K.A FAZALA HOZA HOZA MY VOTE
Yaaa Dpp sikusunga kape bwino masewela
Bon Kalindo is good guy
Cadet wafa basi
APM activated 💙💙💙💙💙
Awasiye koma dziwani kuti pali madera ena amawinira dzina la chipani ngati kumwanza balaka ndi thyolo mulanje lilongwe tchisi ndi dowa
Apm the great man!!!! My vote achosedwe tisanyengelere zisiru za anthu ife zauthira kuwiri ayi!!
APM is the only hope for Malawi
Tikufuna kuti tidziwe zoona komaso akamatiuza zomwe zinachitika kuti ndege igwe adziwe kuti sife Ana komaso sife Anthu osaganiza bwino and mikuluwiko timayidziwa 😢
Ma cross over omwewo
Ukuchita kudziwa kuti mkaziyu sakugwilika waponda mwala za iwe sakusamala umuyitane amveke ndili buzy bwerani tikambirane ndatanganidwa ndiye chopangira za ukwati ndi chani kuthetsa kupeza wina APM simwanatu ayi ndiye enanu mukungolubwa apa zamkutu achotse ma virus mu chipan amene angaononge kusogoloku .
Peter anakalamba mutu wake udasiya kugwira ntchito bwino bwino
😂😂😂😂 just imagine 90 yrs kumafunabe u president musiyen adzagwa ndi BP gogo ameneyi
we love u peter mutharika❤❤
Ndipo live zusonga makape thawi imeneyo tilibe
Chipani chombwambwana dpp. Mwayiwala 2005 dpp chitangopangidwa chinalibe phungu ngakhale mmodzi. Aphingu anapeza ochoka kuzipani zina. Bingu anakanitsitsa kuti section 65 igwire ntchito. Musatinyanse
voterani adadi mulungu satayawache chipepeso 1biliyoni ngatizonama ndiyeeasawine mbavazozichoke
Page iyi ndayamba kuinyumwa!
More fire malawi dziko loop mulungu ilo . Ayerekeze wa kumidima kuvomeleza zopusazo.
Usi suyaka popanda moto, zauku mwapita uku mwapita tataya nazo Achilima, amenewo achoke akuphesani chifukwa mutamange uku Iwo azipita nazo kuchipani chinacho kukamasula ganizanipo bwino pamenepo dziko lake si ili
Nzeru yabwino aku Mibawa kuthandiza cipani cacitetezo, cilungamo ndi citukuko.
Vuto ndi respect aphunguwo alibe respect nd chipani chawo dpp kuchotsa anthu amenewa ine ndikuwona kuti vuto palibe what we need is respect.
DPP mukuchosa anthu Osayiwalatu kuli 50+1 mukwanisa km 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂kkkkkkkkkk uyelekeze....udzasamuka muno Malawi....ukwat umakhara pakat pa mwamuna ndi mkazi
DPP ikanawasiya anthu amenewa, tionana chaka cha mawa. Nthawi yatha kale.Bola taona mawanga awo. Akaime ngati independent tizaone ngati atazawine.
Pita muthalika simuthu wamba akudziwa chomwe akuchita pothamangitsa agalu amenewo
Khonswe owononga ntedza wambeu amaphedwa bas sakalamba, amenewa achoke ndikonswe
Dpp inatha kale,nde bolanso chikomeni kk aphunguwo sakuonamo sogolo ata
Eeeee achoke ndithu amenewo bwana ...
APM vote vote vote
Powerful!!!! inuyo mumatha guys, proud of you ❤❤❤
Achotsedwe basi chifukwa ndi anthu adyera amenewo .
Mpaka ayitane aphungu a mcp zachmba eti
Sefa WA DPP Ali boo siwamataya akunyodola boo
Steve amandiwaza ati aise honorable uyerekeze 😂😂😂😂
Musamazimbaise omwe azakumangeyo ndiyemwe anapha
We a wise man like APM🙏
Koma dpp ikuganiza bwanji kumabudulabe anthu mchipani zowina zitheka bwanji abale?????
Wawona patali
Apm my vote
Apm my vote
This man has a beautiful future in the circles of journalism, KEEP IT UP
Apm my vote
Ifeso ndi a Dpp komano zomwe zikuchitika muchipanichi sizabwino ali zii or kususa boma lokubali
Tizaifera mbendera iyi wina aziwaso
Kkkkkkk his brother dump udf for dpp why not impeshed wakula uyu
Steve iwe pano wafikamo 😂😂😂
Kkkkkkkk
Chimkuza mau ….kukapanga gwedwe gwede kuti Aunt Tiwo akhaleno…. UNCLE TIWO…..😝💃🕺
I like you guys you talk and don't fear anyone. ❤
Nkhanga zinapangana kusanapse chokaniko Ku DPP kulibe chilipo pitala ndimu lomwe watsankho chitulukeni chamunthu icho chakwera bomaaa ufune usafune
Adad vote yanga yilipo
Khani yogonana amuna okha okha kapena amkazi okha okha amipingo kwanthu kuno muzinena zoona madziwapo Kathu chifukwa Bingu dziko muno atakana khani imeneyi simunamuyikire kumbuyo kapana kunena ma church kuti asapange ziwonetsero akukana zopusa koma inuyo munali kulemba ma katala kwa Bingu zili zopusa
Bingu anaphwanya gawo 65 kuchoka ku UDF ramulo silinagwire ntchito bwanji??
Steve apoo ponkha Nde wakwiya ndiyamathanyula 😂😂😂😂😂😂😂 amene azayelekeze tizamponda oyankhula zamathanyula
Pano ndi mthawi yot zonyasa zonse zichoke sakulakwa, tisanayike mpunga mumpoto timasankha miyara .
Awachotse and anthu amenewa sazawinaso ku madera awo aphungu oyipa akufuna azikapha anthu ndi anzao a mcp
vuto anthu Andale ndi ozikonda especially when to black leadership
❤😂❤😂❤ very nice 😂😂😂no man to man no guys no lesbian ❤❤❤😂😂
Kkkkk zawo izoi😂😂😂
Apm bomaaaAa
Why apply to others, and not others?
Chosan basi AAA atibowe
Kodi mnyumba mwako mwana wako akamasapota mdani wako ungasangalale naye?
Wina anakhuza ni Mr khafula womwe anachoka ku mcp kupita ku UDF
Galu ndi Peter muthalika musogoleri wopanda nzeru
😂😂😂😂😂😂Cadet wa MCP
Kuyankhula kwa bwanji kumeneko uli ndi umunthu koma iweyo?
Even Makolo ako ndi apanda nzeru, mchifukwa anabereka mwana opusa ngati iweyo.
I don't like Peter munthalika
He doesn't even know that you exist 😂😂😂😂
Koma dpp ikuthani ndithu ziganizo za dad kaya tiziona 2025
We need a wise man like APM ❤❤
Good Messnge guys
Guys mumavala boo big up.
💪💪💪💪💪 DPP my vote 💪❤
We don't care
Mbola zonse kumeneko azichose basi .
Achita bwino awachose apeze awo aDPP
Amaitha ameneo
Ndipo live akazitape kuno aiii
Ause muntendele amenewo alute
Aphungu Adelaide amenewo
😂😂😂😂
My vote
Paja DPP ndi Briefcase party osamadabwa zizindikilo zakutha kwa chipani
Anali a nsanje central
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Malawi tivotele Atupele muluzi chifukwa his mind is very fresh
Osati Chakwera
Fire💥💥💥
Osamasunga njoka
Cadet kuzngulira mutu
Awachotse osanyengelela
😂😂😂akumanga tu
As a DPP supporter, I agree with your idea of not fighting those members of Parliament because it's pointless anyway.
It's better just to leave them to finish their remaining period and find their replacement peacefully and smartly
Kma agalu A dpp amatikwana bwanj
Galu ndiiwe uli ku mcp weee
@@Chisomo-dh2gq Aise ine siwa MCP ine ndwa UDF kmano timaona chinsogolo nde nd DPP ngakhale ine ndli wa UDF popanda DPP ife a UDF sitingawine ndchifukwa ine ndmadalila DPP kut mwina 2025 ngakhale ndli wa UDF
@@Freedomchennl47ndechifukwa can muku nyozo muli wa UDF sibho
Msiyen ameneyo mutu wake sugwira ntchito galu ndiyeyo
Bon kalindo simuthu wa bwino pkhani ya ndare chifukwa ndi munthu amene amangofuna zabwino zikhare zake basi alibe fundo zeni zeni zoti ineyo ndi ngavepo or pang'ono
Dpp namalomba panyapako ndi gogo wanuyo...
❤❤❤❤❤❤ dpp sakulakwa
I love you Selina , I need your number ❤
AI sapanga nao mathanyula Selina