HOT CURRENT - 28 JULY 2017-WAS MUTHARIKA RIGHT TO CALL CRITICS STUPID?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 11 พ.ย. 2024

ความคิดเห็น • 35

  • @macksonsimkonda9172
    @macksonsimkonda9172 7 ปีที่แล้ว +2

    The problem is
    most of the clever people left outside
    koma manganya you are really clever and Honest man
    Thanks

  • @salimajida138
    @salimajida138 4 ปีที่แล้ว

    Khulakhula zoyonandithu 👏👏👏👍

  • @yusufmakwinja8958
    @yusufmakwinja8958 7 ปีที่แล้ว

    awa nde mayankhulidwe anzeru osati nthawi zonse zomwe timaona apa zongokangana this is real debate osati zikumachitika zinazi chief editor uja please he must try to avoide taking things personal debate izimveka bwino bwino this was good mkonzi mr Brian zilili bwino thanks to times tv

  • @BobZumani
    @BobZumani 7 ปีที่แล้ว

    Chidule munthu akakunena kuti "you are stupid!", iwe umangoyankha kuti " thanks, you too!"; basi life goes on

  • @fredchiyimh2982
    @fredchiyimh2982 7 ปีที่แล้ว

    kumeneko ndiye kukoza Malawi wanthu kulakhula mopanda mantha kuti chilungamo chiyende ngati madzi ...!!! umakwana manganya ndi wankulu big up sepickng no fever without fear........

  • @dawoodmdoka3960
    @dawoodmdoka3960 6 ปีที่แล้ว

    ZIKOMO MR USI mumatiimila

  • @seventhday103
    @seventhday103 7 ปีที่แล้ว +1

    koma anthuwa iwo sanavotere mutharika komanso ndi osusa boma awa kkk

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 ปีที่แล้ว

    Kagulu katiyika mmavuto kaja ndi aka eti lero tikuvutika kwambiri
    Akudalitseni nonse

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 ปีที่แล้ว

    Chiwanda cha wansembe ichi

  • @thomassawati7918
    @thomassawati7918 4 ปีที่แล้ว +1

    I don't see any problem with what was said by Mutharika when it comes to politics,how many times did Bakili use such words but nobody took it seriously. The problem is that your now enjoying freedom of expression but you don't seem to realise that, during the leadership of Bakili u couldn't have chance to vomit such nonsense. Manganya ,Banda komanso iwe wansembe wa fake stop talking trush

  • @trustbanda6577
    @trustbanda6577 7 ปีที่แล้ว

    kuzuzula komanga kt olakwisayo amve nde uku osati Kasakula amangolalata,kutenga zinthu personal

  • @tracymatewere6012
    @tracymatewere6012 7 ปีที่แล้ว

    Zilibwino

  • @dawoodmdoka3960
    @dawoodmdoka3960 6 ปีที่แล้ว +2

    FATHER AKAFUNA KUTUKWANA ATUMBUKA AMAZUNGULILA BWANJI KKKKKKKKKKK

  • @denniskhalamba9655
    @denniskhalamba9655 5 ปีที่แล้ว

    Mpitho khunyeliwa 🤣🤣🤣🤣

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 ปีที่แล้ว

    Wansembe wakuba uyu

  • @strandholyvoicesanglicanch4332
    @strandholyvoicesanglicanch4332 7 ปีที่แล้ว

    Koma yah..... Manganya ndakatundu pa m fundo.

  • @hassamnaulanamaulana2721
    @hassamnaulanamaulana2721 7 ปีที่แล้ว

    zina ukanva mmmmm

  • @saideosman1617
    @saideosman1617 7 ปีที่แล้ว

    Manga kunzelu zokha ndiiwedi basi kuzindikila polankhula that's right way

  • @kaitanokagalu
    @kaitanokagalu 7 ปีที่แล้ว

    Kikkkkkk bwana Manganya kutsamwa kumeneko, mizimu yakanatu pamenepo hahahahahahaha!!

    • @BobZumani
      @BobZumani 7 ปีที่แล้ว

      Hahahahaha

  • @noelngwira3923
    @noelngwira3923 7 ปีที่แล้ว +1

    Akumpoto ndianthu aphokoso ndiye iti imeneyo Father ?? Ndimayankhulidwe anji amenewo

    • @keithbanda3007
      @keithbanda3007 7 ปีที่แล้ว +3

      Dada Ngwira mwafumba makola, but what Father meant was that North is not the only Region to mind when it comes to regionalism. However, because of their general Tumbakaness, they may seemingly stand out uniquely vocal. Since South and Centre share most of their cultural elements, including Chichewa, most of the times people forget they are different regions. Nevertheless, Centre is also a region to include when making appointments. God bless you Father Mlomole and Elder Usi for your educative and balanced remarks. We pray for the president to respond kindly.

    • @phillipgomez1335
      @phillipgomez1335 7 ปีที่แล้ว +1

      Noel Ngwira ati amakonda zolongolola kkkk waiwala atumbuka zomwe achita

  • @alexkaunda-oi8jf
    @alexkaunda-oi8jf ปีที่แล้ว

    Muthalika too much nyaupe

  • @elwinchirwa1218
    @elwinchirwa1218 7 ปีที่แล้ว

    yoo makosana mwayakhula zomveka zokhazokha

    • @HussainAli-ex3xr
      @HussainAli-ex3xr 7 ปีที่แล้ว

      Manganya kukhosomolela pressure atafunsidwa kuti kodi ya Moses ndiya stupid ikugwirizana bwanji koma mfundo ndiyakuti mau oti stupid sakufunika kutuluka kustate house actually jus say president

  • @alexkaunda-oi8jf
    @alexkaunda-oi8jf ปีที่แล้ว

    Stupid bambo ake ndi amayi ake

  • @awuzenikutimediaproduction343
    @awuzenikutimediaproduction343 7 ปีที่แล้ว

    Manganya sadzathekaso basi basi!!!!!!